Inu azibambo a COSOMA mukundisala bwanji? Wafunsa Jetu
Jetu walira chokweza pamene bungwe la Copyright Association of Malawi (COSOMA) silidamupatseko yachipuputa misonzi pamene bungweli lapereka makobidi kwa oyimba osiyanasiyana mdziko muno ndipo iye akufunsa kuti a COSOMA akumusala bwanji? Jetu wayankhula izi kudzera… ...