Man arrested for wearing camouflage

470

Police in Mulanje district have arrested a man for wearing a Malawi police camouflaged top.

Mulanje Police spokesperson Gresham Ngwira has confirmed the arrest of Jonathan Maseya who was found wearing the police attire.

Ngwira said Maseya was arrested on Friday and when asked what his profession is and how he got the uniform he failed to give convincing answers.

Currently, the suspect is in police custody and when investigations are through he will answer the charge of unlawful possession of articles provided to police officers contravening section 151 of Police Act.

Maseya hails from Kadewere village, Senior Chief Mabuka in Mulanje district.

Meanwhile police have advised the general public against wearing police uniforms or unlawful use of its equipment.

The law enforcers have said that anyone found will be arrested and the long arm of the law will be against him or her.

 

Share.

470 Comments

 1. Aliyense amadziwika ndi identity yake, so ngati nditenga ID, yanzanga anthu aziti chani?? It’s like am impersonating, umene ndi mulandu!!!!!!

 2. This behave is not good just bcz know were freedom time aliyese Ali ndiufulu enanu tchito mumayitengera pangong’o musamaone ngati kusakhala wa Police ndiumburi ayi koma ulondao enafe sitimaufuna mulungu adzakulangani muzisamala

 3. If u r ignorant just shut up dot mek nonsense comments, adzavala nawonso akadzalowa police bt for nw amangidwadi. Kagureni Dzamu China mudzivala.

 4. a Malawi uphawi unatipweteka kwambili,that’s why timangomangana zilizonse,kuno athu amavala chisawawa,koma ngati ukugwiritsa nchito molakwika ndiye amakumanga

 5. POOR COUNTRY U HV TO DIFFERENCIATE THESE CAMOUFLAGE UR TTALKING ABT DO U CAUMOUFLAGE THOSE COLOURESS U BUY FRO CHINA THEY TOKING ABT THE REAL ONES

 6. Really misunderstanding is similar to madness. Listen you deaf commenters, dis crook has arrested through found wearing Malawi police comouflaged top not just comouflage once again Malawi Police Comouflaged Top. So r u condemning police for arresting dis idiot? Where dd he got dat top? Is it sold in shops? Why don’t you appreciate the well done job by the police?

 7. Tiyeni uko apa…..kunotu siku RSA/ Watever u may thnk,dis is Malawi,ok? So whether u r outside ds country don’t dare compare Nyasa laws to where u r. U can’t compare rugbay rules to football rules, they r totally different. Ife tili kunofe(nyasa) ndife mbuli chabwino ndiye anthu ngat amenewa amatibera so big up Police, deal with them!

 8. Just like that,Zovala! will bring Volovolo in Malawi. Am in Namibia now! Bvumbwe Police Station bewarw of this, passed the same insdent where by a Police officer took a cap,Chinese cap from me!!! will deal with him!

 9. Aaaaaa ndiye dzichaninso idzi ndidakomana ndi asilikali a malawi army pachingeni nditavala kabudula woteleyu mu monkey bay mangochi tili ndi marline trooper timacheza nayo titavala zomwezi ndipo amachita kudzikana kuti si uniform yathu imeneyo dzamngofanana ikadakhala uniform ukadawonapo nyota kapena chizindikiro cha usilikali ndiye kaya mwina malamulo akumulanje akutero poti paja tisayiwale kuti ndidziko palokha kkkkkkkkkkkk

 10. Wel done officers ,,,, they must respect the law ,,,,,ithink he was trying to comitte crime ,, investigations still continues any one found will be arrested at charged for committing crime through police unform ,,which is realy acusing police officers

 11. Chovala chili chonse chimasonyeza zomwe zikuchitika amalawi tieni tilemekeze udindo wa anzathu.chifukwa ndi ife tomwe amalawi timayakhula monyoza.let me ask,kod minthuyi akanapezeka akuba tikanati amabayo ndindani?pamenepa sitikanati apolice ndiokuba?apolice arrest them pamenepa mukukonza mbiri yanu pajatu amati fumbi ndiwe mwini.

 12. Zonsez Zmacitika Cifukwa Ca Umphaw,Njala,Matenda n Nsanje…….Malamulo Oletsa Kuvala Camo Ndi Opusa Kwambir………Ndipo Omwe Anapeleka Lamulo Lmenelo Anali Citsilu Ca Munthu……….Maiko Anzathu Wina Aliense Atha Kuvala Camo Wa Asilikali Enienio Koma Smudzawaona Asilikali Akulimbana Ndi Anthuo Ai………Ndipo Asilikali Amaiko Anzathuwa Samapanga Zopusa Zija Amapanga Asilikali Akwathuko Zomangolimbana Ndi Anthu M’midzi Kaa M’ma Town Ai……..Amagwila Ntcito Yao Mwadongosolo…………Osat Kungot Mukakhuta Mowa Plus Camba Kumangomenya Anthu Osalakwa……….Omwe Anacita Asilikali Aku Malawi Uja Ndi Umbur Weniweni……..M’malo Momagwila Ntcito Yoteteza Dziko Amalimbana Ndzithu Za Ziiiiiii………

 13. Amafuna azikavala iwowo kusowa ndikusowa ma uniform kwaoko,if sum1 is wearin sumtyn written malawi army,malawi police,immigration officer e.t.c ndye ali ndi mphanvu yomumanga,there’s no democracy in malawi,we r nt free at all,but they makes us thinks we’re.

  • I think you should get a copy of your countries constitution. Kutereko umangokhala osaziwa malamulo adziko lako? I feel pitty for you though you look like well educated. Mxiiii

 14. Ignorance police ur failling 2 arrest thugs n corrupt pipo ur arresting some1 jst for dressing shame wake up come n arrest me here in SA coz i also have a camouflag

 15. Ine ndikuti awamange kumene chifukwa camofreji wa apolice ngati akufanana ndi yemwe anthu akuvala thats a very big mistake,tisiyanitsa bwanji kuti awa ndi apolice awa ndi anthu wamba?komanso monga kuno ku RSA ANTHU AMAVALA CAMOFREJI KOMA NGOSIYANA NDI WA ASILIKALI ATHA KHALA OFANANA ATHA KUWAMANGANSO
  ;
  ;INU MUKUTI AKULAKWA KUWAMANGA NDINUTU OSAZINDIKIRA

  tizisiyanitsa bwanji apolice ndi munthu wamba,? Amangeni amenewo

 16. osakamba zambili apa,am not a police man koma kuvala zapolice usali wapolice or army ndizolakwika aliyense amadziwa zimenezo koma matama ndi kuyesana.

 17. Akuba wokhawokha agwirana.Lembanani chabe ntchito mnzanu akusilira.Mmangolembana pachibale.Tikhalitsepo malaya akuwaya anatuluka bwanji?Alipo anakuuzani kuti ake anasowa?Sono ngati inu mukulephera kuteteza zovala zanu za muthupi nanga kuli ife mayine!!!!!

  • Kanyamule matumba iwe sukudziwa kuti malamulo amaikowa amasiyana? Anthu ena amati akavala choncho mmesa amabela anthu nde ukufuna azibale ako unasiya kunowa atetezedwe kumene? Kuno mkumalawai, amamanga amphawi okhaokha olemela ayi!

 18. What law? Your just lucky kulibe anthu olimba mtima. Laws my ass! Ati section’s 191. Olo itakhala 411, 911 , 997 NDE tiope? Akuba nde a police WO . osaletsa bwanji even zogulitsazo ? Zaku …. Mbo. Osagwila anapha chasowa, ngauje OR Focus once your bunch of of unsolved Cases. Useless service MPS USELESS

 19. Koma ulendo uno enafetu tikayiwonadi mawula. After mwano ndi a police taphuzirawu. Lol! ‘Mpaka kumaumanga munthu, mavi ankhani yake imeneyi. Chamba2 sopano

 20. Hey guys!!!! Let’s go straight to the main point, the system of using camouflage is not allowed in mpanje, we all know and remember very well. If bafwethu la emzansi are being allowed to use such stuff, that’s y people are crying each and every single time coz others they do get advantages of doing robberies in the name of government. If it’s allowed let be maybe it is their culture who knows? ???? Paja2 amati mwai wa galu sungagonere munthu panja.

 21. Kukhazikika moyo wauchitsilu inu zoona munthu akamangidwe chifukwa chachovala. A police akwathu munakhala bwanji kodi? Ndinu anthu omvetsa chisoni koopsa bwanji osakamanga omwe akumagulitsa bwa????????

 22. Ameneo musatuluse bicoz anthu otelowo n amene amakha akutisautsa mtendere muma location momwe takhala ndie chondex1000 musamvele zonena za anthu

 23. komaso anthu ambiri mukapta pa RSA mumaona ngat mwaphuzira? ngat munachoka ndi umbuli ku malawi sukulu itakukanikani tamangohedani matumba ku joniko osati kutsutsa malamulo adziko la malawi. pajaso a misala ambiri ku joni nd a malawi, kuyenda mmabini kutoleza. malamulo asiyen agwire ntchito osati zilizonse kutsutsa. komad umbuli nd democracy siziyenderana.

 24. Poti amatigulitsa ma police attire ndi apolice omwewo, muyende mumakukamu ndi zambiri, amatigulitsa ndi eni ake apolice omwewo, munthuyo anangosangalasidwa kuvala siokuba!

 25. Fuck that munthu aliyense ali ndi ufulu wakavalidwe nd zovalazo zimangofanana mitundu but za a police kapena za a silikali zimakhala ndi zizindikiro zake. ..Fuck this lamulo

 26. apa pali anthu opanda nzeru, cifukwa chani mukufanizira malamulo a ku Malawi ndi a maiko ena? ngati boma la Malawi sililora civilian kuvala comouflage each and every citizen has to abide,,, osatenga malamulo a maiko ena kuika ku flames ayi, ine ndili ku Mozambique ndipo kuno comouflage ali paliponse anthu amavala mwa ufulu koma ndimamvetsetsa cifukwa ndikudziwa kuti Malawi ndi Mozambique ndi maiko osiyana,,, good work by Malawi police and thats a good law by Malawians

 27. Malamuro opusa amenewo, mmalo molimbana ndi ka ndalama ko kuti mwina kakhale bwino koma busy ndi za ziiii,

  Dziko limeneri lafikatu pa Zimbabwe, just imagen mpaka 2000 nakhala note imodzi zoona????

  Pompano mukhala ndi 10 000 chipepala chimodzi

 28. Fuck that, that law must be amended, if someone rob by lieying that he is police then police are the people who rob the people, release the person I can even mention people in Malawi who are not in military but they posses the camouflage clothes but yet they are not attacked in any way just because they are artists, ukuba ndinu a police

 29. Koma tizitha kusiyanitsa malawi ndi maiko ena,

  Malawi chitukuko chawo ndi chimenecho,

  Taonani pa AS pompa apa munthu wamba amatha kuvala even za asilikali ndipotu asilikali anuwakewo ndikumadutsana nawo ma Game , ma Shoprite , ma Spar, ma Pick n pay mu koma samamanga munthu kamba kovala chovala

  Koma eti malawi ndi South Africa sangafanane pakuyamba kulandira ufulu, pamenepa ufulu uli patipo?????

  Malamuro ophusa ngati amenewo akufunika kwasintha,

 30. Malawi w’ll never be sorted.Even that rubish uniform or whatever u calle .why you fail to arrest chaponda and other cashgaters. Instead of focusing to those people who lost their lives on road accidents,you busy watching what people wear in daily bases.

 31. Basi…chimanga…chikutuluka kunja…mukukanika
  Kugwirapo tchito….koma…zopusazi….yet u have never
  Gone to war…timasalare..tonyenyekaso ngat timeneto..

 32. Aaa malawian poliçe insted of arresting pipo thy r invloved in a cashgate issue ur bizy arresting savege pipo u thnk it is ur victory tht it is crazy ok

 33. police yaku Malawi kumanziva u camouflage fyi a police muzivala ma kabudula osoka aja. camouflage ndiya ma soldiers. Sitingasiye kuvala camouflage…. Takupasani ntchito mutimange ovala camouflage ife hahahahaha

 34. Lamulo ndi lamulo… mwina apolice akusekelelani.. koma ife ma soldier tikampeza wina atavala zimenezi kufuna kuphwekesa ntchito ya ife.. tiphwanya mutu

 35. How is it that some policemen / women don’t arrest people (civilians)who wear such clothes in other parts of Malawi especially in Mzimba.

 36. I have understood that these media post a story just to get likes and comments. izi ndizammalamulo, police z there just to force the laws, palibe chachilendo apa.

 37. Wapolice Mukuona Ngati Wangodzuka Lero Kukamanga Munthuo,,,mesa Wagwilitsa Ntchito Lamulo Pogwila Ntchito, , , Mungovomereza Mwaziwako Kuti Kuli Lamulo Limeneli,,,chimakhala Chani Ufiti Chani,,

 38. By Bright Malenga July 8, 2017

  Police in Mulanje district have arrested a man for
  wearing a Malawi police camouflaged top.
  Mulanje Police spokesperson Gresham Ngwira
  has confirmed the arrest of Jonathan Maseya
  who was found wearing the police attire.
  Ngwira said Maseya was arrested on Friday and
  when asked what his profession is and how he
  got the uniform he failed to give convincing answer

  Currently, the suspect is in police custody and
  when investigations are through he will answer
  the charge of unlawful possession of articles
  provided to police officers contravening section
  151 of Police Act.
  Maseya hails from Kadewere village, Senior Chief
  Mabuka in Mulanje district.
  Meanwhile police have advised the general public
  against wearing police uniforms or unlawful use
  of its equipment.
  The law enforcers have said that anyone found
  will be arrested and the long arm of the law will
  be against him or her.

  enanu simuwerenga nkhani yonse mumangolalata,,,you make noise as if u know what u are talking,, Malawi at 53 eeeeesh ,,

 39. Zausilu Basi Mwasowa Anthu Owagwira Eti Tili Ndi Oyimba Ambiri Amavala Ngini Yomweyo Koma Osawagwira Bwanj Monga China Lucius Banda Ndi Zake Uyu Timati Charles Msaka Chifukwa Choti Alindi Ndalama

 40. ine area 23 ndimavala camouflage andi namuza ngwira kut ufuse komwe mnaitenga but is shupid mwapha kale ana 8 what do you want akabawi …. amphawi (apolice )mutayeni @#dpp boma lanu laukape .laumphawi. la kupha . losowesa mtendere

 41. ine area 23 ndimavala camouflage andi namuza ngwira kut ufuse komwe mnaitenga but is shupid mwapha kale ana 8 what do you want akabawi …. amphawi (apolice )mutayeni @#dpp boma lanu laukape .laumphawi. la kupha . losowesa mtendere

 42. Anthu simukonda dziko lanu,komatu kuti akugagadeni muthamangira kupolice konko,ena ndiye mungoti kutheba eeee theba,muzikhala konko osadzabweranso kuno,amavalira matama akudziwa kuti nzolesedwa,lamulo ligwire ntchito

 43. Enanu muli ndi maonekedwe abwino, koma ndinu opanda nzeru, iyeyo ngati akufuna kukhala wa police osangokayiyamba bwanji, anthu ambili anabedwapo ndi anthu ovala za police, kungoti lamulo lodana ndi mbava ambili mumalidandaula, wina aliyense amene akuti amasulidwe nayenso ndi mbava, alinazo zovalazo, akufuna kuti adzitibela nazo, apolice chonde mukamugwila mudzimu menyako pang’ono chifukwa amatizunza

  • Iwe malamulo adziko samafana, zovala zonse zili padzikozi osavala chikakome ndi cha police, umbava eti, mumangidwabe olo mudandaule, ndipo silisithidwa, ngati ukukumbuka pazalewa anagwira munthu atavala za yonse, anali ndi chamba. Ndiye adziwaleka? Amangidwe basi

 44. Kusonyeza kuti camouflage yemwe ndikuvala mwaufulu kunoyu. Yemwe akugulisidwa mwaufulu kunoyu ndikabwera kumudziko ndimuotche? Kapena uyo anali special camouflage wokhala ndi ma stars ndi mayina? Koma Malawi sazathekadi eish!

 45. Stupid police that just is a piece of garmet nothing wrong with it we must re amend it where is freedom of dressing wake up u so called malawi police

 46. Why most Malawi artist they don’t get arrested when they where camouflage when they perform on stage? ..ndakhala ndikuona oyimba ambiri Ku Malawi amavalatu zovala zimenezi koma simuwagwira bwanji..inuso a police makhala muli konko …masuleni ameneyo siwolakwa alakwa ndi omwe amapanga clear katundu ma boarder mu

 47. Akawamange amene anamugulista zobvalazo becuz chinapezeka pa nsika kaya shop iye anagula and akubvala ndi ufulu wake why kumumanga ….ndipo lamulo limeneli sitimaliziwa enafe atire imeneyi tilinayo mukakhome mu ma bail kaya ma shop malamulo okhuzana ndidzobvala

 48. Commenting without knowledge of what you are commenting the tradition of many Malawian social media zatipeza mochedwa amvetsetseni basi kkkk. Garbage in garbage out!!! I rest my argument!!

 49. Ok tanva koma ndilamulo lathawi yau samunda zinthu zasintha lichoseni kodi athu akupha albino aja akumavara camofreg ,mulimbana ndi ogulisa kiwilele angontumizira azukulu ache ku joni ,mbava kuzisiya zikubera boma aaaa mukhare madolo apolice osamanga ajao bwa???#jst sayng

 50. Don’t comment what you don’t know,,kuthamangira kuyankhula yet sukudziwa kanthu…Police camouflage is special for Malawi police ndipo sapezeka pansika ndiye kuvala usali attested member of Malawi police ndimulandu..Kazivalani kma tikumangani tikakupezani

 51. Why are men arrested and women are not. I have seen many women putting on camouflage but they are let Scot free while men suffer all the abuses and torture even when they put on a Cap.

 52. A lot of people wear camo. It’s just more of a style instead of military. On the side note, I love camouflage when am fishing, you know… So the fish don’t see me coming… yahh.

 53. Amalawi penapake tidzithako kumatsatila malamulo adziko lathu ngati palo lamulo lakuti munthu wamba asamavare camouflage ndibwino kumvera ndikulemekeza lamulolo ndiliti lina anthu anayamba kumamangidwa ndinkhani mgati yomweyi ndiye tiziti sitinamphunzilebe kuti tikavala camouflage titha kumangidwa nazo ngati tili kumalawi???zotengera tengelazitu zikatiponya kophopho makamaka anzathu omwe tili ku SOUTH AFRICA chifukwa anzathu kumeneko amavala camouflaged momasuka ndiye tikabwera kumudzi Kuno mukumathamantha kuyamba kuderera malamulo kuiwala kuti dziko lililonse limakhala ndimalamulo ake…

 54. Zats nonsense kumalawi now kumanga munthu poti wavala camouflage cloth za usilu eti we are still under ignorant mind wake up malawi camouflage it’s on fashion now please kkkkkkkkk koma kusauka kwa dziko kupangisa anthu onjoya with our dressing fuck the malawian police leave him. Stupid police.

 55. I don’t know who will redeem Malawi from the case of ignorance. In other countries people wear anything from their Wardrobe. The only difference is when it comes to showing the professional ID that ur a Police Officer or A Soidire. People wear those things like normal

 56. Achitha bwino kumanga muthu otero ndi amene amaipisa mbiri ya apolisi kuba kwadyera madzira anthu Kumudzi kumwa mowa atamvala uniform yo kunaminza kuti ali paholide kwawopsesa anthu izi ndikuba basi .Ndinawelenga newspaper yochokera Ku South Africa bamva zinapanga galimoto ngati zapolisi anamangidwanso .wakuba ameneyo akhale kudede zaka 5

 57. ITS understandable if the person wear full uniform with the reble of malawi police he dsev to be arrested but if h has wear camoferge without malawi polic log the ur killing it freedom

  • Isaac, wayankula ngati wizindikila
   Kungoti uniform imenetija iri ndika special design koziwisa kuti ndiyawo, coz anthu amata kuba nkuka Xhosa logo, nde chani belo chimaziwikaso

 58. Kwathu ku Malawi nzoletsedwa zimenezi. Koma ndi udindo wathu ngati nzika kukambirana ndi otiyimirira ku nyumba ya malamulo kuti akakambirane mwina nkusinthako lamulori. Kung’ung’uza apa nzosathandiza konse..

 59. Who told you that any camouflage is prohibited? Kumadzisata kaye before commenting. U can not expect a civilian wearing police, army or prison regalia get away wth it SIZINGATHEKE ZIMENEZO. If u want make your own country and laws.

 60. Vuto ndi boma lamalawi limalemba ntchito a police oti Ali ndi school report zimenezo ndi zomwe a police athu amakhala ndi u mbuli wakagwilidwe kantchito yawo .funso kumati bwanji boma limalora makapani opanga zovala kumapanga zovala zofanana ndi uniform ya a police? bwanji ngati malamulo a dziko amalesa kuvala zovala zotelo zikuvuta pati kulesa opangawo.wakeup Malawi osagulisa mtendere kamba kamnsanje

  • That initial comment was in response to what somebody argued on this post. The person said it’s prohibited and even gave a section.
   I only avoided responding directly to that comment coz I wanted to try avoid anthu opanga argu mopusa ngati iweyo. People who are not critical.

  • Check this comment by Evelyn Grace Kachingwe:
   ‘For Starter s,Section 191 of Malawi Penal code ,Wearing ANYTHING which resembles Police uniform is an offence Punishable by Law.
   AMALAWI TIZIKONDA KUWERENGA MALAMULO A DZIKO LATHU,and this offence has been there since 1911.

   Don’t comment what YOU DONT KNOW’

 61. HE was put on the police attire this is a big case wen you see some writing no trespassing you should know that this pkace is prohibited under the law his not suppose to put on Malawian police uniform or any attired for the security uniform of Malawi government unless putting on un government uniform if you don’t belong to them you are not one of them

 62. Enanu kaya muli SA,but home sweet home,RESPECT THE LAW OF YOUR COUNTRY.NO MATTER WHERE YOU CAME FROM, READ SECTION 191 OF MALAWI PENAL CODE,and come again to comment, YOU can download the pdf of the law pa google be SMART

 63. basi ndizomwe angamachite??? zausilu kukanika kumanga akuba ndalama mboma ambiri akungoyenda free mkupangisa inu nomwe kulandira malipiro mochedwa moti mufufuze kt waphesa anthu ku stadium ndani kt ngozi ikuchitika bwanji pa mseu katangale atha bwanji etc km mukulimbana ndi munth oti anangovara nt fair mesa mulanje kumazizira inu simudziwa???? zausilu….

 64. basi ndizomwe angamachite??? zausilu kukanika kumanga akuba ndalama mboma ambiri akungoyenda free mkupangisa inu nomwe kulandira malipiro mochedwa moti mufufuze kt waphesa anthu ku stadium ndani kt ngozi ikuchitika bwanji pa mseu katangale atha bwanji etc km mukulimbana ndi munth oti anangovara nt fair mesa mulanje kumazizira inu simudziwa???? zausilu.

 65. Ine ndili nawo top and down camoufrage tsiku londigwira simuzaphulitsa teargas koma live bullets ndipo ndizakubwezerani ndi live bullets mukuzolowera comoufrage yanu ndi yosiyana ndiyomwe anthu amagula mushop,muletse ma shop ogulitsawo

 66. For Starter s,Section 191 of Malawi Penal code ,Wearing ANYTHING which resembles Police uniform is an offence Punishable by Law.
  AMALAWI TIZIKONDA KUWERENGA MALAMULO A DZIKO LATHU,and this offence has been there since 1911.

  Don’t comment what YOU DONT KNOW,

 67. This shows how ignorant Malawi people more especially the so called leaders, cause that’s a normal clothes and there’s many companies that makes those type of clothes and shoes.

  • Muvesese chizungucho akut wearing Police Comourflage top ndie sindikuxiwa ngat kuli company ina kumalawi yomwe imapanga zithu zimenezo hope zapolice ndi special thus y muthuyo wamangidwa

  • They all look the same, Ndi identity yokha imene imadziwitsa kuti uyu Ndi wa police Kapena ngati inalembedwa the duty number of an officer inside of the shirt or top. Nde amene watumidza nkhaniyi adzipeleka Ndi ma details onse kuti anthu tidzimvetsetsa kaa

  • Mr phiri mukundiuza kuti inu kumalawi kuno simunalowepo mu shop ndikupeza top ya comourflage ? kkkkkk OK ndikutha kukuvesani , chovala chaku ntchito chimasiyana ndi chovala wamba,ngati uniform yathu ya police akuno kwathu ilibe chizindikilo chosonyeza umwini wachithucho ndiye vuto ndi boma lathu ,mwachisazo,,zipewa ndi zovala zamakono za anthu ovina (beni)zimafananila fananila ndi uniform ya a police athu koma sipakhala vuto lililonse chifukwa zovalazo zilibe chizindikilo cha Malawi police. Komanso ngati munthuyu anavala comourflag oti Ali ndi chizindikilo cha Malawi police ndiye ndivuto lake

  • By Bright Malenga July 8, 2017 Police in Mulanje district have arrested a man for wearing a Malawi police camouflaged top. Mulanje Police spokesperson Gresham Ngwira has confirmed the arrest of Jonathan Maseya who was found wearing the police attire. Ngwira said Maseya was arrested on Friday and when asked what his profession is and how he got the uniform he failed to give convincing answer Currently, the suspect is in police custody and when investigations are through he will answer the charge of unlawful possession of articles provided to police officers contravening section 151 of Police Act. Maseya hails from Kadewere village, Senior Chief Mabuka in Mulanje district. Meanwhile police have advised the general public against wearing police uniforms or unlawful use of its equipment. The law enforcers have said that anyone found will be arrested and the long arm of the law will be against him or her.

  • Palibe amene Ali ophunzila, kwambili malamulowo ndikonko Koma ,nanga anaphunzitsa kale anthu mawonekedwe Kapena kutsiyana kwazinthu dziwiridzo ngati? Mpakana tayamba khala mbuli tsopano kkkkkk.

 68. Zachamba basi nanga ngati inali ya malemu ankolo ake,Malawi change its high time 53 year independence your still doing things for 1999 aaahhh am bored with Mulanje police

 69. Koma bola la kumpanje limazisata zakamangidwe ka munthu komanso ndondomeko yowapezela ntchito ndikumasowa abwere kuno kamofoleji wakeyo azasinkhasinkha atasiya job yakeyo chifukwa cha free style

 70. all of u criticizing police u dnt knw that police are law enforcers .these laws are made in pariament with there penaties .kkkkkkkkkkk plix mmalawi go to xool and atleast know smthing abot laws . kkkkkk poor malawians . blame the pariament for making the law and not police

 71. That’s really bullshit here it’s all over in the shops n its in fashion zomangana mopusazo zitheeee zovala zanu zili ndi #, iyaaaa

  • I think the word bull shit apply to you because ukuoneka wozondikila kunja kokha koma mkati mwaiwe muli empty.
   Chovala chapolisi olo uchotse logo chimaziwika, zamu shop nazo zimaziwika. Nde muziyamba mwaganiza musana lembe ma comment anu opanda mdundo pa gulu. Mxiiii

 72. Kuno ku (RSA)Durban town mutatenga sewu we queen street muli shop ya African hardware adzilonda onse a shop imeneyo dzovala dzake ngat dzomwedzo mukwamangila nawo anthudzo kuno dzovala adzilonda. Some rubish thing plz plz don’t post in English

 73. KKKKK, KOMA POLICE AKU MALAWI PAMENEPO WAPEZA NTICHITO. KOMA ABALE KUNO KU SOUTH AFRICA NDIYE KULI MA MIRITARY SHOP AMAGULITSA NYANGWITA ZOSE ZA USILALI ZA KALE NDI MA TENT WOMWE. POGULASO OSATI ZOFUSANA KUTI IWE NDANI AI. KOMA NA MAIKO ATULO NDICHOMCHO BASI.

 74. Mmmmmmm dzamanyadzi dziko lanthu, komatu ndidadzanenatso poyamba kut Malawi 24 nkhani dzina mukamapanga post plz stop post in English coze kunoko kwa aluya kuno amatitseka akamawerenga nkhani dzanu dzoputsadzo, dzovala idzi kuno dzimapedzeka palipose

 75. What’s wrong with wearing camouflage? Inali ndi nyota? I think it’s time Malawi police should have police IDs that they should show to prove their poloce-ness. Camouflage is just a clothing anybody is entitled to his freedom of dressing.

  • awaso nda chitsiru bwanji sadziwa kuti zovara zinazi zimaletsetsadwa ena amapezerapo mwai obera anthu ufulu munenawo muuganiza mwa umburi ndi 53yrs muganizabe mwa umbiri zoona?

  • muuzeni ameneyu achangamuke tulo timuthere. ma camouflage aife anthu wamba alipo ndipo amasiyana ndi apolisi kapena army uyo wavala ya polisi.work up ma men!!!

  • was the man wearing a police uniform or camouflage..i don’t c anything wrong with a camouflage but police uniform i do understand…with tht said why do malawi police wears camouflage…?

  • Iwe kumayakhula ngat munalowa class mwanva Wapolice aliyese ali ndi ID ndie sindikuxiwa kut ID yake ukunena iwe ndiyitiyo? Komanso kuvala Comourflage usali Wapolice kapena msilikali ndi mlandu even kuvala uniform ya xool koma usali ophunzira Wapa Xool imeneyo ndimulanduso koma vuto liri kumalawi ndiloti athu ambiri sumuxiwa malamulo ndie thus y mumaphwekesa zithu

  • All you telling me I don’t know what I’m saying tell me a law or statute or section in the Malawi Constitution that says “a man shall not wear a camouflage clothing”.

  • If you read carefully, the article says a man arrested for wearing camouflage. Not arrested for stealing or threatening people using a camouflage

  • Did the guy wear a police uniform or a camouflage.? If he just wore a camouflage no matter how scary it looks there’s none wrong. Y’all need to reason not just talk. If just wearing a camouflage is wrong then kuvala jombo is wrong cause police use those shoes. What matters is the “nyota” on the camouflage otherwise it’s just a clothing.

  • By Bright Malenga July 8, 2017 Police in Mulanje district have arrested a man for wearing a Malawi police camouflaged top. Mulanje Police spokesperson Gresham Ngwira has confirmed the arrest of Jonathan Maseya who was found wearing the police attire. Ngwira said Maseya was arrested on Friday and when asked what his profession is and how he got the uniform he failed to give convincing answer Currently, the suspect is in police custody and when investigations are through he will answer the charge of unlawful possession of articles provided to police officers contravening section 151 of Police Act. Maseya hails from Kadewere village, Senior Chief Mabuka in Mulanje district. Meanwhile police have advised the general public against wearing police uniforms or unlawful use of its equipment. The law enforcers have said that anyone found will be arrested and the long arm of the law will be against him or her. uziwerenga kaye nkhani yonse usanalembe zopanda mutu zakozo ,,malamulo umaziwa iwe nde atiwo??s ,,,

  • If you break the laws of a country and get caught you wll be arrested, laws are not the same in all countries and police and army regalia is protected by the law and it won’t be abused in anyway. Whether if you may twist words to suit your situation, it won’t work, umangidwa basi!

 76. Ntchito yabwino apolisi ndi mbava imeneyo ikufuna izikaba pomaopseza anthu kuti ndi wapolisi.Chita nayeni aziwe kuti mumaivera kuwawa kuti muvale uniform imeneyo

 77. akawina mlandu pa khothi. kodi ayilembapo ‘malawi police’? inapangidwa kuti? apolice akaonetsa top ina yofanana ndi yapakaunjikayo? never! after releasing hin, akawasumiranso! kkkkk.

 78. kodi boma lathuli kumakhala kusazindikira bwanji? m,mayiko akwanzathu zovala ngati zimenezi zimapezeka m’mashopu zili mbwembwembwe,amagula namavala without being questioned by police or any higher authority,mukukhulupilira kuti mumanga anthu angati poti pano zangolowa mu fashion,Lol come and arrest my sofa too, chifukwa inapangidwa ndi materias angati uniform ya apolisi

 79. Hahahaha!!zaziii mmalo mokamanga okuba ma million. akulimbana ndi ovala comeflage Malawi sizathekaso ife mayiko ena timavala no questions

 80. Vuto lagona pakuti amagulitsa okha maunifolomu apolicewo.Munthu wamba angayipeze kuti uniform ya boma.