Mnyamata wadzimangilira kamba kodzudzulidwa
Mnyamata wa zaka 18 zakubadwa yemwe anali mu fomu 1 wafa atadzinjatilira pa mtengo ku Mponela m'boma la Dowa kamba kakuti amadzudzulidwa pakhalidwe lake lochita maubwezi ndi atsikana osiyanasiyana. Nkhani yonse ikuti mnyamatayu yemwe dzina… ...