Zipatala zambiri mulibe mankhwala – Phungu wadandaula
Phungu wa dera la kummawa kwa boma la Machinga a Esther Jolobala wadandaula kamba ka vuto lakusowa kwa mankhwala mzipatala lomwe lakula kwambiri m'dziko muno. Phunguyi anadandaula za izi dzulo ku nyumba ya malamulo. Jolobala… ...