Mkulu amene analonjeza zokhululukila okuba nkhuku atha kukakhala ku ndende
Ukayenda siya phazi, mulomo umatsata. Mawu awa atha kukhala ndi amene akulingalira a Saulos Chilima pamene atoledwa ndi a polisi poganizilidwa kuti anachita za katangale ndi a Zunneth Sattar. Bungwe lothetsa ziphuphu la ACB, lamanga… ...