Police in Neno are keeping in custody a 44-year-old man for raping his 11-year-old biological daughter.
Public relations officer for Neno police station Raphael Kaliati identified the man as Madalo Kasese.
He said on the material day the suspect’s wife was attending a village banking meeting within the village leaving behind the victim with her father.
The suspect got some space and called the victim into the house where he raped her.
When the wife came back the victim did not say anything because she was strongly threatened.
After some days, the victim was observed by one woman in the village that she was having problems when walking.
When asked the child narrated the whole story.
The woman then reported the matter to the community social welfare representative who later reported the matter to police.
Madalo Kasese, 44, hails from village Hiwa, TA Chekucheku in Neno district
He is in police custody pending court where he will answer the charge of incest.
he must be jailled for 4ysz since 11 goes int 44 . . .4 times
amangidwe ameneyo akuwoneka ngati ndi khalidwe lake azolowela
Sign of last day
Is wicked man
Wanders
aaa! ndiokhwima ameneyo nanga mwana wake yemwe pali nzeru pamenepo.
Chamba musiye chimapangitsa anthu Zodabwitsa zoopsya.masiku osiliza ano,kaya ndikukhwima but it’s too much
Zikanakhala kuti timapeza mofanana,nkuluyu sakanaganiza zokakhwima
.koma Bible linanena kuti zimene tili Nazo
Uwu nde ufiti weniweni anthu oterewa akufunika asmawaserese ai amuphike zenizeni kt ena atengelepo phunziro
Its really an omen! Into your biological daughtet what stupid man is he. He deserve astiff penalty.
Febia mwila style! shame on u!
Kukhwima plus Satanism,komaso azimayi chonde auzeni ana zamavalidwe abwino
Psychopath
Ameneu ndi chikaphonya pa make chili kwa mwana, amai anatalikila kudyela fungo lamake anawa akuyesa zida zotchelatchela chipala chakale amwene no mthubulo
mdara uyu asamangidwe koma angomudura zidaxarasha kut asaxapotenso tchito bz akutiipitsira mbiri komans in the cantly mahure nde ndi +
Musiyeni wakuwononga katundu wamunyumba mwake..
Ufiti umeneu
Koma ngati ndi ufiti ayi ndithu muyaluka nazo
How fool is him ?
This type of rape is existing but scares,….(father daughter rape)
shaaa koma Dpp yakwiyadi guys eee
Ku Neno ndi khalidwe lawo palibe chachilendo apa
Kkkkkkkk mwatero kodi?
Heey mamama chief justice’ kill that insern gentroman with longlife imprisoinment
Mdala uyu anaganizanso bwanji mpaka biological daughter he could have just musterbated otherwise he has dug his own grave for sure!!!
Amafuna kukhwimatu ameneyu anyway,,,ngati salapa akayakha
Nkhani yabwino kwambiri, mumange pang’ono cos ndimwana wake, akanakhala wa aneba pakanavuta
imagne mwana nthawi zambiri kumapolamila kwa atate wake. ife azida za original tingatani?? Sex iz food kudya zimenezi… hahahaha
kkkkk
mmene ndimatotela inemu eish womatiyo step daughter aah
Rabish.
Mmmmm my Malawi
Koma ngati satamba ndiyekuti kulibe otamba
What the fcuk… this man should be stoned to death… not behind bars..
Zinangwa zikudibwa ku Malawi ndizimene zikupangi 44 kusewela ndi ana akaseve basi
she must hve had good figure to
Kkkkkk phiri ayi wangokhala Tombolombo Bamboyo
kkk ndimaona ngat mwnaa anaposa amaketu
Kkkkkk lol ayi winau ndi ufiti
kkk kukhwima bwaa
Ameneyo Ameneyo Amafuna Kulemela Mwachangu, Azione
Koma chinalowadi?
Thats taboo or in other ways its an incest an act of the evil..according to our religious beliefs…and we dnt allow ppo to dpractice thos acts..in our community
Indians culture,,,,no shaken at all,,,.kkkkkkkk
The dpp cadet kukhwimira zisankho za 2019. Muduleni nthangala zakezo kuti asadzafesenso mbeu zake zoipazo.
Zikugwilizana chaninso APA ndi DPP candidant chilichonse dale basi,
Wodya zake alibe mlandu
Facebook judges they’ve judge and I taltary agree with them just wait for chief justice to announce how long you will be behind bars you idiot
Nkhuku yamwa mazila ake kkkkkkk
Ndiziwanda izi.
Kkkkkkkk adya profit man awa kkkkkk kamwanako kali cute asaaaaa ok
Odya zake alibe muland!!!!!!!!
There is a herbal doctor that treat HIV, i was positive for 9 years and using ARVS until I was cured completely of the virus by Dr. tiam. His herb is very powerful with no side effects. Call or WhatsApp: 2348037284837
It might have worked for you but not everyone could be cured
This is tested and trusted. It worked for everyone
Scam
i think the doctor is rich!!
He’s from which country?
You must not lie saying you did diagnosed positive and got cured , you are such liar believing in Satanism . That kind of practice are the put life in danger,
This is no satanism or any kind of religion, am writing my testimony because I was really cured completely. And I need other people get help to
Tell us where exactly is this man
Misconceptions…..
The man is in Nigeria .
Kooooma chimakhalani chani azibambo kuchidziwisitsa chisembwere mpaka wako mwana thya thya thya Kkkkk
matsiku osilidza zamanyadzi bwanji!!
Ma university anadula he want to get degree in prison majoring in hard labour no sick report.
Akulu kkkkk no sick report?
Social medias comments kkkkk@ happy
Penapakensotu ana akazi akuvutika chifukwa cha usatana wa azibambo
koma nde mukumangidwa ma sapota a mcp pofika 2019 Ambiri mudzakhala kundende
Ndiweso mbuzi iwe eti,ndani apa akukamba za chipani? Kapena anakuuza kuti ndi wa mcp ndindani? Akutuma eti??!
Guyz akufnika firesquad ameneu
Koma zinazi ,akamati stepdaughter zimavekako pang’ono kuti mwina amati fungo ndilamake koma mwana wako weniweni???hitting the bottom rock…
Ni check this out kkkkkk
Kapena anaona mulu wachinthu.kkkkkkk
Anthu akupanga zinthu kunjaku mmmmm ,,amuononga mwana mentally sazalungaso ,
Chimfiti!!!!!kumwa mazira ake mxxim!!
Akachuluka mazilao amamwedwa
what eeeeee a shame
Aphedwe
Kufuna zithumwa kapena chani? He deserve life in prison
Uyo ndiye galu wene wene ngati akugona ndi mwana wake kulinji wapadele he deserve to rot in jail
kukhwima basi…#ufiti
Zovesa Chisoni Komaso Kuchtitsa Manyaz, Mwana Obala Wekha! Wakundende Basi
kudya zake zomwe eeeish just go a rot in jail wankulu
Amafuna zizimba galu ameneyo
Ufiti Umenewu Ameneyu Apatsidwe Chilango.
Bodza
Akfunika Shabalakatakariiiiiiii Amneyo…….
alandila panishiment yoyenera kt anthu ena atengerepo phuzilo
mukut mwana wake shame mmmm akangwile jele ameneyo
Sindinganeneletu ngati nkhuku imamwa madzira ake
eish koma
Umenewo ndiye timati umve OK it’s fine give him life in prison it’s enough for him
Angomudula jododoyo, ena atengelepo mphunziro
kwanuko magetsi akuyaka??
Kkkkkkkkk
Zikugwirizana bwanji?
kkkkkk
Kkkkkkkk
Sanayake
kuno ayaka kkk
Ndiye akuti athima nthawi yanji?
athima usiku chamma 9
Hahaa!
wachifundo andgaileko crdt pliz… magetsi athima kuno ??????
Ndikanakugawira koma foni yanga yathima. Kkkkkkkk
kkkk muku user yo ndchan? kkk
Kkkkkkkkkk
kkkk ?????????
Kkkkkkkk
Ndiku user mose wa lero
klkkkk nde smatheka kutumiza kkkk
Ilibe # button kkkkkkkk
kkk mmmhh bodza
Hahaa
kkk muku user smartphone inu ???
Za azungu zimenezo amwene
kkk oky
That psycho must rot in jail.some people they don’t deserve to stay among the community.shame.
End time scenarios (Latter rain)
Chiwanda cheni cheni
Rest in peace ✌ this guy must be fool to the fullest
zibwana2 izi kutetha uku muzika saver so jail.?
Mmmmmmmm shame
Nkhuku kumwa mazila ake kkkkk
shame on him