Kutchuka kunandisandutsa mbiyang’ambe – atero Martse
Katswiri oyimba nyimbo za chitawuni Martin Nkhata amene amadziwika ndi dzina lodyera loti Martse wabwera poyera nkunena kuti kutchuka kunamusandutsa mbiyang'ambe. Martse waulura izi dzulo kudzera pa tsamba lake la Facebook ndipo iyeyo walangiza anthu… ...