The Chinese Chamber of Commerce has donated 12 million Kwacha to Lilongwe City Council to be used for the reconstruction of Lilongwe Central Market which was gutted by fire a week ago.
Presenting the cheque, Chinese Ambassador to Malawi Shi Ting Wang said the money is to assist vendors who lost goods and money to rebuild their stalls and continue with their businesses.
In another development, the People’s Republic of China has pledged to construct five community colleges in the country.
This was disclosed in Lilongwe by the Chinese Ambassador to Malawi Shi Ting Wang during the 67th Anniversary of the Founding of the People’s Republic of China.
Ambassador Shi said the construction of the colleges is one of the many projects his government has embarked on in Malawi. He added that China is committed to strengthening its cooperation with Malawi to achieve economic growth.
In his remarks, Minister of Justice and Constitutional Affairs Samuel Tembenu said Malawi could realize its full economic potential by embracing the three pillars of development advocated by President Arthur Peter Mutharika.
11 million ivaya mu ma account a abusa ndi akulu a mpingo 1 million imangilidwa msika
boma la mbava ili, amaba ma billion what about 12 million? thus ya ku shopping mwinanso pano yatha kale, chinavuta ndi chani kuti mukamange nokha then mutiuze pomwe mwathera? akanganyawa pa Cash simumawadziwa??????
Thanks china God bless you
True friends comes in tough time like this and no shame to say thanks tat donation I think government must take their time to find good contracters so that we can see good Lilongwe central markert than before and let us start doing things for permanent not like we are going somewhere tomorrow
nthawi yopanga Donate ku ,Malawi surly inatha,China shld have knwn better,why cnt you jst build it alone as u did wth stadium?K12m mukazawapasa muzapiteso after 1 week checking th account u wil see and shocked tht kwangotsalako K5milion while Njerwa,thabwa,mchenga,cement even a single nothing is there nt even an invoice….asking them thy wil tell yu we are still working on a #plan…..anyway mwina nanunso akubatizani,koma chonde mukumbukeso Lilongwe Bus Depot mwina nayo tingoyasa
A rat in the ceiling
China Gvt shud rebuild da market themselves rather than giving money to da Council.
Which market are they going to reconstruct I thought the vendors have already done the job zidyedwa ndalama zimenezo
Thats good development & u city council ndalama zimenezi musaike mumutumba anu.
Thank you…
Why China
thanks China, K12 million is not enough but we shall ask well wishers from other angles to top up
Malawi government is fucken stupid, even the market they can not build the better ones
K12m for Lilongwe market??? That’s not even enough for a well planned 2bedroon house
Zopasidwa Sumadelera, Ndi Ntchito Ya Lcc Kumanga Nsikawo Ndi Ndalama Zawo
Oooo mistake alakwitsa a China kupereka direct ndalamazo ku LCC aziba ndithu bola iwowo a china anakakonzetsa okha, mbava izi
Zibedwe tsopano, a Malawi mwantchito zawo anyambitire msuzi. Ngati amaba zamisonkho ya anthu kulibwanji zopatsidwa ndi anthu olemera? shaaaa
Nyanga zonse zinathe momwemo anthu analila kumeneko ,osati chifukwa chakatundu kapena ndalama ayi koma mbewa njoka amphaka ndizina zotelo ,ayambanso one
Tatopa nanu.Mukumaotcha dala misika cholinga muziba ndalama za chithandizo.Agalu
Ndalamazo amangile zimbudzi bcz ma shop ( Hawkers ) aliyense akudzimangila
China ndi DPP family ndi chitseko ndi felemu sure….!!!
Welcome China
Igwire ntchito ndi one million Inayo ndiyokambirana mmene tingamangire msika!!!
This is welcome development
ok
for the best live that money to the Chines to do that work in short period we can see progress but Malawian contractions mmmmm ….ma badget too much mpaka ndalama sikwana.
They should build it alone from human resource to building materials even sand and bricks to avoid inflating the trips don’t give them cash it will end at Nkopola in Mangochi just hand over the finished market
tikayala chinangwa ndi kachewele @ Felie Mikel Kotton
Tionera ngati sizindibwa
when what you need is one pin a good rich friend does not give you two kwacha
why a whole country donate only k12m when my prophet can donate k50m?
Mudyenso agalu inu ndalamazo mwamva? Zikom kwambir a china.
Malawi
Just too little
enanu macomment anu akusonyeza kuti Malawi yalakwa kupasidwa chithandizo..zimenezo ndezaboza poti palibe dziko silithandizidwa…mayako kaya achisilamu nawo ali muma mabungwe amugwilizano amathandizana.. Europe nako alikonko…Brintain inalowa chisokonezo chifukwa cha Brix muziwa zomwe zimatandauza mesa ndinu aanzeru..kamba koti kungotuluka zinapangisa 20% ya anthu omwe amathandizidwa mu EU asafala.ndepena muziyamikila kuti dziko lomwe tili nalo paubale lathandiza osati kumangonyoza ngati inu mwagulilako olo njerwa imodzi kuti amangeso msika umenewo.
ZINALI BWINO KWA BOMA LA CHINA LIKANANGOMANGA LOKHA NSIKAWU OSAPRLEKA NDALAMAZO…. CHIFUKWA NDI UMPHAWI TILI NAWOWU MAKOBILI AMENEWA AYAMBA KUPITA KWA ZIBWENZI NDITHU
Thanks China. Please Malawi govt zigwire ntchito yake
Chinese yachita dala kupeleka zochepa I think so cfk akuziwa kuti ndalamazi zidyedwa
K12m mtindalama tochepa kwambili, kuyelekeza ndi katundu yemwe adaphya,kungoti China ikungofuna kudyesa ma stuff a Lilongwe City Council kumene kuli kukolezela nkhalidwe la Cachgate.
Is that not for just 1 shop?
Zikubedwaso zimenezo.Poyenela kuti zifikilepo zifikapo zochepa.
which is 240, 0000 randa in SA…can this is silly
Ndalamayo igwira tchito yanji athu amaliza kumanga okha.
Ok m’maontchera dala eti pofuuna ma donation?
12mk is not enough,
My name is Mira Kalonga and this a testimony of how i became HIV NEGATIVE, i have been suffering from HIV for the past seven years, i have spend a lot of money finding cure for HIV/AIDS until i found this true man who cured me completely with his powerful herbal medicine, i have tried different means to get this virus out of my body, all the possible ways i tried did not work out for me, i came across doctor olumo through some amazing testimonies concerning how Dr Olumo has cured different people from various kind of sickness like HERPES,HIV/AIDS, CANCER, with the help of his powerful Herbal Medicine, so i was encourage and i contacted Dr Olumo i told him about my Sickness, He told me not to worry that he was going to prepare some Herbal Medicine for me, after some time in communication with Dr Olumo he finally prepared for me the herbal medicine which he sent to me through courier service and he also gave me prescriptions on how to use it, after taking the Herbal medicine for some days, i went for test to confirm and the result was totally negative ,i went for test again in a different hospital still the same negative , Today i am fit and healthy to live life again, I am so happy for the good work of Dr Olumo in my life, if you are having a simillar problem kindly email HIM on { [email protected]} OR CONTACT HIM WITH HIS NUMBER OR CHAT WITH HIM ON (WHATSAPP) (+2348138956767)
Money from China fokong zosalimba 12million kumangila msika
donating money to a corrupt system ain’t good ….let them construct the structure
Chonde ndalamazo tipatseni kuno timwele mowa ndikusutira chamba. Coz omwe mwawapatsawo sizioneka mayendedwe ake
Though it’s small and wrongly directed many thnks to e chinese pipo 4 e support
Tidye nawo basi zimenezi iyya imadya Pomwe aimangililatu
Kkkk koma zina ndye mwati zingati
Ndie zomwe zimakusangalani kumangothandizidwa basi mawa timvaso market Blantyre wapsaso
K12 m amwera kuchindira ma hule…bola kugula Chimanga
wina abaposo muwona moti athandizikilepo ena. Malawi sadzatheka ataaa!
Nde tikayalamo chani
Let them build it too…if we are to have a better market
Aaaaa aigawana ndalama imeneyo am’boma
Koma pitala!wapempha kale?Ndiwed Dolo pa mphanje pano.
thanks china
If it was govt’s budget munakamva 5 billion kwacha nsika omwewu
Azidya
Next time do the reconstruction yourselves. Anganyawa ndi ma thieves zedi. You will see substandard structures.
thanks China government, Malawi government pliz no need to go to san’n’sand for nonsense meetings that will only waste this money,all you need is to get a proper contractor who knows and will finish the job,thats all! koma adyeranu tikuonani mutatengana muzimagalimoto zanu zofufuma zodula wakunyanja kunamizila kukakambilana koma kuli kukagawana ndalamazi, #not gud @all
Well spoken men
kkkkkkkkkkkkkkkkkkk
They should have given materials not cash…. (GATE)$$$$$
you are right Firouz ,actually the China government was supposed to come to Malawi, reconstruct the Lilongwe market using their own resources, kkkkkkkkk ,after finishing everything, then then just hand-it-over to the Malawi government, kkkkkkkkkkkkk,koma bwanawo ndiye angadandauletu kkkkkkkkk
but those guys have already built there shops as we are talking now
kkkkkk olo atatipatsa materials uvakuti anthu aba koma ali mwabwana omwewo atangawana ndikupeza madobadoba owagulitsira. tafikapa otithandiza mungobwera nokha kaya ndi chimanga zatingawireni mpaka mutaonetsetsa kuti ovutika alandira. Koma ndalama mwaperekazi zinyambitidwaso ndi mimbulu
kkkkkkkkkkkk koma #Wil iwe,talking the matter fact, mumawonjeza ndithu
Zadyedwa kale!
Uselless !Ababy of 50 somethng years old but still he cant stand and walk on hiz own alwys realy on donors.Shame
SiZioneka ntchito yake ndalama menezo
its too little
Mwachanje Satafuna…..Bholabee!!!!…..Ngat Zachepetsetsa..inuyo chitamponi Kanthu…….
Koma zimene zagawidwa ndi 1.2 million the rest pa thumba.
mabwana ali dovu chuchu kufuna kuzinyambita basi
Afriend in need is afriend indeed so thats chinese though abegar is’nt achooser bt if the figure might b k12mln *ten ok,
bola zigwire bwino tchito
Zikomo
What is needed is to force each cabinet minister + those 2 first citizens to be donating a K1m each every 2months. They milk too much money without paying back. In so doing, we gonna see who wants to serve and save this poorest nation
zidyedwa zimenezo!
2 milion yokonzela…8 milion yamastaff member …2 milion yogulira zakudya..madzi ..matea ndi ma transport ama staff member
?
CHINA ILI BEST KOMA BOMA LATHU YIYYY AMAKONDA ZOKOMA ZAKUTHIPI
Amaotcha dala kut aitanidwe kudzamanga…kkkkk koma #china ndi yochenjera bwanj!!!
Ndalama zilowa nthumba mwawo izi.ayi ndithu anthu alemela.amapezela momwemu.
NAMBALA YANDALAMA NDI K12.M KOMA YAWO ASAIYNILA ACHOTSA K5.M AYIPATSA NAMBALA YABUKU LAWO
Gud dvpt but make sure all needy are reached
Alemekezeka wa mwambayo
Thanks koma zitagwile ntchito ndi 1million,zina zisowa zina zithela ma meetting
That’s the great problems we HV in our country ndipo atakhala matenda aumbava ndikati akuposa chorela
12 million kwacha ungangile market
Amalawi Tilibe Pabwino Kulephela Kungonena Kut Zikomo Kudelera Donation!
kma china iiii a tnk these pple are benefiting alot pa chinachake ndithu watchout bt afta o thanks
Mmmmm alakwanso? Hahahaha koma ife anthu akuda sitizathekanso basi…shaaaa!
koma Ndiyedi..Munthu..mdi Galu…Athandize walakwa..alemere walakwa akut wa satanic…….Amalawi..munafika pa uchitsiru…..
waganiza ngati bakha
That’s how it works a dona nothing for mahala, unfortunately here in Malawi we want free stuff
Aaaaa kaya! Ndiye chingakhale chani kaya!?
kkkkkk alakwa chani…palibe dziko lomwe limakhala paubale ndilina opanda chopindulisa..olo malawi benefits more kuchoka kwamayiko omwe alinawo paubale..thats y anathamangisa Taiwan poti mabenefit anatha.muziyamikilako pena
scratch my back then i will scratch yours. ngakhale moni masiku ano umayamba walipira ku service provider wako then you will be able to pass the greetings. afta o nonse mumakhala mwapanga benefit. palibe chaulele
Thanks. guangzou hung sh tong hong