A kadaulo a zofufuzafufuza a ku sukulu ya Oxford mu dziko la Mangalande ati tsopano apeza zinthu zodzetsa chimwemwe pa moyo wa munthu. Ndipo ati si makobili ayi.
Malinga ndi tsamba la nyuzipepala ya Telegraph ku Mangalande, ati chuma chimadzetsa ka chimwemwe kochepa chabe pa moyo wa munthu.
M’malo mwake iwo ati chimwemwe chimabwela kuchoka mu kugona tulo tokwanila, komanso chiwerewere.
Akadaulowa ati anafufuza pa ma banja ena ndipo anaona kuti anthu akayamba kupata chuma, chisangalalo chawo sikuti chimakhala cha nkhaninkhani.
Ndipo iwo anapezanso kuti anthu ogona tulo lokwanila ndiwo adali a chimwemwe kudzanso anthu amene amagonana molongosoka.
Kafukufuku uyu wapezanso kuti kukhala ndi abale ndi anansi a chikondi ndi aumoyo wathanzi, nazo zimadzetsa chimwemwe.
za ziiih
So anzathuwo are rich enough to take care of their kids than mMalawi
zaziiiii ndizomwe inuyo zimakuchitikirani osatimunamize athu
for serious you guyz mwapala,mwakalanya, mwanyika any way ur stil learning.
atopa amenewo
Koma inu chichewa mumachidziwa,mawu mwagwilitsa ntchito sakugwilizana ndi nkhani
Ya I can see kuti atolankhani xool inawavuta ndithu failing to translate sex to a chichewa world
Try to write stories that are touching and helpful in somebody’s life not such that are stink/bad will just create more problems in the society, it is only a peaceful mind that brings joy in man’s life not sex or sleeping
Mukanati kugonana pakati pa Bambo ndi mai monga banja mnyumba kumadzetsa chimwemwe.Kugonanaku si chiwelewele.Mulungu ndiye anakupeleka kugonanatu.Ndipo nkwabwino.Satana naye anabwela ndi zakezo zomangogonana chisawawa zotchedwa chiwelewele.
Aaaaaaaa,kuteleko!
sex and sleeping are healthier than eating
Apart from the wrong word chiwelewele I don’t see anything wrong with this post. The fact is that nobody is obliged to believe in it
? ?
This is stupid news,idon’t like it.Please endeavour to sending us veracity news.Xool yawo ndi manyaka kkkkkk….!!
Chewerewere what do yu mean ,,?
Chiwerewere nditchimo.Anthu okwatirana sapanga chiwerewere iwe admin yankhula bwino
koma muwaphetsatu aMalawitu
This is what we call the science of the stupid, devil’s workshops.
Mwina kwa ziBambo, koma ifeyo mmmmm ndakaika
Azungu asazipope kuti iwo ndi akatswiri aziwakufufuza. University degree busy kufufuza izizi? Ifetu izi tidaziziwa kalekale. Try to make research things that at the end will assist the society.
Osati kupemphera ayi? Mayiko akunjawa ndi achikunjadi eti?
Basi zaziii moti mugwilizane kuti musise mowa buzy ndikuchindana mwafasako eti kupoli kwanu
in world new order
aaaah apa zaonetseratu kuti zolemba zatithera osapeza chochita china bwanji
so what malawi as country ll benefit through this nonsenc story? don’t spoil the reputation of journalists with ur unproffesional reporters. if u dnt hav news ideas u better writ nothng. or tel us we shud share with u
Mhu its trick amwene
Aaaaa za ziiii!!!!!
Zidzetsa chimwemwe kapena umphawi?
Mmmmmmmmmmmm
see my brus Adkon Ndi Jahman Joseph Wa Kawaja
kkkkkkkk this must be a joke
The original English story of this article says sex and that doesn’t necessarily mean chiwelewele in Chichewa. I am sure there is a better word you could have used
Last days. This is useless news
akadaulo azitulukila kumene ife tinadziwa kale kale hahhhhhh
kwambiri
Ndangodutsa
Kkkkkkk
aeeee chokama kwabiri
Alaaaaah shuuuupiti
Afufuza ku Malawi? People in Malawi to be happy they need stable peaceful country, good leadership, jobs, good salary, osati chiwerewere. Chiwerewere won’t put food on the table, only it will create fightings, killings, orphans, diseases and high number of divorce.
On Point chabe vuto ndi liwu lomwe mwagwiritsa ntchito “Chiwerewere”
Owoooo
Chiwerewere??????
Can’t you find a better word kodi nanunso?????
chauta ndiye odzetsa chimwemwe
mmalo molemba nkhani zanzeru, nkumalemba zopanda phindu izi? kusowa nkhani eti? ngati nkhani zasowa osangokhala bwanji?
Eyaaa Ndizoona.
Do you really know what you mean by chiwerewere? Please, don’t mislead people here. Chiwerewere means kugonana chipwirikiti cha akazi kapena amuna mosaganizira za umoyo wako kapena wa anthu ogonana nawowo. In English it simply means adultery or promiscuous behaviour. Is what the so called experts have found? Kapena mumafuna kunena kuti kugonanatu?
Eee zoona zake
Mulungu ndi amene amabweretsa chimwemwe osati za nyengazo.
kkkkkkk komaaaa
thats why we said the warm hart of africa so dont forget that money is a key for every thing
Without money chiwerewere sichikoma komanso opanda dollar tulo sitibwera zikuoneka akafufuku amenewo mitu yao sikugwira ntchito
please Malawi24 bring things that can help our country not this useless research
Simdazikonde konse izi.
Girls are like mangoes, while you are waiting for them to get ripe,My brother others are eating them with salt.
Khani ndimtendere wamumtima basi .Ndiye umoyo wamunthu umayenda bwino.
koma inu nde masowa zolembadi.Ndipofunika mutsekule what’s app tizikutukwanani by the voice.
Azungu ali kaliki liki kuyesesa kupanga nthenda yoti izipha ntundu wa anthu achikuda okhaokha, ndiye musamale
Kodi olembanu mumaphunzira chani kusukulu kwanu? Kapena simuphunzira mokwanira kapena aphunzitsi anu ndi mbola. Zoona mukukanika kutanthauzira nkhani mpaka kugwirisa ntchito mau olakwika? Tanthauzo la “chiwerewere” mukulidziwa?
Kkkkk! I like this comment lol!
Eti sex is not chiwerewere indeed akadati kugonana……chiwerewere si uhule kkk olo aldutery eti
Chichewa Chavuta Mtolankhani Kkkkk!!…
Ndipo inu?mmmm
Musakhale ngat mumatha kutanthauzira chingende inuyo. Mot sukudziwa kut the word “sex” is translated as “chiwerewere” while the word “adultery” is translated as “chigololo”? Iwe ukufuna uoneke wotsata uli wosatsata buanj?
Koma abale zomvetsa chisoni kwabasi.
Jason Makavelian Kayera ndichifukwa chake mumalemba zosokonekera. It is mere dullness to translate word by word from one language to another. You better go back to the classroom. Umangoloweza eti? Content mater is substantial and overrides.
Hahaha mbuli ndi zambiridi pa malawi pano. BYE!
Ahahahahaha mr jason kuzangopalaso pamene paja.
Kkkkk! mumayankhula chichewa tsiku ndi tsiku koma simukuchidziwanso.Akati sex tanthauzo lake ndi kugonana,pamene chiwerewere ndi kugonana kosavomerezeka ndipo kumachitika pakati pa anthu omwe sali pabanja,pamene chigololo ndi kugonana kosavomerezeka komwe kumachitika ndi anthu kapena munthu amene ali pabanja ndipo amazembera mwamuna kapena mkazi wake kukachita chigololo panja
Ama user Google translate app osadabwa
Ife ma africa tinayitulikila kale kale
So wat??????????
Mhuuuuuuuuuu…
:v :v :v pungarisation.com
Mkazi ndi mwamuna amene ali legally married akamagonana sichikhala chiwerewere. It’s irrational kugwiritsa ntchito liwu loti chiwerewere in this article. Coz the moment munthu wangowonapo mawu oti chiwerewere nkhani yo yakwiyitsa kale okonda zopemphera yet the article is just as clean as a health education.
Komatu wolemba nkhaniyi sanalakwitse, inuyo amwene nde mukulakwitsa!
awadi ndi akadaulo ndi kuona ngati kufufuza kwao mkoona ai ndingoti ulemu wanu inu akafukufuku
KKKKKKKKK
Money is key
hahahaha ine monga black man ndinapeza izi kale kale iwowo akufufuza kumene???? infact its true…no one cn ignore it
Hahahahahahahaha…….koma guys!
When a white man creates a phone and you video chat with your brother you call it technology but when your Grandmother in the village uses a mirror to see you while you are hundreds of kilometres away you call it witchcraft. It’s about tym we value our own Africa products.
kkkkkkk a fact bro
3:) 3:)
As long as it doesn’t harm others
the problem our grannies use them in darkness
On Point bro
Kkkkkkkk koma zinazi
Agree with u 100% bro
? ?
kkkkkkkkkk sexy
Ine Ndinachita Chi….. Lero
Kkkkk
Pankhani ya chiwerewereyo bailulo likuti chani, zoona padziko lapasi pali malamuro koma nakoso kumwamba kulimalamuro