Oyimba HipHop yemwe akukhala ku America, Jolly Bro, wati akuona kuti udani wakhoswe ndi mphaka omwe wayambika pakati pa iye ndi oyimba mzake Lulu siwutherapo ponena kuti Lulu ndiokura mtima, sakufuna kugonja. Jolly Bro yemwe… ...
M’khalakale pamaimbidwe Peter Sambo wati chamba cha lege chomwe wayamba kuyimba pano, chimuthandiza kuti afikile anthu ochuluka ndi uthenga wabwino kuposa momwe amayimba nyimbo zauzimu. Nkhaniyi ikutsatira kubwera poyera kwa oyimbayu ndikulengeza kuti kuyambira tsopano… ...