Amene mumagundika kupita ku ma bwalo kumapeto kwa sabata kukaonela mipira ya Ligi ati mwina pena mumakangoonela ndado basi chifukwa mipira ina yakuno ndi yosalongosoka. Pena mwina ukuonela utha kumayesa anthu angosewela ndi ndodo.
Malingana ndi mphunzitsi wa tsopano wa timu ya Flames, Bambo Ronny van Geneugden iwo ati ataonelako pan’gono mipira ya Supa Ligi adziwa kuti mpira wa ku Malawi ndi mphwepwa, panja penipeni.
Malinga ndi malipoti a nyuzipepala, Bambo RVG ati iwo ananena kuti mu ina mwa mipira imene anaonela, anangochoka akupukusa mutu basi kuyesa kuti mwina zimaseweledwa pamenepo zinali ndado osati mpira wa miyendo.
“Ndinene pano kuti ndaonela masewero ena a mu Supa Ligi koma ayi ndithu ndi panja penipeni. Anthu amangodunyula mpira basi, ali nawo ali nawo, wa 12 koloko Nyasalande. Zopanda tsogolo zenizeni,” iwo anatero.
Bamboo RVG ananenanso kuti koma mu masewero ena, zimaoneka kuti tsogolo lilimo ndithu dipo atolamo anyamata ena amene akufuna kukabindikila nawo pokonzekela masewero a mpikisano wa COSAFA.
Kkkkkkkk,he is talking rubbish
Kukhala coach Wa Malawi sichinthu chapafupi…… Get ready to tek the blame iwe akuti ndani kaya.. Rvg…. Kuno ndkumalawi…. Chikhalidwe ndi mpira omwe…..
Nonsense
A Mw chomwe timatha nd kutamba bax
Chasala Kungosiya Kumawonera Mpira
chilungamo kuwawa
enanu mumangoxiwa kuonera simungathe kusewera koma kunyoxa basi timu yamalawi ikanakhala kuti ikuwina iyeyo ntchito sakanalembedwa ndimau akewo waxiwikiratu kuti palibe chimene angachite ntchito sakuixiwa kape ameneyo he must fired foseki
Zoonad akochi, amen to that
Nkulu ameneyu salunama ayi… Ndimaonera game ya Noma ndi Tigers on MBC tv, oh akulu nkhunda zenizeni, or chilakolako cha mpila kukhala ngati akukwawa. Boxing nde eh akumamenyana wina wagwa wina pamwamba… Poor Malawi zambili zotivuta
upita bwanj mpira patsogolo chkhalirenicho anthu akulandra ka 15 mita the whole year,,,,at kaya super league???? manyaka enieni
kufera zakunja muone mmene azidyere ndalama za ku malawi mpira wake sowe vuto ndi osewera mpira samatha basi kuvomereza ndino zinthu zikamakanika osakakamira ntunda opanda madzi,tiyeni tizingokhulana ndi achina chingambwe omwewa basi masiku namapita.
Kkkkkkkkkkk
Kkkkkk azimka2 ndie
Zoona zimenezo
Kusukulu Timapita Kut Tikakumane Ndi Aphunzitsi Omwe Ali Odziwa Ntchito Yao Ncholinga Choti Umbuli wathuwu Uthe So Ngat Tidalemba Ntchito Iyeyo Asatinyoze Ndife Mbuli Tavomela So Tithandizetu Tsopano
Kuno nichivwanda a coach pala mundaonerepo chivwanda mwachisanga.
kkkkkkkk
Tathokoza kuti wawona kuti ndindado iyeyono akhazikitse mpirawo mu group yomwe tiliyi zikapanda kuyenda adzipita
This man has no history abt coaching, he is talking rubbish.
Zoona coach!
Zoonadi amangotenga azibale awo akhale player
Motocar ija aibweze basi
Sananame ngakhale pang’ono. Ngati anthu amasowa chowonera Ali mstadium momo. Kuona ma player athu akuthamangathamanga ngati MBAWALA. Koma onenera naye akulongosola zazitsa ndimapesi. Zinthu zinasokonezeka Basi.
Anaona sulumba ndi kakhobwe. Ndiye paja ikaola imodzi kkkkkkkk akapitiliza kunyoza timuthotha
Ngati timakhutisidwa ndimpira waku malawi kuno ndiye tikuchedwa kwambiri.
Wanena zoona
koma chimene ndimaziwa ine munthu ngati nkhani kapena chilichonse akungoonapo chofooka chimene munthu ayankhula sitipeza yankho nkhani ndiyoti kodi zimene ayankhulazo ndizoona kapena ayi komanso player aliyese azione kuti akupanga bwanji I think tikhoza kuona kusintha
Sakunama vuto si coach wa National Team but club level pali mavuto.
Zoonadi sakunama RVG
akunena zowona
Kochi akhonza koikonza flames
100+% chilungamo ndipo ndi masanje akupulayimale anja,osewera tisanavale panti
Kodi Team Ikalemba Coach Ndekuti Reason Yake Saiziwa, Ndichifukwa Amati Xul Simatha
FAM was supposed to hire a coach who knew the type of football played in Malawi. He is confused now, yet he had promised to deliver.
ameneyu waonela bullets being pples team 3 games no any goal bullets sizatheka
He is talking about the standard of play at the super league level not at the national team leveling
Most of us here we are missing the point the new coach is trying to emphasize!
Kkkkkkkk chiso wanena zoona anawa ndi mfiti za mapiko athakati enieni sadziwa kanthu biiiii, hahaahaaa nkhwezule izi anaming’omba awa
Ngati Iyeyo ali coach wodziwa bwn ntchito, ayikonze kt team yo ikhale yapamwamba. Kuonera Dwangwa Ndiye Kt Wamaliza Ma Team Onse? Asathe Mau!
so if Malawian foot ball is thrush, what is he going to do?. is he going to take players from zambia? a bad carpenter always brames his tools, thats what I know , Kinah Phiri anayesera bwanji kuichinya Egypt ili mu form,, Kape ndi kape, alira ndipo sanati.
It was like he was watching tennis thats what he said!
Iyenso coach nde manyaka osangoonetsa ukadaulo wake bwa?
Iwo nde asintha znthu??
Mpatseni transport azipita asatinyase. Akufuna akhale ngati ndani iyeyo?. Zazi.
Yah but the thing is I blame the FAM president, instead of developing football he and his board members are busy cashgating. So ya kulira tizamlekapo yayi unless the entire board is dissolved. Look at what kinnah did, he took the flames to AFCON ,of which many coaches from outside the country have failed to do. But they continue to hire coaches that doesn’t understand our style.so its better to hire coaches from within the country that understand katchayiro kabola lithu .these problems will never end without dissolving the board. If he also doesn’t want to coach the flames he can go osati kuti walyenge Waka ndalama zithu chaa! Tukhumba maresults yaonekenge.
Coach odziwa azitero mwina zingasintheko.ena mmalo molemba nkhani kuti imveke bwino mukukemba zoziwa nokha ngati ngati chili chidule mukulephera chifukwa maganizo akupelekedwa apawa ndioti anthu ambiri awerenge kuti kodi inuyo mwalemba kuti chani? Nde ngati mukuona kuti chichewa ma sentence ake akumatalika zilembani English alipo omwe analowa mkalasi awerenga ndipo akumvani kuti mukuti chani
Before the doctor give treatment to a patient he first detect the problem. So the couch is probably right but let’s see how he is going to change Nyasaland soccer.
Rvg akunena zoona kwathu kumalawi mpira tikulephela.Chikufunika apa kumaprimary sukulu ndikumasecondary sukulu kukhale mipikisano tikatero timu yathu izakhala yamphamvu.
Ikumukanika team ya malawi, nanga bwanji kinnah phiri anayipitisa ku Africa cup player ake omwewo amu super league.
Iyeyu adalembedwa kuti achotse ndado waziwonazo ndiye ndi ntchito yake kuthetsa ndadozo ngati momwe anakonzera Kim zaka zapitazo kuti achina kamwendo adzitchuka
Poti wabwela atiphunzitse mpirawo asangotokota apa
Amalawi tidakhala bwanji kumadabwa mtswamtswa wathu womwe this coach is right kodi unduna wazamasewero umapanga chian?ndizaka zingati achititsako maphunziro aucoach macadamy ampira alipo angati ngati dziko chabwino talimbikitsani masewerawa pa primary level zikuvutaso moti zowona ntchito ingokhala kulimbirana ndalama zapagate mastadium basi please try to improve.
NDIZOONADI MPILA UNALI KALE
Mpira wathu ndi amateur palibe kunena mopsatiranso apa.Olo atatenga Mouronho,Conte olo Guardiola nothing will change
may be he right, let’s wait .
Amalawi Coach Alibe Vuto But Fam Yasanduka Yakunyumba Kwa Nyamirandu
Akuti miyendo yathu Ku Malawi siyampira?aaaaa koma ameneyi, koma penapake akunena zoona,Nanga dziko lopanda striker odalilika.
he is employed to change things not to complain,he must implement what he thinks will emprove the current situation,he must come with solutions thats what he is paid for..if everything was fine on the ground he could not find himself there..the officials went as far as looking for acoach outside the country bcoz the knw the problem..go on mr man and do ure job all we need are results and better be good
osamadana ndi chilungamo_ wanena zoona
Mmmm izi n’zabodza ndithu
ufit wachuluka vuto,akuyamb ndi ma coach zitsamba(flames sidzava kmas anatilodzay e ndikatundu)
zoona zokhazokha zimenez(zimezo)
Zoona zake
Wangofuna kupezerapo mwayi team ikamaluza azipeza polankhula kuti azinama kuti paja ndinanena kaletu kuti mpira kuno kulibe,iyeyo ngati wapeza bvuto alikoze team ili mmanja mwake zisamulephere nthaei yomweyi asatinamizepo apa
Ndizoona akunenazo mphunzitsi wa flames.
zoona
RVG can deliver if he can be given miss mw
Ndintchito Yake Coach Kut Akonze Team Yathu Mmene Iye Amkabwera Kuno Mayesa Anazithemba Kut Ndiwoziwa Ntchitoyo,amaganiza Kuti Apeza Team Ili Yoziwa Kale Iye Azingomwa Tea, Ngat Saziwatu Ntchitoyo Basi Go Back To Theway That He Come
Nde malawi kkkkkk
RVG calling a spade, a spade.
kma guys kusapota flamx eeeh!! kukuwawa jxt tanganixan munthu kumakhala patali ndi chingwe evn mpeni game ikamamenyedwa
Ndizoona koma sakunama ndado
Musatinamize a kochi ,sikoyamba kulemba kochi wachizungu,awonetse chamuna pamenepa ngati luso la mpira Alinalo!!!
Kkkkk tinazolowela ife olo uyankhule flames simasintha
he actually thought we are going to World cup
DZIKO LATHU AMASANGALALA NDIWOBWELA TISADANVEKO KUTI COACH WAKONKUNO WAPATSIDWA FONI YA 400 000 ZODZIWA NYAMIRANDU ZOPUSA ZIMENEZI.
He’s right, the system of standard of playing has gone completely down since the generation of like these list of players resigned.
Andrew chikhosi
Johns Nkhwazi
Sherry Msuku
Gift zakazaka
Peter Mgangira
Chancy Vin gondwe
Chikondi Banda
Hendrix Banda
Albert en Bob Mpinganjira
Wilfred Nyalugwe
Grant,Lungu etc
Footbal pano si ili muja moti inkat ikakhara dabby BB n Noma, wina akakachinya uku within aminute wina kukapanga equalise. Lero kulibe now this game full of immature stars so they are diluting the flavour and the taste of the game of football as they do at home Diluting like super dip of wakawaka, Davita or Baks. No sweet soccer. Soccer has been miserably diluted.
Amenewo ndi chabe man but the likes of kinnah phiri , jack chamangwana,bernett GONDWE, frank sinalo Kennedy and Holman malunga,damiano malefula,Boniface maganga,donex gondwe,spy msiska, zoro msiska,mavuto lungu, Clifton msiya etc
Man Aubry Matenje, inuyodi ndi _1, mumazitsata ndipo mukunena zoona chifukwa mastandard ampirawa akutsikiratsikirabe..
Chifukwa kagulu ndinatchula kaja nkuthekadi nkotsikadi kusiyana ndi mizwanya mwaitchulayi. Big up Bigman potikumbutsa
Am on his side. Low
quality football
100% true ndi khwanya weniweni!, koma poti chilungamo chimawawa m’mutukwana
Ndiye unkabwelera chani buluzi iwe?
Thats why we hired him as coach to giv us better quality of football.
100% right osamadana ndi chilungamo ayi
Its nosens spich from your coach shupt
Sitimatha tingovomereza
Sakunama,akazi basi
The Coach Z Here To Improve The Game Instead Of Working On The Mistake He Has Started Blaming Thats A Bad Carpenter The Cooperate World Too Z To Blame 4 Giving Hm A Free Car Decoder And A Phone Hw Abt Gerald Phiri Senior And Dekilek This Guys Need To B Given Aswell If We Are To Make A Better Flames Coz These Guys Will Not B Happy
Modern Colonisation
Make us to be proud of you then
SAKUNAMA sumasangalasa kuwonera wa phu phu phu and ma player ake amakhala ngati sanadye
Ku Malawi kulibedi Mpira just bcoz we don’t have its academy
Wayambapo!…
RVG this is Africa and not Europe.If u cant change the mindset of players just pack up and go
RVG wouldnt talk like this in Zimbabwe for sure.This is being very primitive.That is why he was hired inorder to change our national team
Kumalawi kulibe mpira
Iyeyo ndintchito yake timuona ngati angasinthe zinthu
Hahaha ndado waidziwilakut zungu?????
Kochi apa wathoka live. Ine sindingakwanise zinthu zodulazo kwa ine ndimpasa bakha akachape nkamwa
Money problem
He is right za football kwathu kuno ndi phada kapena tinene kuti jingo weni weni and we don’t want to learn from our mistakes hence we continue with the very same blunders . Nanga tikane kuti ndimbwelera mpira wathu?
I dnt think he is right being a coach he wasnt suporse to speak like that bcoz he is like a leader.
He would have just say he has failled not blaming our league.malawi has good quality and skilled players all we need is to motivate them in all sectors
Hes ryt ada if u know football .. research n compare ndi mipila yanzathu we far from them ndepoti wanena chilungamo..truth pains
How long are we going to try motivating the players?
The bitter truth hurts.
Soccer in Malawi will take years to improve especially at the National level.
We need a miracle….!
akulu mwalankhula zoona olo ophunzira kumuza kuti mutu wake
akulu mwalankhula zoona olo ophunzira kumuza kuti mutu wake ndi madzi amagwa ulesi and amakhumudwa. mukuyenera kukhala mphumzirsi osati mfundo za ena zopanda pake
Tiphuzire kulakhula chilungamo amalawi mpila kwathu Juno sulibwino .RVG sakunama tisithe masaweledwe anthu .
The best way to solve a problem is to identify some weaknesses that’s what RVG has done cause frankly speaking our nation team is a total disgrace
Kkkkk mavuto Ku akolinto
Adzachoke Walter ndi azinzake kaye mpira udzayenda bwino
Trizah Isaac Chilembwe Evelyn Biliat
Zomwe wanezo ndizoona…
Koma ma player akumva chizungu.mapeto ake azingoti yes Mpira tikuluza
Ya that’s true, even you Admin, you don’t have even Dstv so that u can see what happening outside your country, to have tv doesn’t mean you have Dstv, let’s start putting Dstv now.
Ndithu zoona sakunama koma kuti izi zisinthe zonse ndi ndalama kupanda ndalama palibe chingasinthe tiyeni tibvomeleze.
Amalawi tisiye kukhala ndi maganizo oti player weniweni ndi was bullets kapena was wanderers, yafika nthawi sono yoti tiyambe kuona ma player Ama team angono angono
Ma team odzadza ndi ma defenders kuchinya kumavuta kkkkkk
Kkkkkkkkkkkkkkkkk
Kkkkkkk akunena zoona anaonera Makombora omwe amaponyedwa potsegurira League mpira bola ukafike mugolo kkkkk koma Noma ndi KB
ndiye malawi amene ndimawaziwa ine ameneo tikukukwiya chan apa iye ngat wanena kut mpira wa kuno mw nd phala nde tidikile kut apanga xotan kut tiyambe kuchta bwino imeneyo nd nchito yake iyeyo, nde mungot azipita azipita kut? nanga akunama ngat?
Flames bola iyambe kusewela mpira wa chokulunga… Sakunama
Word RVG. kumatenga dzi ma player dza Super League bola kumakatenga ana a FMB under 20 league at least they play football that has identity. Super League coaches chitamponi kanthu phu phu phu si zampira. Player wa super league kumakanika ndi ball control yomwe?
The truth. Pains ayiyaaaah
guys know that truth shall set every body to be free,kunena zoona couch sakunama athoka chilungamo,kumalawi Juno mpila sitimatha,kma chigololo,kachasu,kupondelezedwa,apo NDE tili pa number wani,koma mpila simbaliyathu.
Peter K Nchacha E!Man Mwalankhula Chilungamo Koma Poti Chilungamo Chimapweteka Azingotilalatirabe Basi Sinanga Iye Ndi Mnzungu!Kkkkk Moti Kulankhula Kumeneko RVG Wayankhula APM Ali Kuti!Iiiiiiii Amalawi Ndiye Taphweka Bwanji Ndiwobwela Omwe Mpakana Kumayima Pachulu Hahahahahaha!
Chilungamo. amamenya ngati wachikulunga ku primary pa break
kumalawi mpilakulibe or,atabwela morinyu palibechingasinthe.anyamata athuamakondakumwamowa kachasu,ntonjan,akangontchuka pang,onotzibwenzinkat
Zoonadi paja amalawi timadana ndichilungamo ndiizo mwazimvela nokha kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Zoonadi paja amalawi timadana ndichilungamo ndiizo mwazimvela nokha kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
mwaziwa lero….ndipo mpira wake uti….kuno kunayamba kwakhalapo mpira…?
sakunama mkulu ameneyu,kumangoti nebaneba za ziiiiii,mpira omakoma kumvera pa radio koma kukaonera pamaso zeroooooh weniweni wekhaso kumadabwa kuti olengeza aja amalengeza ziti kodi,kk apanso akuononga mpira ndi olengeza anthuwa amakokomeza za ziii,ali timu mmene ikusewelera omvera tukuuzani ili bwino mxxx zausiru bax
Nde iwo atani kuti zinthu zisinthe???
Malawi is good at rewarding mediocrity. This RVG thing has started with losses yet he has been given a car, phone and decoder. What are we promoting?
Is RVG a mediocre? in what respect? he brought new tactics and the players he found in camp were not picked by him and were too rigid to put his tactics into practice judge him akasankha squad ya kumtima kwake. chomwe nduona zakuwawani ndi zomwe ampatsazo. but using the word mediocrity on him is unfair and just shows how you dont understand football
Eti inu zonsezi why him not Kinnah uja?a Malawi amaopadi nzungu.lero a tnm amupatsanso unlimited units.za ziii
Kunyambita nzungu basi yes bwana lisitone
That’s it. achieved more than all azungu coaches combined. Yet was not treated as such.
Amnzathu ofira nkhunguwa anabadwa a mwayi baxi….
timuona iyeyo kut aitani flames
Kkkkkk ok
True …ndipo radio ndiyomwe impatipusitsa ngati kukumenyedwa zenizeni…watch pa TV guys nyasi zenizeni
Kkkkkkkkkk
Zaziii
Munathamangisa kina phiri muisova
Bwanj iyeo osangopanga zot mpira upite patsogora
Kungoziwa mpila woponda basi kumalawi kulibe boz.wanena chilungamotu apa
Zooona kulibe mpira ku malawi
Zoonadi RVG sukunama, komabe dziwani kuti a bad carpenter blames his/her own tools
Mpira wathu udzapita patsogolo ngati makampani ndi anthu akufuna kwabwino mu dera lanuro akadzayamba kutenga nao gao mu mpira , tiyeni tiyambe kuthandiza mma primary komanso ma secondary school kuti kudzitiluka ma players abwino then tidzaona maligi athu akuchita bwino
Wandyakhulila Bwno Pamenepo,iwed Umazixata
Wanena mau
Sakunama ameneyo wanena may
Nde timadabwa enanu mukamati ndimakonda team iyi, kundimvetsa kukoma, kundimwetsa wa mkaka ziri mbola zokha zokha
Phala lake limaseweredwalo! How can we expect flames to perform well when our superleague is trush. What government must do is to invest on youth talents
uyu ndi coach wa nyamilandu anapeza othandiza kulipira salary ndi iye, ine chomwe ndimadziwa ndichoti ngakhale mutatenga ma coach a Chelsea,man u, barca , arsenal, spurs kukocha Malawi sitingawine ,vuto sima coach koma players ,
So we want him to change it into real football as he knows
koma akunama ngati?
Tiona mwenzi wa june ngati akunena zoona,asamangowanyoza amalawi.
Tell him kinnah worked heart and soul together,and took the ndado he’s talking about,to afcon
Timaziwa kale kuti team yathu ndi mbola,koma akuyenera kuonesa ntchito yake ngati Coach, koma ngati walephera basi azipita,asationongere ndalama
Kusula mohwepwa sichinthu chamasewera chimatenga zaka zambiri that’s why kwa anzathu kuli ma academy a mpira koma anthu amasulidwa kuyambira ali mafana …. Super league yinkakoma nthawi yomwe ma teams anali ndi ma youth clubs bcoz zimapangitsa kuti ma first 11 awo akhale ndi madolodi oti akamakankha Chikopa timayamikira kuti zoona sitinabetse dollar koma zinalowa chibwana
Ifenso amalawi tikuziwa Chilungamo kuchinya 45 mins 2-0 koma kuchinyidwa. 89mins 2-3 or 2-2 nanga pali nzeru pamenepa
Palibe wanena chabodza APA sizampira kuno
Kkkkkk wabwera ndi chipongwe kape ameneyu eti? Kkkkk
chlungamo chokha chokha
Ndiye flames imeneyo coach mpira anamaliza ndi achina Mponda.
He must fix is his job now
Ndikomwetu kumachokera ma players ngati gaba umaima mu psl ngati sum of de best players in tht league
Kkkkkkk chonsech dzulo walandila phone ya new one
sakunama
I completerly agree with u bigman
Kkkkkkkkkk masewera a mpira ndi nkhani zina
Vuto ndi ma club athu ku malawi kuno sauna kuphunzila mpira wamakono
Ndi zoona, ndi chifukwa ine ndilibe team… ….
Kkkk
Nyamilandu tamuchonse ntchito uyu mwachangu asanaulule za zithumwa za maplayer
Apakire bas, azipota ameneyo.
Mzungu anthu amenewa amakhala ngati akumva upite nawo ku ground ukaona wekha
Iyeyo Ngat Coach Achita Bwino Kudziwa Mamistake Athu. Ndiye Amanena Kut Timasewera Ndado.Ndado Tingasithe Bwanji? Ndi Ntchito Yake Ya Coach
He is right,chilungamo kuwawa. Kulibe mpira kuno.
Kkkkkkkkkkkk Mpaka Ndado? Koma Ndiye Xakunama Mpira Wakuno Nd Manyaka, Mbodzole, Zilapi Zenizeni
Ndimbweleradi …
Ndipo maplayer ake owuma hevy
we are far from real futbal
kwathu kuno kukanakhala kt timadziwa mpira sibwezi ataitanitsa iyeyo iye agwire ntchito yomwe anabwerera kt timuyo isinthe ifikepomwe iye akufunapo ndezomwe tikudikira ife,,
Zoona zake ndi zimenezo, tisadane ndi chilungamo apa,
ADZIPITA
zazii coach aziteroso
Akunena zoona mkulu ameneyu kwabasi ndiye bolaso pa zambia. Panopa yatumiza under 20 ku world cup chomwe ndi chikho cha achisodzela osapitilira zaka 20
Kkkkkkkkk
truth pains!!
Zoona zake vuto la amalawi sitivomera kuti mpira sitimathe koma kulimbikira kwake eeeeeeeee paja anthu osatha kulimbikira
Watching Malawi supper league, is like watching kids playing in the street .
Mmmmm Coach asathe mawu iye wabwera kudzaphunzitsa masewera ampira.Kungoyerekeza Flames kumenyedwa mu Cosafa ameneyu anyamuka basi.
Truth hurts, he’s just being honest, plain and simple.
If it is like that just show him the door to go back where he come from. I think the time he was signed acontract with FAM, they told him what he is suppose to do. Ngati kunoko kulibe mpila ndiye amadzataniko?, just fire him before it is too late.
comment yakoyi ndimbola yeni yeni ngatiso mpira wa ku mw,kudana ndichilungamo shame
#Apeter mkudanandichilungamo ndizoona ifekuno mpila sitimatha,ndife opelekeza timangosewela za kholowa yokhayokha
Peter K Mchacha pass me the weed please. coach wants super league coaches to improve on the style of play and zoti Super League timamenya therere ndi zoona. so super league coaches have to improve
He is 100% right,,mpira wa kuno ndimanyaka enieni.
Ndiye mwano umenewo adzipita kwawoooo
Abwezatu galimoto ija.
Chilungamo Chinayandikana Ndi Mwano Kkk
Ndizoonadi kuno kulibe mpilatizangoononga mbili yake
Amavomera ntchito asanaone kuti ikhala yotani?
Lol..
Truth hates
sakunama mpira waku malawi ulibe standard
Sakunama ai
zoona mpira kuno kulibe mungoganiza zija anafuna kupanga sulumba pa bingu stadium kudabukila kugolo kwake chosecho ali pagolo ladani
He is Wright anthu timakwiya ndi chilungamo that is why we can’t improve we have good. Players in Malawi but the system we use is not good . Start with the grounds we use very bad nanji Ku nursery kwathu Ku lower league gati po dyera n’gombe
Very true ..a Malawi sitifuna kuuzidwa chilungamo..
Kkkkkkkk ndizoona bro
Very true
Ndikutiko team imapita kukasewera mpira suterday n Sunday
Izi dzikuchitika kwathu komkuno,chomcho mpira suzatukuka mpaka kalekale
Kkkkkkk
Sakunama mpira waku malawi supasana njala ndimadabwa anyamata ochuka kumwetsa zigoli mu supa ligi amalephera ku national team how mitengo imawapusitsa kwambiri mpira wakuno mitera mmmm ayi zanyanya
Then he must resign and go, Analiko anzake achina Kim omwe anapanga zotheka ndi anyamata ake omwewo, osachulusa kunyoza
Eya apa ndiye walankhula zoona
zosewera za wanderers zija ati bola agoletse, i agree with RVG
mpira kumalawi watha tsapano
Nayeso thawi yomwey wazolowela kale zolandila et? Pita uka brouse ulele uko R!! Ndakwiya nawe
Amasewela ngati chomanga.
Ndiye Apanga Bwanji Kuti Flames Iyambe Kuchita Bwino?Komanso Mmene Waonera Ma Team Mu Super League Athandizana Bwanji Ndi Ma Coach Akuno Kwathu?
Thanks am Swahili people frm Tz, 2day I realize that also Chichewa is a Bantu language b’couse it sounds like Swahili language..
MPIRA WA KU MALAWI UMAKOMA KUMVETSERA PA WAYILESI KOMA KUWONERA mmmmmm
sakunena boza R V G ku Malawi chomwe amaziwa ndi ndale zopanda mutu basi
sakunena boza R V G ku Malawi chomwe amaziwa ndi ndale zopanda mutu basi
Its your task to change the way Flames is playing and that is why we are paying you ….. In addition to that, failing to lift the Flames up into Cosafa you’ll be sent back to Belgum and we’ll take back Kinah and Edie. Get note of that.
Koma akunena zoona monga mmene kunali surestream muja inkamenya bwino barca barca nice football koma kulowa mu league kungowaponda ati mpira akenyela kwawo its more physical than creativity
azngot pta kwawo bax astwonongere ndalama malaw szampra
Kochi ndiwabwino koma ma plays anthu amadalila ufiti. Tsono akakumana ndi osatamba zimativuta tizingo sewela supa ligi basi. Fiti zokhozokha.
Mawu mawu
True but we are waiting for him to show us the great thingis, may be our neirbours will stop roughing at us
Azipita kaya, mukumusungiranji??
lol truth hurts
Extremely truee
Sakunamana but that’s what he was hired for in the First plAce,to change ndadozo to football!
True
Xukunama zoona mpira mbola
Chilungamo chimawawa
Kkkkk juuuu
SAKUNAMA KOCHIYU, ine ndinazolowera kuonela English premier league, nde ndikamaonera za kumalawi izi zaphuphuphu aaaaa sizikoma ataaa. Mpira wa umozi umozi satimautha a Malawi kunena Chilungamo.
Paja anaka onera traning ya noma ndi a zamu
Ife a Malawi zampira izi ayi ife kuba kudulana ziwalo bolani
Ife tikuziwa kale
Coach woyamba kuyankhula za nzeru
ameneyu ndiye fodya akuyankhulayu! imyeyu tinamulemba ntchito kuti atithandize kulephera kwathu ndiye basi akonze osati adziyankhula za chingambwe zakezo.ngati zakoza adzipita kwawo coz adzingowononga ndalama zathu zamisonkho.
koma kunene chilungamo man mot zomwe akunena mr mzungu zi ndizabodza? akunena chilungamo
eyetu ndiye akoze thats why we employed him
haha so u think angakonze hw chitipa utd plays.
Koma munthu ameneu mutu wake sulibwino,amabwera kuno amati akudzata?
even nyasa palibe akusewera.so if this is the case then we might send him back
ameneyu akungofuna kutha chuma chathu
man wat u r saying is a non starter………even my Europe ma national team coach their job is to apply tactics according ndi opponent kukumana naye……zambiri ma player amakhala amakuziwa from their club’s……..wat u r saying it means iyeyo azikochatu team ili yose ya super league? to be honest pa Malawi pano soccer zero
@ Norman, tell them. Even pa company ntchito ya Chief Executive sikuphunzitsa anthu ntchito. Talent or skill ndi zachibadwa. Pali anthu omwe ali mmidzi omwe ali ndi skill than omwe akumenya ma clubs. Koma, exposure alibe. eg Mabvuto Lungu amkamenya ku mudzi, Mr. Gondwe ndikukamutenga kuti a bullets amuyese ndie munamuona bwanji?
Norman umatsata mpira. Ntchito ya national team coach sikuphunzitsa anyamata kaseweredwe ka mpira koma ma tactics. Kulibe soccer kuno.
thats correct then he might implement tactics to the national team he is going to select.
kwa amzungu amzathuwo amalowa kaye mkalasi kuphunzira theory kenako practical pa ground.
kudana ndichilungamo,nzungu akunena zoona mpira wa pa mw ndi 10 pa 0
Tinazolowera kunamizidwa that’s why tikuwona ngati chilungamochi ndi mbwerera …. Am a soccer fanatic koma it’s now a decade super league sindionera …. Soccer is in rural areas as Wellington Nowa has said ….
kodi akutsutsa ndi ndani?zomwe mzungu wakuyankhula ndi zoona ndiye imyeyo akoze zofowokazo. ndakudziwani enanu ndinu akampopi fc timu yanu ikungomenyetsa manja pamwala thats why mzungu wayankhula mawu amenewa coz adaona momwe achina sulumba,mulozi, sayilesi,chimango,anong’a,mkwate kumangopanga pakala pakala okha okha pagolo osapawona. tithokoze mzungu potiyankhulira
kodi Iyeyo akonza bwanji zofooka. ma coach a super league akuyenera kukonza hence atabwera ananena kuti he will work with super league coaches kuti the way of play in the league should match his tactics so its all up to super league coaches
Akonze Team Ndiyimeneyo, Asamangokwera Ma Motor Odula Ngati Kuno Tilibe Macoach.
Bitter truth
Ndimangodabwa, Eh! Ine ndi wamaule, eh! ine ndi wamanoma! AA! Mpira ngati wakung’ombe! That’s why I don’t support any team in Malawi. Suprisingly, some people still think the coach can play soccer. HA!
hahaha you are right
Players are made from clubs and not ku national team.
His duty is to identify capable boys who can make a strong national team which will yield good results.
ngat ukunena zoona ndeno iyeyo amafuna apeze zakupya kale nde amadzatan asanikwiitse wadyakale zambili!amalawiso tili ndisanje 2much rvg kumufewetsa mpamene mmalawi osamupatsa ndinjinga yomwe!!kupya ndimafupa omwe kulupodi
NDADO MUKUNENA NDINU A NYUZI IYE AMADZiwa word yoti ndado.mukuzisisa nokha simunganene direct zomwe wanena iye mayazi koma muonjezere shot.kwanu ndikuti
Kkkkk Dats wy we cal u to help us,so r wettng 4 u to change de sesuatn here in malawi.
Kkkk oooh Phada weni weni?
Ndiye ngt ndindado azipita
100% mbola mpira panyasa kkkkkk watchaya nad DOMU ngeboza
I know how hard is to swallow the truth,well said new coach,kukhala big fan wa flames mkulimba mtima wawa,moti ine sinkhumbira yayi dhala kuopa ngazikhweze!
Yo read this, this coach is rude Benji Pogba Tembo
Akunama??. Sangadziwe dunyu?
??? eti
Nchifukwachake tinamuitanitsatu kuti achotse phalalo
Ndipo ameneyo akunena zowona eti kumangotinyana wokha wokha kubwera timu ya Kuja kumangotinyidwa shem
Tikadali Patali Ndimpira Kwthukuno.
Ndikugwirizana naxo zomwe coach wanena!!! Palibenso team yomvesa chisoni ngat Flames
Absolutely true
Kkkkkkkkkk wakula watha aziona azisinthe ndado izo kukhalo ma player kkk
Sakunama sititha mpira kuno
Ndiye ntchito ya coach imeneyo kusukulu ana akanakhala odzindikira zilizonse bwenzi kulibe mphunzitsi.
Infact what we call football here its total trash,its something like football.Lets find a better name pliz
kkkkkkk! koma u
thats why we emplyd hm.let hm shut his mouth and tel the boys what to do rather than talking hogwash
Mtengo okhota, sitipala matabwa. Timangosema zipande basi
maganizo opusa ngt RVG taona maplayer ife akumakanika kuchinya afta some tym mkukhala maplayer odalilika pochinya zigoli.
couch do play a big role in players.zili ngt sukulu zimene zija akulu if th teach z gud its more likely kt ana atha kuchita bwino.
sizamatabwa zakozo apa wangofuna kundiuza zomwe umapanga.awaphuzitse mpira!
Supported
Itrue l saw that story in Nation news paper yesterday akumenya ngati Tenies
Angathandauzile mulimosemo nkhani kulibe mpila olongosoka
Mthamangitseni Asowe Ameneyi
Kaya sananene koma zoona zake ndizoti mpira pa Malawi pano ndiosasilirika, kazionerani mbwerera zanuzo iyaaah!
“Ndado” , meaning?
Aaaa mesa ankati mma player a flames ndi dihlu
Fake news kkķkkkk
Ndado ziliku Bullets ku kulibe zigoliko
Translation ya chizungu sititenga each word kwa odabwa ndado….sindkudabwa ndzmene wanenazo poti ayiniake we oredy knw mpra wathu nd phalad compared nd pa zambia pompa wat am interested in ndzmene ngat wayankhula kut tithetsa bwnj u phala wathu if nt then azpta
Zoona otherwise ine zomwe ndawerenga from The Nation newspaper RVG wati watching the way some players were showing skills in the Superleague was like watching “tennis” ndiye poti chichewa nchathu a Malawi tennis atha kukhala “ndado, mbwelera, phuphuphu, etc”
Hehehe true gift tennis eesh nzungu wawelengadi uyu
Ndado, panja penipeni, mzungud anganene zmenez?
English translated to chichewa umbuli bwanj a malawi
Ndye inu omwe snu mbul tachtanino translate ndado to english, panja penipen to english.
Musamangochta reply kut muwoneke oziwa m’mutu mul empty
“Child games” osamangokhala otsutsa nthawi zonse.Muzatsutsa ntchentche ponyera..
kkkkk sakunama Mwanyaka weniweni mchabwa wastage of tym and resources
So what did he call Ndado in English?
‘Child games’.
Wow!
Hahaha wasima omweu tiziwinana kulibe mpira kumalawi
Wakuuzirani kuti…..? Zaboza basi…. RVG ndado akuzidziwa..?
Nayeso Ndado waidziwa liti? kwa azungu kuli ndado?
kumapanga ma comment othandiza ,iye amalankhula m chingelezi olemba walemba chichewa zomwe mukutsutsa ndiziti pamenepa ,kulemba bola dzila latuluka kuti simusowa ,mumapanga comment pa fb ,zosapindula
Mayaz musamuopseze,iyedi mzungu ndado waziziwa kut?boza bas Malawi24
Then olemba waa supposed to translate the way it was said… osakokomeza nkhani.
But chilungamo mpira wakumudziko (MLW) ndiwochitsa manyazidi, imeneyo ndemfundo yankhaniyo
A gladwell ndevu pepeya u mean to say u don’t know about figures of speech, metophors, muchichewa ndi mikuluwiko.haha haa
tru