Wakalamba wafuna. Mstogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika amene akhale ndi zaka 81 pofika 2019 ati iwo ndi kamnyamata kachisodzela ndipo azapikisana nawo pa chisankho mu 2019.
A Mutharika anena izi mu mzinda wa Mzuzu pamene anayima kuti apelike moni kwa anthu ena mu mzindawo.
Iwo anati mu chisankho cha 2019, apikisana nawo ngakhale kuti azakhale adakali agogo.
“Anthu masikwano akukonda kukamba nkhani ya achinyamata. Ndiye upeza anthu a zaka 50, kapena 60, ngakhalae 70 imene kuzitchula kuti ndi achinyamata. Inensotu ndi wachinyamata, ndipo 2019 ndilipo ndithu, kuzathamanga nawo kuti mwina ndipambane chisankho,” anatelo a Mutharika.
A Mutharika anati chifukwa mayiko a ku Ulaya anawasankha kuti ndiwo otsogolera achinyamata mu Africa muno, iwo ndiye kuti ndi wachinyamata basi.
Zokamba za a Mutharika zachititsa jenkha a Malawi ena amene amayesa kuti a Mutharika atha kusiyila mpando kwa wachiwiri wawo a Saulos Chilima amene ali achichepele.
Zinamvekanso kuti a Mutharika akuganiza zosankha bambo George Chaponda kuti azatenge udindo wawo iwo akapuma koma a Chaponda atakhudzidwa ndi nkhani ya kuba chimanga, zinakhala ngati zasolobana.
Anthu ena ankanenanso kuti a Mutharika akuganiza zosankha a Ben Phiri kuti apitilize udindo wawo mu 2019 umu.
Kkkkk kamnyamatadi eeeee not yet developed in his mind kkkkk .no wonder he tell lie after lie after lie.anyamata kunama is their habit
amakwana peter.Kufunika kumujambula curtoon bs
a hambe khaya its good time for him to go to the old age homes .he must tell mugabe to go along
Munthu asaseleule inu mukuzitenga serious. Mmaso mwanu mxiew
Mayi m’bereke tkamuone gologoyo wakakamila !! iiii gologoyo pamtengo wakakamila by Mlaka Maliro !!
kapaligowe kkk
kapaligowe kkk
mbuz ya munthu
A Malawi 24 ndinu zitsiru ndithu imeneyi ndi nkhani yoti mungatiwuze ife a Malawi itithandiza chiyani ifeyo ngati mumadana ndi a president nde ndinu opusadi ife tizipanga Debate nkhani yopanda nzeru ngati imeneyi? inuyo kumeneko muli ndi zaka zingati! stupit!
One of the symbols that u r a great liar is to lie about your own age!!!
Munthuyudi ndi mwana, mkamwa mulibe mano.
Sakunama 81 ni 18 ozondoka ena amat wamisala president wachichepele 18 years
Boma iloooooooooo 2019 untill 2024
Mr Ibu tsopano kķkk
Ndie akunama?????? 2019 Boma aaaaaa aaaaaa aaaaa
Looool koma yeah
Vomelezani kuti ndinu nkhalamba madala kkkk
So why do the same government say when a person reaches 60 years of age should retire
Amene akuchemelela mkulu uyu ndi zitsilu komaso kut mufufuze ndi mbava zili mu office ku commenta za uchitsiru analowa mu office chifukwa cha chinyengo.
Wakalamba iwe apatse anzako alamulire
MY VOTE FOR APM
Kkkkkkk koma
Zopusa basi !!!!zaka zambiri mbiri ukhala bwanji wachichepere wagwa nayo watinyoxa mokwana .
Kanzake ndi kaMgabe.kkk
#funny
shame on him
He is young like mugabe galu wachabechabe
X
We won’t vote 4 u Mr Peter,25 hours continuos #blackout!!!First time in Malawian #history,no ways voting for DPP
Gogo iwe
Ndiye chavuta ndichiyan?
He he he heeee! Zafikano Pa Amugabe.
mmmmm, mmmhuu amalawi zalakwika pati zomwe zanena mkuluyu, aliyense ali, ndi ufulu oyankhula m’ene iye akuzionela palibe chifukwa choti tikamuthele mau, kunena za chipongwe zili zonse anthu ambili mwalankhula za mwano komabe chomwe mungaziwe ndi mtsogoleli wanube basi. aaaa tiyeni tizikondana. inu nthawi zina tikamalankhula za mwano kunyoza, tisanayambe tizikhala pheeeee, mkumati kodi tsiku langa limati mumakwana ndi makonzeka mkupita kukapemphela cholinga Changa ndi chani? 1 tizaone za chikondi 2 ulemu 3 kulemekeza 4 kupilila 5 chiyambi cha mnzelu mkuopa mulungu pa zonsezi titaziganiza tisanamuyankhulile mnzathu zoipa ndi kunyoza titaganiza bwino mkuona kupelewela kwathu mwina sitingamatere tiyeni tisiye kunyozana wina akanena ndiufulu wake oyankhula m’ene mulili inu, tisangoti poti ndi mtsogoleli koma nayeni aiiii
Kkkkkkk
chitsime chimaoneka chakuya chikaphwa ndi ulesi wanuwo mukharila yomweyo yomanyoza peter
Mbava, cash gate ikukoma.
Akunena zoona akuziyelekeza ndi uncle Bob pa Zimbabwe.
muuzeni kuti adzaluza unless aike munthu Wina adzaimile ngati candidate not iyeyo
Kkkkkkk wayamba kubwebweta sopano..81 ndiye a kt ndimufana…wamwa kachasu mwina chikoke yani?
Anadya Fodya wamkulu ameneyu
Kkkk koma life ada iyi nde ndina ndina
Nyasaland walowa macheza.com
mr ibu zaka 81 mkumati ndunu mwana ???????? kkkkkkkkk koma zinaz gyz
Munthu pala wawelera kuwaniche mahara yakuchepa, chikulongola kuti mudala uyu mumulomo mino alije kweni waluwa kuti wana chipala mmulomo
Musamunyoze sanakalambe akunena zoona Kkkkkkk
Kkkkkkkkkkkkk shaaaa wakalamba wafuna etiii pa Chizulu timati. . #Ugugouthandayo……
Kkkkk koma agogo awa……anganga anga hahahaha!
Kkkkk chinyamata ndi chokoma
Nkhalambazi zikuononga africa,mugabe,zuma,ngaanga inayinso,choncho ife tizingoti tizalamulira pomwe nkhalamba ina iyi ikufuna kukhala mnyamata
paja Malawi ali mbali it la dziko lapasi
*Mstogoleri*
Stupid zako Pitala
Sakunama munthu akamakalamba amasanduka mwana. Kungoti mwana wakeyu mwano too much even ma advisors ake akungomuyang’ana kuti nyanga ya nsatsi izamufotele yekha.
comment on ur opinion loading. . .
Azigogo alero amenewo kukana kukalamba kikikiki kunva kukoma misokho yathu eti kape iwe
Mnyamata olankhula ngati amvumatitsa bwemba
mukamanena zamtsogoleli musamaphatikize ndizamtundu ndizigawo musokoneza chifukwatu chitsulu chamisala chandala chopanda ndalama chilindimwini
Young cadet ameneyu
Ngati uli wachisodzera bwanji ukanika kupereka mimba
Fumbi ndiwe mwini. akulu amatero. Osadikira munthu akuyamikire. Sizichitika. Wekha wa munthu.
Dramma in this leader of yours. Eisdh koma abale Peter? Uyu nde Puludzu weniweni osati ujayu. Kkkkkkkk!
Kodi azakhala alimoyo amutharika kkkkkkkkkkkkkk?
Nanga mikuti ana ndi atsogoleri amawa NDE anawo azalamulira liti poti nkhalamba zikukakamila?
Wakalamba wafuna
Ndiyengati ndikamnyamata kachisodzela,ife tikufuna munthu okhwima mzeru ndi odziwamavuto osati kamwana ayi kaona zambiri zikumuvuta.Anyamata azikhala ma khansara ndi ma mp nangaonse akakhala ana aziuzana nzeru zotani?
zinazi mumangoonjezera akalungusese inu anyau party page
Nde apanse mimba kadzi wakeyo
Kamnyamata kopanda Mano aise tamuuze peteryo andopheze kumbayani kuli tansikana ta std 7 tikachinde paja peter anazolowela kubunyula uzazipwetekatu
At 81 wina mkumati 2019 Peter woyee mulibe anthu a chichepere mu DPP?
Pamenepa ndipamene tadziwa kuti mwakalamba MR IBU kapumeni nthawi yatha
Uhule atsikana akopeke taoneni
Koma nkuthekadi that’s why palibe chikuyenda
aaaaa Mwatembenuza si 81 koma 18 ndipo zamukwiyitsa izi
Anyamata samaganiza mofumbwa chonchi ayi magogo iwe kagwele dziko lakukanikani vomelani
My
yeah i agree! mwana uyu akumera kumene mano, i can c!!
He is a serious pathological liar kkkk
vote yanga ndi yanu mr president
Chakwera sangawine olo zitavuta zitani
2019apeter boma
Are You Sure,ukumva Kukoma Eti? Bola Osamadziika Ndi Chala.
Udakali Ndi Zeru Zachiabwana! Kkk
Am here just to lead the comments
Mpaka Munthu Kumadziiwala? Mmmmm Inu Simnyata Ayi.Ndnu Agogo.Kkkk
Kkk koma yah
Hahaha
Peter adzawina wina afune olo asafune Dpp 2018 Boma
Wakalamba Bas
Malamulo akumulola kuimaso ndi umfulu wake kutero koma ine komaso iyeyo sitikudziwa chakudza mawa
Wachisodzela ndi choncho thinking capacity imakhala low l see ,thats why malawians we are panic in any way round for more ask the journalist now
Iiiiiiiiiiii kaya bola osazalira pasikulo
Wina aliyense akungowanena akulu amenewa mmmmm kalipo kalipo pitala zidabwe ndithu dziko la malawi lakukanika
Kkkkkkkk ka std 2B pa HHI primary xul
Munthuyi ndi nkhalamba asakane ai.umboni ndi uja anagwa panthawi yodzala mitengo.afuna umboni otani iyeyu oti wakakamba
Kkkk Malawi yanunkhiratu bas……mpaka a peter at iwowo nd mnyamata et kkkkk ok takumanvan mr president
Ichi ndichizindikilo choti amuthalika ndabidza ngakhale akuti kuwanenakuti ndabodza mkulakwa ,munthu wanzelu sangati ndimnyamata pomwe ali ndi zaka 79,kuwavotera mu 2019 mchimodzimodzi kumanga nyumba pamchenga mvula ikabwera imadzangoikokolora,…vuma wakara sekuru….
Kkkkkkkkkkk Koma peter
Kkkk koma zomvesa mutu kupweteka asiyileni anzanu mwakula magogo inu muzivomereza kuti mwaba ndithu musamalize zonse anzanu apeze poyambira
U never ever to change Malawi that’s why I leave Malawi 5 yrs ago I will came back until further notice
nice nice. you should also be attending grammar lessons wherever you are
of course english is a difficult language but its not too late
kkkk, that’s why I leave Malawi 5 yrs ago and I will came back,,,, koma yeah zinaliko tikuthawira pawindow opopa magazi
kkkkkkkkkkkkk koma ada mwaojexa heavy
Kkkkkkk koma ndiye azungu amavutikatu komwe uliko wth ur useless English , apa takuziwa kale unasiya xul nikuthawila ku #South_Africa
Koma mulikuti 5yrs mukupanga communicate ndi eni nthakawo??? bola osachititsako manyazi mother malawi land, olo mrefugeeyo anngalembe chonchi???
Kungomukoza ..abale munthu z2 uyu..kut nxt tym.asadzalakwitseso..madziwaso.kulemba ndikuyakhula.zosiyana..koma i blve kut tonse tamuva zomwe amafuna kunena..so.plz kukozana ndikwabwino
man dont coming here again, lived there forever Man. Malawi is sinked here, even netball we are losting.
you could have just spoken chichewa chizungu sitikukakamiza
Kungoti ndinaphunzira nthawi yakamuzu kkkkkkkkk
muphunzitseni pamene walakwisapo
mukumunena ndiyeee adziwa bwanji???
ku RSA kulibe zosekanaziiiii taaaaaa
ndiku malawi Konka dziko loose lapansi umanenedwa ukalakwisaaaa chingelezi
Kkkkkkkk
Ee Zavuta Kumpanda Mwana Otsekeledwa Uja Wapasidwa Mimba
Indedi that’s an ironically I am speech osamaiwala paja munthu ukakalamba umakhala ngat mwana wakhanda ongokhalira kuyamwa… Kk I think he is just getting so exhausted by his position end perhaps pompano we would hear that he want to resign stepping down udindo wake
???
Ndipo ndizoonadi inenso ndikugwiridzana naye kwambiri ndipo ndikanyamatadi kachisodzera,
Zikubwera mochedwa kusirira atakhala mnyamata, pepani Bambo vomerezani kuti ndinu Agogo, dziko lakukanikani kulamula, iwalani zoti mudzawinaso Agogo
Ubomba mwibala alya mwibala Ichibipilekofye chimo,namukota kabiyeni mutusheko nokwangalako notwana pang’anda lekeni abanenu batekepo.thankx boss
kkkkkkkkkkkk
Madala ndinu agogo mbuya but our constitution does not bar you to take part. And we want even you as DPP to compete in primaries not imposing. I see young guys in the party with calibre like Getrude Munthalika, Ben Phiri, Chilima, Nankhumwa, Mgeme, Don Kalindo etc
ndimwanadi munthuyu,ngati akulephera kuthesa ka vuto kakang’ono ka ESCOM,ndiye ndiwamkulu?
Mchifukwa chake nkhalamba zimagwilira ana. Mtima wake ndi womwewu. Shana!
wakula ngakhale malamulo athu palibe Edge limit makamaka ’35’ and above inde kuima adzaima koma sadzapambana 1.old edge 2.wataya moralo on the ground e.g ma blackout,electro reform bill,pointing of top govt officials ,tribalism etc…
Kodi ndekuti upresident ulibe age limit???ku Botswana ati asiyira VP kutakhala chaka chimodzi kuti amalize term yake.
If mugabe can at 90+…… He can 2….
Wayimva kukoma misonkho ya a Malawi
Phwaahahaahaaaaa kulakalakaa hahahahahaaa koma abalee.
Malawians will never be mocked,when they get disappointed,no reverse,they mean it
nyamata wachisodzela opanda mano….haaaaaaa ndafa ndikuseka ine
Hahahahahaha chamba si embassy
Ya,he is,that’s Y he has failed 2 boost de country’s economy.He z nt matured.
Kkkkkkkkkkkkkkk nde choncho angasiye moyo wozikundikira??? Ngati munthu yekha akukanika kuzindikira kuti wakalamba do you think angakuthandizeni achinyamata. Watch out!!!!!
ine zondipala mkamwa ayi a 24
Siyilani onyamata bwana
Kuzimva kukoma ndalama za misonkho ya amalawi osauka.kkkkkkkk
No strange thing since he is afreind of Robert gabliel mugabe
Ine ndie sindinabadwe2
RGV akukufuna ku flames uko. Iwetu ungachinye bho
Kkkkkk
Museum material. Akumavala thewela akuluwa. He’s 108 years old. Akachotsela zimene amadwala 87. 2019 paulendo. Chakwera ndinyamuleee!!! Bwampini watilephela!! (Singing).
Hine hikanyamata kashishoshela you got voice man!
Kkkkkkk dead
KKK this is for limit bra apa mkuluyu mwamuonjeza ndithu
Kkkkkkkkk
kkkkk kma Alick Wandikomola Mkuseka Hahahahahahahaha
Kkkkkkkkkiest
Kkkkkkkk??????
apa wakukwiyitsani kkkk
HAHAHAHAHA Wakoma mpando ongowukakamira mchifukwa chake adalowa usiku anthu akugona chonsecho palibe chomwe angaloze chamzeru chomwe apanga ndi k2000.00 komaso k5000.00 kuti amalawi adziwe zoti munthuyu ndi professor weni weni
Mmmm yisiyeni gogus ya ine
akugoyenera what he speaks is un understandable not only wachisodzela but under five kid
You nailed it
We Need Some Change Indeed
kkkkk! wat i know wachinyamat ndimunthu wazaka kuyambira 1-45yrz kwnako ndazigogo athu amenewo.
nkhalamba iyi koma pitalayu ndi pathological liar 81 its old enough to retire mbwerela too much ok his government
magwelu ali thooo!! mkumat am young peter zopoira bas
Wazimva Kukoma Ndalama Za Unamapopa Mnyamatayu
Zitsilu zizake zipezeka pompa zochepa mzelu kumati bwana bwana akhala bwanji bwana pamene ntchito mugwila koma malipilo sakupatsani nenani kt mbava musaope
Broaliyesealindiufulupakayankhulidweinusomwayankhulamaganizoanuazanusoayankhuleawonzandaleizi
we need some chang
man phitha sakunama
kadolo kaja nd ka teen ager ma play njee
Peter nd ifeyo mpakana kuduwilana
Kkkkkkkkkkkkkkk…. Eeeeeeeeee koma ndichisozeradi… Paja 81 amatha kukhalaso 18 ukatembenuza
Wafikapo mpakana pamenepo”