Chaka chino si cha maule. Ataoneka kuphukila sabata latha mpaka ena kumati azitolela, maule apezanso mavuto lero mu mzinda wa Lilongwe.
Pa masewero amene anali ovuta a pakati pa Bullets ndi Silver, akatswiri a ku Blantyre abwera chimanjamanja atakwapulidwa ndi zigoli ziwiri kwa chimodzi.
Kunali kupsetsana mtima ndi chimkulilano matimuwa atakumana koma pakutha pa zonse, a Silver anali ataonetsa kuti akamuna ndi iwo ndipo kugonja kwa pa 6 July kuja kunali chibwana basi.
Masewelo amenewa anaonanso zipolowe pamene mapalestina otopa anagenda miyala kwa Masapota a Silver.
Ku Dedza, manoma akonza kwa dzulo atagonjetsa Masters Security.
Dzulo nyerere zinanyozeka zitagonja kwa Civil ndi zigoli ziwiri kwa duu koma lero yakwilila chitonzo chija.
tikudziwa tekha kutsogola sikufika wamva neba.
Kkkkkk manker’s woyeeeeee
Nellie phokoso
Kkkkk Team yopanda sogolo imeneyo
Umenewo ndye mpira nthawi zina ku wina nthawi zina ku luza otsanyozana apa palibe dola pa chikopa team iliyonse imakumana ndi zovuta munthawi yake maule maso chitsogola bas
Home and BTS (900)
chomchobe basi nabola moyo sitikutaya mtima zithu zitiyendela bwino izi
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk 10 games 15 points zaulendo uno mauleeeee ulendo basi
wachita postwe chendelako usazabwereze utsiru wakowu.Anthu ngati inu musamalembe nkhani
osadanda gyz ife ngt masapota tngokulimbkitsan bas
Well done silver
Ma team aku BT satha mpira. Koma achipoperanji bax LL city teams mwaaaa
Ma team aku BT satha mpira. Koma achipoperanji bax LL city teams mwaaaa
They have been silenced hahaha
Alira amenewa nyanga zasuluka
Noma ndiyomweyo sizasithaso ndipo ikutimvesa kukoma
Tidzabweza chaka cha mawa pa 6 July osadanda
Yinali TNM super league or not?
Mawule ndima Gwalada amakhala ndmata akanyamula mfut same to mawule akangowna but uuuuu ndmakape
Mawule ndima Gwalada amakhala ndmata akanyamula mfut same to mawule akangowna but uuuuu ndmakape
KOMA GANYU BASI, EMBEKEZA MAGANYU AZAKUPHA NEBA
Hahahahaha chapompano timva Kananji ndi Fisher awonesedwa msana wa njira 11 games 15 points
aibwanyakula … aifwafwantha …aikuntha.. eeeishhh matama azakupha neba
kkkk
Kudziva ameneo aziona apa ndipang’ono angoyambapo kkkkkkkk
Continue losing neba 2017 siyanu
John Chitawo, Bullets Sizamva.
Masapota a bullets ndi afodyadi kusangalara konse kuja kuti manoma aluza nanga lero ichi mchiyani? Linda madzi apite ndiye udziti wadala mwamva makape inu?
Vuto a bb kusavomereza ndiye mukhalira yomweyo yomanykzayo amzanu akupita chisogolo
Kkkkkkkk huhuhu ndiana kwa silver amenewo
hahahahahahah makape awa
Team kuchita kunyasa ndidzina lomwe #nyasabigbullets
Comment Loading….
Chaka chino BB ivakuwa aziona kd kamulepo ali kt?kkkk mukuchita kusungira athela ku kapu angolandira zaule aaaa ine kuva kukoma ndi noma yanga manoma chingolero
Munanyanya kuseka kwambiri, kkkkkkk
wakwiya kwiyu -( mchitidwe wokwiyitsidwa) ndimfitidi!!!
timayipatsa mpata kuwinako pang’ono zaulere pakafunika zantchito kuying’ambang’amba bullets,mabankers more fire!!!
A Malawi 24 Mukunama Game Sinathe Itha Lolemba Cha Mma 5 Am
Tibweza Basi: Hahahahahaha Khoso
toiei pontino
thcco
Mau ndiomweo m’bale.
Owooo Malodza
Ine wa Silver ndili phe wamkaka basi…
A nbb musiye phokoso mukawinako znthu zdzayambaso kuyenda bhobho pa 6 July silver inali ndichison ndianthu anafaaja komaso chison ndi bb KT iwineko…osamaderera
Nyerere zilibe phokoso koma action kkk
iyindiligie musaiwale inu Abb, chinebasitipangandi many ifekwanthu ndikusunga ndalamazo mongamudZiwa moyowamabankas ngatimukuzifuna limbikilani liwilo tikugayilaniko komazufunikanphavu asatimanjalende atm yanundiliwilo basi or 000,.
We its revenge big up.NBB still NBB
Linda madzi akapita mpamene udzati tadala maule ndi round 2 musakhale ngati mwaiwala
Kupezerera za ulelere bas
Maliro ateam pamenepa yatha bullets
Ndikanakhalaine wabb mdikanasintha chikwangwani,komawa bb iweusaiwalekutimabankas sasekapandalama koma pafreind timakusangalatsani apamutengepo phuzilo nose ABb from KU
Game ya mpira samawina matimu awiri imodzi imayenera kugonja basi………more fire maule
Bankers Forever
Nebaa!Mau Nsamatha.Dzulo Ndidanena Kuti Linda Madzi Apite Ndipo Uziti Ndadala.Lero Ulankhura Chani?Ona Anzako 22points Koma Sulira?
Kd BB yamenya ndimatimu angati? komwe inalowelako 2 .1 kuluza kwabwino nanga zazulo zj 2-0 nkhondoyi ine ndikt sinathe muzinena scnd round kusogola sikufk
Anyamata woyambitsa zipolowe pa ground nthawi ndinthawi awa amadzitembelela okha.
Ndinayiwala akungofanana ndi a Chitipa United bolanso aChitipawo
Anong’a akuti Sakundandaula Bola team yabwerako ndi moyo kkkkkkkk Manoma Pachiongolero
Wazionaa Wa Bullets(Chingabwe fc) Pamene Manomads Akumwa Wamkaka Iwe Wapanilira Wamandimuu Napepe Kudzimvaaaa Usiye,nyc Work Ma Banker Mumathaaa
NBS:Ma team awili akalowa mu ground iliyonse imafuna ku wina ndiye palibe zodabwitsa apa,koma choti mudziwe mawa ndinu musawone ngati muli 100%
Amati angatan koma ndi kuti mmene anatokotera dzulo muja hedee ayi ndithu kungozipatsa minyama! NOMA more fire!!
Mikodzo fc
Komaso musaiwale kwambili kuti silva nditimu yaikulu bb so ndiyaikulu ma cooch so ndi aku malawi komweko juju pomwepo haaaaa mwandikwiitsa kwambili amalawi
kkkkkkk MA BANDITS BAKU NDIX sizitha mpira iziiiiiiiii
Kachamba fc aitswa
kkkk kkkk neba anyani sasekana michira neba sorry
manyaka a team kkkkkkk taiisambitsa chokweza lero pa Civo musiye matama ma ule mwava
Kkkkk, akatswiri akuti? Admin uchepetse mwano umenewo!!!
Mpila ndi choncho kwamene amatsatila sa bwino
Umene uja sunali mpira achimwene!
Wamagazi uja!
Umene uja simpila koma demostration. takumbukilani anthu omwe adatisiya aja ndi ovulala aja.
ndakunvani
Komaso unali waulere mateam sanapezepo kan2 pamenet iyi ndi league.
Anzanu amawna 3 pnts inu kazptlizan kuwna zaulerezo
Nkhani izitha guys, tingokhalira nkhani yake imodzi basi tsiku lonse?
Ana achepa!!!!
Muona chaka chino maule tidakakwapula
The people’s team, people’s party. Masanza okhaokha dzulo ndilandira zipepeso koma mmene lero neba watulusira maso ine kukanika nane kukapereka chipepeso changa
Hahaha nde mwat chaka chino sichamaule???… Anyway … Bullets will steal remain the peoples team or italuza chotan….NYASA BIG BULLETS THE PEOPLES TEAM!! I LOVE MAULE !!!
Bulets ayikong’onkha ayikwapula ayimetampalaopandamadzi ayiyendetsa uyouyo ayimenyera
Noma ndi more
Aneba anakangalika kuseka dzulo koma anayiwala zoti kwatsala tchile ndikomwe kumapita moto.Ifeyo nde ndi be forward zinazi ndi manyaka.
Zimachitika Maule Amnzanga, Zonse Nd Nthaw Masku Sakoma Onse.w
Zavuta Kumpanda NBB ingolimbikila Ganyu basi madzi nde anapanga katondo kalekale
Wizard is better than Bullets and Tigers is even better than Brantyre united but Manoma ndi more
Angofanana ndi aChitipa united!
mwatero
Eya Maule, pepani kma season ino siyanu!!
ubwino wake ndi first round sitinganenere2
Ngakhaleso ana anja a lesita timkatero nde tiye nazoni!
anyapapi muvutika, kwatsala moto ndi komwe kumapita tchire
Kkkkk anyapapi via ya maste
ndi inayake
Neba kumbukira mawu aja “linda madzi apite uziti ndadala”
Bullets Kupanda Kukhetsa Mwazi Wa Munthu Musamayembekezere Chipambano. Zinthu Zinasintha Coz Anamwalira Aja Anali Amfumu Achikulire Pamene Nsembe Yaposachedwayi Tinali Tiana Ndie Akuti Sitokwanira Kupereka Chipambano Pama Game Ambiri.R.I.P Otisiyawo Plus Bullets.
Afana ukugeya mwano bwanji ? kamlete,chiukepo ali kti ?
aaaa gyz musalankhule mokweza wina angaafeso apa chonde koma tiana tija tinavutitsa maneba tatipatsa chigoli chomwe chija kapena tapanga +
Anyanya matama kkkkkkkk
maule ndimauli awine ngakhale aluze ndimaule basi,osato bt dayz will come soon
ZOONA I SAY AYIKWAPULA CHAKUMATSO IFE ANYELELE SITIGONJA TIWONA
ife timaona ngati pamene munagetsa mwanzi ku bingu stadium timkaona ngati basitu simudzaluzaso koma mmmm shame on u achiganbwe fc zimachitika kkkkkk.
Neba Kulephera Kumudikira Dzulo naye akukayimanso ndi silver? Kkkk basi ife tatsogolo utipeza kuntundaku
Tasintha dzna la Team yoluzayi pnp ndi Elliah ka
ZOONA I SAY BULLET NDIMANYAKA OKHA OKHA
Ma neba anga onse ndi amaule ndiye akumangolira momvesa chisoni amvekere nkinkinki wuu wuu koma bullets, ukulilitsa akuluakulu chakwawo
Tonse ma supporter a NBB kumakumbuka kugula before game isanayambe chonde
Team yanga siipanganika.
ife a Bullets Chisangalaro timachipeza mu ganyu
kkkkkkkkkkk nde yaked mapale
For life
Kkkkkk ndiye mwati atakwapulidwa?
Ndimai3ra bho more fire maule!!!!
Zilibwino zoti aluza tigonako lero kkkkkkkkkk ife manoma woyeeeee
ndi mene moyo umakhala mawa zizayenda
Ndiye game wakula wantha adziona.
ulenje umasimba wako pepa neba
Zilibe kanthu or bullets yaluza sitingatsiye kuisapota pali team yomwe sinaluzepo?mundiyankhe football is a game of loss, win and draw so what?
kkkkkkkk bola mwaziwa kumene mukulunjika mwene kkkkk
kkkkkkk zimachitka mwene osadanda bola mwapezeka pa line azanu athawa makama amayina othela kuti Wa Bullets
Twalick ndi Happy ndakuyamikani ponditonthoza inu mumauziwadi mpira ena angotitukana pomwe lero ndife anamfedwa kkkkkkkk mukazaluza muzanya
Oho! Wayamba Kulumaxo?
Braz Mwayiwala kut amene mmasewelanawowa sanaluzepo ma tornament onse amene asewelebwa cakacino?
Sindinaiwale big
Mary,sindikuziwa comwe ukutanthauza sorry come again
Sliver Sinaluzepo Kuyambira Mu Top8 Mpaka Mu League…
nde inu pomwe mumagundika kunena noma itaruza simumadziwa kuti mpila mdi loose en win kkkkkkkk mwanya nayo
Henry,dikira silver izaluza mowawa imbani zidebezo lero mmawa muzagwira mmutu mutakhumudwa ndizigoli.Koma Cynthia wa Noma akuganyula ngati mpira unali wa bb vs noma kkkkkkkkk anamfedwa amasekana? Kkkkk
Kma ndie yakutumulidwa ngati nkhuku yachipumphu masapota atimuyi adandaula chifukwa chakusosoledwaku
bb koma pakamwa mpira ndye ndi akazi enieni
Kuli Second round yosayamba , dont talk much ,
anauka friendlyo??? kkkkkkkkkkkkkkkkk kampopi ndimanyaka heavy
Nbb Ndmanyaka Okha Okha
Kodi Ernest Kakhobwe Amakupatsani Ndalama Eti Esaniko Goalkeep Wina Muone Kusitha Koma Gaga Ndi Munthu Modzi
na mabankar sakulora kufa kawiri wamkaka basi
Mm….nde mwati chingambwe,kamlete fc.ayibwanyangula kkkkkk
Wozindikira Sachita Phokoso Pagulu,phunzirani Kwa Mabankers.
Madolo bolakukwera mabankers sitidanda pano tikumwawankaka wovalazared aziverechisoni.
Uku ndikuluza komaliza a BB
Kuluza kotani? Kkkkkkkkkk hahahhahaha uluuu
Komaliza Neba Kkkkk
Koma kumeneko nebour wazionaso amayesa ndi pa 6 July iyitu ndi tnm super legue
muzikangomwa nkala bongo bas??
neba unalimbikilatu pa 6july panja Nanga lero chakuvuta ndi chani”’??? umayakhula kut zayamba kusitha Nanga lero Wataniso neba. neba! !! neba. !!! mpira ndimu ground wosati pakamwa..
Pajatu pa 6 july anathira nsembe ntchifukwa chake anawinatu kkkkkk
Kkkkkkkk Koma Ramsey
dzulo ndiye anasokosatu lero kuli ziiiii alibe mau
mabanker sawina zaudzu koma zandalama ana achepa awaaa!!!!!!!!!!!!!!!!!kkkkkkl kkkkkkkklllll hahahahahahahaha hhhhhhhhhhhhhhhhhh uyoooooooooooooooo zamuonekera
KUGENDA FC ayiphwasamulanso kkkkkkk!
Iwe anakuuza kuti bullets yadzuka ndani? Kodi wodwala akasekelera ndiye kuti wachila? Zinazitu bwino nazo wamva!
Vomelezani kuti mwakanika anyamata omwa midoli inu.
kkkkkkkkkk koma #mpango
Chinenecho ndichiyambi Neba sunati umwa madzi wometera ndevu chaka chino
kkkkkkkk amatitentha nzilankhulo yawa
Owez bb!!!
Mabankers omwewo kutimwetsa wamkaka!
a bullets ndi dzitsiru dza wanthu amangodziwa kunyoza ngati iwowo samaluza, lero ndi izi zawonekelazi achita bwino kuluza
BIG BOSS AM AGREE WITH YOU
Zitsiru ndinu komanso matimu omwe mumasapota
Mwene Ngati Team Yanu Ya Wina Musanyoze Anzanu Ayi Wonani Zanu Ku Bullets Chikunkhudzani Ndichiyani?
Girbetto ndiwe waku Mocambique ndakuona pa profile yako ndiwe chitsiru bwanji ukutinyoza a bullets ngati ku Tete kull osewera mpira?
MWAZIONABE YINU PANO NDINU ANAMALILA BASI KWALELOLI
MPila Sitiquela Timu Kutengela i Ndiyadzikolathu
Choka iwe dazi losakuyeneralo anthu adazi akudulidwa mutu iweyo ndi dazi lakolo uzizimvera cisoni mmalo moti uzibisala ukulimbana ndi bullets
kamlete fc
Midoli fc
Ayi inuyo dzulo mmaseka kwambiri
mwakudzumulidwabe inu mulira lira chani apa yango pangani masamu a 10 games 15 points basi
Zoonad Za Bullets zimangodziwa kunyoza Mighty ikaluza mot ine zandiwaza kwambir
kkkkk tahit fc imathaa mpiraaa wapakamwaa chabe…..timu yamasavege
Midoli team kkkkkkkk
Kukukwiya lero mmesa munayamba kusapota silver inu mwaiwala padzana
kkkkk more more fire the BANKERS!!!!
bankers 4va…..kkkkk ana achepetsetsa awa
Ikakondwa amalonda Ali PA fupi ndi izi Lero chisangalalo chadzulo Lero chasanduka kulila. Bwanji pamenepo?
kkkkkkk komabe ndie mpaka 2 kwa duu akunamizila kut anawapininga..
Mai mudziyakhula bwinotu kkkkkkkkkkkk
Aneba amokonda kuseka maliro akakhala kwa anzawo, lero maliro ali kubanja la bullets! Pepa neba!
Neba Zako izo usova ino ndthawi yako yoti uimbe dzandiolotsen…… pamene azoko tkuymba ndlibe problem wi r lukin 4ward mwazna lathu
Neba neba neba zamuonekera
Ndiye mpira umenewo, amene musamatha kusatira za matsewero ampira mukuwona za chilendo.
AKananji team yakukulilani,anakulembani ntchitoyo analibe Vision
Bullets ikufunika deliverance basi kuti iyambe kuchita bwino kkkkkkk
kachingat?? mose ayambira aaaa
Defeated twice consecutively……ana mwachepa inu…!
Zili kuno mahule kukwapulidwa
Amwene osangoitska team_yi bwanj?
Kuluza kumeneku akumangani a POLICE
ofunika kudya misa ina apa kkkkkk,,,,,,,bullets matama,,,,aikong’ontha
Good news
Mmh zovuta
Siampira awa koma kusuta ndikumwa midoli
Musamakhake ngati mfiti ,amati mulire ndi olira, ife tikulira inu mmalo momva chisoni kumakondwa
Kkkkkkkkkk
Pepa neba dzulo umatokota lero bwa
Makape
muule musamasewerere ma refu panga team simungakhumbire mabankers adasura anatu
KHWASUKHWASU!
ikufunika mapephero baxi mumaona ngat zadzulo kunali kufuna uziona kananji fc uuhu!!
ikufunika mapephero baxi mumaona ngat zadzulo kunali kufuna uziona kananji fc uuhu!!
bata bullets…
Am Still Supporting Mabule
kkkkkkkk uvula jenzi chaka chake ndichino ayse ndikhulupilire kkkkkk
Sapota saluza ndi bullets basi.
Kkkkk chipongwe
Kkkkkkkkk aziona
Kkkkkkkk silver tipha ambiri a bullets kkkkkkk silver
akulu akale amati”osamatha mau,mulomo uzakutsata,ndipo chaona mzako chapita,mawa chili kwa iwe!” anbb angosangalala kuti ndi ma champs a 6 july basi koma zoti lig/cup angatenge,aaah! izo aiwale.
I like that video
Olo titaluza bwanji koma ine victor ndine wa maule basi manyaka enawa ayi akagwele uko.makaka ngati nsalu ya maliro
Kkkkk team ya asasamba ama sachet kugoletsedwa kuyamba kugenda nde chani mwatiwonatu ana a mtawuni ku 47 takuphani kkkkkkk
Auze asasamba
Zoona Pakuti Munazolowera Kuluza Simungaisiyedi Kugenda FC.
Nafenso sitingakwere chingambwe FC kkk
Guyz Zinthu Zimasintha Silver Yatipan Tkuvomela Ok
Kodi Inuyo Anyau simubwera kumwera kuno round yachiwiri ?
Tavomeleza kut silver yatimeta nd sidze zomwe,ubwino wake sitidaswe macup “tidzamwaso”
Nafeso sitingasapote manyaka achingambwe fc
Muzikhala Ndiulemu Silver Mpakana 2 Koma!!
Central bankers forever………yayayayaya.
Ms bankers ndimire mumatiyimirira
Where is internation Kamulete Andy?
Tawafunsani
kkkkk kombola fc
nawe olemba nkhan pamutu pako sipakuyend bwinotu aaah zausilu et
Timvanso kuti mfumu in yamwalira and bullets is to blame.
kkkkkkkkkk
Tatiuzeni iiiiiii
Say it again
Moto kuti Buuuuuuuuuuuu kuno ku capeTown Nyerere Manoma Woyeeeeeeeeeeeeeeeeeeee
Mmmmmmm moto wake uti,mwatibulidwa dzulo 2-0 ndi Civo. So lero mukuti chani plz.
Neba pepa zavuta
Kkkkkkkk its too early.
Kodi Wa boma watha bwanji?
Kodi maule kapena mahule
hahahahahahahaha koma kandudu
Mwaona tinaona ife dzulo a bullets,hahaha musovenge,Wamkaka kt Mwaaaa!!
kkkk Bullets 4 sale ndiamene akutlakwtsla team ya fuko
Dzulo Anawawata Makolo Awofe Tili Pamwambabe Ngakhale Dzulo Taludza Tikusiyana Ndi Neba 7points Ife Tili Ndi Game At Hand Iwo Ten Games 15points
PEPA NEBA,DZULO IFE KULIRA INU KUSEKERERA RELO NDINU,KKKKKK
Kkkkk SIZATENGASO CHIKHO IYO
Ndikutha kuona neba akukasewera ku devision hahahaha
U talk toooooo much.. komanso simuchedwa kuyiwala..!
Kkkkkkkkk koma ndye zikukudinya bwanjiiii????☝
Neba wakuchipiku
Kkkk kut juuuuu
Midoli fc sidzatheka
Ndudu fc kkkk
ANKANGOMVA LERO AZIGWILA NDI MANJA
Yack
Koma sliver ilibe chisoni osaona position ya anzao kamulete woyeee
Hahahahaha koma ndiyeeeee!!!!
Ine kumangomva kukoma
# Noma
SORY NEBA DZULO UNAKOKA NDI KUSEKA,LERO MALIRO AGWANSO ,UZIONA WAKULA WATHA
Lero Waferetsa Munda Wake Omwe Kkkk
Linda madzi apite uziti ndadala!Dzulo a Chiphamafumu ambiri amayankhula mo2mbwa m’townmu
Kkkkkk Maliro oyenda NBB
Koma ulendo utalikilenji uwo kukatengako palibe.
Bola yabwelako ndi 1 kkkklllklkk. 2 -1 awapasa 1 point
More fire the Bankers
sizampira bullets
Imayenda mmbali ma bankers agwira ntchito yabwino
Am agree with queen
Neba kwake ndi kunyoza ona wamkaka pa dedza .
Noma for life
Team yanga yangotsala dzina pano I think likanasithidwanso dzina limeneli
Yr givin up kkkkkkkk i love NBB
U not real supporter..!
Ok ???
Choka kape iwe @alick wayamba liti kusapota mpira ku nyasa
Kkkkkk zaulendo uno!!!!!
Watch your mouth #Limbani
Inasinthatu dzina pano ndi chipha mafumu f.c
Tsogolo ndi la mdima this season
Flora ukuzitsata eti? ??
Eeeeya!!!
Mavuto
Kulimba mtima bac
Shaaa ma supporter omangosangalals ku ganyu basi pakhomo pawo ayi…kuteloko Silver ikamadzasewela ndi Noma adzapanganso ganyu ku Silver…kkkkk
#Antonio ganyu ndiye ndiyosamba kuteleko ku Malawi ndili ndi ma team 2 BULLETS ina ndi iliyonse yokomana ndi Noma-yo ???
Linasithatu pano ndi chipha mafumu football club.
Kodi bullets kumazulo zakale eti
Kazembe, unaonjeza kunyoza Noma italuza pano ukumva kuwawatu, kkkkkkk BB returns to losing ways
..chaka chino sicha Maule? What do u mean? Ndichifukwa chani chaka ndi chaka mumafulumira kuyiweluza Bullets?
Chifukwa ikuluza daily.. Kapena mutenga league?
Tionge, ndkuyankha tsiku lina..!
Bola pamenepo
Akayiphwasamula
Hahahaha hehehehe hihihihihi hohohoho huhuhuhuhu, mwano amapanga dzulo uja uli kuti Hahahaha Hahahaha Hahahaha
Dzulo ananyanya kukondwa lelo zawachitikila kkkkk
Ganyo yadzulo IJA lero muchitenso Ganyuyotu chipongwe kuchemelera Moira wa ganyo wanu mwalepheratu
Kkkkkk
“Pole jilani mwaka uhu sijuwi” Nyerereeeee!!!!! 0yeeeee!
Iwo amapusa ndi friendly IJA, Yomwe inaphetsa anthu ambiri? Silver inali pachisoni .
Ndamuza kale ameneyo kuti umene uja sunali mpira wamagazi a wana osalakwa uja!
Kkkkkk vuto anthu a bullets samamvera.
wamkaka kuno ku DZ:koma Mabankers timakwapura mwana wa neba coz chosuta chingambwe pamaliro aNomar pa civil stadiumkikikiki
Ma bankers more fire
it happens in football,bullets are not the first to lose.Remember barcelona lost to juventus
Nde dzulo mmatokota ngati kulibe mawa bwa?
regret comz late man….yestardy u waz talking too much….
Koma dzulo munatokotatu
zkomo popeza chipambano km ndalama mukufuna after all ife tazpeza selling sailes.Bullet woyeee!!!!!!
Tikamati team yamphamvu ndi imene imawina osati kugulitsa ma players
Ma blues woyeeee moto kuti buuuu enakhumaaaaa eiishi
maule osafooka osaonetsa kutopa
NBB is still a gud side, kungoti anakumana ndi akatundu omanga ndi mawaya
Iwo amaona ngati Silver ilimbikile friendly match ya 6 July ija ? kkkkm koma Kananji Fc
Iwe admin osamati akaswiri aku BT abwera chimanja manja uzit bullets yabwera chimanja manja ndipo choti uziwe akaswiri aku BT ndifeyo aku MANONA NYERERE
U dont kno wat u talkinabout..!
Usakudzwa ndiwe!!!!! ZANU zinada kuvomeleza ndi bwino man!!!!! Team koma iyi yotimwetsa mkaka posawelengela kuti ukudula bwanjiiii!!!!! Kkkkkk noma moto Kuti bhuuuuui
maule 4 ever
kod league unatenga lit iwe?
awa ndi ma bwate achilendo ase,osafunsa za ligue,ma cup nde timalowetsa simungafunse bwaa?just wait and see.
Akataswiri aku BT ndi manoma kumene osati chpha mafumu fc
Vuto la ufiti ndili meneli sumavomeleza zithu zikakuvuta pamene yafika bullets pa ndiye uziti akaswiri akaswiri ake opanga chani
NEBA CHAKA CHINO NDI CHOKWAPULIDWA BAC
Atumbuka amati ‘kuseka nkhwambula’ akulanga mesa? Bwanj kukoma? Big up ss
Chaka chino Neba achimva kuwawa kwambiri.Neba ukumva bwanji?Ife kumwa wamkaka and we’re going forward mwa dzina lathu.NYERERE WOYEEEEEEEE
Fichser wakalamba posachedwapa ayamba kulowa ndi ndodo mu pitch
noma sisekeleranso team
Peter Muthalika nde Vuto
kamulete bullets
aiswaswanya
Kamulete woyeeee
Zakhala bwino anatiseka kwambiri dzulo osadziwa lero zili panyumba pawo
bema ukunena zowona amatiseka zuro osaziwa kuti mawa chiwagwera iwowo kkkkkkkkkkkkkkkk
Kkk Kom Ya Chwona Nzako Chapta Mawa Ndiwe
Koma yeah!kkkkk