The suspects that took advantage of the current blackout to steal 15 Galvanized pipes which support a fence wire at Bingu National Stadium have been apprehended.
Following the incident, a manhunt was launched by the Malawi Police leading to the arrest of three people and confiscation of tools that were used to cut the fence.
According to Lilongwe Police, the theft occurred during the night of 20th to 21st December, 2017 at the facility when the law enforcers were patrolling the area.
This was the second time for the facility to be ransacked despite being just over a year old.
In April last year, thieves stole eight water taps at the facility that were installed in one of the toilets of the stadium.
Currently, the value of the galvanized pipes is not yet known.
The facility has no electricity due to unpaid bills of K25 million.
Mukaba muziti MADALA amanga chosalimba
ENAFE SITINALOWEMO NDIE AKUBASO AAAAA
Ameneo don’t sentence them
Bring them one day kukaZakhala game mzalengeze kuti akuba aja ndi awa!!!!!
Tizalange tokha
Stadium need to given to army or police and the perimeter be guarded by them
Kuno ku RSA ndi dziko lolemera, ndiye mukufuna kundiuza kuti kulibe akuba? Kodi anthu enanu mmalankhula bwanji? Dziko la ameleka kulibe akuba? Ndiye inu kumalankhula kuti aa dziko la Malawi ndi umphawi ukuchititsa kuti anthu aziba, ndi zoona zimenezi? Ok, mukufuna kundiuza kuti boma lisiye kupanga chitukuko chifukwa choti dziko la Malawi ndi losauka? Nthawi zina, usanachite any comment, uzisiganizira kaye usanachete comment yakoyo.
Throw them awy from Malawi we dont need them close us
Punish them,evil people.
That is malawi i know,sitfuna zinthu zabwino,shame!!!.
Kkkkkk wakuba alibe chitukuko…
They must be kept in custody anthu odana devlopment
Bet
vuto lamunthu ndilimenelo pamene chitukuko chikubwela ena aku ononga, kayaa
vuto lamunthu ndilimenelo pamene chitukuko chikubwela ena aku ononga, kayaa
Atchule anzake ameneyo sangakhale yekha,anthu osowa khalidwe
Masapota a Chakwera awa
Ndizathu tisaononge amalawi
Amalawi bwanj kudana nd chitukuko?asawalekerereyi akatsekeredwe ena atengerepo phunziro
Those shud face capitol punishment since they r rivals of development
These shud face the capital punishment
Kill dem all anthu opanda pabwino,anthu a Jabu
Please forgive him, sankadziwa chomwe amachita.
Odala mwaganizavbwanji samadziwa chimene amachita ungozindikila adula mapolo?
I commit them to prison for fifteen years with hard work
Stadium iyi ngati tsiku lina sitikayipeza mwa mgona ndi mwayi ..mumm zawonjeza.
Alangidwe zenizeni
Death sentence for them ideots
Dziko losauka chocho tikuzibwezera mbuyo koma Malawi sazatheka
Well done police……. ..
Kod Pamene Anthuwa Amaba Zinthu Zimenezi,apolice Adali Kut?Chifukwa Ku Bingu Stad Ndi 24hrs Security.
Kkkkkkk
Malawian Heart
Hate developments
@delio keyala ,,,do yu think kamuzu he was a Malawian,,,,don’t fool yourself,,,,
Ironically, Kamuzu stadium was built by Atsamunda…, kkkk
They deserve a stiff punishment for they’re enermies of the state.
I have my stadium called kamuzu not this, that is for show for aLOMWE TRADITION THING, BITE MALI
machende ako kapolo iwe,udzafa ovutika..
Aphedwe basi or life imprisonment ena asazapangeso
MOTI MPILA UKUKOMELAMU KU MW WINA MKUMAPANGA ZA MTOPOLA NGATI ZIMENEZI.AKADZATULU
KA KUMENEKO,BURN THEM FROM WATCHING FOOTBALL FROM ANY STADIUM IN MW.
TANGOMUOTCHANI AMENEYO.ANTHU AMAKHALAIDWE OYIPA NGATI AWA SITIKUWAFUNA
ufiti chani kudana ndchitukuko mmmm shame on devil
Make them 79 years in jail
Akalowe basi anthu obwezeretsa chitukuko mmbuyo amenewo
THEY MAY ARREST CHAPONDA TOO
just feed dem with duracrete cement
They MUST be dealt with
Aphedwe basi ena atengelepo phunziro
si makako basi pamenepa nanganso adzikatha ngaiwa kundende ?
Please! Kill Them
Wat about the maize gate scam
agalu amalawi ndaamene mukumaba kumaononga zithu boma likachita chitukuko after that kumalibulema boma zachamba basi
Ooo! thats stupidity kkk! anasowa ya xmas?
Ofunika kudulila2 manja ameneyo
Winau koma ufiti
Opanda chitukuko
KKKKKKK palibe chachitikapo apa umphawi wachuluka and umbana umachulukanxo chitha ndikubedwa chimenecho akusatira misokho yao kkkkk kenaka ku state house koko
Kkkkkk boma lathu siliganizla achinyamata
MUKUYANKHULA NGAT MBUZI ZA ANTHU. akumangilani stadium lero mukuti boma siliganizila achinyamata. oky.kuwabweleka ndalama amenewa angapeleke? muzionako zabwino
Kkkkkkkk ine mbuzi yatonde kkkkk ndingongole baba from Chinese government moti tikubweza… Kmanxo BOMA ndi abbreviation so, try to find it’s meaning
Enemies of development, punish them
Ok
Mphoto yauchimo ndi imfa. Ankhaulitseni basi. Awapulumutse dyabulosi waoyo.
Koma anthu ndi oyipa guys shaaa!! kaya ndiye atakhala masapota angakhale a team yanji kaya………. kkkkkkkkkk
KILL EM ALL
Koma pple tidzakhalako ndi zinthu zabwino? Uwu sukhala umbuli koma uchitsiru
Mayaz…. maluz
Yap Good Job They Must Punished Throughly
Life prison anthu oyipa opanda Chitukuko
Thats very bad and am sorry for hI’m coz kumalawi kuno milandu ngati iyi imakhala ndichigamulo chachikulu bola akanaba ma million a boma mkukhalaso wa ndale .
Ukalodzedwa sumanunkha kkkk
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Make an example of them!!! Selfish bastards…we can’t be vandalizing the little infrastructure we have !!!…lock them up and throw away the keys….kodi a Malawi tinakhala bwanji?
Anthu opanda chitukuko awa alangidwe bas
Mbuzi za anthu
Lazy people
Anthu akuntandire sadzathekaso
Stealing and vandalism: our culture, our pride
Iiiiiiii agwesa nasi Stadium ija chifukwa chamakasu ayayayaya koma ulova sizinthu mmmmmmmh
Siulova nkupusa uku….kupepera chitukuko cha dziko samaononga
Aaaaaaaa amalawi sazatheka basi,how they can steal water pipes and taps for what?just kubadwa ndi evil altitude
Ufiti basi kuzolowera umphawi
good job for police but the good thing to do is just to kill them because they are people who don’t think and care about Malawi so why should we keep them burn them
Yes KILL EM ALL
Malawi nchifukwa liri dziko losalira timazibwezera tokha pambuyo kudana ndizabwino kaa.
Muwakhaulitse anthu amenewo ndipo ndi amene akubwedzera chitukuko m’mbuyo
Hang them
Odana ndi chitukuko aal
Anyapapi aku mtandile amenewa
Palibe Chachilendo Pamenepo. Mmesa Apolicewo Imeneyo Ndye Ntchto Yawo? Mmafuna Awagwre Ndani?
mulungu wayendele athu amenewa
kma amalawi tilibe pabwino mwayambanso kuthyola ma pipe ku bingu aaaaa muthu okuda ndi otembeleledwa basi aaa!! Mh…
death by hanging
Let free them. They need to enjoy new year.
kkkkk what do you think about development of malawi ????
bwanji achina chaponda akungowaleka paja amadziwika ndiwakuba nkhuku eti?
kkkkkkk kma ndy wauswatu mwano amaba khuku ?? Kkkkk
kkkkkk
nanga dpp officials adaba ndalama enuakewo amkati blue night party. Chaponda adaba ndalama zogulira chimanga osewe sizidziwika kt ziripati. Lero busy kulimbana ndi wakuba mapipe kustedium, awasiye asangalale 2018 wabwino.
Ndalama or utaba millions sakumanga zaka zambili ai uzaese kkkk
kkkkkkkk akayese kubako
Fundoless kapena ndiwe ukumazuza anthu usiku?wait latsala laiwe tsiku lokunjata
very stupid u r comparing those niggax with millionaires? ndiwe opusa heavy
Well done to the police officers who done that great job keep it up
dont leave them but punish them with a hard labour so that others can learn a lesson from them. munthu wamtundu wanji wodana ndi chitukuko.