Minibuses are back on the roads of Blantyre today after intra-city public transport was disrupted on Friday.
A strike by minibus drivers and conductors led to chaos and disturbed business.
But Minibus Owners Association of Malawi (MOAM) general secretary Coxley Kamange has promised that they will resume business for transport in the commercial city of Blantyre.
Kamange further faulted drivers for being violent during the strike.
The drivers and conductors staged a strike that turned to be violent as they demanded a reversal of penalties recently introduced by Directorate of Road Traffic and Safety Services.
Teargas canisters were used to disperse the rioting drivers and conductors, a situation that witnessed some roads not being impassable.
The protests witnessed some minibuses being smashed for being found on the roads.
The angry drivers and conductors also torched three police units in residential area of Machinjiri in Blantyre
vutotu ndi atraffic amaonakuti drive watenga athu ambili ndie akamuyimisa aziti tangopanga kenakake ndie kupusa kwake akaaasa
Kkkkk kl
koma boma likupanga za!!!!! nanga mesa tageti yabwana sikukwana.chifukwacha atrafic akumangoti tapanga yamidoli zuwalonse
Ngati simumafuna kupanikizika min buss just buy your own car but don’t say min buss driver are the one who makes roads accidents aaa bull shit!! amene amagubuduzika ali wokhawo?ngati kunalembedwa kuti mudzafa ndi ngozi ya pa nsewu mudzafa basi or mulikwanu mudzagundidwa komko!! don’t blame min buss drivers blame yoself for failing to purchase car 4rm Beforwad Japanise, pemphani amabungwe akugulireni galimoto yanu ine ndilibe koma sindinganyoze ntchito ya ena asiyeni apange mademo!! What kind of pple are you??
Asamayese zida
The objective was to raise some fares basis…
m’bawa
Ti ma post tanu ena ndationa tofooila pofuna kuyankhula mudziva kae kut ma driver WO akudandaula chani? mukanaenda kuona anthu mmene anavutikila lachinai madriver akukana kuwanyamulila katundu wao, ena mukudalila timagalimoto timene anakusiilani malemu ndiye muganiza azanu alinato
amati atan?
HOW FAR CAN THEY GO!
Ku malawi
Kkkkkk koma
Drivers of minibuses why don’t you respect the sitting capacity which is ensured in terms of emergencies. Why don’t you respect your bosses which are the passengers. Are you sure that you can make a strike to force the government to authorize you to OVERROAD PASSENGERS.
Mumati munga mungatani amphaka inu kupanda kuyenda pansewu mukagula ndichani okomani
Iwo amati azidyanji akapanda kupita ku msewi
AMALAWI ZITSIRU TAZiwoneleni. Kuno Ku theba akati strike boma limanyela matudzi. Shupit
Kungotaya nthawi ndi nzazii lero abweranso okha palibe waitana pena tiziganiza kaye amalawi tisanapange zinthu nchifukwa sitipita patsogolo malo mogwilitsa nchito ubongo timagwilitsa mamina mxwiiiii
M’phavu kuwathu umadziwilatu
Apindula chani?
zangovuta kuti eni minibus amalemba ntchito anthu a fodya,amati angapange chiyani pa nyasaland pano?
think about the next generation
kkkkkk umphawi ngovuta kkkkkk strike yopanda cholinga
Was objective achieved? What is conclusion? Did govt bow down to demand by drivers to stop law endorcers from what it was termed as harassment, abuse and exploitation??????
Amati atani…
a nation without law is a nation without despline, such a nation is not worthy of that name’.
Mmmmmm !!!!!”” Pano kukwera mwa ufulu koma nanga ka thumba ka chimanga mpaka hayala???
zavuta apo
Kod amalawi maesa tili ndi malamulo okwela amaminbas aporice ap mseuwo tonse tikudziwa malamulo akumalawi apanseu koma apolis apanseu ziphu phu
Ngati malamulo akhala taugh ngozi zichepa panseu
koma abale,mwati kathumba ka chimanga tidzitani nako? penapake zikundiopsa,bag limodzi,dengu limodzi latomato nkupangira hayala?pa 3,3 zilibwino koma no oooo ujeniii nde eeee.pokhapa tiganizireni ife okwera.
Nanu musamasokoneze malawi
Kkkkkkkk
Nde mbolatu kukwela galimoto ina katundu kukweza inaso iiiii
wakaatenganso ndani?
Anangoyenera kubwerera pa msewu.Dzulo nawonso aluza ndalama zambiri.Nanga ndani safuna ndalama?
Dunderheads! No kind words for these hooligans. Destroying public property just out of savagery. Mxiieee!
very true my brother! a bunch of idiots
Kulibe zobela bwana this time….apa pokha boma lapanga za nzeru
Amatani atani….ndi imbwa zimenezi
We rapid transport system in Malawi cities.
m’matimungatani lnu zitsilu lnu tangotsatilani malamowo basi kkk
Makape inu ku Malawiko mumapanga zinthu zopusa dziko losauka ngati limenelo,taonani mwaononga ma buildings omwe mabungwe anathandidza pomanga,pamenepo mabungwe akakwiya ndiye mudziti boma likudya ndalama kapena ma Members of Parliament(MP)a Malawi tidzasukusula liti abale kumangoonjedzerabe kusauka dziko losauka kale ndi kale
moti inu munapeza citizen ship kumeneko? muzatipeza
Ntae ndikape kwambiri watsala pan`gono kuvala teyala amenei
Iwonder Kuti Anthu Ena Mukapita Kujoni Mmanyoza Amalawi Anzanu Chimakhala Chili Chani Makamaka? Mind U East West Home Is Best Munthu Wanzeru Sanyoza Kwao Komwe Anachokera
Aona kuti wine samwedwa
Agwiridzana zotani? Misewu apysere
Adya chani kkkkkkkkk
I beg traffic police should punish the drivers and conductors who deliberately breaking the law on the roads
Sukudziwa chimene ukunena axe
fuck you and you mini buses..you stink shit with your call boys
hold up man…..control ur emotions minibus operators ares jus malawians tryin to earn a living at the end of the day…
hold up man…..control ur emotions minibus operators are jus malawians tryin to earn a living at the end of the day…
mwapindula chani kuotcha mapolice units blantayre ndizopanda ntchito
Aphunzitsi akanyanyala salary imalowa ndithu but iwe wangotaya nthawi tsonotu apa wa mushosha wa traffic akukakamira sakusiyanitu mlandu ungono ngoni muzitulika thukuta pankolokolo vakufinyani ndithu
Ndimadabwatu ine zoona dzulo kukafika paden minbus driver opanda mphoda(black oper) ndi buledi za panyumba madam anawabweza kuti ukuona ngati ife tidya mademo pakhomo pano nanga ine phoda wantatu umaziyesa ngati iwe msambizi
Akondakitala ndi aminibus driver kupusa eti inu munthu amadalira kususa daily ndekumaliledwa kusagwira ntchito aaah sakundipatsa chilimbikitso anyamatawa amenewa ndi ayona ndinthu kumalora kumezedwa ndi msomba aaaaah kkkkkkkkkkkkkkjj mbuzi za wanthu
Kkkkkkkkkk
Kodi ku Moam kulibe democracy? I think anthu kumipandoko akhalisa no wonder they are failing the association
Really brother man, thus why they say money, more money does not make a being a being kkkk
Bwererani kopanga zionetsero tiwone kuti mudya Chani. Minibus owners deserve stiff punishment for all the damages
Dziko limayenda ndi malamulo,lamulo siligonjela munthu koma munthu asatile lamulo.Pamseu pali malamulo,yemwe safuna kusatila malamulo apa mseu ndiye asayendese galimoto pamseupo.Akayendetsa mosasata malamulo,malumulo agwire ntchito basi.Ntchito watopa nayo siya,bwana anuwo alemba wina woti adzitsata malamulo,kusiyana ndikumapha anthu osalakwa pamseu.Munatchuka ndi kudelera malamulo apa mseu lero dziko lakuonani zisakuwaweni,kutasa kumakhala ndi nthawi ngati yatha,yatha basi.Tsatani malamulowo zonse muwona kuti ziyenda bwino.
muive Khan yake bwino bwino nde muziyakhula mbwerera zanuzo man
Palibedi chanzeru chomwe mwalemba chifukwa nkhani yake simunaimvetse man.
Zanu zimenezo@ Alichawe mphande,time is over and over now.
Nda boma lalora zomwe amafuna zija
Sizinabebe tsiku limodzi
Sitalaka yopanda masomphenya!
koma zoona mpaka “some roads not being impassable?”
Useless demonstrations……..
So what next ?
so what WS the objective of yestrdays demo-.
…..sometimes wisdom of intelligence has to bestow upon…….u do a demo without objective a day later ya back in the streets…with business what’s that?
Kkkkkk kufoira mzeru.
Ma sachettes
Midoli bwana, ma demo oyenera kupanga ndima passenger osati ma driver
Eeee! Guys Ndimene Zinalilimotu Sanali Madriver Ndi Maconductor Okha Fans Inanso Inalowelera Mpakana Kuotcha Mapolisi Unit
Amati atani
Hahhhaha well done dudes!!!
amangozichedwetsa basi
Wat Hv They Beneft After That Strike,,,,,,,,,,,,savage
Hahah was about to write same thing
They should have started on Tuesday
Apangeso Ths Next Wk,,,,ife A Tax Titoleleso Ngat Dzulo,,kk.
Amati atani? Adya mchenga?
f
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk dzulo nkhuku kunyumba sanalandire komanso midoli siynamwedwe kkkkkkkkkkkk
Ife timadziwa kuti mukagona ndi njala mutifuna.Palibe ntchito inayima m’ma office chifukwa choti minbus sinayende.Agwape!!
kkkkkkkkkk Koma man mpaka #Agwape kkkkkk
Kkkkk! A kalulu??
Kkkkkkk..Kuganiza ngati nyama
Nkhululu zeni zeni
kkkkkkkkk koma?
Akanatani anthu odalira kususa daily
#capital #city tipanga strike tuesday
Lamulo liposa mphamvu woooooo
Amati atani. Si abwerera okha. Anakakhala 1week tione akanadya chani.
Bro Levi Spikiri,ndimbuzi zaanthu zimenezi amaona ngati angasauke ndindani ndi ka strike kawoko?zopusa basiii!!!!
Bomatu silachibwana ndipo silinyengelela zopusa ngati zimenezi..
Mukati boma silachibwana ndiye kuti chani,that’s slavish mentality my brother.
ma driver amamenyela ufulu ngakhale wa munthu okwela minibus chifukwa munthu samayenda ulendo opanda chikwama.
Mmene maluzi amawakwapulira anyamata amaminibus angapange strike or 2 days
Zitsiru zimenezo”amafuna kuononga Kaye zinthu kuti azimvetsa bwino?ngati ka #Min bus kachepa sizingatheke kuti kazipeza phindu lofana ndi #bus zazikulu . NDE pano awononga zinthu zochuluka akufuna #boma lipange budget yomangira ndikukonza zowonongedwazo,Iwo monxemuja samadziwa kuti Ali ndi #bungwe lomwe limakonza mavuto omwe Ali nawo?vuto akuvuta ndi #Anthu osauka omwe alive ngakhale ndi #tayala lomwe.pomwe #Mabwana awo akukhuta kunyumba kwawo,Iwo Ali busy kuphwanya nkuotcha matayala mu msewu.chomvetsa chixoni mitengo ikakwera Iwo malipiro ake sakwezeledwa,mwinanxo akangoyamba kupempha kukwezeledwa amauzidwa ngati sakufuna achoke apeza wina.(zinthu zopoyira bax)
Serous bro ukunena zona
mbuzi za anthu zatenga nthawi zisanabe zimafuna zipezerepo mpata okuba katundu wa anthu basi mbuli zeni zeni
Point
It happens everywhere bro Ali pansewu lero ndipo uthenga wao waveka ,ma demo abata boma silimawatengera serious,, do u think amapangazo abungwe samadziwa kkk never amakana ngati sakudziwa kuopa kumangidwa …I lyk it coz b4 kupanga impose malamulo azipanga kae consult anthu ….well done minibus drivers
Geo you have to learn to speak as a civilised citizen.
Kuwotcha police station what information are they conveying?
Be civilised dude
Iweyo walemba post yi ndiwe mbalame choyamba udziwe
Mr innocent even in USA people anthu amapanga ma demo,,,last wk in south Africa ma minibus anatsekaso misewu nkhani yake yomweyo yomaika malamulo opusa….how can I be civilised while they imposed uncivilized laws on me????
Amaona ngati boma limamugonjera munthu?? Mwapindulapo chani ndie???
Kkkkkkkkk ha ha angoluzapo ya bread dzulo kkkkkkk
munseu munyaseso
I hope the minibus sitting capacity is in conformity with Road Traffic Directorate’s rules.
ndie apangapo chan.? boma ndi boma ndipo siligonja amagonja ndi athu
amati atani apa ndiye kut avomelezala la mulo lija
Pamene abwerera pa mseu ndie kuti lamulo lachosedwa?
Silinachotsedwe,anthuwa ndi mbuli amwene.
Bwana, lamulo silingachotsaedwe chifukwa silalero ayi. Za capacity ya 3-3 a minbus akudzidziwa kuyambira kale.
Koma avomela kuti azitha kunyamula katundu.
Lamulo ligwile tchito basi