MCP wants Malata-cement subsidies abolished

Advertisement
Juliana needs to retain her seat.

Malawi Congress Party (MCP) has called on government to abolish Malata -Cement subsidies arguing that funds should instead be channeled to Farm Input Subsidy Program (Fisp).

Juliana-Lunguzi
Lunguzi: Funds should be channeled to Fisp

Speaking in the national assembly, MCP legislator  for Dedza East Juliana Lunguzi called on government to add more funds to Fisp.

“In Malawi we haven’t reached a point of  subsidising houses, we are  very far on that. If we can have subsidies on production people can have money to build decent houses.

“As of now there is no food for the very sick people in public hospitals and the country is facing hunger situation, if more funds would have been channeled to production of food things can  work,” said Lunguzi.

Malawi government, through the Ministry of Lands, Housing and Urban Development, launched

Malata – Cement subsidy  to provide decent houses to Malawians.

The programme which was approved by the National Assembly in the  2015/16 financial year is expected to use K7 billion.

Advertisement

180 Comments

  1. Zungulirani dziko la Malawi mupeze kuti kwamangidwa nyumba za muprogram mupeza kuti ndi budget zikusiyana.Budget kukula nyumba zomangidwa kuchepa kuno ku BK anthu anauzidwa kuti malata awo abwera pano patha miyezi pafupifupi itatu kuli zii.

  2. Stonald Chinjala; Mwadziwa Bwanji Kut Iye Ndi Mbava? “Use Athief 2catch Athief” Ndiwe Mmodz Wa Iwo” Mcp Lakula Ndi Dyela Komanso Paja Nkhanza Nzachibadwa Mudzakhala Otsutsa Mpaka Kutha Kwadziko, Achakwera Mukalambanso Ngat Ambuyanu Atembo Then Resin Shame On U! M C P! Mdziko Zimalamula Zipani Ziwili? Kamalaw Kakang’ono Zipan 10 Dyeraa Bas M C P Shut Up Ur Mouth & Watch

  3. Cement and malata subsidy siyolakwika coz they are fulfilling what they promissed in their manifesto. Vuto ndi loti ma Malawi china chilichonse pamalowa chinyengo, just imagine anthu a ku boma/ kuunduna okayenda kukakumana ndi mafumu pofuna kusankha ma beneficially a mu programuyi akuti ma allowansi okhawo posaphatikiza ma envelope opereka ku mafumu zitha kukwana kumanganso nyumba zitatu za anthu osauka. Pomaliza kupanga ndondomeko yonse yolondoloza kuti nyumba iyambe kumangidwa pamakhala patapita ndalama zankhaninkhani. Chisoni anthu osauka lero akugwiritsidwa ntchito ngati chida chobisalira pokuba ndalama zanga zamisonkho. Mulungu adzakulangani ndithu. 14 billion ya budget ya last year towards the same cement / malata subsidy inatha pongomanga nyumba 17 zokha.

  4. Amene Akuti Malata And Cement Subcidy Sikuyenda Bwino Zake.Nthawi Ya Mcp Amene Ankalembedwa Kulowa Mu Club Ndi Ndani?Mesa Munkapanga Nokhanokha Inu.Ndiye Lero Ziwawe Chifukwa Choti Akupanga Ndi Ena??Palibe Yemwe Safuna Kugona Pabwino Asiyeni Anzanu Mmesa Subsidy Ya Chakudya Ilipo Kale.Kumayamikila Poyenera Kuyamika Amalawi. N

  5. Azisiye kumene zmenezo akagona bwanj nd njala? Enanu mumakhala ngat mi2 yanu siyiganiza bwanj against MCP always? Go 4wat thy are sayn not da chipani pilizi

  6. Ineyo ndikudabwa, JB ndi chipani chake cha PP ndi amene anayambisa programe imeneyi, and amaitcha kuti mudzi Transformation, and anthu mumkamuzuzula with that, even DPP was in front kuzuzula that programe coz amati munthu timuphunzise kugwira nsomba not kumpasa nsomba yaulele, and DPP inapitiliza kunena kuti sizamangira munthu nyumba koma izasisa mtengo wamalata ndi cement , and mtengo wake uzakhala wabwino oti aliyese azathe kugula malata ndi cement and ndikumanga nyumba. Nde panopa mfundo ya dpp ija ayithawa ayamba zomwe amkazuzula zija za JB, za Mudzi Transformation. Pali mzeru pamenepa?

  7. Manifesto adpp munali subsidy imeneyi anthu anavotela kuti mwina nkumangako inu manfesto yanu anthu sana votele ndiye mudikile 2019

  8. Kkkkkkkkkk apaseni cement ndimalatao azikaphika siment nkumakhuta malatao akakhomeko mapoto kodi munthu azapindula chani kufa ndinjala kufela zina lanyumba ya cement ndimalata kkkkkkkkkkk koma kodi akamati kulemera nkudya amathandauzanji???????? Kkkkkkk koma anthu akumbakira peterwa kodi ngati chipani chisali mboma does it min azingoyanganira without voicing out?????????? Ayi apaseni siment azikaphikapo nkumadya kwina akumanga nyuimba kkkkkkk this is the tym i enjoy politics

  9. That is true thinking of atrue leadership,we need,osati za political appeasement akuchita awa aDull Propaganda Party. Kodi kuuma mitu kwanuko,mupweteketse nako anthu? Ma donors,ma economist,ndi ena anayankhula,koma aGONTHI inu osamva ayi? Cardiac will also arrest him.

    1. U R 100% Correct My Bro. Let Us Think As Heads Not As Tails.

  10. All subsidies (malata cement and fisp) should be abolished bacause poor Malawians are not beneficiaries of these subsidies….For example; Poor Mw’s are requsted to pay an extra/entry fee of K4,500.00 on top of the recommended fee of K3,500.00 to buy 1 bag of NPK and another fee to buy 1bag of UREA… Making K8,000.00 for 1 bag…. ACB where are you???? SELFISHNESS PEOPLE WHO DOES NOT LOVE THEIR WARMHEART MALAWI… SHAME ON YOU!!!!!

  11. Malata Subsdy Inayamba Chifukwa Mai J Banda Anayambitsa Prgram Yomangila Nyumba Anthu, Tsono Inu A Mcp Ngati Mukufuna Kuti Ithe Best Way Ndikungobweletsa Program Yanu Yokhudzananso Ndi Malata.

  12. You approved this budget in the first place. Kkkkk. Yavuta ndi nsanje a Congress coz this programme is a plus to the current DPP BOMA. Mukadzalowa mboma do abolish inuyo. This is a Blue print of DPP manifesto. Tisiyeni………

  13. MCP…..This is what made DPP win.They promised Malata/cement subsidy..Inuyo simunawine because we all know kuti MCP yomwe inatukula malawi No one is remaining except the last man onthe touch line JZU…. This programme is even happening in Israel already developed nations zimangosiya mayina….U guys in MCP are afraid of DPP approaches of following its manifesto kkkkk.Wakeup Lunguzi u are too young tobe reasoning mwa chikongeresi……Try to abolish it and see what the beneficiaries will react like…..Once again Cheat ur wives/husbands on The goodness of mcp not US….tikuziwani bwino!

  14. Nazoso izi! Malata ndi cement zotsika mtengo zikugwilizana buanji ndi kusowa tchakudya mchipatala? Paja musaiwale kut a JB adawoletsa chimanga mu mkhokwe za mdziko muno. MCP mbolish!asatinyase! kungova kut ndi a all-oposition basi tizingovela iwowo? Next term all-oposition idzakhala UDF, popeza DPP idzawinaso

  15. You approved this budget in the first place. Kkkkk. Yavuta ndi nsanje a Congress coz this programme is a plus to the current DPP BOMA. Mukadzalowa mboma do abolish inuyo.

  16. Zopanda fundo zopanda mchele nde bola musinthe zomalipilisa odwala mzipatala za zikulu zikulu zaboma than za cement coz moyo sagula

  17. To hero with mcp ma failures come up with your swagga zoputsa basi. No one can stop us we are proceeding to what we say we would deliver to Malawians

  18. mbuzi za mcp musalowerere za mbanja mwa eni manifesto amenewa ndi a Dpp not mcp inu muzipanga za manifesto anu bwanji mukulibana ndi manifesto achipani china mwasowa zochita eti muli ndi manifesto anu ku mcp ndani anakuuzani kuti manifesto awa muchotse foolish kongelesi

  19. Economists will agree to MCP idea of abolishing subsdy…… Politicians will agree to DPP subsdy program….. They say: Usampatse msomba koma mpatse mbedza adziwedza…. Malawi z agro- based country….. Investing in Agriculture, we go inject more money into our economic circle…. This subsdy programs wont take us anywhere……..

    1. yeah t hav to wait…… but it has to shout out when the driver seems to be slping…… they say subdising cement and malata to enhance poor peoples standard….. however, if that program get into system…. do u thnk its the poor who go benefit from it? if a person is failing to buy mbeu how can he/ sh manage to buy cement…… think broo b4 u politicise……

    2. They say MCP does not provide alternatives, whats this? An ill timed subsidy. Improve the economy and I assure you Malawians will build houses and better ones than those you are building for them.

    3. R u kidding @Kelvin Mpango? Why didn’t most poor Malawians build decent houses during the economic boom of Kamuzu Banda and Bingu administrations? Even FISP has proved to be the waste of resources coz it is not transforming de lives of de beneficiaries. It has helped to instill dependency syndrome among our small scaled farmers. It is de same people every year which should not have been the case. So if MCP says it (malata and cement subsidy) is not good for our economy but fisp they r just trying to divert our minds. I would say both have their pros and cons coz shelter is also a basic need a human being must have and they hav implications to our economy.

    4. subsidy aint bad Joseph Diverson…… but u cant subsidise your commodities when your economy is at trough, now Malawi is trying to recover its economy, thus, can subsidy help in recovery plan? …. subsdy is a program to go when your economy is at boom in order to solve inflation….. during Bingu administration our economy was at boom….. subsidy program was a welcome development……

  20. here is a lot of Malawians that think, that politicians should start taking responsabillity and grow up, instead of chasing the next vote. This Beloved Country of ours is bleading.Who carers. We all want our freebees without thinking about this country of ours and where are we taking it to.Love you Pauline. Keep up your hard work.

  21. i do agree with them unless thy change the system of identifying those to benefit, zikufanana ndi imput sudsdy yomwe amapindula ndi anthu ochita bwino…

  22. Eeee thts gud bcoz zinthuzo sizikugawidwa angopanila ndi atsogoleli. Ine neba wanga akugulisa 5500 ali nawo ambirimbiri malomoti zifikile anthu

  23. MCP,NDI BOMA,TILI PA ULENDO(2014=2019) Wochokera Ku Eguputo Kupita Ku Kenani.Mlungu Akudaliseni Nonse Amene Mukutisatira Ife(mcp)

  24. Osamakhala ndi moyo ozikonda tose ndamalawi kupezanso ndkosiana nde ngat cithandizo capezeka cbwino kukhomelerana, munabadwabwanj kod? Moyo umeneo nkana maiko ena akukanika kutthandza, zkuambira pakhomo pompano

  25. Kodi wa MCP woonda chonchi komanso wooneka odwalikayu mwati ndi ndani?Za ziiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii…Kwacha!Kwacha!Za ziiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii…chikhalilenicho nthawi ili 2 koloko dzuwa lili ng’e!MCP idzawina akadzasiya za kwacha zawozo komanso tambala wawo akadzakhala woyera.MCP inatimvesa kuwawa kwambili.

  26. This misguided and marauding dpp thiefs will never abolish this programe ndikumene akubako zambiri kumeneku, ndiye mwati atseke mgodi eeeeh.

  27. Kutsitsa mtengo ndie mzelu zimenezo osati kuwamangira manyumba mukatsitsa aliese adzalimbikira kupeza kangachepe mkukagula koma zimenezo ziendera kudziwana kuchipani mpaka muzibale mwao more fire mcp

  28. Zowona Malata Subsidy Yithe Ngakhale Farm Subsidy Yithenso,chifukwa Pa Zaka 10 Boma Lingowononga Ndalama.Njala Yosatha.Anthu Womwewo ,yikafika Njala Amalandira Chakudya Cha Ulele.Izi Ziku Sonyeza Kuti Boma Likuwononga Feteleza , Chakudya Pa Banja Lilonse Pachaka

  29. Ndaona ichi ndi chibwana chamchombolende zimene likupanga boma la dpp ndimasewera akulu palibe chimene amalawi angapindule ndi ulamuliro uwu manyaka mathanyula apm mbava yaikulu pa malawi pano

    1. #steve ndi #evelyn mwaonetsa kt an2nu simugwira ntchito akamat kutbera akutanthauza amene amatidula msonkhofe osati inu …. Nde nkhaniyi mukanapanda kuyankha

    2. @mfune ndi chivo ndakunyadilani kwambri kt mwadziwa chimene ndikutanthaluza ine kodi alipo anthu ena adabadwa osavetsetsa ,ndaonela @evelyn ndi anzawo @steve ,simatama ine ndimapanga busines tikapita kokatenga katundu kuli mavat kaya akudziwa zimenezi akulimbana ndi ine ndani amene pano anganene kt zikuyenda bwino or mahule zikukhodza mafuta amene amagula amakhala ndi misonkho ndiye ndikudabwa @evelyn akunena za ine koma kuwona dres imene avala kaya tax saidziwa koma amadziwa kuwombela mmanja apm akamanama bodzi

  30. Power is derived from people, electorate or voters. If some people won election on promise of decent and affordable housing program let them run the program. If it fails people will vote them out. But if there is no money for the program, government will be forced to review the implementation process. They will have to go back to people and say, look guys, wait until we have money for that. This is simply about money. But housing is a very important for developing countries. Talk of poor like me. Those who are rich, oppulent and well to do may see the program useless. Remember UN sustainable development goals. Gender, climate change, fighting poverty, child mortality, shelter, decent clothes, food, basic education………. they are all very important and priorities as per UN goals.

  31. Chipani cha MCP ndi chopondereza zoonadi ndi chifukwa chakedi nthawi ya Kamuzu munthu ukamanga nyumba amakupanga interrogate. Asiyeni nawowonso amphawi apumeko kukadula udzu chaka ndi chaka. Ngakhale kuno ku RSA boma likumamangira anthu nyumba mwinanso za ku Malawi zo ndi zabwino.

  32. Nd nkha zaku malawi zimenezo ku mangolimbani zazi!! Osapanga maganizo achitukuko azanu anazitaya kare zomalimbana ndi nkhani zandale kodi ndinu amalawidi koma ndinu ntundu umodzidi?mcp ndintundu wanji wa anthu? Ife tatopa ndi nkhani zanu day to day tidzingomva nkhani zanu mwatinyasa kupusa kwanu nose amcp

  33. komadi ineso palibe chazelu ndikuchiona mmu chitukuko chimenechi pamudzi a2 awiri si tsakho limeneri .bwanj osangowapatsa fetereza kut akhala amoyo wathazi.chifukwa dziko limene a2 ake ndi a nthazi ndilimene limatukuka

  34. I agree with mr Amos Phiri good for nothing y am i saying so? Corruption is the system.Where can poor MALAWIANS get that addition money for u to buy food?kkkkk Malawi sadzathekanso.Oh! Lord we need u most in our country Malawi.

  35. Koma anthuwa a mcp ndi Lazaro wawoyo mitu yawo yikukoka? ndimayesa mu manifesto yawo pa nthawi ya compaign amati azathesa subsidy ya agricultureyo? ndiye panopa atalephera pa chisankho akutiso athese subsidy ya malata na cement kuti ndaramazo zipiteso kwa chimene amakanacho, kodi pali zeru pamenepa? nanga zonse zimenezi ndizoyambitsa ndi azawo azeru akumawa a Prof mutarika ndi DPP zopindulira mumalawi wokalamba,wovutika, wodwala,wolumara, chokolo,wamasiye etc ndiye ati sithesedwe, koma adakali kupenga kumeneku ndikuyamba chabe kwa misala moti usogoleri wa katakwe prof APM ndi umene ukuwasokoneza A MCP wa, anakakhara ena anakango thandizana ndi aboma kukweza zikoli, so let us incourage DPP to continue with all thr promises asave za agaru wopengawa ndi wolephera

  36. Amene akufuna kuti boma lisiye kupereka malata kaya cement yotsika mtengo kwao ndiolemela kale Lunguzi yo abambo anapanga kale madziko anali olemera kuno ku 25 kuli ma plot 3 pali manyumba akuluakulu. Asatitenga ife opusa iye akhale shasha. Ngati alibe chokamba ku parliament ankhala chete kumagona shaaaa!

    1. Iwe ndani anakuuza kuti zaulele sasamala@Evance. Vuto la enanu mudakulila mu town ndipo simuziwa kuti anthu kumuzi akukhala bwanji, ngakhale kamuzu ankamangila anthu osauka nyumba mwina Lunguziyo sakuziwa pakuti ndimwana. Ndiye zinazi mukamasusa muziyangana kuti anthu ena akukhala umoyo otani

    2. Kodi inu, nyumba zo zikufikira anthu angati? Tafusani-fusani or pa mudzi pakwanu mupeza kuti palibe uyo ndi mmodzi amene anamumangira nyumba yo, ngati alipo its either ndi member wachipani cha DPP, and chomwe ndikudabwa ine ndichakuti nkhani yomangira anthu nyumba yi idayamba ndi JB ndichipani chake cha People’s Party timati Mudzi Transformation, and anthu ambili mumamudzuzula with ths programe, even DPP was in front kukuzuzula zimenezi coz mumati munthu timuphunzise kugwira nsomba not kumpasa nsomba yaulele, nde pa campgn yawo a DPP anati adzasisa mtengo wamalata ndi cement nt kumangira anthu nyumba, nde panopa mfundo zanu zakukanikani and mukupitiliza programe ya JB yomwe mumkainyoza ija, pali mzeru pamenepo?

  37. Mnthu agone mnyumba yamalata bt osadya? No logical! If pipo hv prenty to eat they can sell & build houses on their own, wamva iwe?

    1. Iwe tiyen ndale tiyike apo,food is engeen of development.wen bingu was in power(first 5yrs) pipo were buildng houses on their own ndiye mmalo mot zonse ndalama ayike ku subsdy akulimbana ndi za ziiii. No logical @ all

    1. Lets work hard komaso omwe Ali ma town kumalimako ku mudzi, alipo anthu ambiri kumagofuna chakudya koma salima komwe. To Malawi producing country it has 2 start at household level

    1. mcp ili ndi mapolicy oyipa,okhomerera sadzapedza mpata wolamulira dziko amta ndi anthu ngati akuchitira nkhadza pologram siyawo nanga itakhala yawo paja kamuzu amkalesa amalawi kumanga nyumba zabwino kuopa kufanana naye foolish democracy tu iyi not one party system

  38. Ever since subsidized or free commodities have never benefitted all Malawians. Bakili had free farm inputs, Bingu had FISP, Joyce had Mudzi Transformation Trust and Ng’ombe zaulere and APM has Cement-malata….we were there.! I choose to disagree with MCP.

    1. Davie o u don’t know wat u are talking about how can u work hard without resources for the work. Can u work hard when your salaries are lower than you spend, before comment mukuganiza. Just stay quite if u don’t know anything.

    2. Yes we have 2 work hard, kumadikila kuti boma likupaseni chkudya kulemmbera kuzipezera chkudya chokwanira pa banja. Lets change our mindset

    3. Kkkk the funny thing ur still complaining mamvuto sadayambe lero man anthu akulemera akumanga zinyumba kugula magalimoto #watson

  39. Boma likanangotsitsa mtengo wazipangizo zonsezi kuti wina aliyense adzitha kufikira.Otherwise we are all malawians&Lets move forward plz plz plz plz.

  40. Chiyambi chabe ichi !! Zambiri zikubwera…..nthawi yolakalaka imfa ikufika pompano. Tidakalira mokweza chifukwa tili ndi nawo maso koma sitikuona, tilinawo makutu koma adankhontha sitikumva.
    Mateyu 24 6-8.
    Udakadikililabe kuti dziko lidzasintha from bad to better,,,,, stop kutaya nthawi yanu kumatukwana boma ndinthawi yakuuka kutulo ino, tizifa tili okonzeka.

  41. kodi mukulamula boma ndiinu a mcp?…..inu ngati mukugona nyumba zabwino zabwino azanu ovutika asagone nyumba zabwino…..kungokhuta kwanuko basi lero ndi boma lisiye cement and malata subsidy….chipani chama bolera

    1. Kugona mnyumba yamalata ndichan nanunso kuposa kudya? Koma Malawi anthuake sakuganiza,zinazozikanakhala bwino kut chuma chikuyenda bwino,ndibwino anthu azikhuta kayekenakoaka gone mnyumba yamala iiiii

    2. hahaha mutsamutsutse munthu mukuona ngati anthu nyumba zaudzu amakhaliramo kukondwa eti? Ndani safuna nyumba yamakono kapena kuti yabwino mukamakhala nyumba zabwino zabwino mukuona ngati nafenso amphawi sitimafuna eti muzilankhula bwino ngati mukudziwa za nyumba yaudzu mmene ikhalira chaka ndi chaka maintanance ndani safuna pabwino maganizo a kongeresiwo ndiopepera paja anadzolowera kupondereeza amalawi munthawi yawo nyumba yamalata inali sanjika basi ndie akufuna libwerere kale ndi nthawi ya democalacetu iyi not 1 party

  42. In true sense all the subsidy sakupindulira eni nthaka koma kagulu kochepa zomwe zikuchititsa kuti boma lidziononga ndalama zimbiri4 nothing&Zikungolemertsa anthu ndikumayendera galimoto zodula.

    1. Boma sikuononga ndalama ayi,koma likupeleka kwa eniake amalawi.inu ngati munazolowera kudulitsa makadi nthawi ya kamuzu izo ndizanu,MUSOVENGE.

  43. Salute Hon Julliana ‘Mwana Ma MAI’ Lunguzi cos sikwabwino kunkhala ndi nyumba yopambana koma opanda chakudya its bettet kunkhala nyumba yosalozeka koma uli ndi chakudya nthawi izakwana yoti tizachita bwino ndikukhalanso ndi nyumba zabwino chakudyanso chambiri not Akuti malata-cement subuside am on ur back Hon Lunguzi

  44. I agree with MCP zithu zafika on finishing line zoona mpaka odwala kumapephetsa zakudwa mumidzi kuthawa njala muzipatara. Bwana APM stop your campaign mapilisi a TB ndani angamwe asanadye.

    1. Mukamakamba zinazi muziganiziranso anthu omwe amagona nyumba za udzu kuti amavutika bwanji kuti udzu upedzeke. Ask me, nonsense!

  45. Very intellectual idea honourable Lunguzi. What this government is doing, it’s like it has been put in a bottle so that it cannot further liberty its thinking capacity.It is very pathetic to see people in vast areas,struggling their lives for food while the government is diverting alot of money to Malata Subsidy Programme. This is the extreme typical sign of failure. They just think as if everything is good. They don’t visit the rural areas where the duty of the government needs to be shown. This pains me really.

  46. In mature democracies gvt . takes note of such briliant ideas and go back to the drawing board and adjust their projects. But in Malawi such is taken as nonsense because only gvt. has the best ideas. But surprisingly if on the next day the same idea is brought by the donors and mind you these are young boys and girls from IMF and World Bank the whole government machinery trembles. What a shame. Malawi needs to do business unusual otherwise we are doomed with this mindset. Bravo Juliana for the courage. Look to God for more wisdom.

  47. Nkhaniyi ndiyomveka ndithu koma ndimene limatangwanitsira dzinja nyumba ikakhala yosalongosoka umachita kusowa mpoika feteleza komanso zokolorazo mwina kumaonongeka kumene, mmalo mosamalika kuti zizagwire ntchito yake bwino.

  48. Kukhala Mu Descent House Bt No Food,dat Make No Sense,,cement Subsidy 4 Wat!!

  49. Hungry people sleeping in decent houses kkkk! There is no need to introduce other programmes when we are failing miserably to implement already existing ones. This is madness at its best.

  50. Hahaha mmesa inu a Congress mumati a Malawi amagona mnyumba zosathonya? Juliana! Juliana!Juliana! Ng’oma yolira kwambiri sichedwatu kung’ambika. You think by making noise in the parliament you will gain anything? Talk to the government on one to one then you will get what you want. Politics of confrontation has never worked in Malawi. Ukhalira kuwuwa choncho akufinya suzamvekanso. Fusa anzako ali kuti lero? Kodi suwona wolemekezeka ali kumenekowo akhala 15 years the likes of Njobvu yalema but they don’t talk trush like you do. Uzadabwatu tsiku lina zitakuonekera. Politics is a dirty game! Ask the spirit of your late father to guide you.

    1. Man osamuwopyeza Juliana a Malawi opusa ngati inu sindinakuwoneni mukufuna munthu asalankhule chowona jst bcoz ndi gvt kkkkkkkkkkkkkk……. I support Juliana’s idea and its true.

  51. Why was the program approved by the parliament in the first place? Where were all these brilliant ideas that time??

  52. Munthu oganiza sangagone mu nyumba ya malata ali ndi njala. We Malawians depend on Agriculture, government should think twice on that.

  53. THAT MAKE SENSE HON LUNGUZI KEEP IT UP TO WAKE UP THE HOUSE TO SORT YOUR IDEA

Comments are closed.