Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera wati zomwe lapanga bungwe la IMF povomeleza kupeleka kudziko lino ndalama zokwana pafupifupi K90 billion, ndichisonyezo choti mabungwe akunja ayambiraso kukhulupilira dziko lino pansi paulamuliro wawo pakayendetsedwe ka… ...