A week after three people were found decapitated in Bunda Forest, a man has also been found dead in the same forest.
According to a person at the scene of the incident, the victim whose particulars are yet to be identified was found hanging from a tree in the forest on Friday.
The source said some people at the scene claimed that the man had been murdered elsewhere and dumped in the forest while others suspected that he hanged himself.
Police were not immediately available to comment on the issue.
Recently, three beheaded bodies were also found in the same forest. The three were a woman, man and child.
The bodies of the three people were taken to Kamuzu Central Hospital pending for identification.
Chiteam chavuta ku premier League 4 tiana tija 2

Zataninso
Zataninso
Has bunda foret turned to b an evil forest?

Ndiye anthu audindowa akuchitapo chiani? angokhala basi? aonese udindo wawo osati mu Office pheee wakeup Malawi.

Boma lichitepo kanthu,i thnk, what they should do z achotse Nkhalangoyo ndikumanga manyumba

Oky
Oky
Pepani anamalira
Pepani anamalira
Nice journey to hell
Nice journey to hell
So sad
So sad
Anthu akubunda ofunika amuziwe Yesu
Anthu akubunda ofunika amuziwe Yesu
Evil forest
Evil forest
Anachita kumumangilira munthuyu i think
Anachita kumumangilira munthuyu i think
Dpp woyee
Dpp woyee
Amachita kukawamangilira anthuwo.
Amachita kukawamangilira anthuwo.
kodi chingwechi munthuyo ali kuti zachamba eti

Tikudikila oweruza
Tikudikila oweruza
Bunda Forest Y U?
Bunda Forest Y U?
KUMITUNDUSO NDAMVA ZOTI WINA WAPHEDWASO
KUMITUNDUSO NDAMVA ZOTI WINA WAPHEDWASO
Asaaah
Asaaah
Anthuwo akuziwa kuti Ku nkhalangoko Anthu akuphedwako, Chimene amafunako ndichani Anthuwo? Pamene mbili yakumeneko Akuyimva,Dziko lamalawi sililibwino lavuta:
zikuoneka kt munthuyo waphedwa kwina mkukamupachka pamtengo

Kalipo Kalipo.
Kokhakokhako Anthu Kumatha Chonchi….????
Kalipo Kalipo.
Kokhakokhako Anthu Kumatha Chonchi….????
Evil forest
Evil forest
pali gain pa Bunda forest ~~~~~~Anachita kumumangilira

This erea so called Bunda it’s surrounded by thugs! I do remember long time ago most of the people were killed and loosing their bicycles. And it’s a worse place to stay.

May malawi
May malawi
Guys think big zikhoza kutheka kuti uyuyu anaphedwa ndikummangilila kuti anthu aziti wazimangilila zikufunika tactict investgations munkhalangoyi

Bunda forest ilibe bvuto lili lonse kuyambila mkale muusogoleri wa anthu akale. Bvuto lili kwa mtsogoleri yemwe ali pampandoyo ndamene akuyenela kucitidwa check bwino

this forest is now becoming a death trap not so? can somebody tell me kodi ndikuja anthu amakapempherako?

mesa apolice amat chitetezo chilipo chokwani kumeneko? Poyankhura ndi adzitora nkhan? Patapezeka matupi aja opanda mitu, ndy apa atiuza chan ife amalawi apa? Tidzit mdziko muno muli chitetezo kma? Dzulo dzuloli ku bangwe kwa mvura anthu enanso aphedwa! Ndy tidzit chani ichi tsopano amalawi!….

Anthufe tikutananani kod (God help us)
Anthufe tikutananani kod (God help us)
Stupit Coward Ican’t Take Any Sorrow Rensposible 4this Condrolence Imagine Our Beloved They Are In Hosptal Looking Agud Life& Get Sm1 Hanging Himself Reason Why?Iwish If Iwere There B4 He Died!
don’t be a bozo bro,the guy was drafted.angomupha nkukamumangilira.that’s my assumption

Bunda forest ikuyenela kufufuzidwa bwinobwino anthu akuphedwa kwambili munkhalango imeneyi

Good news
On what aspect is this news good?
ETI INU?
she thinks she’s reading the Bible
Sorry
really?
Deranged
Tikupunguka
Thats realy agood news coz the more some pple r fiting 4 their lives in de hosptals the more others wasted their lives by hanging themselves stupid pple
No any sober person can hung himself without under influence of something evil. So just thank God that His grace is saving you and you have the ability to control yourself from committing such an act . So don’t blame these people just be praying that the devil shouldn’t conquer people and influence them to commit suicide.

Bunda yatani kodi?
Bunda yatani kodi?
Basi adzitsogola nafe tili mbuyomo mwina ifenso imfa yathu idzakhala ngati yomweyo Rip anganga