Police in Dedza have arrested a health worker for raping a patient at the Dedza district hospital.
The suspect, Thomas Banda aged 29, is reported to have raped a patient who went to the hospital for a fistula diagnosis.
Banda is reported to have offered K2000 to the patient after raping her.
The victim then reported the matter to authorities who referred her to police.
Dedza Police spokesperson Edward Kabango disclosed that the suspect has already appeared in court where he has pleaded not guilty to charge of rape.
Kabango added that the suspect told the court that he never raped the lady but they agreed to have sex.
The health worker claimed that the woman charged him K2500 but he only managed to pay K2000.
Banda comes from Kambalame village, Traditional Authority (TA) Mavwere in Mchinji district.
Its inhuman,unprofessional manners are happening even work places God come and judge these fool’s
Amuchose tchito ameneyo
Shame
Mpaka kugwilira odwala fistula???
Anthu ngati amenewa amayozetsa ntchito ya zawo iwo simbali yawo ai akanakhala eni bar ilo… bolani well educated health worker can not do that…mumangeni basi 7 years enawo atengelepo phunziro..
Kumwa Gondolosi mpaka kugwilira patient. Munauzidwa kt komwela kwake nkuntcito . Nangano odwala tinthawile kt ?????
Too bad. Malawi watani kodi?
Too bad
Mmmm shame
Dedza chaka chinochi nde Yatiimilira kunena zoona!
Ooh it sounds to bad
How we can trust DR
Bwanji samakuwa patient amaneyu. Nanga bwanji analandira ndalama? Asati
Mapatient enanu mumanyanya kuthimbwidzika,asa m’mati atani
Most Counsellors, hospital attendants, data clerks and even HSAs always make these blunders. They don’t know jack shit about work ethics. Maphunziro amakhala opelewela. Charging patients for shady services, hitting on patients, stealing drugs and other government property are the least of things they like to do.
So bad
mmmmmmm koma
Malawi Akufunikira Mapemphero,Just Imagine Munthu Wakadzamkodzo Mpaka Kugwira?Bwanji Osakakoka Hule.Punish Him Hardly.
Malawi Akufunikira Mapemphero,Just Imagine Munthu Wakadzamkodzo Mpaka Kugwira?Bwanji Osakakoka Hule.Punish Him Hardly.
Zinali zogwilizana,vuto sanamvane mtengo
Jah Jah!!!!!!
Ine m’mene ndimadziwira, kugwililira sikophweka ! Ngati nkazi sakufuna sizingatheke olo pang’ono! Ngakhale nkaz wako ngat mwayambana, czingatheke kucita!
We are now controlled by the demonic powers
Healthy worker walakwisa kuchipatala sikopangila chigololo ndikolandilila treatment so akanafuna kunyenga akanapita ku bar shupiti mumatinyengela azikazathu eti ndakuziwani
ine kno akandfusa zakwathu ndmakana kt kwathu sikmalawi …..koz nkhani zonyasa zachulukisa ..kaziko kakang’no ngt kameneko kma zochitkazo mpweche ……kma pankhani iyi apolisi ndbwino amusiye koz znali zogwirizana izi ..nkazi asakane kma vto kmalawi akazi alipatsogolo kposa amuna vats y tht man arrested bt thre nothing to arrest him.
ine kno akandfusa zakwathu ndmakana kt kwathu sikmalawi …..koz nkhani zonyasa zachulukisa ..kaziko kakang’no ngt kameneko kma zochitkazo mpweche ……kma pankhani iyi apolisi ndbwino amusiye koz znali zogwirizana izi ..nkazi asakane kma vto kmalawi akazi alipatsogolo kposa amuna vats y tht man arrested bt thre nothing to arrest him.
Men at work
Kkkkkkkkk
Zoopsa
Zoopsa
Kkkkkkkk kutha kwa dziko
Sanamugwililire anagwirizana bwanj sanakuwe only de money oznt enough fo dat woman
Sanamugwililire anagwirizana bwanj sanakuwe only de money oznt enough fo dat woman
One Hausa man just called me I told him it’s wrong number, the man called me back and ask me if I know the correct number
Tiwapempherere awo madokotala kt abadwe mwatsopano ,chifukwa ngati atabadwe mwatsopano adzimuona mkaz aliyetse ngati mulongo wake ,komanso azimuopa mulungu matsiku onse.Amen
hahahahahahhaha……..
Let it serves as a lesson to those of you that are not allergic to the women’s privacy. Had I known always comes last!.
If the woman asked for sex that’s another issue of which she could not charge any money. But asking for sex to a woman he was treating, that’s rape in the sense that the woman was supposed to be treated on private parts and she could not deny him access. No apologies.
SHE Z PROSTITUTOR AMENEY APOLICE TAMUTULUTSAN AMENEYO KMAS IWE SUKADANGOPITA KU BAR BAS NDIWE CHITSILU
Thawi imene amamugwirirayo bwanji sanakuwe kuti athu amuthandize akudziwana awa
Zinali zogwirizana etiii? Shupiti!
mufuseso kuti anagwirisa ntchito condom kkkkk
mufuseso kuti anagwirisa ntchito condom kkkkk
guys tavesani akanakhala kuti amugwilira bwezi atakuwa mesa kunali kuchipatala koma anapangana Mwina sanavane penapake
Kugwirira? tafufuzani bwinobwino mwinasotu wodwalayo amapanga nawotu! komatngati samapanga nawo a Health worker ndinu achitsiru! becauz we don’t 4c love mwava?
Inform ikufunika inform pamenepo azibambo asamapezeke kochilila azimayi amimba halamu
Thus our online newspaper Malawi 24,sintha kunena chilungamo,mawa muzamva akuti health worker wapopedwa magazi ku Dedza
masiku ano akazi ambiri kwakula ndikukonda ndalama ndiye akumakamba nkhani zakugonana cholinga mwamuna afile ,kenako mwamuna akapereka zochepa amafuna apolisi kuti awathandize popeza dziko lamalawi limakondera akazi ndiye penapake apolice mufunika muzitsetsa mmene aliyese akufotokozera osangothamangira munthu.
He didn’t rape her, they agreed. Only that he couldn’t pay the other k500 that’s when the patient changed the story but anyway. Plus he’s not a doctor. He’s a counselor
a police mangani onsewo kumapeto chilungamo chipezeka
Yoh! Shame
Oooooooo http://www.malawi.com
no comment
zofoyila patient yo ….analandililanji ndalamayo …..nao awo aclearne chan? koma nyasaland eish…..mulungu abwere atiweluze ndi chipatala momwe
That health worker is a gormeless for doing such disgraceful
mhhh! ine ndikuona ngati mamunayo akunena zoona pakuoneka ngati panali kugwilizana pa awiliwa vuto linali pankhani yandalama mkaziyo sanasangalasidwe ndindalama yopelewela
atolankhani pachiphwisi panu.Kodi rape mayidziwa? ngat mulibe Nkhani muzilemba zopopa magaz osati kuononga cv ya ena.Kodi sukulu yake ndi it? nonsensical
I think ndibwino kuwelenga Kaye nkhani usanapange comment zikuoneka kuti health worker sanalakwe
Please munthuyu ndi opereka uphungu ndi kuyeza magazi who is employed by light house.He has no formal education in clinical work. Si dotolo ayi koma councillor musaonjeze kuloza zala madotolo omwe nkhaniyi sikuwakhudza.Paja layman amati aliyense ogwira ntchito ku Chipatala= dokotala ngakhale okolopa.
hahahaha worker watha zithu
mumat atani nzanu zitamuvuta..? nanu apolisi muzionesesa kaye nkhani mmene yayendela osamangofulumira kmanga munthu koz ngt analandra ndalama ndekut nayenso amafna kt ztelo koz mmene kchpatala kmazazila anthu bwanji amaleka kukuwa kt amuthandize? nde nanu apolice beware muzakalangidwa zaulele….nzanu mmati asaufile…..?
Kkkkkkkkkk eishhhh
Fake!! Patient yo amalekelanji kukuwa ngati amamugwiririra
Arrest him seriously the other mentally ill workers can learn from hi
Rubbish arrest da burger n gv him 40yrs.
Odwala ena amaonjeza kuminula
zogwiri zana izi
Kubanja la msogolo akaz akamakachosa mimba mesa amagogodedwa ? Kungot saulula
Komanso nthawi zina azikaziwa amangofuna kutipanga business,ndipo ine ndimakhulupilira kuti ndiochepa omwedi amakhala kuti agwilira,koma ambiri kumakhala kugwilizana,mamunayo akalephera kupeleka ndalama yambiri amamtembenukira kuti wamugwilira,nthawi zina malo omwe amapezeka kuti wagwilira,amakhala kuti ndikunyumba yamamunayo.Mwachisanzo,tsopano fuso mkumati mkaziyo popita kwa mamunayo amaganiza kuti akukatani iye okhala mkazi kunyumba yamamuna awiri wiri?????.PLZ KUGWILIRA,NDIMMENE WAGONA NDI MWANA OCHEPERA ZAKA 18,KUPITILIRA ZAKA ZIMENEZI PALIBE KUGWILIRA PAMENEPO,CHIFUKWA AKUZIWA MKAZIYO MAPETO OPEZA AWIRI WIRI PODUKHA PHEPO NGATI NYUMBA.Apa ndangonena momwe ine ndimaganizira pa nkhani yogwilira.
Kugwirira ndiko ndikumukakamiza munthu kuti apange zimene ukufuna pomwe iye akukana. In this story, kugwirira kulipodi ngati patientyo amakana nde dotoloyo nkumamunyengererabe komanso kumugona pogwiritsa ntchito mphamvu mpaka kumukwera. Ngakhale m’banja tikukhalamu, azimayi amagwiriridwa ndi azimuna awo koma azimayi samawulula powopa kuzunzitsa ana ndi iye mwini. Ngati mkazi wamnyumba wakana kuti lero mwambo wamisa suchitika, nde mamunawe kumukalipira, kumuwopseza kapena kumumenya kumene, pamenepa mwagwirira ndithu moti lamulo limeneli lilipo ndithu lot azimayi azikagwada mnyumba za ndende akakamizidwa kugonedwa ndi amuna awo. Mkaz atha kunena kuti watopa kuchipindaku,,sumtymes zimakhala zoonadi nithu coz naenso ndi munthu amatopa. Mkazi amatichapira amunafe, ana, kutiphikira, kuchezetsa wana, kupita kumunda ndi zina zambiri.
Inde health worker, imadya pomwe ayimangilira. enawa nkusagwidwa chabe. amene sanachimwepo amgende health worker. kkkkkkk
hahahahaha
kkkkk….awadi ndmapeto a ziko…kmatu athuwa anagwrizana koz sangayende awiri asanapangane.
kkkkk wadya uyooooooo
Malawi news
kkkkkkkkk Shame.
Iiiiiii kuchinda odwala kkk
amene mulibe ma bundle Khani ndi iyi*Police in Dedza have arresteda health worker for raping a patient at the Dedza district hospital.The suspect, Thomas Banda aged 29, is reported to have raped a patient who went to the hospital for a fistula diagnosis.Banda is reported to have offered K2000 to the patient after raping her.The victim then reported the matter to authorities who referred her to police.Dedza Police spokesperson Edward Kabango disclosed that the suspect has already appeared in court where he has pleaded not guilty to charge of rape.Kabango added that the suspect told the court that henever raped the lady but they agreed to have sex.The health worker claimed that the woman charged him K2500 but he only managed to pay K2000.Banda comes from Kambalame village, Traditional Authority (TA) Mavwere in Mchinji district
Thats true. I heard the same statement
Mesa its against ma ethics to date patients if you are a health worker?
Thanks.
He is a disgrace, justice must take its course
He’s a evil man
I always said i can only trust the doctor than a pastor but now i got no one to trust
aaaa ndekut anagwirizana…. nanga wogwiriridwayo amalandiriranji ndalamayo?
Mmmmmmmmh koma dziko lafikapo
Or Atagwilizana Nde Azipangila Ku Malo Antchito Komanso Nthawi Ya Ntchito? Yalakwa Basi He Deserve A Stiff Penalty
Big Up Ali Banda
Ndimomwedi ndithu
hee mmene fistula itulutsira chifungo chophatikizana mkodzo ndi bibi pamodzi zose ndikumatuluka patient’yo anamusilira chotani mpaka kupanga naye kawerere..zanyasi azibambo ena mmutu mwanu mwangodzaza abongololo ndithu
Ur the man
Ndipo abale mmene fistula inukhila muja mmmmmm
Kkkkkkk kma guys
Kkkkkkk kma guys
Alibe nyansi ameneyi kukhwima chani?
Mmmmmmmm?
hahaha medical ethics igwire ntchito basi nde nanga poyika female catheter zimamuthera bwanji ngat wapanga izo kwa munthu Wa fistula? Anayamba kalekale kugwililira ma patient uyo,
Go through the text,they had a mutual agreement.H/worker is not guilty.
He is double guilty… Wrong place, wrong time
Kodi nkhani imeneyi tiike mgulu lomvetsa chisoni kapena loseketsa???
kma abale chimakhala chan ufti?
ufiti umenewo
So If Health Workers Are Raping Patient, Where Will We Find A Help.
at church
You Are Right, But Hospital Has Also Part To Play.
Komaso odwala ena mavalidwe””
KKKKKKKK
Nanga umuona munthu akudwala wavala kamini ndkugona pabedi sikumuyesa doctor kumeneko olo ndtakhala ine””
even ineyo,ilakweilakwe,
I don’t think it has anything to do with dressing if its about dressing that means all girl fathers can be easily attempted by their girls or even the doctors
Koma nthaw zina ndbwino kuzipatsa ulemu malingana nd stuation imene ilili apobi ma doctor athana nanube””
Munthu akudwala basis kumupanga rap kusaganiza waziwa kuti akudwala chani
Kkkkk eeeeeeh koma pa malawi?
Tnchito Zina Azagazopweteketsa….. U Sing
Malonda anji osachotsela
Zativuta
Mmmm eish kweni guys tiyeni tipewe ku jail nkhuwemi yai
It wasn’t rape, read the article.
ma patient ena amaziyamba dala.ogwira nthito nchipatalaso ndi munthu
kkkkkkkkkkkk #fact
the best way arrest the man and let him roat in the prison wakukhozga soni tawa ntchito za hospa
Amenewo ndi mr njala mchiuno
mwina mankhwala anali amenewo kkkkkkkk mwina odwala amava nsana kuwawa kkkkkkk
Ndiye chiwewe….
Hahahaha munthuyo akudwala akufuna thandizo lamakhwala osati kumugona ayi shupiiti dotolo ukanafusila ntchito ya ubalamani zikanakuchita suit
‘Health worker’ is somehow General, Mwina nd Okolopa M’ma ward
Ndiye Healthy worker yaka ameneyo
Okolopa ndi floor worker kapena cleaner but health worker ndiokudza miyoyo ya anthu
wolemba wati health worker msamutsatse mzanu poti wapanga zolakwika, eeeh! kkkkkk
Muphuzitseni nzanu pakuti english sanayive bhobho guys sharp
aponyedwe muziwe la ng’ona ku nsanje
Mmmmmmm shameful
LOL
Mmmmmmm shameful
Mmmmmmm shameful
Nyere za mtundu wanji abale??
Mbetafe tili phwi makwalalamu ….
Nayenso patient pofika pomugwiririra amaifunamo iyaaaa
Muziyankhura ngati muli ndi nzeru pali matenda omitundu mitundu tangoganiza uli iweyo uli seriously sick nde akugwilira tingati umayifuna?
M’malo momuthandiza munthu basi kumubayaso ndi Jackson opuma kkkkkkk chimangeni chimenecho chisaipise mbiri ya hospa
ZA Masiku ano sheeeeee!!!!!!
ntchito zinyake za viyezgo, pala mukumanya mungajikola chaa kunjira chaaaa!!!
Siku Nyasaland kokha kuno ku South Africa doctor adagwiririra patient. Ngati widwalayo ndi chiphadzuwa zimakhala zovuta kwa awo ali ndi nyere ngati nkhumba.
mwina anamufulasha hevy!!!!!y
©®™ conductor wamenya passenger kkkk this s strange
nyaapapi
This is evil. Why don’t some people fear God
Doris izi zinali zogwirizana nanga mkaziyo amavula bwanji mpaka health worker kumukwera aaa palibe nkhani apa nyere inamuvuta patient
Mmmm mwikho
Mmmmm
MMMMMMMMM Koma kunyasalande pamene kwafikapa ndikumalakalaka osadzabwelanso ngakhale mau amati kwanu mkwanu koma nkhani zomwe ungawelenge nthawi zonse zochita manyazi kwambiri
waiting for comments
Aziona
Mbuzi.
iii disgraceful
oooh oooh ok