Titulitsireni ng’anga yathu, amang’ara anthu ku Mzimba
Khamu la anthu ochokera m'mudzi wa Mujinge mfumu yayikulu M'mbelwa m'boma la Mzimba lakhamukira ku polisi ya Mzimba komwe akufuna kuti a polisi atulutse sing'anga wawo yemwe akuti amachotsa ufuti mwa anthu m'mudzimo. Sing'angayo yemwe… ...