A 25-year-old man in Ntchisi district has committed suicide by cutting his own neck using a panga knife.
The incident happened on Saturday June 4 2016 at Chimkombero Village.
Police have identified the deceased as Leonard Zakalia of Chimkombero
Village in the area of Traditional Authority Malenga in Ntchisi.
A police report indicates that the deceased who was living with disabilities moulding bricks and after his work he went to his house where he cut his neck using a sharp panga knife.
The deceased was found lying dead blood oozing from the neck.
Police visited the scene of crime and took the dead body to Kamsonga
Health Centre.
Postmortem conducted at Kamsonga Health Centre revealed death was
caused by loss of blood due to a big cut wound on the neck.
*Gladson Mbumpha is Police Publicist for Ntchisi district.
atola nkhani nkani simugwirizana ndi boma eti kulemba za bodza kwambiri
Mmmmm nkhani yake ya mpira yomweyi or what?
The sharpest panga knife on earth tu…eeeh takambani zenzeni abale
Eish wat a courageous man.
Eish wat a courageous man.
Eish wat a courageous man.
Mankhwala.or.ufiti.siziphindula
Wachitabwino kudzipha yekha kulimba mtima kumeneku adakachedwa adakapha ambiri.
Y mapolisa of ntchisi failled to perfom ur job indecent.takin a murder to de hospto instead ov takin him into the custody.iz nde zobwande zobwande
Amalawi amene ndimawadziwa ine koma amenewa omatchuka ndikudzipha / kupha anzawo basi
Ndikuona Ambiri Akukayika Kuti Anazikhapa Bwanji? Wina Atenge Chikwanje Amene akukayika Ayese Kuzikhapa Pa Khosi Ngati Zingatheke.
You mean he cut his own throat
Kudzipha yekha ndi boma zikugwirizana bwanji?Enlighten me please
Kodi Iwe 24 watani ? Wayamba bodza kumanamiza anthu, munthu angadzidule yekha ndi chikwanje ?
y ntchisi this stories of sucide everday,pliz mojor 1 (bushiri) where iz ur GOD ?
kodi boma la Ntchisili bwanji limatchuka ndi zozikhwezazi?
Ummmmm malawians
According to rlthe post mortem, it is saying that death occur duje to loss of blood through cut wound. I’ve quoted “cut wound” which means he was cut by someone not himself.
kkk,a kuzkhapa nkuthawa, ? Ndzingoseka ndkaganiza
A day is closer, the western people are rushing to Palastine to see the coming of Jesus . Ameen
ZABODZA PA TSAMBA ILI. How can you cut your own neck while alive,?? try and give us the answer.
Ndiye anazizinga bwanji?
Amayesa zida, kutereku anamalira musamale naye.
Latani kodi dziko lathu lamalawi abale…likulowera kuti? Kuphana, kudzipha, zingozi ndiye osanena …ambuye atiyendere ife tonse ndi dziko lathu lomwe liyenderedwenso mmmmmm R.i.p
That must have been a very sharp panga..
Hahaha this z very funny
week simatha tisanamve za ku ntchisi ku ntchisi ku matchuka ni nkhani izi: kuphana, kuphedwa. kudzipha. kugwirira ndiyo ntchisi imeneyo
Ooh! So reckless man!! MPaka apa?
He cut hs own neck and run away..police is serchng 4 hm,
Uyu ayenekela kuti azemba kenakache, mwina aphapo anthu ambiri makamaka ma Albinos. Tsopano awona kuti akapitiliza zokhapakhapa zakezo iyenso azakhapidwa nde wangozipangapo yekhe. yimfa ya plan. siyangozi. ine ndingachite chisoni.
Koma zona adm
Oh Malawi,,,, selfie ndikupha komwe,,, lol,
Anasuta chamba ameneyo kkkkkkk
Musiyeni wakhuta ameneyo
iii ayi koma mbomali ndaona zodabwisa zambiri maka ulamulilo uwu. Kaletu sitinkamva ngati izi. Or kutha kwazikoko langotha kumalawi kokha??????/??
Rest in peace
Nanga mkutani dziko la Malawi Makosi a wanthu akuthadi asadati
Moyo ukomelamu nkuwuchotsanso? Heeeee akafike
Lol lie
give him an award he deserve one
Kkkkkkkkkkkk koma amatha…. akangotipelekelako moni
Its imposible how can you cut your own neck with a pamga knife?
One of u is lying,its either malawi24 or that dude. Nzosatheka wekha kuzidula khosi ndi chikwanje
Exactly
zoonad
I agree…unless anadzibaya and he bled to death. kudzidula khosi????? kkkkkk ayi zosatheka
Bodza Limenelo.
Zovuta kuvetsa izi
Tiyeni A Malawi Tipephere Molimba, Dzikoli Mwalowa Ziwanda Zosatsukika, 2dy Ngozi,2mrw Ozipha, Fdy Ogwilira,etc Zanyanya.
Kkkkk How i wish i was there mmm its like watching a live horror movie… All the best bra!!
Kkkkk ulendo wabwino man.
Guys Thats True Munthuyi Waziphadi Mpaka Khosi Kutsala Pang’ono Kuchokeratu The Probelm Is That Kulumala Kwake Anali Osayakhula So Bad Rest In Peace
What a suicide? akuthawa chani? bwinobwino2.
If i were there, I would av chopped the Head completely b4 calling d Police. Lost In Pieces F O O L I S H
Koma
Koma
ndi nkhalidwe lake ameneo last yr adapangaso zomwezo
So tell me plz can aperson cutt off his own neck using apanga knife??? Thats total lie just bcoz you can just wund yourself!!
U changed now kkk,those deiz ago u said someone kill him,,statement is changed, now he killed by himeself what afuck are u tolkimg about?
arrest him
Koma ndiye zafikapo.
aaaa!! akafikira kuti??? this is inhuman!!! munthu wabwinobwino sakangapange zoopusa zimenezi or mavuto atakula bwanj!!!
I like his courage….
Nkhani yachikondi ndiyovuta azimayi akutitengera ku manda
Munthu siungazidule khosi weka. Something happen there
Guyz Sindidavepo Munthu Kudzipha Motero Mmmmmmmm Ndikukaika Ngati Wadzipha Ekha
Mmmmm Guyz amuna akusowa, let’s stop solving our problems by commiting sucide.
Pray for Malawi
That was a very dangerous man who r very few in ths world. Its gud that he has killed himself
Lifespun Yake Basi Inali Choncho,satana Akakulandireni Bwino
Self judgement! Hop he had proper resons, to slaugher hiself, we will never know. So bad to friends and of cource relatives.
Aaaa wanachikanga
Hey its strange
Lol….who helped him . I guess it was like watching a horror movie .
He was so brave ,what was the problem?
#RIP braza mukatinenera mwatipanga represent
don’t trust these assholes….shit
Imeneyo ndiye ntchisi
now its no longer Malawi i used to know
Zosatheka wekha kuzipha ndichikwanje how? Muyambirenso kufotokozerabwino
Killing himself with a panga?? Can’t believe this story coz it isn’t possible
Something fishy here
ameneyu anaganiza zozidula khosi chifukwa sinanga ndikulumala sakadatha kukwela muntengo mkuzimangilila ndi chingwe,, that was a wise decision
Zake izo
Koma Kwathukuno Vuto Ndichani?Malawi 24 Ikalemba Nkhanizodzipha Ndiye Kuti Ku Ntchisi.Mavuto Akakulamsinkhu Tifuse Thandizo Kwa Anthu Ena Zodzipha Ayi.
Bomalo likuziwapo kathu.
All the best
kkkkkkk mavuto achula kapena?? bwnj nkhan zmenez kuchuluka chaka chno, dzana tmaika wna kuno kumwa poison mnyumba mkuenda kukafera kumtsinje!! zafkapo bwnj!
Shame
Kunama basi stupid
Ali bwino
Zingathe bwanji kuzidula khosi munthu yekha???? Bodza basi
Hahahahaha izi zoseketsa osati chisoni,khosi lako lomwe kma kumenekooooooo
Tiredness
Ayende boh iyeyo. Ife zinjoy diwazi tangoipaka pa easy man
What a retard!
How???
so sad mzimuwake uwuse ndimtendele,Ambuye timenyeleni khondo kuphana kwafika posauzana.
shaa!! what a bravety.
Munthu kudzipha yekha ndi tchimo lalikulu
Zofuna zimenezo!! munthu wamkulukulu ngati ameneyu amadziwa chomwe akuchita
Ayi Chilango Chozilanga yekha.Magulu Opha Anthu Awa ndi Amenewo
That takes skills
That takes skills
Thats redicurous
Mmmm ai awonjeza adawa ok RIP
Doesn’t make sense. A panga?????
Sound practically impossible to me
That’s what happens when you employ unqualified police officers
how?
Aju suta ameeyo?
Kafukufuku waonetsa kuti chiwelengero cha anthu ozipha okha chikwera kwambiri chaka chino makamaka ku mpoto chitsika pakati pano pamene ku mmwera akutsogola ndikale
Ufiti
Alibho wathawa njala yavuta kumalawi kuno
Zake Zmenezo Wafanso Ekha Zosadandaulitsa.
suziwa kt ufa umaona ngt sufa
Bomali ndilotembelelendwa za Ufiti bac asa,,,tili samuse kumalawi kuno
wausilu ameneyo mmangeni…..
Ndy Paja2 Ukazpha Zwa Kut Kumwambanso Kulibe Chako, Akafike Bwno Kujahena.
Worse suicide ever
thats gud enough instead of killing albino
Nidzake idzo ife tayenda mukuvina Dandy Crazy ku Estadio de Levy(Ndola Zambia)
it’s done by the name of our nation(malawi) flames,ndichifukwa mabvuto sakutha
kapume aise pakuti zofuna zako zakwanilitsidwa
koma ali ndi skil yoopsa mpaka kuzidula khosi yekha
Koma mene munthu umvera ululu ukazicheka podula ndiwo nde uyu kukalimba mtima khosi choseni hmmmm
Kafike bwino aise, anzako a Satanic ndi amene akuthandiza maganizo ako opusawo.
Better killing urself than 2 be a threat 2 others. RIP
What a shame if it was a Tumbuka??? Plz arest the guy!!
Aaaa, dziko likupitadi kumapeto,, pompanonso sitimanva zankulu wina amene anadzipha yekha nkuthawa, mokuti apolisi alinkati kumufufuza… chikondi chija chapita kuti abale?
Amene Wazipha Yekha Nkuthawayu Mukamugwira Mutidziwitse Tizangomuona.
Kkkkkkkkkk
Ameneyu musakaikenso zikungoyenela kutelo basi, coz ndimoyo wankhanza kwambili wachitawo, akungoyenela adzawonedwe basi
Guys sindikumvetsa;mwati wazipha yekha nkuthawa?how come?
hahahha!zalowa libolonje basi!
iiiii palibe akutha kunvetsa man, koma ndithu wazipha nkuthawa, panopo mokuti apolisi alikalikiliki kumusakasaka kuti amugwile akamuimbe mlandu odzipha yekha kkkk zumakhala ngati zoseketsa koma ndizonvetsa chisoni ndithu
kkkk, koma nde libolonje libolonje, kuzipha kwalowa lasha uku
akagwidwa amutsekele ndi chiloko mu coffin,
apolisi anenetsa kuti amuchita zimene sanachitileponso aliyense amene wakhala akupalamula milandu yokupha, akuti this one z 2much…..nde tonse tionela limodzi zomwe amuchite bola amupeze komwe wathawilako
Koma ameneyu wachita bwino kuthawa chifukwa mwandu umenewu ndiwaukulu kwambiri
Ndava kuti wathawira ku Joz Ndiye zoti a police agwirila ndakayika ha!! Ha!! lkkk!
aaaa, zoona?, sizingatheke kuti alumikizane ndi apolisi a Joz wo achigwilie konko chigawenga chimenechi?, atha kukaziphelanso konko ka
Kkkkk koma guys munthu kudzipha ndi kuthawa?
Stop smoking buddy
Mcfield, kuteleko aliyensenso kuno sakunvetsa, olo apolisi akumusakawo sakunvetsa, munjila ina palibe aliyense akinvetsa zaupandu womwe munthuyu wauchiyawu iiii, dziko ili
Kuteleko thats the only solution remaining 2do, smoking 2puffs atleast i may understand abt this incident…. @ Maxy
Munthu ndi kuzipha Kenako kuthawa sindikumvesa, mesa mwati munthuyo wazipha nde athawa bwanji
Hmmm, alinafe palibe akunvetsa ndikuti, aliyense wangoti jenkha ndinkhani imeneyi, komabe all in all tikukhala kumapeto anthawi. apolisi akamugwila mwina mpamene titi tinvetsetse
zaboza bax, kuzipha nkuthawa nde kut chan
Kuzipha nkuthawa nde kuti munthuyo wazipha nde wathawa, pamenepo ndukhulupilila ndamasulila bwino THANK U VERY MUCH FOR ASKING
Paja ndi five years uka banda kamodzi eti??ndumaiwalatu..,.,.,kkkk
Chomwe simukuvetsa ndi chani ena mpaka mutu kuwawa zomwezi kkkkkkk anthu asacheze
kkkkkk, yesephe anatsitsatu pano ndi miyezi chabe, akuti nthaka inaguga ilibe manutrients kuyelekeza ndiyakale
yohane etieti inenso sindikuwanvetsatu momwe asakunvetsela iwowomo
????izi ndi zina izi…
hahahahah dziko ngati likutha anthu nawo ndiye akupengatu
ameneyudi akuyenela kuti inali misala, nanga mpaka kudzipha yekha nkuthawanso, nde amadziphelanji? munthu wabwinobwino sangapange choncho ayi i think Ordney u r talking
Akulu amenewa ndi dholo bad
realy
Mmmm hw can it b possible? Mmmmmm
A hand of applause. Wow!
chilipo siulele ai
He must show me hw he did it
Who whoa- whoa- whoa,” on hw….ae maan dats a lie….come on…
evryone wants to break a record
It make sense?
Yho! Some people are courageous indeed, its better a rope unlike apanga knife,, we can write rest in peace but you can’t because this is a painful and stupid death.
These are lies! Logically, how can you chop of your neck? Admin took you for a ride!
How posible can this be??
Ndi mkazi uyu akanakhala mamuna sakanapanga izi
Samurai
logically this is not true
People have ever done it before, obviously your logic is illogical.
I have never ever heard anything like ths unless there is a better explanation
“Postmortem conducted at Kamsonga Health Centre revealed death was caused by loss of blood due to a big cut wound on the neck.”…… Just because you’ve never heard of something, it doesn’t mean that it’s illogical.
Something is fishy here just think deep about it
the post mortem doesn’t conclude that the person commited suicide
Much as we agree that death was due to loss of blood through cutwound but I strongly beliv that was not a self inflicted wound….on ones neck,my foot!
Emmanuel Maulana thanks For thinking deep because we don’t hv just to believe anything without analysing the story u earn my respect
you are not serious!!
Really?