Mayi athawa atapha mamuna wake pomukoka katundu
Mayi wina yemwe dzina lake silikudziwika Boma la Zomba wathawa atapha mamuna wake pomukoka malo obisika. Wofalitsa nkhani za apolisi Boma la Zomba, Sub Inspector Patricia Sipiliano watsimikidza zankhaniyi poyankhula ndi Malawi24. Sub Inspector Sipiliano… ...