A PP kodi mulipo? Pitani ku maofesi a chipani chanu chifukwa Mtsogoleri wanu ati akubwera ndipo 2019 akhala akupikisana nawo pa chisankho.
Malinga ndi malipoti a olemba nkhani, Mayi Banda alengeza zoti azapikisana nawo pa chisankho cha 2019 kudzela mwa mneneri wawo a Andekuche Chanthunya.
Ngakhale a Banda anena zoti azapikisana nawo mu 2019, iwo sananene kuti afika mu dziko muno liti potengela kuti zipani zina zikuoneka kuti zayamba kale kampeni.
Padakali pano chipani chomwe adasiya Mayi Banda cha PP chasasuka ndipo ena mwa aphungu awo aoneka kuti akulowera ku chipani cholamula cha DPP.
Chigonjeleni pa chisankho cha 2014, Mayi Banda anachoka mu dziko muno ndipo mpaka pofika lero sanabweleko.
Mmbuyomu Mayi Banda akhala akulengeza kuti akubwera ndipo anthu akapita kokawalandila, iwo samabwela ndi komwe.
oooh yes todays drm…!!!
Kkkk Timadalira Mutharika Jb Sangawineso Anatha Anali Kare Kkkkk
MCP ndidiru ngakhale zitsilu zina za MBC zapanga program yoyipitsa mbili akuti Never again akunama ana achepa akumuwopa chakwela ife program yomanyoza munthu amene anamwalila sitisangalatsa kampeni satelo tiwonetsana 2019 ngati simupitaso Ku amelica kukakhala mukuluza
Oky
Mayi opusa ngati ameneyi
Achita bwino adzaone malawi coz ndikale anachoka,,,mai landilan vote yanga ndimakunyadilan
sheeeeee
Akawalala Afwiti Panyo Panu
KUVOTERA JB NDIYE AYI, BOLA CHAKWELA. She managed to dump her pp supporters and went on Diaspora osabwelanso, osalankhulananso ndi omusatila. Ndiye lero akibwera kuzawagunanso kuti amuvotere? Only fools can
Joyce banda sangabwere nkudzaimanso pa ticket ya pp ngati mtsogoleri wao. Akuopa nkhani ija ya cash gate, ndipo akangoonekera basi zake zadalatu.
Abwele azapangise ID chifukwa alibe
Anatithawa ameneyo
Kkkkkkk stop dreaming JB
Now lets see the competition of three parties on social media…lets see hu z real..kkkk
we are waiting for you joyce banda,and 2019 iwill vote jb.
Mai bwerani takusowani kkkkkkkkkk
Amayi osochera abwere aluzenso mochititsa manyazi kawiri
Izi sindimakonda koma Na awawa ndi maloto a chumba ndithuuuu ndangodusa
HETINI KKKKL
JB ndi mbuzi ya munthu angawasiye anthu kuthawira kunja ndiye lero abwere kut anthu amuvotere. Ngati kuli Chitsilu cha mtsogoleri ndi JB. Ndi opusa amene atamuimbire m’manja Jezebel.
Ibwere mbava yaikazi imeneyo inatidyera ndalama Ibwere ndithu tikudikira ,atipeza peter ndi owinawina kale
Abwere adzalembetse za mzika osati ndale hahaha
Welcome home mama but osaiwala to bring back our money cashgate
Hon Lady deserted her own country, why coming now? Prof the incumbent wagwiratu mseu, zoti mumulanda mpando muiwale.The empty coffers he inherited are now full to the brim…..Tiwonetsana 2019.
zopoira mukukangana apaz ine ngakhare ndili ochimwa ndikufuna ufumu wakumwamba ubwere 2019yi isanafike kut mwana wamunthu asalamulilenso kwakwana
Abwele tizawamenyele limodzi ndi Chakwelayo basi
Koma zinazi, kkkk a dpp akatelo nje nje nje hehe ife pa Easy Chakwera on Fire
Only fools will vote for Dzakwera
4 billion surplus
bwera mai kwanu mkwanu mthengo muyanja njoka
Hahaha!! Abiti Maloko, mbava!! Anathawa chani Ku Malawi? Size yake ndi Chakwera not DPP!!
Masapota azipani Mupindula chani nokha nokha kumenyana mumenyerana zinthu zaweni ayini ake ndi olemela angoyenda thima lili zi
Ur news reporting leaves a lot to be desired
ANGOBWELA AZATIGAWILE NDALAMA ZA KAMPENIZI KOMA ZOTI AZAWINA AIWALE
MAI BWELANI TAKULANDILANI MALAWI NDIMOMWE MUNAMUSILA PALIBWE CHASINTHA
Zabwino zonse mayi
Wakuba sitikumufuna
Ha ha ha akubandulilani kumozi ndi jb + chakwera DPP NDI BOMA
Kkkkk TAKURANDIR MAMA
same how be happy my poor friends its time to wear new clodes bcoz its the only thing our leaders can offer for us (Malawi)
DPP imawina kale opanda oithandizira abwere tikudikira iyeyo kumene,mudzaluzire limodzi
Bweran Mayi Maluz Kuno Nanga Sichithumba Cha Kwacha Munatenga Mwina Pano Chapanga Mature Munyumba Munatimangira Zija.
Abwele timulandila
Azibwera basi zingwe zikumudikira ndikale lija
Ndalama izo
Anali kuti nthawi yonseyi?
Bwerani mama takusowani muzakonze zinthu
Zaziiiii
Kapolo wachabechabe uyu
mbavai amunthalika musadzaimange mudzandikile mudzaigwetse ndi voti pambuyo pake mudzamange ndimulandu wakatangale uja oba ndalama zathu zija
Who cares?
Aaaaa kodi panangoutola iye mpandou angoti basi ,mama time is over, palibenso zoti muzaununkhanso mpando umeneu ,mpaka siku lakubwera chauta,
Ambili amangidwa ena kuzipha chifukwa chaiwe pano Moti wasala ndiwe kuti ukayankhe mulandu uja wakutibela ndalama zanthu zijaya.Tikulandila koma osati ndi mtima osangalala.
Ngati adalephela kuwina ali m’boma what more if she’s outside the government? Mumuwuze asavutike mkugawanso zina ng’ombe. Ife sitikumufuna. Ndiye lingakhale dziko lanji lolamulidwa ndimzimayi.
Kmaso ng’ ombe zake anatilanda ndye azizati chani
Kodi ng’ombe zija adalanda? Aaah nanga ndiye angakhale pulezident ameneyo.
welcome mam JB 2019 Boma
anyamata kozekelani thawi ija yafika apatsopano ndiye akuwonekela.zilandileni zimasowa izi
Ndiyeso bola kamuzu chiwambo angaopse osati joyce b.
OK ife tikuzavotera Chisi
jb ali ndi ng’ombe źanga zot andipase mumuze kut sindinaiwale
We don’t need her, who is she? very very bad woman!!! ngati amkafuna kuzayimilanso amkathawilanji? kholo angathawe mkango m’nyumba muli ana ake?
Kod jb wake oimbayu
kweni wasowa zochita uyu, bwanj osamangokhala ku exile kwakeko ife tidzavotera chakwera basi
mapazi ako ndi mayi akowo wava olemba nkhaniwe
alibe ntchito jb but real man chakwera basi dpp mbava tione zina
Welcm momii
Mbamva
KKKKKKKKKKKK SUDZATHEKA
Kkkkk kodi wandiona et kkkkk
Kkkkkkkkkk kwambil zed
Anakubela chain??? Kkkkkk
KKkkkkkk mayiwa aaaah salibwino kuba kuposa mphongo kkkkkk basi iwe atimangatu apa kkkkkkkkk
Kkkkk kkkkkkkk kma ndiyedi akawamanga akapita kupanjee
Hahaaa paja ine ndikugwira ku defence force sangandimange kkkkkkk
Awanso inu Kodi amawona ngati a malawi ndi anthu opusa kwambiri eti????? Amathanji nthawi yonseyi????
Mama I wll Vote 4u Mumakwana
Kkkkk
Carhgate woman.Pobwera osaiwala kubweretsa ndege munaba ija amayi.
90 days yatha kuti tivotenso?
Kodi Mwayamba Kufuna Kuno Muzabeso Achisiru Inu Manyazi Mulibe Okuvotera Inu Ndiye Ndi Ana Anu Osati Anthu Amaganizo Ngati Ife Ukunama
Kkkkkk…… Ndikachan Kameneko Kut DPP Itutumuke? Anali M’boma Koma Anakhala Postion 3,nde Angapange Chan Pano? Iye Azipanga Phada Wakeyo Ndi Lazalo!!!!!!!!
zopanda chikhulupiriro chifukwa muli mau oti ‘ati joyce banda akubwera’ anthu akhala akumva zomwezo kanthawi.
Waiting for her to arrested just soon voting time is far just to step in home land is already case kkkkkkkkkk
BWELANI MAYI WATHU WATHU. Mzakhale leader of opposition Chakwera mapulani amuthela
Kodi PP iripobe?,kungotaya nthawi
Mayi wakuba ameneyu sabwela azafela komweko kuvotela wasiketi kubesa.kuwina ameneyu amuna onsee kumangidwa.
Abwele Tidzamudyel ndimaluzi ake amenew. Komsikut tidzsku votel Jeeeey uiwaley
ma generator Amai sizuyenda bwerani
Wakuba Uja Akubwela Adzatibele Mbuzi Zathu Koma Eeeeeeeeee!
Good move Tiye Nayeni timpanikize ,,,,Imfa sithawika….
She is really a threat to pitala, Chakwera ndi machine osamamuyerekezera anawa
Anawa akunama Chakwera ndi machine, enawa kumatso ngat awathila tsabola
Tatien timvotele Chakwera gyz, very handsome
Kuvotera chakwera mpakana? kkkk
pitala anjenjemela sanati
Kom chakwera aaaaa ndi one
Zinzinyengani ndi chala chocho azanu akuzinyenga zeni zeni DPP woyeee
Fundoless munthu anagwa alimboma ndiye bwanji alikunja kwa boma kkkk ine chakwera ai
Zimenezo uxan enao nt dpp
Kkkkkk amayi tsopano takulandilani kunyumba koma musayembekezele kuti mumaka 2019 chifukwa dpp ipitiliza kulamula mwina mwabwela kuzasamutsa katundu otsala
Zanziiii
Is JB alive? she’s welcomed.. bt she might be careful.
We don’t want her again & she must stay where’s right now because she’ll be lose again.
Hahahaha do u think angabweledi even atabwela only fools will vote for her. Munthu anatithawa uyu titamuvotela
Kkkkk sanathawe man or akanakhala komweko palibe chomwe akanachita she is here in capetown south africa ndipo akubweladi dzaimilira inu mpeee
aaaa umafuna amagidwe ayenela kuthawa kumene koma ife timamukondambe
Man hestings vuto amalawi sitimatha kutsata zithu Joice akanakhala kuti anaba anakamangidwa kale kale vuto timadana ndi chilungamo Joice Banda anaima pachulu ndikuuza mtundu wa amalawi anthu omwe ndikungwila nawo tchito akuba ndalama zaboma and anthu omwe anabawo anamangidwa tilitu ndi international criminal court anakatha kumumanga kale kale ubwino wake peter muthalika chilungamo chake akuchidziwa
kodi mukulimbana chan apa
onyoza amai ndiwatsonga ndipo khoma lanyumba lizamugwera akamyoza nakubala
zaziiiiiii
onyodza anyodze ife maso pasogolo ami omweo
Kkkkkkkkkk Abwele She is not a threat to DPP but to Mr Chakwela
Hahaha kma abwerere ma office et
Abwere athana ndi ine koma apange changu
there is no differance bitwin J.B& APM both are thieves corrupted leaders
Com Bak Cashget
Presidential compitetion is open if to mad people if they have money to squander.
Afuna abeso kachikena avotele ndionawo
Ukatha mano usaswe phale kd ujeni!!!!!! Tateleka phala tidye tizipita ku ganyu ife kunja kwacha uku
Abwere basi,
Dpp mukungoyiopa koma ngati jb angaime nde dpp iwonjezera mwai otsogolera a malawi beyond 2019. Personally i believe kuti ngati jb ayime mu 2019 nde kuti chakwera ayiwale zozalamulira malawi…therefore mama u r welcome kuno ndi kwanu zaimeni basi
titakate bawo yopanda nkhomo sopano
Kkkkkk! Which JB! The One Who Was Defeated In 2014 By The Same Mutharika? Oyenera Kuchenjera Ndi Wogonjayo!!!!
Man City 3 Arsenal ng’oo’pakwawo B-)
??✊
Kkkkkkk ukooo
Pp yomweyo…..tamwanso tea wankaka
JB is a threat to MCP not DPP! Reason; The North is pro PP! JB did not perfom well even in Zomba, her home district!
Not Mutharika but Chakwera…she will be competing with opposition parties…
She will be among opposition to unseat current weak gvt,how can she compete with oppos?
Or ur telling the nation thatDPP is already dead?
They will be competing on position two….meaning there’s already no one there…m not supporting DPP…but if u can see the manifesto of opposition parties I don’t see them defeating the ruling party
she is a fugitive, her friend has just come, waiting for her to answer charges. oops!!!!
Only fools will vote for her.
Tatopa nkumangomva zoti akubwera, akangoyerekeza akavalira Khoza la a Police pa ma Steps a Ndege.
ndikangolembesa kufuna ka Id kuvota njeeeee
Kkkkkkkk maonangati munenakuti Tembo wayambaso……JB nkachani?
Oh! Mama mulipo kodi?
Sanalapebe?afuna awoneso za 2014,akumunamiza.
Kkkkkkkkkk ndosamva ngati Rev. ujeni kkkkkkk
Inu muli pambuyo pa mbavazi kodi mmmmm just worsting time for nothing
Abwele adzadzitsutsa limodi ndi Rev.uja Ku Parliament kkkkkkk
She has the right to
Ndiye amaiwa ndi abushili akhalale candidet ndiye ndani?? koma akafika sadzafikila mmanja mwa polibje?