A religious group called National Repentance Malawi in conjunction with the Great Calling Ministries has asked people in the country to pray hard for Anti-Corruption Bureau (ACB) director, Martha Chizuma. This is according to National… ...
Articles By Archangel Nzangaya
M’modzi mwa oyimba odziwika bwino mdziko muno yemweso ndi m'busa, Mlaka Maliro, wati nkhani zomwe anthu akufalitsa zokhudza mkazi wake Bernadetta ndizabodza ndipo waopseza kuti athana ndi aliyese olimbana ndi mkazi wakeyo. Nkhaniyi ikubwera kutsatira… ...
The Super League of Malawi (Sulom) and all super league clubs have ended their disagreements concerning television and broadcasting rights. This was disclosed on Friday at a press briefing in Blantyre where Sulom and Club… ...
Boma la Malawi kudzera ku unduna wa zamalonda lati makampani onse opanga komaso kugulitsa mafuta ophikira mdziko muno avomera kuti atsitsa mitengo kuyambira pa 1 mwezi wamawa. Izi zadziwika potsatira mkumano omwe boma linapangitsa sabata… ...
Yemwe adati chikuni chachikulu chimasunga moto adalinga ataona kaamba koti mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera wasankha mtsogoleri wakale a Bakili Muluzi kukawaimilira ku maliro a mtsogoleri wakale wa dziko la Zambia a Rupiah… ...
Gulu la madotolo mdziko muno la Society of Medical Doctors (SMD) ladandaula ndi kuchuluka kwa mankhwala a zitsamba m’misika ya mdziko muno zomwe lati zikukolezera matenda ena pakati pa anthu. Izi ndi malingana ndi mtsogoleri… ...
Spokesperson for Prophet Shepherd Bushiri, Ephraim Nyondo, has quashed reports that the Bushiri Bursary Scheme is only open to students in private universities, saying students in public universities can also apply. This is coming amidst… ...