Bwalo lalikulu la Milandu tsopano lamasula khonsolo ya mzinda wa Blantyre kuti ndi yololedwa kugwetsa nyumba zonse zomwe zamangidwa mu phiri.
Khonsolo ya mu mzinda wa Blantyre inauza anthu onse omanga nyumba mu phiri kuti asamuke. Koma anthu aja m’malo mosamuka anapita ku Khoti kukatenga chiletso.
Kwa zaka zisanu, a khonsolo akhala asakuchita kanthu ati kamba ka chiletsocho. Koma tsopano chiletso chija chachotsedwa.
Ndipo tsopano a khonsolo apeleka chenjezo kwa anthu amene akukhala mu mapiri a Soche, Ndirande kudzanso Mpingwe kuti asamuke ndi kugwetsa nyumba zawo.
“Ali ndi masiku 60 anthu amenewa, miyezi iwiri yeniyeni. Ikatha tikubwela tokha ndi galimoto zathu kuzasalaza,” anatelo mneneri wa Khonsolo a Anthony Kasunda.
A Kasunda ananenanso kuti a khonsolo apeleka malo kwa anthu 65 amene asamuke.
Iwo anati pamene nkhaniyi imayamba, anali ma banja 65 okha amene amakhala ku phiri.
“Tsopano alipo 300, koma enawo anabwela akudziwa kuti malowa ndi osaloledwa kukhala,” iwo anatelo.
Zagumulidwa kangati nyumbs zimenezi?
Nde nyumba zithatu btz popeza nyumba zambili zili mmapili pafupifupi location ina iliyonse
Kkkkkkkkkk
amkot alozesa azawo ogumula enawa ndi amfit
Kubwezelesa chitukuko mmbuyo bwanji munthu wamanga nyumba yake inu nde mugumuleso? Tamayendani a Malawi muziona mmayiko anzathu nyumba dzao kuti zili kuti pamwamba penipeni pa phili boma ndikwasatilaso komweko ndinseu opambana kwambili koma kumalawi iiiiiii mmmmh
Kazisasuleni bc azaona ngati boma ndilopweka
kodi boma limangoonelela mmene nyumba zimamangidwa,nanga malo amapereka ndani? osamalowetsa ndale. ndindalamatu kumanga nyumba.
Agumulidwe basi
Zaulendo uno
Malo ake omwewa a Chauta Namalengawa mukuti ndi a inu a boma?Ayi zikomo mukhale ndi moyo opanda malire inu ndi anzeru anuwo oweruza mosaopa Mulungunu.
Komaso boma apeleka warning kangati amwenyeso mugwetse apo ayi timenyanq
Amenewo achoke sioyamba kugumulilidwa nyumba mukafunse anzanu ku Bangwe.
MCP 2019 bomaaaaa!!!
Khothi lalakwa pamenepa anganize bwin
Njanja Panja Munalandisa Akanakamanga Pompo
Anthu onse okhuzidwa apite akatenge chileso chogumula nyumba zawo ku court konko mpaka nyengo yamvula ithe kuti azathe kupeza malo kwina ndikumanga nyumba zawo.
Power to people balibenso zogumula.dziko.and anthu
Kugwesa nyumba ndi mlanďuso
Poti mavoti ndi next year.
EEEEE KODI KANI
DPP mukubetsa ma voti apa izi mukanadikira zisankho zidutse kaye. Otherwise I don’t expect munthu woti mwamupanga chipongwe chimenecho will vote 4u.
Ndiochepa ma vote ake koma chilengedwe tichisamale
That’s y Malawi samatukuka fukwa chopembeza vote..agumule …basi…
Imagine it was u
aaah nde tilephere kuteteza chilingedwe coz ov ma vote !!?????
Chala mwamba
Ufititu umenewo a jaji, mene ankamanga simunkaona?
Mumati Anthu Aku Mj Ndiovuta Wandale Panga Zamalo Atea Onse Achoke Timangemo Ife Iya Tilowelekuti Dziko Onkhala Wanthu
musaiwalenso ma building aamwenye omwe munaika ma red star aja mpaka piano kulizii koma za amalawi osauka sichangu chake
This is Unfair!
-Kod phiriro ali gumula pomanga nyumbazo? Koma akanakhala azungu nde kuchita kuwapasa kut mpakana mmmmmmm kuwa mmm”ndayiwala”
Pangani ku Sochi komwe ko mukafika ndix tidziwa boh boh
A malawi tiyeni tizimvera malamulo akati apa osamanga kanthu tizimva taonani mwaononga ndalama kumanga nyumba zimene zitagwetsedwe chifukwa chosamvera malamulo makani opanda nawo phindu ena atengerapo phunziro. Amalawi umbuli uzatithere liti?
nanga kunyambadwe ndikusanjika agumulaso mesa mwati mmphiri kkk?
Yoo ku ndilande ko sorry
Koma bola akanakhala azungu omwe amangawo??
anakati anzungu amakonda cool place
anakati anzungu amakonda cool place
Wina angoyelekeza ku gumulayanga akhala ndi:diso limozi,mkono umozi,mwendo umozi.
Khothi lalakwa pena silinalakwe kumanga zinthu malo osaloledwa ndi mulandu khothi lalakwa pouza kuti agwetse iwowo mmene anthu amamanga amangoyang’anila chifukwa chani ngati agwetse anthu alandile chipukuta misozi
iwo samawona malo abwino oti atha kugula
Anawapatsa malo ndani? Ngati panalibe dongosolo lopezela malo asamuke basi. Komabe boma liwathandizeko ndi kokayambila kwina. Phiri ngati la Soche, zoonadi linali phiri lokongola koopsya mu zaka za mma 90s koma lero ngati bodza.
Serious akuyeneradi kuwachosa mopanda kuwanyengelera, tiliso munyengo ya mvure nde tiyeni tizinganiza tokha zoteteza moyo komanso katundu wathu, mupite pa Phiri la Soche mukaone mmene anthu amangira timanyumba pamenepo yet just some 3 years back we lost a lot of people in soche east ndimazi amphavu omwe amaseseleka kuchoka mu phiri muja, ndipo fans yomwe imakhala mu phiri muja mmmm inafa yambiri and ena anavulara modesa nkhawa, lero nde mukubwerelamoso? Ngozi ikachitikaso then muzipanga blame boma kuti silinakuthandizeni? Zinazi mumaziyamba dala cholinga zikakugwerani muzilandira zinthu zaulele kuchoka ku boma, mipingo komanso kumabungwe, I think this time mukapanga makani then akakusiyani wina aliyese asazakuthandizeniso bcoz mumapanga dala!
Apatseni masiku kuti akonzekele ,akafufuze pokakhala,chifukwa alindi ufulu ,monga mmalawi.
Iwe Waku khoti mboliaya yako
Ndi wa mkazitu kkkkkkk
kkkkkk awona kuti apanga bwanji
Kkkk kkkk koma yeah
Zausilu eti nde muganiza kut anthu akakhala kut?
Wooh
Changu
Apatseni anthu malo oti akakhala Palibe kanthu kuti e nawo anabwera dongosololo lilipo kale mukawachotsa moteromo Akakhala kuti anthuwo Ali ndi ana?
Apatse Mmene ankapita mmenemo sankaziwa mmoletsedwa,?
Mukati samaziwa kt molesedwa kd malowo boma likupanga nawo chani chitukuko ayi kma kulimbana ndi dzika basi kuzisowesa mtendele
Ankadziwa komano chinawapanga kuti apezeke mmalomo ndichani? ( amalawi tiyeni tiphunzire kukhululuka ndikulorena wina ndizake mulungu azatikhululukira bwanji ngati tikanika kukhululukirana tokhatokha
Ngati dziko sitingapitilire kumapanga zinthu mosatsata malamulo. Manyumba agumulidwe
Malamuro akuyenerah kutsatidwa kumene, komano Vuto ili ndalikulu munthu a muchotse opanda kukamusiya penapake akakhala kuti
Akakhala Kuti Masikuano Ungapeze Malo Chisawawa Ngati Akukaniza Mantchile Amamakolo Anthu Omwe Bwelani Muzaone Mene Anthu Akuvutikilakusowa Pokhala Pamene Wina Wazala Bluegum 10 Klm
Wakumudzi basi asaaa
Tkamanga Pa Nyanja Muona
Nde zavutatu
Zgwetsedwed basi cmalo omanga ma den …ndimoletsedwa
Kma Nde Ma Mansion Onse Aja Basi Wautali
Timvenso kuti anthu afa angati. coz mnkhutukumve sizisamuka.
koma inu ndie kt akufuna kuikapo chian?pavutad apa
eeeesh pavuta apa
apandiye ationonga palibe kuchitila mwina ndikusamuka.
Achotsen, Km Mwanena Kt Pachiyambi Analipo Anthu 65 And Pan Alipo 300- Ndiye #Fuso, Mkumat: Kd Akhosolowo Awapezera Malo Okwanira Anthu 65 Kapena 300- Monga Mmene Aliri Panopa, Pls Gv Answer,
Athamngitseni basi anthu anji osasamala chilengedwe? Kodi mmene anamanga ku phiri amati anyani, apusi ndi nkhwere zikakhala kuti?