“Zeze ndili naye pulani” – Jetu achenjeza Cash Madam
Eeyo! Tiyeni! Tiyeni! Tiyeni: ngakhale kuti “K100 miliyoni sindalama”, koma Dorothy Shonga akuyenera kuchengetera bwenzi lake Zeze Kingston ngati dzira kamba koti Jetu waopseza kutsomphora chikhwayacho. Ndi mkazi uti samafuna mamuna otulutsa K500, 000 yandiwo… ...