Zikhulupiriro zikubwezeretsa m’buyo ntchito yolimbana ndi nthenda ya Khate – Thindwa
Ogwira ntchito pa Chipatala chachikulu cha Rumphi ati ntchito yothana ndi nthenda ya Khate ikuyenda pang'onopang'ono m'bomali chifukwa cha zikhulupiriro zomwe anthu alinazo zomwe zikulepheretsa a chipatala kufikira anthu ochuluka. Poyankhurana ndi nyumba yolemba nkhani… ...