Minibuses back on Blantyre roads

Advertisement
MINIBUSES

Minibuses are back on the roads of Blantyre today after intra-city public transport was disrupted on Friday.

A strike by minibus drivers and conductors led to chaos and disturbed business.

MINIBUSES
Minibuses now on the road. (File image)

But Minibus Owners Association of Malawi (MOAM) general secretary Coxley Kamange has promised that they will resume business for transport in the commercial city of Blantyre.

Kamange further faulted drivers for being violent during the strike.

The drivers and conductors staged a strike that turned to be violent as they demanded a reversal of penalties recently introduced by Directorate of Road Traffic and Safety Services.

Teargas canisters were used to disperse the rioting drivers and conductors, a situation that witnessed some roads not being impassable.

The protests witnessed some minibuses being smashed for being found on the roads.

The angry drivers and conductors also torched three police units in residential area of Machinjiri in Blantyre

 

 

 

 

Advertisement

123 Comments

 1. Ngati simumafuna kupanikizika min buss just buy your own car but don’t say min buss driver are the one who makes roads accidents aaa bull shit!! amene amagubuduzika ali wokhawo?ngati kunalembedwa kuti mudzafa ndi ngozi ya pa nsewu mudzafa basi or mulikwanu mudzagundidwa komko!! don’t blame min buss drivers blame yoself for failing to purchase car 4rm Beforwad Japanise, pemphani amabungwe akugulireni galimoto yanu ine ndilibe koma sindinganyoze ntchito ya ena asiyeni apange mademo!! What kind of pple are you??

 2. Ti ma post tanu ena ndationa tofooila pofuna kuyankhula mudziva kae kut ma driver WO akudandaula chani? mukanaenda kuona anthu mmene anavutikila lachinai madriver akukana kuwanyamulila katundu wao, ena mukudalila timagalimoto timene anakusiilani malemu ndiye muganiza azanu alinato

 3. Drivers of minibuses why don’t you respect the sitting capacity which is ensured in terms of emergencies. Why don’t you respect your bosses which are the passengers. Are you sure that you can make a strike to force the government to authorize you to OVERROAD PASSENGERS.

 4. Kungotaya nthawi ndi nzazii lero abweranso okha palibe waitana pena tiziganiza kaye amalawi tisanapange zinthu nchifukwa sitipita patsogolo malo mogwilitsa nchito ubongo timagwilitsa mamina mxwiiiii

 5. Was objective achieved? What is conclusion? Did govt bow down to demand by drivers to stop law endorcers from what it was termed as harassment, abuse and exploitation??????

  1. Kod amalawi maesa tili ndi malamulo okwela amaminbas aporice ap mseuwo tonse tikudziwa malamulo akumalawi apanseu koma apolis apanseu ziphu phu

 6. koma abale,mwati kathumba ka chimanga tidzitani nako? penapake zikundiopsa,bag limodzi,dengu limodzi latomato nkupangira hayala?pa 3,3 zilibwino koma no oooo ujeniii nde eeee.pokhapa tiganizireni ife okwera.

 7. Dunderheads! No kind words for these hooligans. Destroying public property just out of savagery. Mxiieee!

 8. Makape inu ku Malawiko mumapanga zinthu zopusa dziko losauka ngati limenelo,taonani mwaononga ma buildings omwe mabungwe anathandidza pomanga,pamenepo mabungwe akakwiya ndiye mudziti boma likudya ndalama kapena ma Members of Parliament(MP)a Malawi tidzasukusula liti abale kumangoonjedzerabe kusauka dziko losauka kale ndi kale

  1. Iwonder Kuti Anthu Ena Mukapita Kujoni Mmanyoza Amalawi Anzanu Chimakhala Chili Chani Makamaka? Mind U East West Home Is Best Munthu Wanzeru Sanyoza Kwao Komwe Anachokera

 9. Aphunzitsi akanyanyala salary imalowa ndithu but iwe wangotaya nthawi tsonotu apa wa mushosha wa traffic akukakamira sakusiyanitu mlandu ungono ngoni muzitulika thukuta pankolokolo vakufinyani ndithu

 10. Ndimadabwatu ine zoona dzulo kukafika paden minbus driver opanda mphoda(black oper) ndi buledi za panyumba madam anawabweza kuti ukuona ngati ife tidya mademo pakhomo pano nanga ine phoda wantatu umaziyesa ngati iwe msambizi
  Akondakitala ndi aminibus driver kupusa eti inu munthu amadalira kususa daily ndekumaliledwa kusagwira ntchito aaah sakundipatsa chilimbikitso anyamatawa amenewa ndi ayona ndinthu kumalora kumezedwa ndi msomba aaaaah kkkkkkkkkkkkkkjj mbuzi za wanthu

 11. Dziko limayenda ndi malamulo,lamulo siligonjela munthu koma munthu asatile lamulo.Pamseu pali malamulo,yemwe safuna kusatila malamulo apa mseu ndiye asayendese galimoto pamseupo.Akayendetsa mosasata malamulo,malumulo agwire ntchito basi.Ntchito watopa nayo siya,bwana anuwo alemba wina woti adzitsata malamulo,kusiyana ndikumapha anthu osalakwa pamseu.Munatchuka ndi kudelera malamulo apa mseu lero dziko lakuonani zisakuwaweni,kutasa kumakhala ndi nthawi ngati yatha,yatha basi.Tsatani malamulowo zonse muwona kuti ziyenda bwino.

 12. so what WS the objective of yestrdays demo-.
  …..sometimes wisdom of intelligence has to bestow upon…….u do a demo without objective a day later ya back in the streets…with business what’s that?

  1. Eeee! Guys Ndimene Zinalilimotu Sanali Madriver Ndi Maconductor Okha Fans Inanso Inalowelera Mpakana Kuotcha Mapolisi Unit

 13. Zitsiru zimenezo”amafuna kuononga Kaye zinthu kuti azimvetsa bwino?ngati ka #Min bus kachepa sizingatheke kuti kazipeza phindu lofana ndi #bus zazikulu . NDE pano awononga zinthu zochuluka akufuna #boma lipange budget yomangira ndikukonza zowonongedwazo,Iwo monxemuja samadziwa kuti Ali ndi #bungwe lomwe limakonza mavuto omwe Ali nawo?vuto akuvuta ndi #Anthu osauka omwe alive ngakhale ndi #tayala lomwe.pomwe #Mabwana awo akukhuta kunyumba kwawo,Iwo Ali busy kuphwanya nkuotcha matayala mu msewu.chomvetsa chixoni mitengo ikakwera Iwo malipiro ake sakwezeledwa,mwinanxo akangoyamba kupempha kukwezeledwa amauzidwa ngati sakufuna achoke apeza wina.(zinthu zopoyira bax)

  1. It happens everywhere bro Ali pansewu lero ndipo uthenga wao waveka ,ma demo abata boma silimawatengera serious,, do u think amapangazo abungwe samadziwa kkk never amakana ngati sakudziwa kuopa kumangidwa …I lyk it coz b4 kupanga impose malamulo azipanga kae consult anthu ….well done minibus drivers

  2. Mr innocent even in USA people anthu amapanga ma demo,,,last wk in south Africa ma minibus anatsekaso misewu nkhani yake yomweyo yomaika malamulo opusa….how can I be civilised while they imposed uncivilized laws on me????

Comments are closed.