Saulos Chilima

BBC Itipepese – aMalawi

Nyumba yosindikiza nkhani ya m’dziko la United Kingdom ya British Broadcasting Company (BBC), yawonjezera mkwiyo komaso chisoni cha a Malawi pomwe yanena kuti malemu Saulos Chilima anazengedwapo milandu ya katangale m'boma.   Lachiwiri, BBC Africa yatulutsa… ...