
Abambo awiri omwe ndi a Austin Meleka komanso a Kondwani Denison amwalira atagunda sitima ya pamtunda ku Salima pamene bambo wina m'modzi wavulala kutsatira kwa ngoziyi atagona mu njanji. Malingana ndi mneneli wa apolisi ku… ...