Bambo wapha mkazi wake pomumenya m’mutu ndi mwala
Bambo wa zaka 32 yemwe dzina lake ndi Dickson Kachikuni ali mu chitokosi cha a polisi ya pa Nkhunga ku Nkhotakota kamba kowaganizira kuti apha mkazi wawo Leah Ngoma wa zaka 21 pomumenya ndi mwala… ...