The ruling Democratic Progressive Party (DPP) has claimed that the party will win the general elections in 2019 saying those who think DPP will lose are dreaming like a barren woman.
DPP’s Secretary General Greselder wa Jeffrey disclosed that the five year term that the party has had is for developmental foundation.
Wa Jeffrey added that the ruling DPP will defeat opposition parties in Malawi with votes in 2019 to have a second five year rule.
“Kuluza? maloto achumba bwa, boma sitilikutuluka, ndipo sitikutekeseka (DPP losing? That’s a dream of a barren woman, the party is to rule again and we are not afraid),” said wa Jeffrey.
She further urged Malawians to vote for DPP during the forthcoming tripartite elections next year.
“A Malawi okuona kuti zinthu zikuyenda, omwe akudandaula ndi a opposition chifukwa cha nsanje, akufuna mpandowu (Malawians know that all is well, opposition parties are the ones complaining because of jealousy),” she added.
Meanwhile, the DPP has disclosed that it is to hold a convention to elect its presidential candidate for the 2019 elections.
President Peter Mutharika who says he will seek reelection in 2019 is expected to stand on the party’s ticket.
DPP kudzalamulaso?ndakaika
Aaaa Ine Ndikuona Tsogolo Loluza DPP Dziko La Mw Ndikukhala Lanjala Kwa Zaka 5 Koma Kulimagetsi Ovuta Kuyakanso
Hahaahaa!Dpp is still having dreams of winning 2019 election aaa!thats crossing the bridge before reach it
linda madzi apite ndiye uziti ndadala.
U floosh woman do u think dat de malawian are stil driming about ur crazy profesor?4get abt dat gangstr wil win 2019.
Nonse makape plus opposition ovota Ali pheeeeeeee vote sitipanga pa fb ndipo wina sadziwa m’komwe zoti kuli fb nde uli busy kulimbana apa zaziiiiiiii
Mzimayi walankhula mau onyazisa azimayi anzake amene akusowa ana pamene akufunisitsa atakhala ndi ana. Azimai mwawalandira bwanji mau achipongwe kuchokera kwa mai muzanu?
Mzimayi walankhula mau onyazisa azimayi anzake amene akusowa ana pamene akufunisitsa atakhala ndi ana. Azimai mwawalandira bwanji mau achipongwe kuchokera kwa mai muzanu?
Koma Phindu lake la Chipanicho ndichani or izawine…???Tatopa naye Peter Muthalika tu ife
Bola wina asadzipheso after elections like 2014
DPP ilibe mbili yoluza mavoti mundiuza kuti ndi chipani chiti chimaluza mavoti every general election
Mai ndinu opusa do u think we are happy ndi Dpp? chaponda anaba koma ali ku? achina Namkumwa milaandu yao ija anamangidwa? 72hrs blackouts? Blood sukers? apa tungodikira nthawi! No one will vote for. Dpp and its thugs mai! MCP ndie Boma likubwela!
I am told she is form two drop out…beauty is her main qualification to her position.what a foul mouth.
Dpp is NOT winning come 2019. Whether you steal or what, but you guys should know 2019 is another we are bringing a change.
Through rigging
Boma iloooooooo!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!! We’re under professor’s readership guys the major one
Ife ovota tikuona masiku kuchedwa pamene inu olamula mukuona masiku kufulumila kaya muziona.
Winning thru real votes or kubera???
In other ways she is saying that the prophecy of the bible will be witnessed when DDP loses?.
5-1 on my mind. Never underestimate the mind of a Malawian voter or you will be in for a big shocker.
No idea
Wait , u are going to say it again in 2019, we are tired of DPP, our mighty party MCP get prepared.
KKKKKKK phungu wanga olephera kumanga mlatho osatha ndi mwezi omwe waphwasuka my foot
Dpp is cused ndithu,even the dead can never vote for dpp
Munthu Wa Chuma Kumulalikira Kt Adzafa, Eeee! Mutha Kudana Naye. The Same Applies To Dpp, Kuwauza Zoluza 2019, Sangakuvomelezeni. Kma Akuluza Ndithu, Cme 2019.
Ine olo atandipopera doom mkamwa, at my Youthful age sindingovotere nkhalamba ya zaka 81regardless any political affiliation. Izapanga chani chopindulira moyo wa achinyamatafe? Maganizo opepera ngati awa ndi omwe awononga Zimbabwe mma 2000. Ma fresh brain atha Ku DPP ko?? ZOMBWABWANA BASI!!!
Mpaka 81 kumalimbikira kuyima u president? ndiye kuti Muluzi, Malewez,i John Tembo, Goodall Gondwe nawoso atha kuyima?
This woman has a foul and stinking mouth,she he thinks she is the only one who will vote,and she has forgotten that’s how exactly she was saying during the by elections period and alas!her might party lost miserably,and ndi you are repeating the same words!we shall meet again on the battle field next year.And u will regret wat you are saying now.
When ever this woman speaks, its always nonsense and rubbish that she speaks.
You fall is near
Suck ur ass if u think DPP wi win
Michael Ussi aka Manganya akusiya ntchito ku ADRA ndipo akufuna kuyamba ndale.
Iye watsanzika kale mabwana Ake.
Ussi wapangitsa kale print ma t-shirts ndi zipewa komanso nsaru.
Man mumavela zbs inu, wodyazake alibe mulandu,
so does this fool mean barren women are useless? Malawi work up
Moya Redson Wa Anagama Sikelo iwoneni moya DPp iyooo pasongolo ndiyomweya basi paka 2020
Kodi guys magets ayaka??
Afikapo phaka pomafoza chochi
Mulungu awankudze
kikikikikik kumeneko
Since DPP has already started losing in byeletions then that barren woman now has at least produced something
Dpp yake iti. Vote yanga ikupita ku MCP
Truee….am gone
Thus for real Mamaaa!!!
Ma by elections paja munawinaxo….
Empty tin making a lot of noise, 5 – 1 in my mind.
kkkkkkkkkkkk for get about DPP winning ,Malawian are not dormant.
EEEE MAN OSAMATERO
Muzawina pokha pokha mukazabera
In 2019 a day after elections we will hear that a certain professor has collapsed after hearing that he is trailing a certain DR by over half a million votes. The professor will collapse bcoz he knows has looted alot. He stole with his brother and is still stealing now. He is shielding corrupt party officials bcoz they share the looted money.
Amwene palibe zobisa apa muzitchula dzina kuti peter muntharika wa dpp wazaka 81 kapena kuti nkhalamba
So u r wishing someone to die?! Shame on u, u need deliverance cos devil is using u
we will turn that barrenness into potence
Ineyo Plus Akazi Anga Azibale Anga Sitingavotele DPP Inu Ofunika Mupakile Mukakonzekenso Chifukwa 2019 Mukabela Kuipa Sure!!!
Ngati waJeffley akhalabe s.g.Ku DPP idzakhala disaster yoopsya 2019. DPP idzaluza koopsya kuja. hule silitha kuyankhula ili. Asayiwale kkuti pa 17/10/17 amayankhula chimodzo modzi koma zinatha bwaa? A Malawi atopa ndi chipani cha nyansi ichi.
Stupid useless woman who always trying to appease her boss mark my words MCP is going to celebrate after an emphatic victory
Who is going to vote. And if you know that you will win why busy sticking nose in opposition. Instead of putting development in action you are busy campaigning since into power. Mulungu simunthu ngati John ndi Mary. Unless they is something that you know and we don’t know. Don’t take Malawians as fools. I see these same people talking today after loosing they will blame one man and join the party which will win. Remember Mugabe was top of game ndinkhuku zokuntha kuntha and other came in and cook it.
All barren women in the Bible after praying they gave birth to powerful men of God.Samson and Samuel are good examples.In 2019 the barren woman will bear a great baby who will deliver Malawi from the bondage of poverty.
Sarah and Hannah were barren yet they dreamed kids. Read the story of Hannah in the book of Samuel or the story of Elizabeth and Zacheria. Keep mocking, Malawi will decide.
Samawelenga baibulo amenewo asiyeni
Achedwe ndikuwelenga bible ma porn videos aonela nthawi yanji?
Ino sinthawi ya baibulo
Bible lilibe nthawi
Malawi want change but not MCP. MCP is a regional party(Lilongwe party),muzazivotera nokha.
Ayenela kudzavota okhadi amenewa kut adzapitilize pa 5 → 1 and nthawi ija anavotaso okha anthuwa
But why make a reference to a barren woman? Is a barren woman not a woman? This is an insult from a rotten mouth once again. A barren person also carries a vote which Dpp badly want. Wise up Jef. This is 2018.
DPP will win…. Bet hundred dollars
SIzodabwitsa kumva zimezi coz dpp anthu sadxiwa chomwe a kulankhula
Nthawi yanu yatha.mwatizuza mokwanila
Mwat DPP kuzawinanso mwina koma kwaineyo ndakaikira kwabasi.
njala kulibe ku malawi palibenso ku votela chisilu siyan bwana mkubwa apitilize
DPP losing its like a dream of a barren woman?….remember, when people saw a barren woman in Sarah, God saw a Mother of many Nations. So you must think twice before speak!
Mwakonza bodza lantundu wanji mu manifesto anu adpp loti muwapusitse nalo amalawi kachikena???? Gileseda sindimadabwa nawe paja kwanu ndi ku nkhotakota komwe kunalimidwa chamba choncho umati ukasutasuta mkumawona ngati tonse timasutaso
Eti ngat akavota ekha
Kodi mayi uyu suja ananamiza peter kuti awina ma by-elections, tiwona pakuti nthawi yayandikira 2019
Asamayankhule Ngat Iye Ndi Mulungu!!
DPP moto kuti buuuuuuuu
MMAI YU AKUNENA ZOWONA DPP SIINGALUZE AI. IKUWINASO 2019. VUTO CHITINI CHOPANDA MADZI PHOKOSO. CHIPANI CHOGWETSA DPP NDIYE SINDIKUCHIWONA AI.
Koma Mzimai ameneyi Ali pa Banja?
Kudzikwata mchala mai uku
Koma mayi ameneyu ngwachibwana kwambiri, basi kumangoyankhula ngati walowa kale mmitima ya ovota…! Mmmmmh.
Out of 44 comments, only 3 r of de view kuti dpp izawina. Watch out!!!!!
even those who say mcp will win are bt and lilongwe and s Africa dwelling northerners
Facebook is the wrong platform to decide votes
Mr phozongo u will never stop to amaze, si inu mmati kumwera kulibe mcp nde mukutchula bwanji blantyre. Vomerezani kuti mcp in unstopable this time.
MCP unstoppable how and where?
Facebook votes.
Anthu omwe amavota ali pheee kumudzi za Facebook sizikuwakhuza
the opposite will be TRUE
Anthu awaa DPP!!!! atikwana ngati m’mene inatikwanila UDF from 1994 to 2004!!!!!!!
Poichotsa mcp inakukwanani pochotsa udf inakukwani, kuchotsa dpp ya late bingu inakukwanani. kuchotsa pp inakukwanani. ndiye mupange chanu chipani chomwe sichidzakukwaneni ngati chingawine.
Wayambaso Hule uyuuuu
Only if They knew the prayer of a barren woman
Wht was it?
Enanu mmalo monena comment yanu mukumati huleli chonde a Malawi tiyeni tilemekezane!!
Iwe analankhulapo zanzeru ameneyo?.kwake nkunyoza ndi chifukwa timamuti ndi hule mkazi wanzeru sangamalankhule ngati momwe amalankhulila ameneyo
Ndiye ndi uhulewo zikugwirizana bwanj?
I dont suprise with this, bcz we know how our africa is( faiing of ruling party are weakness of the party here in africa.
Ooh mukamanga mpumulo wabata wina??ukufuna kunena chani??.Ayi wanena bwino,utsogoleri waziko lino muziutenga choncho apo ayi MWANYERATU.Chodabwitsa munakamanga mpululo wabatawo koma kulephelanso kuwina pachitsankho.General election si by election tu.Palibe chipani chochosa Dpp pampandotu pokha pokha chitayambika china apo zingatheke kuchosa Dpp kapena mupange ufiti wanu munenawo wa mpululo wabatawo nanga sinu amene mumaziwa kutenga zinthu mwachidule apo bii muzaziona.
chipani sichichotsedwa pampando ndichipani china koma amalawi ndiwo amachotsa munthu paudindo wake ngati akulephera,
she is bluffing her master~~~~malawians aint blind nomore……
zomwe wayakhul zmai ameney akukhal ngat akavot yekh hule loyaluka ili mixiiiew
how will you feel if somebody call your mom prostitute. moron
zkugwilizan pat?
Paja muzavota nokha nde muzawinadi
Uzawina mobera momotu other wise ndamenyesa khwangwa pamwala ukuwona ngati amalawi ndi mwamunawako kuti wapanga uhule ukonkunena kuti tikambilane ndi banja amalawi mwawaliza kwakwana mwatiswera masukupamutu kuyambila bingu weniweni ukachita masewera tikamanga wina mpumulo wabata
Mwapanga kale misampha yobera eti? Koma mukunama Mulungu simunthu anthu akuvutika inu mukusangalala
Za chamba..
DPP ndi dilu ndipo ife tiwina
Was she not saying the same prior to the 5-1 crashing iin the by elections! She talks like this to save her post and bluff her master!
Ngati DPP ingazawinesa mzandidure mutu ndikuronjeza mai
Kuribe atazarande DPP enawo ndi akuba
MCP will continue from it stops 5-1
M’mayi wamisalayu akuona ngati kuti chisankho cha chaka cha mawa akavota okha anthu amdela lake lokha ku nkhota kota eti?
Yes they wanna win using the same ways. who do not know them that they are good in thieving than development?
U r taking Malawians as ur Children & servants isnt t? R u de spokes person of Malawians?
he z a spokesperson of we dpp’s
So she z supposed to say Dpp members not Malawians at Large
Eti eti ah, i can never vote for dpp even at gun point
Man, kulolera kufa mpakana chifukwa chosafuna kuvotera DPP,ee nde mukhonza kukhala mmalitiritu,… Mmmmmh.
Man, kulolera kufa mpakana chifukwa chosafuna kuvotera DPP,ee nde mukhonza kukhala mmalitiritu,… Mmmmmh.
DPP members r also Malawians don’t 4get plz
Malawians we are not DPP OR MCP members but some
MBAVA
Some and All are differe
Ndi mmamvetsetsa munthuyu ngwakwathu ndiponso xool mulibemo …
DPP YOMWEYOOOOOO
Mukukaika pati
Mayi Ameneyi Amagwa Khunyu..
Ndale Za Pamalawi Zidasintha Nkhanga Zawona. Ife Odalira Ulimi Mwatigwetsa Kokwana Ndimitengo Yanu Yotibera Mphechepeche Mwa Njobvu Sitingalole Tipitemo Kawiri Asiyeni Anzanu Anzeru Za Ku Mmawa Awongolere Mwina Nkusimba Mwayi.
Zowona DPP yatiwonesa zosawona
Mungozipusitsa amai ndale zalero sizadzana dziko linapenya pano muzakhimudwa
Izawina ndikubela but za normal ndakaika.. Malawians have suffered a lot with this DPP govt…. tikaonana mu 2019
Kaya adzabera koma adzawinabe( mudzapsa mtima zenizeni…
Kaya adzabera koma adzawinabe( mudzapsa mtima zenizeni…
vuto ukakhala olephera u blame everyone for ur fault but for sure this party will never lose
I dont think so…Mmmmmh.
Atibera Party
NAWoso apeze njira zot azabere asamangot atibera chaka chlchonse
2019 sikuzakhala kubera, tinakutulukirani njira zimene mmabera zonsezo zizatsekedwa. Mcp ya chakwera ndi ija ya Tembo ndi zosiyana kwambiri. Chakwera ali ndi team yochangamuka dpp inayesera kuti ibele pama byelections koma zinakanika zizakhalanso chimozimozi 2019 we will be very vigirante.
dpp dont rig elections but has a winning formula. it instills hope to local Malawi. assures people of food security. it promises development and implement what it says.it chooses nice words to speak Malawi. it avoids anger in its politbro ranks.it has mature leaders in its ranks which people from chitipa to nsanje who are trusted by the people. Malawians cant trust somebody who threw the bible down and start politics. impossible
But the same dpp has failed to fulfill its promises thats why it will be voted out. The only strategy dpp has is to rig elections nothing else. Strategy iliyonse akuipanga pano will lead them to lose. Streategy ya mcp nkuwauza anthu ma weaknesses a dpp like corruption, nepotism, kulephera etc. 2014 anthu anavotera dpp chifukwa ankaona ngati izipanga zija inkapanga dpp ya bingu koma ayi ndithu ndi chifukwa chake muzalunzeso. Anthu pano aseguka kumaso adziwa kuti peter mutharika ngolephera he talks alot but fulfills nothing.
Mufune musafune dpp bomaaaaa
dpp promised food security. it promised donor confidence and a return of donors on budget and development funding. it promised single digit inflation .it promised of long term plans like liwonde barrage overhall.it promised Malawians of our oneness thus national ID and inclusion of all people across Malawi in party and government positions.dpp cant fullfill mcp promises.no.it does what its manufesto says
chiyambileni kudzilamulila malawi, ndi dpp yokhayi imene yalephelelatu ndi ulamulilo wa apitala ndi
Kkkkk, koma na mcp imandimvetsa chisoni bwanji. masapoter wawo munthu akalowa dpp chimsinamu, kukwiya wagulidwa. munthu akalowa mkachipani kawoko ndiye kakakaka yakeyo. akadzaluza mudzaimvele atibela. iwowo anawina ti aphungu kaya tingati palibe aliyese wa dpp analunkhula zoti mcp mwatibela ai. koma aphungu amene aja adakakhala wa dpp mukanamva phokoso lakelo losaneneka. koma na 2019 ndiye muliladi mpweeee. itakugayani dpp.
DPP won’t win this coming tripatite election no matter how the tricks they may play… anthu adazindikira pano… mumodzi wa anthu omwe adazindikirawo ndineyo… i was voting for dpp in previous elections .. but now i cant vote for these clueless leaders who lack the will to develop Malawi koma busy kutibela ndi kudzilemeretsa okha
Mcp Ndi Moto 2019 Palibe Opikisana Nacho. Dpp Muli Mbava
Remember we are in a wonderful world just wait for it Mum
DPP yomweyo kuti wawawaaaa!
Fire! jeee wa jefuu
Fumbi ndiwe mwini. Am just waiting for that time! No more words.
sinanga muzavota nokhaa paja..
Kkkkk
100%+DPP Will win!,just wait!
Can’t agree more
yes DPP will win
In your dreams
lets sleep and see who will wake up dreaming