Health worker arrested for raping patient

Rape Malawi

Police in Dedza have arrested a health worker for raping a patient at the Dedza district hospital.

The suspect, Thomas Banda aged 29, is reported to have raped a patient who went to the hospital for a fistula diagnosis.

Banda is reported to have offered K2000 to the patient after raping her.

The victim then reported the matter to authorities who referred her to police.

Dedza Police spokesperson Edward Kabango disclosed that the suspect has already appeared in court where he has pleaded not guilty to charge of rape.

Kabango added that the suspect told the court that he never raped the lady but they agreed to have sex.

The health worker claimed that the woman charged him K2500 but he only managed to pay K2000.

Banda comes from Kambalame village, Traditional Authority (TA) Mavwere in Mchinji district.

 

Advertisement

155 Comments

 1. Anthu ngati amenewa amayozetsa ntchito ya zawo iwo simbali yawo ai akanakhala eni bar ilo… bolani well educated health worker can not do that…mumangeni basi 7 years enawo atengelepo phunziro..

 2. Most Counsellors, hospital attendants, data clerks and even HSAs always make these blunders. They don’t know jack shit about work ethics. Maphunziro amakhala opelewela. Charging patients for shady services, hitting on patients, stealing drugs and other government property are the least of things they like to do.

 3. Ine m’mene ndimadziwira, kugwililira sikophweka ! Ngati nkazi sakufuna sizingatheke olo pang’ono! Ngakhale nkaz wako ngat mwayambana, czingatheke kucita!

 4. Healthy worker walakwisa kuchipatala sikopangila chigololo ndikolandilila treatment so akanafuna kunyenga akanapita ku bar shupiti mumatinyengela azikazathu eti ndakuziwani

 5. ine kno akandfusa zakwathu ndmakana kt kwathu sikmalawi …..koz nkhani zonyasa zachulukisa ..kaziko kakang’no ngt kameneko kma zochitkazo mpweche ……kma pankhani iyi apolisi ndbwino amusiye koz znali zogwirizana izi ..nkazi asakane kma vto kmalawi akazi alipatsogolo kposa amuna vats y tht man arrested bt thre nothing to arrest him.

 6. ine kno akandfusa zakwathu ndmakana kt kwathu sikmalawi …..koz nkhani zonyasa zachulukisa ..kaziko kakang’no ngt kameneko kma zochitkazo mpweche ……kma pankhani iyi apolisi ndbwino amusiye koz znali zogwirizana izi ..nkazi asakane kma vto kmalawi akazi alipatsogolo kposa amuna vats y tht man arrested bt thre nothing to arrest him.

 7. Tiwapempherere awo madokotala kt abadwe mwatsopano ,chifukwa ngati atabadwe mwatsopano adzimuona mkaz aliyetse ngati mulongo wake ,komanso azimuopa mulungu matsiku onse.Amen

 8. Let it serves as a lesson to those of you that are not allergic to the women’s privacy. Had I known always comes last!.

 9. If the woman asked for sex that’s another issue of which she could not charge any money. But asking for sex to a woman he was treating, that’s rape in the sense that the woman was supposed to be treated on private parts and she could not deny him access. No apologies.

 10. Kugwirira? tafufuzani bwinobwino mwinasotu wodwalayo amapanga nawotu! komatngati samapanga nawo a Health worker ndinu achitsiru! becauz we don’t 4c love mwava?

 11. masiku ano akazi ambiri kwakula ndikukonda ndalama ndiye akumakamba nkhani zakugonana cholinga mwamuna afile ,kenako mwamuna akapereka zochepa amafuna apolisi kuti awathandize popeza dziko lamalawi limakondera akazi ndiye penapake apolice mufunika muzitsetsa mmene aliyese akufotokozera osangothamangira munthu.

 12. He didn’t rape her, they agreed. Only that he couldn’t pay the other k500 that’s when the patient changed the story but anyway. Plus he’s not a doctor. He’s a counselor

 13. zofoyila patient yo ….analandililanji ndalamayo …..nao awo aclearne chan? koma nyasaland eish…..mulungu abwere atiweluze ndi chipatala momwe

 14. mhhh! ine ndikuona ngati mamunayo akunena zoona pakuoneka ngati panali kugwilizana pa awiliwa vuto linali pankhani yandalama mkaziyo sanasangalasidwe ndindalama yopelewela

 15. atolankhani pachiphwisi panu.Kodi rape mayidziwa? ngat mulibe Nkhani muzilemba zopopa magaz osati kuononga cv ya ena.Kodi sukulu yake ndi it? nonsensical

 16. Please munthuyu ndi opereka uphungu ndi kuyeza magazi who is employed by light house.He has no formal education in clinical work. Si dotolo ayi koma councillor musaonjeze kuloza zala madotolo omwe nkhaniyi sikuwakhudza.Paja layman amati aliyense ogwira ntchito ku Chipatala= dokotala ngakhale okolopa.

 17. mumat atani nzanu zitamuvuta..? nanu apolisi muzionesesa kaye nkhani mmene yayendela osamangofulumira kmanga munthu koz ngt analandra ndalama ndekut nayenso amafna kt ztelo koz mmene kchpatala kmazazila anthu bwanji amaleka kukuwa kt amuthandize? nde nanu apolice beware muzakalangidwa zaulele….nzanu mmati asaufile…..?

 18. Komanso nthawi zina azikaziwa amangofuna kutipanga business,ndipo ine ndimakhulupilira kuti ndiochepa omwedi amakhala kuti agwilira,koma ambiri kumakhala kugwilizana,mamunayo akalephera kupeleka ndalama yambiri amamtembenukira kuti wamugwilira,nthawi zina malo omwe amapezeka kuti wagwilira,amakhala kuti ndikunyumba yamamunayo.Mwachisanzo,tsopano fuso mkumati mkaziyo popita kwa mamunayo amaganiza kuti akukatani iye okhala mkazi kunyumba yamamuna awiri wiri?????.PLZ KUGWILIRA,NDIMMENE WAGONA NDI MWANA OCHEPERA ZAKA 18,KUPITILIRA ZAKA ZIMENEZI PALIBE KUGWILIRA PAMENEPO,CHIFUKWA AKUZIWA MKAZIYO MAPETO OPEZA AWIRI WIRI PODUKHA PHEPO NGATI NYUMBA.Apa ndangonena momwe ine ndimaganizira pa nkhani yogwilira.

  1. Kugwirira ndiko ndikumukakamiza munthu kuti apange zimene ukufuna pomwe iye akukana. In this story, kugwirira kulipodi ngati patientyo amakana nde dotoloyo nkumamunyengererabe komanso kumugona pogwiritsa ntchito mphamvu mpaka kumukwera. Ngakhale m’banja tikukhalamu, azimayi amagwiriridwa ndi azimuna awo koma azimayi samawulula powopa kuzunzitsa ana ndi iye mwini. Ngati mkazi wamnyumba wakana kuti lero mwambo wamisa suchitika, nde mamunawe kumukalipira, kumuwopseza kapena kumumenya kumene, pamenepa mwagwirira ndithu moti lamulo limeneli lilipo ndithu lot azimayi azikagwada mnyumba za ndende akakamizidwa kugonedwa ndi amuna awo. Mkaz atha kunena kuti watopa kuchipindaku,,sumtymes zimakhala zoonadi nithu coz naenso ndi munthu amatopa. Mkazi amatichapira amunafe, ana, kutiphikira, kuchezetsa wana, kupita kumunda ndi zina zambiri.

 19. Inde health worker, imadya pomwe ayimangilira. enawa nkusagwidwa chabe. amene sanachimwepo amgende health worker. kkkkkkk

 20. amene mulibe ma bundle Khani ndi iyi*Police in Dedza have arresteda health worker for raping a patient at the Dedza district hospital.The suspect, Thomas Banda aged 29, is reported to have raped a patient who went to the hospital for a fistula diagnosis.Banda is reported to have offered K2000 to the patient after raping her.The victim then reported the matter to authorities who referred her to police.Dedza Police spokesperson Edward Kabango disclosed that the suspect has already appeared in court where he has pleaded not guilty to charge of rape.Kabango added that the suspect told the court that henever raped the lady but they agreed to have sex.The health worker claimed that the woman charged him K2500 but he only managed to pay K2000.Banda comes from Kambalame village, Traditional Authority (TA) Mavwere in Mchinji district

  1. hee mmene fistula itulutsira chifungo chophatikizana mkodzo ndi bibi pamodzi zose ndikumatuluka patient’yo anamusilira chotani mpaka kupanga naye kawerere..zanyasi azibambo ena mmutu mwanu mwangodzaza abongololo ndithu

  2. hahaha medical ethics igwire ntchito basi nde nanga poyika female catheter zimamuthera bwanji ngat wapanga izo kwa munthu Wa fistula? Anayamba kalekale kugwililira ma patient uyo,

  1. I don’t think it has anything to do with dressing if its about dressing that means all girl fathers can be easily attempted by their girls or even the doctors

 21. Hahahaha munthuyo akudwala akufuna thandizo lamakhwala osati kumugona ayi shupiiti dotolo ukanafusila ntchito ya ubalamani zikanakuchita suit

  1. Muziyankhura ngati muli ndi nzeru pali matenda omitundu mitundu tangoganiza uli iweyo uli seriously sick nde akugwilira tingati umayifuna?

 22. M’malo momuthandiza munthu basi kumubayaso ndi Jackson opuma kkkkkkk chimangeni chimenecho chisaipise mbiri ya hospa

 23. Siku Nyasaland kokha kuno ku South Africa doctor adagwiririra patient. Ngati widwalayo ndi chiphadzuwa zimakhala zovuta kwa awo ali ndi nyere ngati nkhumba.

 24. MMMMMMMMM Koma kunyasalande pamene kwafikapa ndikumalakalaka osadzabwelanso ngakhale mau amati kwanu mkwanu koma nkhani zomwe ungawelenge nthawi zonse zochita manyazi kwambiri

Comments are closed.