
Karonga United yakaniza Wanderers ndalama za Airtel Top 8
Timu ya Karonga United yamenya ndi kutulutsa timu ya Mighty Wanderers mu masewelo a quarter final yachiwiri ya chikho cha Airtel Top 8 omwe anachitikira pa bwalo la Karonga. Wanderers inayamba masewelowa ili ndi chigoli… ...