Kokuba mifuti sitipita ndi utsi wa fodya basi. Poputa asilikali, kumazimitsila nduduzo. Maule atuluka.
Ndi Kamuzu Barracks ndi Moyale amene atsala kulimbanilana ukulu wa chikho cha FISD. Zivute zitani achitenge ndi asilikali basi.
Timu ya Bullets lero yaonetsedwa zoopsa itatibulidwa ndi asilikali a ku Kaning’ina mu chikho cha FISD.
Pa masewelo amene anachitikila pa bwalo la za masewelo la Civo mu Mzinda wa Lilongwe, anayamba kuonetsa chamuna anali anyamata a Moyale amene anamwetsa chigoli patadutsa mphindi makumi awiri.
Anali mnyamata Khuda Muyaba amene anadzetsa chidima ku banja la maule, kuwasiyila chizilezile mmaso.
Maule anaphukilamo mu chigawo chachiwiri pamene mnyamata wawo Chiukepo Msowoya anamwetsa chigoli kuti ayike masewelo pa 1 kwa 1.
Zinaoneka ngati maule atchola ku Barracks lero pamene anapeza penote. Fischer Kondowe anamwetsa ndithu ndi kuika maule patsogolo.
Koma chisangalalo cha maule chinafanana ndi cha munthu ochimwa chifukwa chinangokhala kwa ka nthawi kochepa chabe.
Anyamata a Moyale anabwelanso ndi ukali ndi kuthila mpholopolo kwa Ma palestina kupangitsa kuti masewelo afike ku kaphelachoka, ma penote.
Uku ndiko maule aona mbonaona, atsanzikana ndi chikho cha FISD.
Pamene Moyale inaonetsa ukadaulo ogoletsa ma penote, Nelson Kangunje wa Bullets anachita njengunje ndi kuphonya.
Marcopollo kwa limwe neba
Idont like this malawi 24 mabodza too much
Kkkkkkkkkkkkkkkkk,,, bakuniela we.
Winstone Sinkhonde,,the ghost has spoken here,probably its last words before disappearing again.
I know you are a family (bullets fans)
Choka we fb ndiya inu makapenu ķkkkk
Kkkkkkkkkkk,,, fyako ifyo.
Kkkkkkk actually am a blue fan the one on the drive seat
Chizyuka chileka ching’anamukeghe mwileke we
Kkkkkkkkkkk,,, oooo! Thought you belong to a cig. Manufacturing company as well.
Hell no, are you crazy?? Kkkk
Now i have believed that malawi24 is not a trusted source… There is no professionalism… You are fool journalists..
Aaaah Anthu Opanda Chisoni Inu Aganyu, Munamvapo Kuti Namfedwa Wamenyedwa?? Kuluza Kwa Bullets Chinali Chipepeso Kwa Namfedwa Wamkulu Monga Tonse Tikudziwa Kuti Asilikaliwa Thambo Lakuda Linawagwela…
#team_Bullets.
Awa koma kugula ma ref
lithumbwi likukondwera
Utola Nkhani Uwu Nde Wammakolatu…..Wamma Public Toilet……..Wamma Public Bins….Hw Long Malawi24 Cant U Learn Being Professionals??????…..Stupidity In Professionalism….Stupid Reporting
neba amuyendesa jibiya jibiya maule mbola.
Kkkkkkkkkkk
Koma….kenako akuswa iweyo maulewo
Ankatiseka ameneyu, pano ma soja aku Kaning’ina, amuminitsa
Hehehehehe amugwiritsa magobo
Neba anatola joker
inde taonanso kut mumatha kusanza mau kma usayiwale kut nawe neba anakugonyomola kale
tavomereza basi
Neba apa ndiye wamwa madzi wometera ndevu kuisiya mkaka. Koma ndinakuchenjeza za Khuda Muyawa. I we makani thoo. Lero wagwa chagada. Akluumbuza, athibura, akuswa, akukonza, akufotokoza, akunyetsa, akukong’ontha, akuyeretsa mmaso, akuipisira mbiri, akuyalutsa, mpaka kuyenda ndi usiku ulendo wobwelera kwanu ku Ndix. Tafanana tonse. Tatuluka mu FISD Cup ndipo tatulutsidwa nd team imodzi Moyale. Machende ako neba. Mpaka umafuna referee akukondere kukupasa penoti. Game sidali yako imene ija. Ndiye Danger/ achimwene aakulu amvekere ife timafuna matimu ang’onoang’ono ngati amenewa azipha mateam akuluakulu ngati BB kuti national team yathu izikhala ya mphamvu. Hahahahahahahahaha koma nebaaaaaa.
Eeeeshhhh!!!!! Ku bb akuluakulu! Chingerezi amvekere “u expectedly it kuwina” chani chimenechi alinafe zavuta zasolobana ku bb ngakhale refu adali kumbali yanu koma Mulungu anali kwa asirikali ndiye poti inu ndizanu zija apo refuyo mumpondeso inu mwakanika basi
Zachaka chino ndi zimenezo.
Iwe mvera kuno kaye, ndiye mpikisano umenewo amafuna apezeke owina m’modzi basi. Sikuti iwe ngati uli pa number1 ndiye kuti ndi iwe wanzeru ayi fatsa. Mpikisano udakalipo, tayang’ ana kutsogolo kwakoko uwone zikubwera.
Apse mtima zenizeni,akumva nyunyunyu.kkkkk
asilikali ndi aukali,azimitsa ndudu zonse,zangoti ndwiii
Amugweba,amutsinatsina kkkkkkkkk
waiwona sniper, umangomva
kkkkk Ayooooooh
Kuthetsa kunyoza aise mulungu wayankha
Ine Ndinaziwa Team Yotulutsa Noma Imafika Final Ndiye Neba Akumwetsa Mandimu.Vuto Umadalira Home Ground Advantage Koma Apa Neutral Ndiye Akufwafwanthadi.
vuto ndilot munthu wabwino nthawi zonse anthu samuonela kukondwa and any mistake nkhani imafika pa air ndepot bb its the best team in malawi u expectedly it kuwina only forgetng that its football ⚽ even barca or Madrid imaluza koma mateam enawo akaluza anthu sayankhula amangot tidadziwa basi …we r still bullets and we w never change
Ayifwafwanfha, ayikhapira kosatwa, ayiyendesa chidibiyachidibiya, ayimeta mpata opanda madzi bullets ayikuntha!!!!!!!!
ine faint
Msongole Nevi moyale yaliza akatundu pepani kwambili a bulless nose zimachitika
kkk akuva pain
A Beletsi mwakhalila mazila anu omwe
bullets ayithena kuchotsa zakunsi kuti ikhale docile.Oooooooooooooooooo!!!!!!akuns
Zikhala chonchi chaka chinachooooo.
Achimwe Pepan Zimachika, Osadandaula Dyan Chakudya Kkkkkk (BABA )
Kodi ili ndi mbalinso yeti !oky
Mapenate albe udolo komatu inu inu smunafke nd kumapenate nkome mesa anakumeta mpala opanda maz omwewa amoyale 2kwa zro palbe zosekana apa.
Za usiru et…
Pathako pakooooooo sumaudziwa mpira kanyimbi iweee
We gonna see the gate collections on that final u will tell me
Wasangalala neba waiwala padzana 2 ~0
Koma asilikali ena mugabe waazunguza
Kma Ndye Zovetxa Chison Am”bare Anga Pot Mavuto Smariro Ubwino Wake Pot Ine Nd Wa NOMA
James Wa Nyerere Taulo, James Taulo
My moyale my team woyeeee
Zosasangalatsa kwa ife a bullets zabwino zonse a Moyale
NDIPO OLO TILUZE SITINGAKHALE Nyerere,nganganga ndi Maul3 4eva j
12 million ija yadula ndthu aaaaaaaaaaaaaa zavta apa
Unyanya neba matama , akuchita bwino
Zimachitika kunonso Polokwani City ayikwapula ayifwafwantha!
Ine sindikuwona zachilendo koma kulakhula umve ndiye lelo waziwona alakhule lelo cholakhulila chagwela kati utsi wapitilila khosi akulephela kulakhula
Bullets Ayikutumura,ayisosora,ayipamantha Yachita Njengunje Kkkkkkkk Kambilanani Ndi Mgabe Zothesa Vuto Lachpongwe Lomwe Ma Soldiers Abwelesa Kkkkk!
Kusuta Kuwononga Moyo F C, Yapuputidwa Ngakhale Lefu Anamugulira Padi Yose Kuti Akamubeleke,Koma Walemba Kuti Leka Ndipo Abweza Padi Imeneyo Kwa Anyamata A Kusuta F C.
Zabwino zonse kwa mapale amoyale, dundu zija azizimitsa.
AMUKULUKUTAAAA
Neba neba kkkkkkkk wayaluka kkkkkk
pajato bb ndi mazulo ndiye tidikile cha ma 10 nimu ithokakuwina
pajato bb ndi mazulo ndiye tidikile cha ma 10 nimu ithokakuwina
the journalist who wrote this article deserves to be the best sports journalist of the year 2017 ,,,,, , ,,,or asakhulupilire athidzimulidwabe
100% true, amayenda m’mbali akumana ndi Tata kkkkk
Best journalist ndowe zake zimenezo??Eee nde mwakomana makape okhaokhatu
Best journalist ndowe zake zimenezo??Eee nde mwakomana makape okhaokhatu
Or zikhale ndowe koma afafanthidwa basi kkkkkkkkkkk
Achipopola matama neba
Neba watuluka basi
Awo ndi asilikali ngat ananyenya nyerere ndi jombo fodya angathawe? Kkkkkkkk!
fisd anakakhala mwana anakampanga kidnap,sakumvetsa kkkk lero nde mumwa wa aloe vera tea kkk
Amuchapa
Moyale yatiimilira iyaaa zokambakamba zinachuluka hevy
utsi phaphaphaphapha kumati muwina moyale??? inaphako ife ma defending champion nde akat inu zaziiiiiii…utsi okhaokha basi
Kkkkkkkkkkkkk koma admin iwe kkkkkkkkkk
timanena ife chalaka noma neba sangatole kkkk ine kunva kukoma mumtimamu
Tilipo tipite kuti
Taluza tikuvomera ngati takana ife ngati ndi mpira ndimene umakhalira
kkkk neba wafa lero
Koma maule mulipo kkkkkkkkk nyamatayu sakukuchezani bwino
makopolo fc hahaha
Iyaaaa
Mankhwala amasulukaso adziwe lelo. adawanamiza sing’anga uja amakhulupilila uja. kuphatikiza apo sanafinyile midoli eeyiiiii mpake athamangitsidwa.
shaaaah
Wanya neba mkanakhala ine mkanapempha mbelo akutibula zochepa zikanakhala izi kkkkkk
Kkkkk Koma Yaaa! Ndangotaya Nthawi Yanga Kuzala Mtengo
Wanderers ikatenga cup,pamatha kaye 2yrs kampopi ixanatenge #team yamasuporta aphokoxo yaludzaa#zithumwa anaziyiwala pa bingu
Amukong’othabe wakwiya ndi Mfiti basi
Mwati neba amutani??!
Kkkkkkkkkkkkk. Amumeta mpala
Choncho Mudziti A Bb Nga Ntopola Amakonda Ndeu Chonsecho Mukutiyamba Dala? Iyi2 Ndi Cup Imakhala Ndi Zotsatila Ziwili Win $ Los Si League Ayi Yomwe Imakhala Ndi Ma Results Atatu Win Los $ Draw Ndie Paja Maliro Amfumu Amamveka Patali Taluza Tavomeleza Umenewo Ndie Mpikisano Ndipo Samawina Awili Ai Tikudziwa Kut Aganyu Munachuluka Ndie Tione Ngat Afam Atolele Ndalama Zambiri Pa Ma Finals Anuwo
Mulakalaka Kumenyela Pa Civo Pomwepo
Apa ndiye mulungu wakanatu after mapale atapatsidwa pennaty yopanda kochokera Mulungu wakana basi zamanyazi ref pepa Neba zaulendo uno ndi zogawanagawana
nyasa wa nyasa
mapale mulipo kuli zi!! kkkkk
Kkkkkkkk koma wazipentayu akayela kosambako?
Mayooooo neba
mugabe has made announcmnt to join Big Bullets following unforgivable loose to soldiers…..
Eshi! Malawi24 mwawadoda bwino amenewa apa n’kalembedwe kanu,,tinsinjiro kukoma ndithu,, akanatumbwa anyamatawa pano,,bravo Moyale.
Moyale lero ikhoza kunyang’wa ngati wakabaza wonyamula ka ngenge komwe sikali kake ukhoza kuyimba beru ,olo kuyatsa ma getsi masana
Hahahaha admin bwerezaniso Mwati chani sindinamve!!!!!!’!’ kkkkkkk Neba pepa eish
Pepa Neba Kangunje Anaonjeza Kutsuta Chonde Achepese,m’cholinga Aziona Pagolo
Amupumuntha wazolowela kuwinila mapeneto ler Silencer ali ku silent.kkkkkkk.Koma goalkeeper Mc donald Harawa!
Wafela pa Graund Pathu Manda Yako meyanja Kupatulako Fisha
Amafuna Abele Nthawi Yokuthayitha Atikupeleka Penate Ngatimunamgula Lefuyo Ndiye Ndalamazapita Mmazi Wanyanayo Neba Kangunje Ayende Wapansi Popita Ku Bt
Nelson Silencer Kangunje…Has Silenced His Team.Kkkkkkk
Neba amupopa magazi kkkk
Wadwala Lero Mulungu Bullets Muliii Bhooo I Mabanka Woye !!!! Levi Special
ZIMACHITIKA SIFEOYAMBA KUIUZA KOMA NDIFE A B B BASI!
Sindinazione anachezela ndi kuziona nawöni guys amatishasa mwadzina lawo
Neba wagang’anthidwa,akufwefwentha,akuswa,akulikha nayo jombo,akuthizimula,akukanthamula.Asilikali bambo sachita m’bindikilo pa nkhani izi.Mwina mum’funse Commrade Mugabe pa Halari.
Kkkkkkk achithidzimula
Ife Asilika Taipwina Bb, Osadelelanso, Moyale Woooyeee, Kkkkkkkkkk
Kkkkkk amubilibinya
ng’o!! bullets forever,mu sova akhuthunyindu inu
Ohoooo!! Asilikali anayiwonela patali game nchifukwa chake ankapempha chitetezo!! a Bullets kodi mulipo?tamakomentani ka
kuli ziii..
Kkkkkkk Matama onse atha,anachayilirayosayiwona
Neba, amukhadzula
UWAUZE ASILIKALIWO AKALANDE NYANJA KU NORTH AKULIMBANA NDI MPILA UKU NYANJA IKUPITA KWA MATAIFA
Kkkkkkkkkkk waluzabe umat utan
Kkkkkk waziziwa liti?
BOLA IFE KOMA IWEYO UDAFA MMAWA OMWE
BULLETS
NDE ifeyo maule
Upse mtima zenizeni
Sindingapse ntima chifukwa tili ndi bus kuposa national team yamalawi.pomwe neba akuyendera min bus hahahaha Kkkkkkk usova ngakhale atandithira doom m’kamwa sindingasapote mighty wanderers.big bullets for ever
Noma idatulutsidwa ndi moyale baracks yomweyo, lero neba nbb watulutsidwanso ndi moyale yemweyo. Zikatero timati zagwa zatha, ndipo anyani samasekana zikundu. Congratulations to mapale amoyale, zabwino zonse kwa opambanawo.
BOLA IFE KOMA IWEYO NEBA ANAKUCHOTSA MMAWA OMWE
Kwalelo Kwalelo Neba Anadzukila Ku Mazele
Bola kangachepe kokha tkapeza kusiyana ndikuluza without anythng
Ndiye mwati anakaba mfuti atazimisira fodya
Inde inde inde
koma nde unganyoze galu iwe , mesa inunso akapado fc idakutulutsani ndi mafco yomweyo? tafanana
Hihihoho. Mutu sukuyenda neba. Akutitu Mafco instead of Moyale. Kkkkkkkk
Malawi24 ndinu anoma etii ndatuka kapege kanuka kikikiki
tsoka a fisd final yopanda ndalama nanga kukasapota timu iti? Manyaka okhaokha
This is wat I was waiting for , thanks Moyale players.
😀 😀 😀 koma ndaseeeeka!
Ganyu lero yakoma palibe wafa ndiganyu lero
Amugweba, amusasatha, amudula mutu pepa neba!!!!
Kudi paja mum at khuda muyaba?koma ameneyiiiiioo
koma oyimbira mpira akumalawi kumvetsa chisoni mwaona mulungu akalemba walembatu
Kkklk ADMIN apa wandisekesa!kokuba mfuti sitipita ndi utsi.klkkklll kandiwaza
Waona polekela matama uyu kkkk
Kkkkkkkkk ameneyo
amunyenya
Aaaaa chitabwino ana amenewa amadelera kwambiri ana achipongwe ife A NOMA tikusangalala
Kkkkkk Neba lero waona zinthu amati Bullets siyiluza i hope lero mwawaona akhalatu chete akanakhala awina mmmhu lero kukanavuta
Chalaka bakha nkhuku singatole
Amachulutsa matama ameneyu amuchita bwino,,, kangunje kutimvetsa kukoma
Filho de putä
Amusosola nthenga
Fodya wake amasutira mu Kalio kapena nyuzi pepala usi wake umeneo Kungoti poti kangunje anachinya penalty yomaliza ndi Noma basi mwati ndichakomaliza
thats y mpira kumalawi umatha ndiziwawa ,athu amapsa ntima chifukwa cha inu azathu atola khani ,mumagwiritsa tchito mawu onyoza team imene sinachite bwino,, kunjaku azathu mpira ukatha they dont talk like amuphanya amuponda kumusi etc, instead of saying that ” what a game we had togather ,both team played well ,they put their effort but all in all the game has ended infavour so and so,
Mwaluzabe kkkk
???????
Ukunena Zoona Amalawi Stisapota Bwno Mpira
hahhahaaaaa km adha…!!!wapsa ntima eti
Ayinolabe zako izo ayigwilisa fuwa lamoto
Kkkkkk kukhala mpalestina week ino mkulimba mtima expect draw ndi tigers Thursday meaning kusiya zonse mu week imodzi
Kkkkkkkk Neba Phokoso,akusasanthabe…Dolo Ndi Kangunje
Mwafa basi, NDE panganitu ziwawazotu kkkkkkkkkkk
, in a game of football only one is suppose to win,,, thats a game .
Kkkkkk walira mpale
Sunapange or kugenda konkuja mpaka ziwawa pa foni kkkkkkk akumva phain
ahahaha akufinyabe iwe wa Bus ibwera friday Fc
Wabangula mokweza mkayidi kkkkk
Yobwezela Kuwawa Matama Akowo Team Yafuko Yamwa Mtonjani Ogona
Inunso ndiamodzi olirawo eti,ndaona kudandaulako pepa neba tsiku lina zizayenda but nt dis coming Thursday kkk
popopopoppipipipipip vuuuuuuuuu ,pipipipipiipiii pachiwongorero cha tnm ,
kulira kwa namalira wamkulu kumeneko….avithyapa, kkkkkk avibwanyula kkkkkk
kkkk akut amuikitsa posaika…amupala mamba (Neba wachita kukhala nsomba chani)…amumwetsa madzi ometera ndevu…amuchita tintin kapena kut amuchita zina ndi zina…kumakhalad kulakwa…kkk
Kkkkkkk wagwa nayo neba kkkkkk akufinyani kkkkkk
kkkkkkk amubumuwa neba
Tadyamula bullets
Tavyapula bullets
Takung’untha bullets
Taphwamula bullets
Takhwengwenesk bullets
Tawambira bullets
??????
Eish koma alipo akuva neba zimenezi.
ife achiyao timati
bullets
ajikasile
ajilosisye losyi
ajididiwukwire
ajipwasire
Its u’re time! ours ‘ll come bt know for sure that one day BB will sting.
Siyani kupanga compare momwe anthu amayiko ena amakomentela kaya amachita bwanji timu ikaphwanyidwa. Anthu asangalare chakwao chaku Malawi mmene akuvelera shuga mthupi mwao. Mchifukwa chake Malawi ili Malawi and other countries are others too. Ndine wa Bullets koma ndiri kuno ku Sasafilika. Yapa ndiye atiphwanyadi bwanawe koma tiwasiye akondwe mmene afunila. Ndinthawi Yao. Nafeso timanyanya kutumbwa. Taona zakuda basi chonde vomeleza neba. Kkkkkkkkkk. Kusangalala sufusa kapena kuona kuti other countries achita bwanji. Kutsalira kumeneko. Learn to celebrate things in ur style.
kkk bullets Nsete zose pamtunda man…. ipsyan mtima zen zen man
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk???????????????? NEBA ipsa mtima zenizen matama inu
Amutsinatsina kkkkkk
Akufafantha munyasa akulikita akubulumunya akumbulinga munyasa akugozomola
amene wapsa mtima apse mtima zenizen
So timuyo yachita kuswedwa, ndiye mukufuna anthu azinena kuti aigwera? Yakunthidwa basi.
koma guys ine ndakomoka kuno klkk bullets ayitani iwe @ Osankha Sankhani Michael
Usandikumbuse maliro aneba please chonde kangunje amamutamanda uja akuti silencer Kkkkkkk kuzapangisa silence masapota ake omwe
kkkkkkk neba mwano eishhhhh
Amayenda mbali zokanika noma iye angazikwanise
kkkkkkkkkkkkkkk atimenyatu abullets ali momuno ohoooo
Komatu mukutiyamba dala eti?
Hahahaha ndangoseka nawo ma comment abwinowo
Zachabe izi bus dvd yafikira musoka sua
neba watenga fisd cup.
Mfumu sipita opanda msamiro, lero si idzi, ine ndimangodabwa kulalata akut neba watuluka, moto umapita kwasala ntchire ase lero wadziona nnaziona zija kkkkkkkk kkkkkkkk
Kkkkkkkkkk katsamiro eti kkkkk koma
Admn,uli ndi mbali eti!!? Ndakuwona lero!!
Neba Wa ona Mazangazime,odi Uko!!!! Timvineko Pelete
Mmm Guys Mpaka Kutukwana,nde Ndikira Umve Tsono , Ayipamantha ,ayipala Mamba, Ganyu Kukoma, Kkkkkk
Kkkkkk Ommar Gamah Hashim Manyamba Shaffie Misonje Davie Chisime Vin Leepunga
xadyeka wadyeka lero….umayenda mbali wazionatu.. aaaaaah nanga mchan uxacotse skafu nkhoc ivale nd2 azkuwonela patali!!!!
Congrats moyale
Atleast work on yo HeadLine never see such on Skysports#LearnFromTheBest
Kkkkkk beautiful headline
No it has to be accomodative i dont think any Bullets fans can read this article#TheyNeedToBeProfessional
Inu mwawerenga bwanji wawa?
Im not a fan of local football but i dont see it as necessary
Akuti kumazimisila ndudu neba
Inunso Anakufafanthani Komanso Chaka Chonsechi Mukungodutsamo No Chikho Ati Kudalira Tnm Koma Dziwa Tnm Nde Tipherana Mu Kwale Neba
Inu amalawi 24 paja mumati the dogs fc?
Kuyesera kuwapatsa kapenalty koma zosayenda neba nde zakuonekera basi kkkkkkkkk tivine pelete basi
AMUPANGA MUDULIDWE KU BWAYILA KKKKKKKK
inu inu bola iwo adzapatsidwa kangachepe 1m koma Neba winawe unatuluka m’ bandakucha omwe Tambala asanalire ……usayankhule kwambiri
Awuxeee kkk
Ayi paja umati etenga Fisrd kkkk
B4w fisd cup alinayo ku club house pomwe kampopi xikuziwa kt imaoneka buaj
Akupalanibeni mavizi kkkkkk.
1 m azanu alandira, inu munalandira chani? kutuluka mmawa omwe bolanso ikanaponya Wonderers Reserve ikanakufikitsani semi final kkkkkkkk
Anakwera basi yamakono ija?
Eya, nde yamuseseletsa mpakana waiwala kwao
Utsi wandudu tolotolo kukalimbana ndi anyamata apelete zoona nd2?awachotsa chimbenene,kkkkk!!!
neba zikumuwaza ngati kuti wafika final ndi n’yeyo!
Hhhhh amusambitsa chokweza ndi utsi wakewo.
Kampopi afc ya kwapulidwa lero, pamene Sailesa wamwetsa wa mandimu manyasa
Ayikhapira Kosathwa,ayipala Mamba,ayimeta Mpala Wopanda Madzi Kkkkkk
#Aikuzula_Sorry_Neba_Zampira_Izi
Ndiyeno
Amuzimisila ndudu zake Neba
Amugwiritsa magobo neba lero kkkkkk
KKKKKKK
Cingambwe fc sorry!!! Asilikali akufafantha pang’ono mwano usiye neba kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk.
Amuchita Mugabe
Kkkkk
Anatipatsa period yolakwika yomwe maganizo athu ali pa Bus
A herbalist in Africa has been curing lots of HIV patients using natural herbs. He has on countless occasions after curing patients presented lab results both positive and negative, together with the cured person. with joy in my heart i will like to inform the general public. i never knew there was a cure to HIV until my sister was cured from the virus after four years of battling the virus with ARV. She took his herbal medicine for a month and some weeks and when she went for a test and she was diagnosed to be negative. you can contact the doctor on WhatsApp or call +2348147299781
kkkkkkk malingaliro ofuna kutenga zikho zomwe Noma inatenga last year atha lero.Bullets aiponda kumusi
Filho de puta
Machende ako galu iwe metsa amawina modzi
Pakholo Pako Galu Iwe Pamako Bola Tinafka Ma Sm
Machende ako galu iwe metsa amawina modzi
Ndimpila uwu anzanu sanatukwane kkkkkkk
Iweso zipatse ulemu wamva stupid
Apalmer mulungu si kangunje kapena kananji yawawatu lero neba wapsa tima kkkkkk
KOMA ATOLANKHANI ENAWA!!!!! Kkkkk kkkkk kkkkk
Zaziii ma journalist amasiku ano a midoli yokhayokha
Bullets ikaluza oyankhula kuchuluka. Izi zimasonyeza mantha pa team imeneyi… ma penalty sikuwina koma ndi mwayi chabe. …vuuuu! Viiiii! Vaaaa!
Only Jesus can cure HIV not aheberist
KKKKK IWE SUWUNATENGE CUP NDI MAPENATE PA NOMA
Man tinatenga koma eee Neba lero wakondwatu ndaona
Wabangula mokweza mkayidi kkkkk
Kuluza ndikuluza man
Can’t stop laughing kkkkkk mayo nthiti zanga,admin wati amutani?,amugweba? Kkkkkkkk
Aahhh Chingambwe FC Yagonja.Sorry Neba Zimachitika.
ndi khunda muyawa,watseketsa company ya fodya
Koma admin iwe ukuwaputatu dala a guluwo akuluma lero
Kkkkkk
Maule woyeeeeeeee
woyeeeeeee i love ma yeam BB
Umeneo nde u man kumasekelera nthaw yolira.
Hahahahaha
Aziona lero
hahahaha adayamba ndiuyo mapale all wayyyyyyyyyt
fodya fc mwachi chiyani kkkkkkkkk
Ndinkhaninso_iyitere
hahahahaha koma malembedwe amenewa
bullets ayipanga wandale,bullets ayipanga mugabe kkk
Kkkkkkk
coment reserved!
Kkkkkkk aipanga mugabe? Kkkkkk
kkkkkkkkkkkkk koma yaaaah
Kkkkkkkk
Kkkkkk
Kkkkkkk Angazalione dziko kuphweka
kkkkkk kakakakaka kukukukuku…bulets ayichita mugabe lol
Odi ukoooo tivinepo pelete apa moyale woyeeeeeee
Kkkkkkk 2010 fc kuti azime amavutatu
Zaziiiiiii
Zaziiii kuti moti akutinamizila kuti taluza
Kkkk