Njala yavuta ku Machinga, azibambo akuthawa mabanja awo
Pomwe njala yafika posautsa m'boma la Machinga, Mfumu Yayikulu Nchinguza ya m'bomali yanena kuti pa tsiku ikulandila madando osachepera asanu ndi awiri okhudza abambo omwe akuthawa mabanja awo kuthawira mdziko la Mozambique, chifukwa cha njala… ...