Aiopela kutali. Olo asanaugunde mpira ndi komwe azitaya. Za CAF zija sanali maloto koma zilubwe. Pano mukamuona mzanu wa nyerere, musayambitse ya CAF mudana, ingokambani ya Super League.
Masiku atangotsala pang’ono kuti nyerere zikaponde ku DRC mu chikho cha CAF, izo zalembela FAM kuti sizipita. Ati zawakulila.
Malipoti ati mlembi wamkulu wa nyerere a Mike Butao alembela bungwe la FAM kuti lidziwitse a CAF kuti nyerere zalephera basi kupita ku CAF.
Mavuto a zachuma ndiwo anthu akuti athetsa maloto a nyerere. Masiku apitawa timuyi inayamba kupemphetsa koma zikuoneka ngati sizinaphule kanthu.
Lero mmawa kunamveka kuti othandiza timuyi a Be Forward analangiza akulu akulu a timuyi kuti za CAF azisiye, asalimbane ndi mtunda opanda madzi.
Pamwamba pake zinamveka kuti ku nyerere kumene kunali chipwilikiti pamene osewela ananena kuti iwo sapitiliza zokonzekela za CAF.
Pofika masana zinatsimikizika kuti nyerere zazitaya za CAF.
A CAF akuyenela kupeleka chilango kwa nyerere.
Kkkkkkkkkkkkkkkkk
NYERERE WOYEEEE
Kusowa zolemba makape inu tikuonerani
Kikikiki neba, neba, neba umati utani, kikikiki wachepa nazo
Zolemba za mtolankhani izi?
Remove this ,now it doesn’t hold water because the opposite is true
Yathu Noma tipange ma league amom’muno kaye . we have indeed withdraw pali chifukwa chomveka
Mumatikwanazo ife a ndalama panya panu mumaona ngati caf ndiyamasewera
Kkkkkkkkkk kma neba iwe pakibetu chomwe ungakwanise mwina kuvina vimbuza kapena kkkkkkkk
Eeeeer Nanthambweeee
hahaha KAMIKODZO / NKHUMBA EFUSI HAHAHA ZILIKO
KKKKKKK Ndalama wathera kulipira kwa Ayaya!
Kkkkkkkkk Usaii/ Ukhwirii, Chichi? Nyerere u talk toooooooooo much..!
Good decision nomards but poor and unskillful way of writting. U are not a journalist!
Noma 4 ever
Zako zimenezo kkkkkkkkkk
Iweeeeeee!!!! Usathawee!!kkkkkk
POOR PLANNING AND MANAGEMENT, life tinamenya opanda sponsor vuto mumaganiza mwau nkhumba
CHOMapitila kubalaka kumakapanga ma donations pomwe muli ndi ntchito yaikulu kusogolo ndi chani zandinyasa
Impossible
AAAA APA NEBA NDACHITA MANYAZI KONDI ANAMENYA CAF OPANDA SPORTS IFE KUMATIKANIKA
Zomwe ndaonazi! Timati tiona chopanga koma anakapempha President
Kkkkkkkkkkk atimenyad
nzosadabwisa tonse timadziwa kuti akapuku amenewa sangakwanitse
Eeeeeee Koma Ndili Kuva Chisoni Ndi A Noma Tindalama Tose Ta Ku Superleague Alipila Ku CUF.
MATAMA NEBA ! SUDZATHEKA
Ana Achepa Caf Sizocheza Imafunika Sposa Yachuma Ost Yaumakaniko Yokoza Magalimoto Akufa Kkkkkkkkkkk Nbb Woyeeeeeeee Zamanyazi Ku Kapado Kapena Kut Kakozo Fc
Mangochi select yawazunguza mutu Kkkkkkkk
Mmmmm….
Zinawoneka!,nanga mapreparations angapange ndi mangochi select!,komanso kupanga draw chonsecho penalty!,ayi apo ndiye mwawonetsa kulimba mtima kubwera poyera kuti sitikwanitsa!,ali ena akanapita nkukarandirako 10 kwa zilo!,ayi takunyadirani!”ZONSE ZIMAYAMBA NDI MANOMA “,apanso mwatiyambira kulephera mutalembetsa!
neba
Ali bhoo Nebayu eeee izo ndizoona osayambisa nkhani ya CAF atimenya nawo kkkkkkkkk
Ndizakhalabe wa nyerere
Eee! koma ndkulimba kwapadera2
Zako zimenezo kkkkkkkkk
Kkkkk I Like This Team Chifukwa Nthawi Zonse Chilichonse Amakhala Oyambirira Kuchita No Wonder I Hate It!!
oyamba kuithawatu?
Eya The First Team In History Of Teams In Malawi To Surrender Caf Competition.
haahaahaa??
N
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk……maloto okanika
kumenya caf mkulimba mtima
Kodi page yanuyi ndiyoti mumati anthu angakukhulupilireni chichewa chake chimenechi no journalistic way of writing skills…feel sorry 4 nomads but stil a #nyerere.