Pandemonium rocked in Mangochi when a new baby spoke to request for a porridge.
According to reports published by one of the local radios on its Facebook, a baby born last night asked his mother to prepare him prepare so he could eat leaving villagers in shock.
“TA Makanjira whose area boarders the Mozambique place where this is alleged to have happened says he also instructed his subjects to abide by the instructions” said ZBS on its post.
According to the report by the media house, the baby died hours later.
Mmmmmmmmm ndiye ali ndimano kale
Kodi olemba nkhani mumangolemba zakumva kapena mumawona chimene chachitikacho?
Basi mukango kumva inuyo nthawi yomweyo mwafalisa ndicho chamba chimenechi poti kuli technology kale kulibe technology timazikhalila pheee..
Koma panopa lokha boza fokofo.
Mwachoka pa a Namapopa mwabwela ndi ya Mwana phala, Izi zimaveka M’dziko limene anthu ambiri ali paulova ndi umphawi,
KKKKKK Kuyankhula chiyawo zosekesatu izi.
Zabodza izi… where is the baby.? Don’t tell me it’s dead to force me believe this mythical story.
WALOSELA NJALA YA 2018 ameneyu
Tili mmasiku omalizadi! dzulo mpomwe ndinawerenga nkhaniyi! zodabwitsa nzoti kuno ku Tanzania mwananso wabadwa ku Mtwaka wanena kut aphike phala la ufa wa kondowole (ufa wa chinangwa) mudzi wonse umwe akapanda kutero kubwera mvula yomwe iwononga zinthu!
Mapeto adziko
So, was it given what it aske4?
Basi muli njenje ndizimenezo?mmalo monjenjemera ndi mau a Mulungu. zamafano basi kkkkk.
Mulungu Atithandize
Malawi 24 why reporting baseless reports?? The story is fictitious. It cant happen in the real world. Plz pple, dont panic
Ine Ndnakuuzan Awa Ndi Asatanic,Inu Nkumakana.Ndye Siizi? Mudzakhluplra Lt Amalaw? Ngat Munth Akmakhala Nd Miracle Money,Inu Mwat Miracle Babies Asakhaleko?
What kind of language ????
end of the days
A lie? Days are still many…
mmmmmm so strange
Ngati anali ndi njala asayakhule..?
Achalume mnjomba patauni kkk
eish!! very strange
wonders shall never end..
Ziwanda
Mwana wanga weni-weni wakumwetsani phala kkkkkkk or ukadakhala mkodzo mukadamwa
Mwayambano kupeka nkhani kufuna coverage ..shame
Sizina ayi kumalawi kwachuluka kuba satanic ndiye mulungu wakwiya nazo
Ine lero sindkomenta km ndzingowelenga nao makoment anuo kkkkkkk
Kuno ku mchinji tamwa phala mmamawa lero lopanda sugar ndi mchere ati wanena ndi mwana ameneyo. Amati osamwa akufa.
??????? really?
Makolo ake sakamudyesa Ali ndimimba yake bambo anali ankhanza asanabadwe mwanayo izizokuchika kumalawi konko Ku mzimba amai wina wabeleka Ana 4 nthawi imodzi Ku mchinjinso Ana 4
Za phalazotu amakamba zoti adye anthu apakwawopo osati anthu onxe
Izi ndizamasiku osiliza kulinso nkhani ina yodabwitsa ngati imeneyi. Akuti ku sobi kwatuluka mzimai ndipo wayenda panyanja amalawi24 tafufuzani mutiuze zoona.
Kkkkkkkkk Muzimwa Phalalo,mukasanduka Mwatofuna,
Malawi24 be serous plz
Aaaa koma angowonjezera anthu zimenezi. Pajatu inakula ndi tadzawonani, mbuto yakalulu
masiku otsiliza so kofunika kusamala
Phalaro lachani soya mugayiwa kapena likhuni phala
Kkkkkkkkk mwana madyela ameneyo hahahahaha kungomva kut wabadwa mu january ali ndidyeletu
Nde analankhula mchiyao? Kkkkk angaseketsetu hehehe
Fake news
Mwana Wamzeru,waposa Aliyese
Malaulo / malodza amenewo ine ndilibe puloblem
Bodza
Pa ZBS anenanso nkhan zamasana ena tamvera
Ana osula awa achina kadonthi….tsoka amakewo heeee ine sizikundikhudza nawo
kkkkk soka ndani?
Amai abeleka nkhanda limenelo…kkkkkk
Ok. Usamale mayankhulidwe ako, next uzakhala uli iwe utachita zodabwitsa pa dziko lapansi.
so confusing. some are saying it is from Mozambique .which is which?
Mangochi Makanjira
Makanjira but baby from Mozambique side
So, is that Malawi?
Anthu okhala m’malire amangosiyana mayiko koma zochita zimakhala zimodzi’ monga kukwatilana ndizina so zitha kutheka,
Ku mangochi ndi kwa usilu
KOMAKWANU NDE SIKWAUSILU GALU IWE?
Wa utsilu ndweo kape
Makape osaphuzila koma kunyela mmadzi basi
Iwe sukulu yake it shupit zako
Mesa paja ukati waphuzila ndiye kuti wapita ku Joni?
Shaaaaaa
zammasiku otsiliza
Zina Ukamva kambangamwalaaa
kkkkkkk is dis srias isue?
Wangobadwa ndinjala?
Chilala too much kwathu kuno
Be serious
This is true
I suppose its connected to magic
This is true. Iheard it from other sources.
zachitikadi kodi?
Usakaike, am in Liwonde koma eeeh anthu kunali kumwa phala lopanda mchere mmawawu uthenga utafika
kkkkkkkkkkkkk koma yaa!!
Amene samwa ati zikhala bwanj?kkkkkkk koma zina
Ati kukubwera mphepo ya matenda ndiye wosamwa phala akufa
nde anthu busy kufalisa usiku wa pa 9 january kuti anthu adzuje aphike phala nde adzimwera mzipande nde eee
Msamatinamizepo Apa
usakaikire
Ok,ndakhulupilila
Wamva udyo admin
nde anthu busy kufalisa usiku wa pa 9 january kuti anthu adzuje aphike phala nde adzimwera mzipande nde eee
Kkkkkk wati chiani???
Zosangalatsa mbiri imayenda motelomo
Abale kodi nkhani imeneyi nd yowona kapena nd ya blind,porridge lopanda mchere chifukwa chani ati???
Ndi yoona man
Maloza awa