Ndife wokonzeka kuchititsa zisankho – MEC
Bungwe lowona za zisankho la Malaŵi Electoral Commission (MEC) lanenetsa kuti kuyenda bwino kwa zisankho zapatatu mu 2025 kudalira kuti anthu amvetse bwino ndondomeko ya kayendetsedwe kazisankhozi. M'modzi mwa makomishonala a bungweli, Dr Anthony Mukumbwa,… ...