Kwatuluka tizithunzi ndipo tikufalitsidwa mu ma Fesibuku ndi mu ma WhatsApp umu.
Mu Zithunzi zimenezi m’bambo wina wachikulire wapanilila ka msungwana mu mphechepeche kunyanja.
Anthu akuti bamboyu ndi a Billy Gama amene ndi abusa a mpingo wa CCAP komanso anali mlangizi wa a President akale a Bingu wa Mutharika pa nkhani zokhudza mipingo.
A Gama ndi munthu okwatila ndipo ali ndi ana, ena a msinkhu ofananilanapo ndi msungwana ali mu chithunzicho.
Koma pamene a Malawi ambiri agundika kuthotha a Gama kuti ndi a chimasomaso kapena kuti a chidyamakanda, iwo akanitsitsa kwa mtu wa galu kuti munthu ali pa chithunzicho si iwo.
A Gama ati anthu aupandu ndiwo ayambitsa nkhani yabodza choncho ati cholinga akufuna awaonongele mbiri.
“Munthu ali mu chithunzi chimenecho si ine ayi, n’kutheka tafanana pang’ono koma tsimikizani ndithu kuti si ine,” atelo a Gama.
Iwo apempha Mulungu kuti awakhululukile anthu amene akufalitsa nkhani imeneyi.
Koma a Malawi ochuluka akuona ngati mkulu ali mu chithunzi ndi a Gama, ndipo akudzudzula abusa.
Don’t ever trust a man,
Nayenso ndimunthu amadya kkkkkkkkkkk
This is not true, Mr Gama is public figure, he can not expose himself in the open…a daylight character assassination.please stop attacking men of God.
If he is not the one then some members of his church are evil, the messengers of Lucifer, who want to destroy him. Pastor open your eyes.
ngati siiwe ndiye ndindani?
Should he be in panick 4 being pastor nayese amafuna kuphaka lyf pankhozatu kukhala 1 jeno January kkk abusa kodya mmafupa mmafupa omwe kkkkkk panga zako aise
Mmmm munthu wa mulungu asaphake life
Draxon Maloya & Abel Walusungu Mhango tamvani
Erick Uledi-Kamanga taona nawo izi
Satana amafuna olimbikayo kuti a mugwese,Mbale zako ngati zili bwino usaweluze mzako koma mupemphelele kuti mwina chisomo cha mulungu chionekele.
we know this person samazisungila ulemu ask mj people they will tell u and nkaziyu tikunziwanso ndi friend wanga
we know this person samazisungila ulemu ask mj people they will tell u and nkaziyu tikunziwanso ndi friend wanga
Eish always lies lies yesyes
Za ziiiiii mwasowa cholemba osangokhala bwanj
Wakoyenera kunjoya
Musiyeni m.buss nayenso ndimunthu amava njala.amava kupweteka.amakhala ndi zilakolako zake.inu kozani chikhulupililo chanu kuti mukapulumuke
kkkkkkkkkkkkkkk
Zizindikilo zakuti dziko lili kumalecheleche
Mbusa ndi Munthu ngati inu…
ndi verse yake iti anati abusa samafuna ku Nyenga guyz. bwino nazo izi
mkazi wake adamukonda. nd ndan safuna zosintha????
kma de wojez
akamati si ineyo ndiye ndindani
https:// malawi.24/
Izi ndzabodza chithunzi ichi ndkuchidziwa mkaziyo anali ndimzake pambalipo apa anangopanga edit ndzabodza izi
Agama kakukhalanitu
Ndiyemweyo uyu. That is not photoshop
Izo ndi zakunyanja ndi momwe zimakhalira. Mwaona zachilendo?.Apopo ndi pa crimax pakunyanja sizoti mupeze choyankhula chifukwa choti ndi a busa? Nanga mutakhala inu mukadatani?
Aliyese mind ur own shit musiye nkhani za anthu
mau oti kuweruza kwa iye mulungu pasamakhale pothira anthu inu.. we are not judging him.. but as a man of God he has to live by example. lets not argue
Kulowa ufumu wa mulungu kufunika kulimba mtima osati kungomuziwa Yesu basi ukalowa mmm povuta anthu ambili amamuziwa yesu koma amalephela kuzilesa pamenepo i
My argument these days is simple. Most of these so called Abusa do not deserve to be called by that holy name, for most of them are just mere Historians who are able to tell biblical events. So my reaction when l first heard about the news was like ” oh! You mean another Historian of the biblical events has been caught in the moment? Thats carelessnes! How could he? That was my reaction.
Aliyense ali ndi zofooka zake ndipo sizikutengela kuti ndi m’busa
Kunjoya munthu wa ambuye eeeee
Kukhala m’busa sindiye kt ndiwe olungama ayi
Amene sanachimwepo ayambe ku ponya mwala (comment)
Mukumphunzira kapena simukumudziwa nkuluyu ndi hule otheratu
Kkkkkkk
Musikana nayowafuna
PALIBE vuto lililonse APA naye NDI muthu ngati inuo ndi ineo amafuna Ku joy mwina mai busao aopako Ku lake ndi Chifukwa atenga kena kake
We are in last days
Nayenso ndimunthu
Who knows this guy deeply this aint strange.I just recieved another photo ndipo iyo si photoshop simunganame if u dnt blv me inbox will share you
i know him very well
share 0998186265
0881900600
Share +27604202475
0999 792 615 share
share…. 0992106662
0888374853
Ha ha ha kuupeza mtumiki
Kodi ndekuti anthu tkayambana tiziyalutsana chi chi? Sibhooo koma ndi PhotoShop iyi
Kkkkk Guyz Just Leave Him Its His Time Musanave Kt Za Mulungu Kudyetsa? Aufile Bas Coz Giniyo ili boo eveen mutakhala inu mungaugwive?
Gama akudziwa kuti iwo ndiotchuka, i don’t think kuti mpaka akalolere kukakhala ndi kachibwezi kaoko pa mbalangata like that & ndikukalola kujambulidwa iwonso akuona choncho. It’s not making sense at all. Iyiyi iyi ndi photoshop. He can’t be that careless.
Akufunika shabalakatari amewo
Kodi mukudziwa bwanji kuti ndi mwana anthu inu mwana ndi waka kuyambira pa wani kulekenza pa 16 kapena 18 uyu ngati immalowa simwana musiyeni munthu asangalala ndi mkazi wake
Komanso kuyaluka ndi mwana wakukhonde bwanji,chilango tidzichiyambira pansi pompano kwinako kokangomalizitsa,nayenso namwaliyo khosi gwede nzoyalukazo,zachitika moteremu kuti alape,you become a thief once you are caught,tisamale ndi machitochito athu,kuweruza mkwake
amene sagwada amugende m’busayi.!!!!!!!
BODZA
Ku ufila mwa ambuye nayenso nd munthu amadya!!!!!
Ambuye anawaonetsa kut apanga zimenezo mwina..
amalawife tilindi vuto la sanje mmmmmmm
amalawife tilindi vuto la sanje mmmmmmm
ngat mukufuna pezani kanu ka bea.osamagokamba za abusa nawo ali ndi zofooka zawo,
Si mbusa uyu inu… ana a satana awa. Maybe those who does not know him, but for me no no..
Yizinkhalaso nkhani poti ndiabusa.Abusa nawo amadya basi.Nayeso ndi munthu.
Luciely potani mpaka hamayoooooo kkkkkk
People Do Edit Photos. Be Careful When Commenting, It Can Be Ma Hater A Abusawa.
Kkkkkkkkkkkkkk
Basi nkhani yatha! Shupiti zanu!
Ndiye mwati Ambusa zakhalabwino atipezera mai Busa mwamuna opanda mkazi sangakhale mbusa
izi mwanena ndinu hahaha
Kkkkkkkkkkk
Cheap fotoshop!
Mukat Abusa. Tawonan Zala Zikukulozan? Ndizitatutu? Ndiyeku Inu Ndiwochimwa Katatu Kuposa Abusawo. Amene Sanachimwepo Ndan? Nayeso Ndimunthu
ok
Nayenso ndi munthu
Ka small meat?,kkkkkkk
Ndendende
Let love lead
YOLO!!
mbusa wanji opanga zakumachende
People of God such as these pastors should be treated with all available respect.
Please,desist from writing such silly things before you are cursed by the power of God Almighty.Go fast and repent.
How can this m’busa be respected yet he does not respect himself?m’busa mu boxer poyerayer apa?wanyazitsa dzina la Mulungu!
Who are you referring as a people of God? You mean this Gama guy is also a man of God? No no..this guy is just wearing that title but for sure some of his nkhosas can be far better than him.
People please ..don’t be cheated..this guy is a notorious womanizer.
These people should be called men of gold for what they are doing. They tarnish the image of real men of Gold
Whats photoshop thats going around.Are you aware of this?If thats what is taking place about the reverend,then I reapt dont play with men of God.
Keep on updating us on different issues. Congratulations. Im looking for a peniple so find for me.
an2 ozitcha opemphera ndi opempheresawa amandikayikisa kwabasi
even utakhala iweyo what’s a problem?
Mafuso anga ndi awa: Abusawo ali pa banja kale ndi nkazi wina? Or is it adultory?,,nanga abusa akunenedwawo chithuzi chake ndichomwe mwaika pa mtundapo? Nanga amene amatumiza zithuzizi pa social media cholinga chake chinali chani? MW24 ndudikila mayankho anu.
Walakwa chani munthu wamulungu? Iye siwamsembe2 so what’s wrong with you people
Non of your business!!!!!!!!
munthu wa mulungu mpakana pamenepa? anaonjeza
Penapake ndikuona ngati anthunu nkhani mwaipititsa mbali imodzi, mukungonena za uyo mukuti ndi mbusayo, nango ako mukuti ‘kabae’ko, kalibe vuto? Ndikuona ngati kachepa nazotu pamenepo… Mmmmmh.
Zoipa sangavomere koma akanati awapeza akubatiza mwana. komabe ngati ndizoona, ayi ndithu munthu wa mulungu mulape kachete chete.
Malawi24 ndikupepheni days ina muzalembeko za ine chonde
Si Mulungu Naye Ndi Munthu, Akalapa Pakuti Palibe Olungama Ngakhale Mmodzi,
ndevuto ndichan walakwits2han mtsogoleri?inu mukuweluza bwanj?zanu adzaweruze ndindan?mukuenera muwadziwe mau amulungu!
Matsiku omaliza
Nkhopeyo akuikana kkkkk
Solomon amene wamu Bible anali ndi tima ‘Bae’ tambilimbili, Abusa awa ali ndi ‘ka Bae’ kamozi kokha koma mufuna kuwatchukisa ngati apha munthu
Koma ndiye zinali zokoma
Koma ndiye zinali zokoma
Tisaweluze, ulendowu mngoyenda ndi mmtima. luka 21 ves 34 koma muziyang’anile nokha pakuti mungalemesedwe ndi maidyaidya ammoyo uno koma mau akuti muziyang’anile nokha musachedwe mkuyang’ana agamma
Msiyeni Munthu Wamlungu Azipepese Aiwale Mavuto
abusa alero amenewo
Hahahahaha kodi satana ndichifukwa chanji amakonda kugwiritsa ntchito azimayi?? Bwanji sangagwiritseko zinthu zina.
Women Are Sex Objects Mukawaona Mtima Sumakhala Pansi
Mmmm koma ndie eetu
Ndi emweyu akukana chan?
Kkk ine sindikuona chomwe akukanila munthu wa Yehovayu
Maybe anamjambula ndimsilam jus saing
Amene mukuti ndi photo shop nu zikuoneka kuti mitu yanu simagwila
This is a real pic
Kumangobakila zilizonse
hahaha ine ndye sindikubakira nao
Ndani sanalakwepo
Sindikuonapo vuto pamenepa,lero ameneyu agendedwe mwala chifukwa zathu zabisika.
Zabodza iziii!
munthu uyu ine ndikamuona ndimakwiyanaye anamupasa mimba mwana wa mulamu wake mpaka kumupasanso matenda….zimandiwawa kwambiri nthawi yakwana yoti ayaluke
Inu mumamudziwa kapena mwangodana naye
sindikudana naye koma ndimamudziwa anakwatila ku mulanje ku lauderdale mmudzi mwa chipoka mfumu yaing’ono mwangala
So what? sinatenge mkazi wako bakha iwe
Nde Mmalawi Ameneyu Opanda Zochita Iam Teling U Busy Photo Shopin Ma Pic A Munthu Wa Mulungu Anthu Mukapsa Ndimaliseche Omwe,
Ah palivuto nanga he is also a human ali ndi life outside church too
Okay? Nde anasankha ntchito yolakwikatu. M’busa amakalika zomwe achita. Ngati achita opposite wa zinene akulalika, ameneyo si m’busa koma antichrist.
Why can’t pple for once mind their own business? Anzako akupanga zawo iwe busy taking their pics secretely. Musiyeni munthu wayehova.
eyetu ndi wayehova, koma iye akukana pamaso payehova yemweyo. waiwala kuti yehova, akumulondola kulikonse iye amapita ndi bae wakeyo.
Amwene Ine Si Wa Ccap Koma Ngati Mkalasi Mudalowamo Kapena Ngat Photoshop Maiziwa Mutha Kuonetsetsa Bwino That That Pic Is A Photo Shop Not A Real Image Mwamva Ajafali?
Ngati ndi ineyo ndayibweretsa pa page iyi, koma umuwuze yemwe anatenga zinthunziyo. ukudana ndichilungamo bwanji, kapena nkaziyo ndi iweyo umuwudze yemwe wachita post nkhani imeneyi osakhala ineyo.
work up jafali this is not him look Sharp wamva ndimunthu wamulungu uyu respect him for God seek he has a family ? dnt be stupid on nonsense things
kodi pamene amapita pamenepo, anayiwala mulungu bambo akowo? iwenso kuyambira lero, udziwe kuti ndi munthu wa mulungu ungachite zinthu zobisika tsiku limodzi anthu azakuwona mulungu akatopa nazo.
Jafali Mkaziyo Siine Sindimapanga Zimenezo Koma Ndimangofuna Kukuunikira That Aliko Amalawi Osowa Zocita Ngat Apanga Iziwa Photoshoping Others Zikumatheka Ndima Computer Ozitsata Timazindikira Mwasanga Osaziziwanu Maipitsadi Mbiri Yaena
zoonadi nanenso ndaona
He is him ,, cant u see ur selfs amene timamziwa billy Gama palibe china chilichonse chokaikila all we kno is this dat Billy nkhope yake ndimeneyoyo
Photo Shop Timatenga Real Image Yamunthuyo Mkumene Ka Mkuphatikiza Ndi Ina Inu Simuziwa? A Emmanuel? Atenga Nkhope Ya Abusa A CCAP AGAMA NDI KAMKAZI MKUPANGA PHOTO SHOP ANTHU OSAIZIWA PHOTO SHOP ALI BUSY MA WATSAP MU Kuipisa Mbiri,nde Mmalawi Ameyu,ine Ngwa Living Waters Koma Bodza Ili Ndikulikana Computer Ndimaiziwa Tawanamizileni Zina Tipeze Chonena Chamzelu Not Photoshoping Yii Pleasee
Si photo shop imeney. Mukusankha kutseka maso coz nd munthu wa mulungu? Mwni akut nd mistaken identity inu mukut ndyemweyo but its photo shop aaah the truth is ndyemweyo bac ena anawajambula Iwo atamasuka
Amalawi Azanga Ine Ngwa Catholic Sanje Ndilibe,yes Nkhopeyi Nja Abusa Agama Koma Chinthuzichi Si Real Image Its Photoshop Amene Computer Amaiziwa Apange Screenshot The Photo Ndiye Mupange Paste Pa Excel,click Zoom Image Then Uwill B Told That Real Image Or Default The Computer Wil Tel U Sikumubakira Poti Ndi Mtumiki Wamulungu Man..AZitumiki Onse Amayalukawa?Achina Bushiri..Etc.. Tikaope Abusa Agama?..##chibisa desire,but This Iz Photoshop Trust Or Not..
Inu ife computer timayidziwa palibe photoshop apa. Po mixer ma pic zimaoneka penapake sipalephela. Onani shadow pansana pa mkaziyo ya mutu wawo
On another note, it is funny to read “ine si wa ccap”, ” ine ndi mkatolika”…No one hasn’t just said “ine ndi mkristu”, Chifukwatu kumwamba kulibe zoti “ine ndi wa ccap, kapena mkatolika, kapena wa ziyoni” Yesu akufuna MKRISTU. Ndipo awo kaya ndi iwo kaya sindiwo tonse tizadziwa tsiku lowerudza Mulungu.
Ndekut wa police wamkazi uja inalinso photo shop yomweyo…
Anthuwa akutero kuti ndi photo shop, komanso Wezzie ndikuona ngati walankhulapo momveka bwino. Poyerekeza ndiwina wake, akufuna iye akhale ngati ndi mphunzitsi wanga asamale ndimudwanyula ndimau ndangomutsungira mau ake kuchipinda.
Maiziwa Koma Nanga Mukulephera Bwanji Kudziwa That This Is Photoshop Wa Police Uja Mukumuziwa Ndi Bwana
Mukumbukira za mbusa uja amati ngwa LWC? Uja adati adaba galimoto ku NB, after some debate, mpingo wa LWC unabwera poyera nkunena kuti he is an ex, nanga mutani ngati mpingo wa CCAP unenenso zina apa…? Mmmmmh.
Only God knows….he used to be our pastor way back …anyway kuweluza ndikwaiye mwini
Chani?
I second you@Wezzie
Kaya ndizoona kaya zabodza but what I know is that we are humans not angels so let a human be as humans. Dont compaire a human and an Angel, and every 1 has his own weaknesses. Ena amene akulankhala zambirimbiri ntchito zanu / zathu ena sakuziziwa
I beg to disagree with u much as he is human but this kind of behaviour along side man of God is uncalled for and very demeaning to the office of his calibre. Mind u he is not a general manager and had it been that he was doing this with his legitimate wife I dont see photos going viral but simply he chose za chikunja ndiye kuchikunja komweko wakumana nawo anzako a azachikunja. Learn that anything done by a public figure is a story hence a call for each and very jack in those shoes to be exempleray to letter
You can mind your own, but for me I will mind on Gama’s business. This guy is a womanizer.
Amene mukuchita challenge yerekezani mutumize chithunzi chanu ngati sindikuyalatsani mtakuonetsa video shopping yanu ya porno. Uwu wapanga izi watembereredwa. Imeneyi imatchedwa mature filtered photo yomwe simungathe kupanga recognise kuti yokwatiritsa ngakhale mutayika pa Access or Excel cant expose it unless software that we use. Send me your photo uyaluka ndithu. Touch not the annointed ones you will be cursed forever.
Kodi ndiye kuti bible lija limanama zakuti palibe wabwino,koma tizapulumuka mwachisomo? This is to show that we are all humans. This is why ena amasiya nazo kupempera chifukwa munthu yemwe amkamuyika pa mulingo wosayenela munthu aziwa machimo ake
Tafufuzani mbiri ya nkuluyu bwino bwino Ku mj mission mumve
Ine computer ndi maidziwawa ndipo iyi si Photoshop.
Zikusonyeza kuti pa nkhani iyi pali anthu ambiri akutsutsa kuti sizoona ndipo akufotokoza bwino pa nkhani ya computer ndiye ena tikungopanga makani opanda phindu cholinga kuti nkhani ikome.sibwino kuipisa mbiri ya munthu muli ndi zifukwa zodziwa nokha
Chochita kukonza chithunzi ichi. Chithunzithunzi cha dzuwa cha mkono wa mzimayiyu sichikuwoneka pa mkono wa mzibamboyu. Kwaine sizimodzi ayi zithunzi izi. Wina wangopanga
ANTHU AWA NDI AMENE AKUFALITSA MATENDA KUWANA WA CHICHEPELE ZIKAONEKA CHOMCHI WAGONA NDI ANA ANGATI. BEAUTFULL OUT SIDE, EVIL IN SIDE.
Wapanga kale tchimo lina koma aliso busy kupangaso lina. Yehova adza kantha.
O Gama M’masankhatu.. Ka Potable.. Kanganyenkhule Bwinotu Akaa
Kkkkkkk comment loading
I know photoshop when i see it…this is real..
Photoshop uyu amwene
I have seen the so called photoshop and the orignal one but the truth is not known amwene
Koma mwni wake akut its mistaken identity meaning anthuwa angofanana ndye inu mukut ndyemweyo koma angomuikilapo mkaziyo? Timvere zit..
Amwene si Photoshop
si photoshop iyi this is real man
Kkkkkk Mpaka Ka Bae,,,asakasiyedi Kameneka,,
eya si iwedi, koma zinthunzizo pali nkhope yako ndi mai busa wachiwiri. nawenso ingoleka kutumikira mulungu basi, bwanji osazipatsira ulemu mpaka kukakhala pa dzuwa ngati pamenepa? inde tikudziwa zoti nanunso mumadya katundu, koma apa pokha satana yemwe anakulowayo ndiye anali mbulandadi mpaka padzuwa bae bwera kuno, bae bwera kuno hmm abusa ndichiyani kweni-kweni?
Billy Gama siameneyo nanunso musamapuse
Asakanedi lakwana la 40
Ben billy gama umamudziwa kapena ukungonena?
Ben billy gama umamudziwa kapena ukungonena?
Hahaha mwina ndi twin bro wawo
komanso kankazika kakuwoneka kowakhala asakasiye
komanso kankazika kakuwoneka kowakhala asakasiye
palibe cholakwika apa azikazi abusa ena amachita mwano kwa amuna awo nde azikanika kukachinda kwina pamene iwowo akufuna kutelo kuwopa inuyo? pezani anu nanunso mudziwupeza ndikukuwuzani simudzaleka mukadzapanga chibwenzi inu.! tangoganizani ngati abusa afika pamenepa? ndekuti izi ndizokoma ndithu
Kkkkkk
Billy gama watopa nazo zam’nyumba akufuna takazi tothina kunyini.akufunana za ululu m’khosi
Ha Ha Ha Akufuna Tamazinga
Kikkkkk Luciely Potani
????hamayoooo eish
Kkkkkkkk
Nde Mwat tothna Ku chan kkkkkk
La 40
ndi xa umulungu ximenezi,kulimbana nd zotayitsa yesu nkati mwa min skirt !!!!!!!!!!!!!!kkkkkkkkkkkkkkkk
Photoshop kugwira ntchito!
Oooh yes dziko lapansi!
Chirombo cholusa ndiye munthu
Manyiwa sianga koma mkodzou ndiye wanga, kkkkkkk!
Kkkkkkkk koma abro
Hahahahaha! Mukudziwa kale Bro
Iye walakwa chani kuti asakaufire ndi bea wake…….just because he is a pastor so mwatengerapo mwai omamuika pa fb pa
Et ? Palibe chomwe walakwa, akanakhala Dan Lu kapena Martse anthu sadakayankhula kanthu koma pot nd m’busa bas anthu azilimbana naye. Let him be, he’s living his life.
kkkkk tsopano ukat siine! ndindan??
Kkkkkk koma ada inu…
akuzikanira nsomba, ati chifukwa anali m’mbali mwanyanja koma ameneyu ndi mbale ndithu. azikanira bwanji nsomba, pamene zinthunzizo ndizake.
Jafali Ine Ngwa LIVING WATERS KOMA NGATI MKALASI MUDALOWAMO MUZINDIKIRA KUTI IMENEYO NDIPHOTO SHOP ZIZINDIKIRO ZIKUCITA KUONEKA DAT ITS NOT A REAL IMAGE
Photoshop ,image Iyo Sanje Ndilibe Ine Ngwa Catholic Koma Alikodi Amalawi Osowa Zochita
Olo Yesu atabwera nati iyi si photoshop, uzamva wina nati Yesu ndi wa nsanje. Anyway palibe kanthu kobisika padziko. Enanu patsiku lachiwerudzo mudzati “eee kani zinali zoona”
koma ndye mukufanabatu,kkkkkkk,ngati sinuyu bambo busha ndye ndi ndani?kkkkkk
hehehe!! inu nzanu amakazipepesa,, ine kudabwa mpingo umenewu kukomda ndalama khani yake imakhala imeneyi eti?
Ndalama zake ziti inu
Ndalama zake ziti inu
MPINGO UTI UMENE UMADANA NDI NDALAMA? YEMWE ANAKAPEMPHA MTEMBO WA YESU KUT UKAIKIDWE MMANDA JOSEPH WA KU ARMATHEA ANALI WOSAUKA? CONCENTRATE ON THE STORY NOT MONEY!
Heeeeee sukunama. Mpingo uwu uwu uwu
Kkkkk komaaaa ndiye anajoyatu