Phungu wa dera la kummawa mu boma la Rumphi, a Kamlepo Kalua, apezeka patatha sabata osaoneka.
A Kalua apezeka lero cha kummawaku mu boma la Blantyre, mmbali mwa mseu.
Malinga ndi malipoti, a Kalua ati anaponyedwa mmbali mwa mseu wa pa Njamba ndi anthu amene sakuwadziwa. Iwo ati anthuwo anangowaponya iwo ndi kubanduka basi.
Atafunsidwa kuti anthuwo amawasunga kuti, a Kalua anena kuti sangathe kukumbukila kumene amawasunga.
A Kalua apezeka atamangidwa ndi zingwe za Blue umene ndi mtundu wa chipani cholamula cha DPP.
Koma a Malawi ambiri anena kuti a Kalua samasungidwa mokakamiza ndipo iwo anangobisala pofuna kuipitsa mbiri ya chipani cholamula cha DPP.
Anthu akudabwa kuti a Kalua apezeka akuoneka osamba bwino, ndevu zometa bwino ndi tsitsi lotchetcha bwinobwino.
AVE MADZI MTUMBUKA AMENEYU , MAYENJE AMENE AMAKUMBIRA ANZAKE WAXAMBA KUGWERAMO YEKHA. MUMU FINYE KWAMBIRI ASANZE MABANZI AMENE WAKHALA AKUDYA
Tiyeni tizingopanga zathu,andalewa alibe chilungamo Komanso tikungotaya nthawi ndikumanyozana tokha-tokha osaukafe.IWo ndiolemela kale.
kaya bola kukandichera ine ndimayamika ambuye komaso kumupempha kuti andininkhe chakudya zikatero nkuyambapo kuthamangathamanga koma dza awa mumati andalewa aaaaaa sanandipangirepo chokma chiyambireni democracy aliyense amangokhutisa mimba yache ndie kuwasapota iz a total waste of time .eeeeetu
kaya bola kukandichera ine ndimayamika ambuye komaso kumupempha kuti andininkhe chakudya zikatero nkuyambapo kuthamangathamanga koma dza awa mumati andalewa aaaaaa sanandipangirepo chokma chiyambireni democracy aliyense amangokhutisa mimba yache ndie kuwasapota iz a total waste of time .eeeeetu
Kkkkkkkkkkkkkkkjjkk
Tisachulutse mitu tiyeni tizione chaka chamawachi ndiujai
MWINA AJAMBA KUJAMBULA VEDIO NDALE ZAKANIKA.
Some Malawians are and will always talk stupidly. ..even on very sensitive matters. .
mayb was his plan pofunakuzemba the trueth about somethng ahead of him
What apariamentarian? Look at him.:
Is this is the way kidnapped person look like? Mother Malawi ……..
Kkkkkkkk kunja kukangoti kukangoch kwacha nkhani zake zokhazokhazo kumangolimbana ndi boma basi,ziti tiziganiza kuti biznezi yanga ingatukuke bwanji,naga chito yanga ndikuyenda bwanji? Ndi zona zotelo, koma eee kamulep eee peter eeee Chakwela eeee Bakili iiiiiiii, muzingolimbana ndi zimene mumapanga pakhomo panu kuti Moyo wanu ndi wa ana and utukuke,Sindine wandale ai ndipo ndilibe chipani izi ndangonena sindili uko muli,ndili uko komwe inu musali
Amalawi Timakhala Ndi Mind Set Ofuna Kuyitsa Mbiri Ya Azathu Khani Ndiyakuti Kaluwa Watchela Ku Paliament Basi Ngati Anali Ku Chibwezi Angonena Akazi Ake Amukhulukila Akambila Kma Osati Zabodzazo
Kamulepo sadzatheka ndiozunguza ameneyi
Gyz umenewo ndiwo ufiti mwanva ne.kkkkk
MMMM, there is no fearless politician in Malawia like kaluwa, let us wait n see
Kamulepo pamafunikanso apolice amange akupanga ndale zopanda mutu
Kkkkkkkkk che Kalua mwangoziyalutsapotu apa
Shit
eyemwe ali wa dpp ndinu zisilu nd kape wanuyo yemwe akulamulayi mwava mudana nd chilungamo mbuzi za anthu
KKKK KOMA AMENEYU
Panji namwe mwetemukome ngeni wala wakale wakakomanga mwachita soni chifukwa wanthu wazuzura chomene
Zamabodza basi,technology kuyitengera pagong’o ndi ubulutu pa democracy
Yakwiya Mizimu Mbava Zonse Zikhaula
Olemekezeka ndi chiyani inu mwatani kkkkkkkkkk
Ife zisatikhudze a DPP tilibe nthaw yimeneyo mufuse bwino akuuzan komwe anali chiwuno amadala ameneo
Uyoyo ndi nbava kdi …..Anaba chan…..???????
I am not a DPP member but this is something else
I’m not surprised at Malawians ladies and gentlemen. True Malawian would agree with me that for along time our enemies have been hunger,disease and jealousy. At least we were done away with the two half way but jealousy is right there untouched. Let’s pray that God should do it for us.Even outside Malawi, you can’t trust your fellow Malawian. It’s better to live with someone else but not Malawian for the same reason ( jealousy)
zabodza izi munthu wopangidwa chipongwe sangakhale pansi atafunda jacket koma osamba bwinobwino,anachita kulawilila mammawa kukatulidwa ndi munthu nkuzikhazika pansi paja atasamba kale wausilu zachamba izooo
God took izeki from us,and give us kamlepo!!!!!!
anabisala yekha ameneyo
Zinthu zina ukamava kt wachita ndi wa mkulu kumvetsa manyazi,kaganizidwe kake kameneka aaa! dzipatseni ulemu.
kkkkk!pamajiga!
Kkkkkkk Kamlepo naye ndi drama
Kkkkkkkkkk koma amalawi sitidzathekadi ndie kuti akanakhala kuti wamangidwa ndi chingwe cha rainbow m’maonekedwe mukanati wanjatidwa ku joni? Ok nanga chikanakhala cha white mukanati chani chingwe ndi chingwe basi vuto ndiloti ife anthu timalephera kusata chilungamo pazolinga zathu,timachuluka nzeru koma osapeleka solution ya vutolo shame to all those who thought they are wise enough than others we are all in the same boat
Tingodikira freddokiss awulura paja ndiyemwe amatiululira mu ndakatulo zake zija “anapha mphwiyo ndani? Mchifukwa chain? Nothing is impossible, yesu anadzutsatu Lazaro atadiwa” π kkkkkkkkkk timumvaso akutokota za madalawa
Kuyambila lero inemwana wabambo billiat ndikulengezakuti phungutisanamusankheazipita kukayezedwa mmutumwake kuchipatala kutimutuwakewasalazakazingati kutiuzungulire akati zitatu ngatiakamulepowa tisamawasankhe
the whole of kalua doing that,,,,malawi full of shameful legislators.Pa dzana wina anagona m,pariament ,lero mukut kalua.Fuko langa,why coming only after the openning of parliament?you are coming and with no explanation!!or bodza ulibeko ayi??ukanangolikocha tikanakhulupilira.Bambo amunthu kuthawa udindo,,l could love if they could take you a place where you could get on the track before joinning the parliament cos theres nothing you will contribute…Shame on you
mwina yakutuma ndiichakwera iwe kumangoganiza ngat mbuz bas
Kamlepo’s action was incomplete metamofosis
Kkkk apenga ndale
Kkkk apenga
A kaluwa ngati ndale sizikuyenda bola kukayamba gen ya mtengatenga ndi mtokoma ku MLOWE pa nyanja ya malawi
Takuthokozani bwana Kaluwa ndikudziwa kuti plan yanuyi mukuyimila anthu akumpoto onse mzelu zanuzilingati nkhuku
Anthuni ndinu atulo,mukungo bwetuka,zoona muzimva.khalani pheee,atsilikali sanena akamapanga chinthu,
Anthu akumukonda Kaluwa,musaiwale munamanga mussa lelo ndi kamulepo.mkanika tiona
qKamlepo ndi dolo pa ma Drama mawa akupita ku china drama ndi JACK CHAN
kkkkkk, akuluakulu, ngat chamba chakukanani chisiyeni! chamba sichabwino a kamulepo!!!
kkkkkk, akuluakulu, ngat chamba chakukanani chisiyeni! chamba sichabwino a kamulepo!!!
Kkkkkk APEZE njira by FREDOKIss
which language it is?…….Study in Belarus
Tazisewelanani timva m’mene zithere mukamaliza
kamlepo amatimilira umanena zoona teach them zandale enawa samazidzwa ngt zinthu szkuyenda osasiya kuyankhla ku boma kumangdwa kulibe ntchto sanakumange pakamwa speak out kamlepo am proud of u….
Kkkkkkk kodi ndimene zinalili aaah koma he must try plan B coz imeneyi yamwa madzi
Asaloledwe ku paliyament pokhapokha, madotolo aku mental atasimikiza kuti ali bwino.
Maonekedwe ake ngati munthu wowuka kwa okufa
Kamulepo kutha kwa mzerutu uku
Wayamba misala Kamlepo komanso kufuna kuipitsa mbiri ya chipani cholamula ndizibwenzi zake,,,,,komanso anawuza girlfriend wake kuti amunjate, chutsiru chamunthu.
Wandale ndiwovuta kumvesetsa kapena kumvela chisoni chifukwa choona amachiziwa ndi eni ake andalewo nde kutaya nthawi za kalua kapena pita kwaine ndikuona zosathandiza anthu ofuna anzawo zikavuta koma pakalowa mbewa ndikumba ndekha
kkkkkkk zaulendo uno…….abwera ali onjata???!……….wawanjata ndindan???
Tiziwapempherera Amasulidwe Ruth Makunje Willard Chikomo Cosmas Kholowa Noel Wathanzi Kasinja Pempherai Likome
Kkkk ndionama bwanji kamlepo akufuna ayipise chipani cholamula kkk wapenga eti
God Be With Him
osachibakira chipani chopanda vision chi zinthu kumangodura,life in malawi is worse.cant you see?mbuzi zawana awanthu
A kamulepo mudakula bwino bwanj , kulolela kukagona pa lound about kuli kufuna dolla kumeneko? Aaa ukhalike ayise ngat munali ku room tangonenani akaxanu mukambilana nawo man osa yokalikayo ayise
Kkkkkk Ndale azanu kkkkk
kamulepo mbava iyii tikuiziwa
Mwana wake wastanic, iwes katchal , akazak hul shaaaaaaaa kma kaluw shame on u
Kkkkkkk koma kumeneko
Akamlepo pliz pliz chamba mukusuta panochi kaya mukumachigula kuti pepani ndithu chisiyeni pliz mubanda udyo kuchita kumposa manganya
Musakambe zambiri ngati maganizo ake mukuwadziwa. Kamlepo ndi khuluku.walemba mmadzi,achule awerenga.waona kuti ma allowance aku parament sawaona kkkkk.Kuthawa anthu anamvotera ku Rumphi kudzabisala kuno.mukutithera malo kuno osakatukula kumpoto bwanji?nkhalango yokhayokha osakazimangirira kumpoto kwanu konko?hehede misala ija yayamba kulowelera
Andale amadziwana.
kkkkk…..wamisala wabwerako yekha njala itamusosola
Bloodfucken kamlepo you take as Malawians fools?
Bloodfucken kamlepo you take as Malawians fools?
The one, who don’t know, that he don’t know” what he don’t know , He don’t know that he don’t know.
Eee koma ma don’t NDE alipotu
Kkkkk..Kamulepo sazatheka
Kkkkkkklk
Chilungamo chankhani akudziwa ndi chauta tikhoza kungochimwapo chabe!
Gayizi Asamachezamotelo Chawona Mzakochapita Wachilipa Iwe
He has been at a ‘kachaso spree mix midori and Black Ponda’.”
mwesesatu mwatchuka anthu akambako za inu big man.
kodi Sugar wayamba kupezeka kumudziko?
dpp z a tormentor, full of hypocracy, tyrant regime etc.
tikukhalangat tym ya adolf hitler, evrythng z terrible.
kkkkkk
Takulandilani mukanasowa ngati chasowa komabe munena zambili kuchita izi ndani kapena Ndi?
Mwatikhozga soni akulu…but u look smart,komwe munaliko mumasamba
Munthu woipa mtima uyu ndichifukwa chake analephera kulamulira Dziko la Malawi.
kkkkk. komaso zakhala bwanji
Ma comments ama Cadet sasowa.
kikiki
Chonjata kapena chinjatwa?
Tinsombati I think tigokhala tingowamba tikoma ndi nsimayi njala…sorry wrong packing
Kkkkkk akitaa saafa amangopezekaa wonjatwaa Kkkkkkkk koma ka juzii kameneka amakakonda Mpakaa makid napperz anampezasoo nakoo Kkkk
Awa ndale zawavuta siyani ndale anzanu apitiliza,zaonetsa kuti chotimuwauze amalawi mulibe mwati mutchuke zamkutu!!
Kamulepo NDI mbuli pa ndale unys
Watha maplan Kamlepo kkkkkk nde ena kumachiikira kumbuyo chimunthu chopusachi
This is exactly like what happened to late Chasowa. He was dumped at a spot where he was not initially killed and remember the stories that were told. Mind you those killers are still out there enjoying normal life. Wait for true facts to come out people.
Sizikugwilizana pamenepo mwaika chigamba cha kutchena pa jeans
Andrew, if you don’t understand and follow issues just keep quiet.
Sizikugwirizana kumene chasowa anali atafa nanga babawa anali nditizingwe ta blue cholinga azinamizila DPP watchera kumwezi nkhanga za thaima Mwana Tchwee
Sizikugwirizanadi.
inali plan,
inali plan,
Kkkkkkkkkkkkkkkest
.,,,
So Mukuliuza Dziko La Malawi Kuti Bwana Kamlepo Zoti Anapangidwa Kidnap Ndi Zabodza ??
kamulepo ndi nganga alephera koma popeza alimoyo aliwuza dziko chomwe chida chitikira
We are too quick to judge even in the absence of all or enough information.
What if? What if? What if the kidnappers deliberately staged the release of Kamplepo Kalua in this manner knowing that people will react exactly the way they have?
He was clean. In tidy clothes. Well shaved.
The only reason or main reason why people are doubting Kamplepo is that he was clean.
Hypothetically speaking, he was sedated. Cleaned and dumped.
Lets see this from another angle.
That said, I am not saying Kamplepo is caught pants down or that the people are wrong.
Just look at it from another angle. Copied from PK
I think your reasoning is better than most of people commenting here
Ummbuli chamba kusaziwa ndale PEPANI kaula uchepetse cocoaine wakoyo
Chiwewe nchowopsa zedi akalandile katemela chisanafike poyipa kamlepoyo
Anangofuna Kut Tikambe Za Iwo Basi!!,
Wa waaa!!! Akamlepo Andala Achikulire Mwatuluka Anthu Atazunguzika Kuchiteke
Angomva kuti paliyameti yasegulidwa ndiye kubwera poyera kuti akatafune ma allowance
Ok..sandikomole ndiphwete ine
Akamlepo tazikulani inu mukungopanga ndale zachikale zachimizi basi
Kkkkkkkk
Hona murara !!
thiuzeni soona bt dis guy stlu live to same the.ry bt. duwhing sath. ulong loock.is not nys guys rykyt dis Dpp ai thik wht too dis ayenela kumpitha. kumeto basi
KOMA ndiye Wa actor. Waiting for part 2. Watchuka kuposatu Aunt Tiwo
Childish tricks by the hounerable person
There was a byelection in Dedza central west in 2001. UDF was in power then with aTcheya at the helm. Marshal the Duke was the UDF campaign director for that by election. It was catastrophic. People were not patronising the UDF rallies but MCP’s. On this day Justin Malewezi VP then had a rally outside Lobi. Marshal and his friends ( young democrats) went there paraded all the chiefs before Malewezi having UDF badges stack on their jackets. All of them unwillingly had been put on UDF t- shirts. Yellow!!! This has reminded me of Hon. Kamlepo Kalua tied with blue strings (DPP colours) to indoctrinate Kamlepo or in other words DPP showing to the whole world they are in command. They couldn’t kill Kamlepo because the whole world was watching with their cameras full throttle. Malawian politics!! I like history to relate events as repeats.
Angonjatidwa ndimahule palibe zandale apa,DPP ndimaMafia koma apa musawanamizire.
Kamulepo Ndiwamkulu ndipo amalankhula mutamufunsa akumati anali kuti?asatipusitse ameneyu mwinatu anakangana ndi dona yake ndiye amakapitidwa mphepo kaya
admini kawauze amakutumao kut alipo angapo akutha kuzindizikira kut mwangokanika kumupha like u did wth chasowa and njaunju… and ali ndi nkhawa kut chilipo mwamuchita
Ine ndingokambako zayapa tsangano yokhayo zinazi mmmm ayi ndingayambe kuchimwa nazo coz Dzikoli lafika pondikwiitsa. Nde mwati a police patsangano anasambisidwa chokweza makofi ndanyamata achipani cha bambo Awo?? kkkkkk akudziwana asiyeni akana kuikoka kwambiri akudziwa kuti awonekela ng’amba ndamodzi amasapota munthu mmodzi nde sangalimbane. akanakhala wa Otsutsa ndithu pano komusunga kusakudziwika, Nde apapa chongofunika ndikumangoyang’ana Kuchitila kuti tikakamba zambiri Abwera kwa wina Mudzina la MRA akufuna kudzakutenga nde eeeeeh ayi tiziona kkkkk koma osamakhala mowopsezana Tonse ndilathu dzikoli
Every element of madness starts at any point like this, surely Mr kamlepo will run mad soon…………………….loading
If he is not already mad
Evil thoughts
ndie ngati a polisi anavulazidwa ndi a chipani, kuli kovuta bwanji munthu mmodzi pano ma cadet awopsya ndie poti anaphatikizana ndi ma young democrate eeeee ziliko ofunika apite ku darfu kapena ku nigeria
Deal unaccomplished
Ok
kkkkkkkk ngati chili chamba #adah kamulepo udsuta bwino wanva.
kkkkkkkk ngati chili chamba #adah kamulepo udsuta bwino wanva.
Political comedian.mbuzi yamadala
Kkkkkkkkkkk zoonadi kamlepo anali ku chibwenzi ku chilimba kkkkkkkkk kunamiza mkazi wake
kkkkkkk this z a drama $ fun akulu amenewa should join Nolly wood
akanika mutha ndiphoka. simisala muzaziona
Maeende akè ameneyu ķkk
kape wasowa chochita
wonder shall never end. kkk
Wht if the kidnappers are smarter than u guise,wht if thy did all tht so tht u shld thnk the way you are thnkng right now
Asiyen man alankhule chilichonse only GOD knws better, but thank the Lord pot wapezeka alimoyo
U know wat Kelvin if this was his first attempt it could have bin another issue but akuti nkachiwiri kupanga film yomweyomweyi…..Last tym he did this in UDF regime that’s why people have lost hope in him
kkkkkkkk kma ma journalist enawa nde chabwno akanamangidwa nd chigwe cha red mukananena kut nd MCP??? Or orange mukananane kut PP…..be profesional wen wrttng ur stories. …aint a DPP supporter bt aaaahh shame on u!!!!
Nonse Amene Mukutsutsa Ndinu Zitsiru Mituwo Adangozika Mulibe Zeru Agalu
ophusakwabasi DPP ndichiyaniso baba zamisalabasi kamlepo ndiwadzelu atuluka posachedwapa ndikatakwe amuna patawuni kumachenjela patawuni baba
kodi ndizimene mwayamba kumuzunza munthu nkuyambaso kumusemera nkhani, kodi osathana kaye ndi nkhani yopunphuntha amene akugwira ncthito
mseweroli anyoni anali kamlepo kaluwa, Giring,ande anali a MRA, Dimingu anali Fredokis ndipo amfumu anali a DPP walemba ndi Kamlepo Kaluwa wakonza ndi a DPP
Umatha bro
KAMLEPO msuzi unatha waona Malawi alipheeee osamuyikila kumbuyo DVD imeneyo siyenda malonda uyisovenge
Kamulepo wayamba kupanga ma drama
Zoona muthuwakuluyo akasowe zachamba kuteloku zachezayela pamenepo sitidziwa watumayo wamulonjeza zingati koma ndalama ndiyachabe ndawonela kaluwa
Mbuzi iwe nkhuku yawanthu
Munthu angajimangilila yekha he ntchewe iwe
Akupasanawo eti ndiwetunduwanjiwamuthu pakakutukwana zomwezi
Ukakhulupila bodzalo ufaphawiase
kusonyedza kuti chilichose cha blue ndi cha DPP eti??
Kkkkk kkkkk Ndiye akuti anali kuti? Kkkkk kamlepo,,!!!!!!
Chiwerengero cha anthu a misala chikukwerebe wina nde nd ameneyi, posachedwapa uyamba kupezeka mmisika iwe, Wapupwa iwe Kamlepo, bambo ache Fredokiss
Anyoku nawuso nawo mbamisala tungwa iwe
Zidzikugwiridzana ,Fredokiss sidzikumu khudza
Kufuna kutchuka.I thought ali ndi nzeru koma mbuli ndithu
Mbuli agogo ako boi
Ndemwati Kamulepo Angazimange Yekha? Lalephera Chabe Boma Kumupha, Analimbana Ndi Kamuzu, Buluzi, Bingu Nde Bwampini Munthu Wopanda Mano Mkamwa Angatani? Tisiyilen Ndiyekhayu Munthu Wolimba Mtimatu,
thts what I know
Ngati ili mbili azionongera okha osati kutchula za chipani, kodi nkhani yake kuti mpaka afike posowa zinali za ndale ngati. a Kalua kulani bwino osati za uchitsiluzo, kusungidwa ndi zigawenga osalandira chipyera a! zabodza izi a kalua, ndale siizi. Nyengo ino tayambayi ndiyokuti tizionera ndikumvera mpira osati zambwererazo. Izo ndi nyakanyaka zanu mwamva…..
Mwina I ‘ll go for Head akanena iwo uja ndiemweyi Kkkkkkk
Mbuzi kaluwa galu weniweni ndale yanji iyi ara kukhala uko mkumanama kt Dpp ikufuna kuwapha kutitenga opha kwambiri chani? Mbuziiii!!!! Ndisaveso 2019 tili mBoma be
ndaale ku Malawi
bastard. castrate him wasting pipoz time
down ball
D just shall vindicate n d innocent ones will b protected only God knows more than us..
Munthu akuoneka kuti amamwabe tea wamkaka achikhala amasungidwa mokakamizidwa sakanaoneka chonchi kkk koma mtundu inai mmmh
Mwachewa imwe nkhuku zawanthu
Pangani vyino pala vyamunyelani pemphani kujumpha muyowoye vyamavi apa
Akanamanga imwe seee
Iwe chakuwawa ndichiyani kapena ulingati finye zakoyo?nkhalupa tachioneni finye
Sindiringati finye zakoyo kuti andimange tulo
hahaha kamulepo sazatheka basi kufuna kupusitsa a malawi
Let’s wait, atiyakhula bambo kamlepo paja anyamata antambo wa blue mumathakupanga chilichose,dzana mwakwapula a police pa tsangano chingakuvuteni ndichani.
hahahahahahahaha ziliko chaka chino kkkkkkkkkkk
Mr kamulepo wayamba misala ndi ofunika kumutengela Ku chipatala cha anthu a misala Ku Zomba. munthu osowesedwa samaoneka ngati uyu. I hope some went missing in his medulla
Wamisala bambo wako wamva galu iwe
palibe vuto bola ndanena chilungamo mukachedwa naye akuvutisani. muthoyu wayamba kuchitisa manyanzi anthu omwe adamuvotela and i don’t think he will win again this coming election 2019
Wayamba misala ndiwe coz you’re just looking on the surface
not on surface but deep down. ndiye ngati alibe misala tamufuseni bwino akuuze kuti anthu anamubisawo ndi akuti naga amusiya chifukwa chani.? this is nonsense
Mmene amalankhulira muja lero angakhale bubu? Kkkkk mifunseni anene bwino asanamizire ububu
Kkkk Kamulepo wayiwerenga kuti ngati angamakhalebe kuchibwezi mudzina loti wasowa aphonyana ndi ma allowance aku parliament hahaha akalongosola bwino kwa mkazi wake
Kuyaluka uku at this age zibwenzi mpaka 2 weeks
Ndipo ikadapanda kutseguludwa parliament akanatha mwezi.
Usiye chibwana.
Ungandichite chani iweyo Mselema Roddy Felix ? Zopusa basi. Ngati Kamulepo ali malume ako uwauze kuti dziko silinayambe ndi iwo.
Kkkkk kamulepo nd mdala kumutu et
outdated tactics!!
KKKKKK Analidi ku chibwenzi awa,konda ine si Wa bho
inu mzanu anali mmavuto(aakulutu Willard Chikomo Cosmas Kholowa Evance Gopanje Noel Wathanzi Kasinja Maxy Kay Phiri Pempherai Likome
Kkkkkkk kamulepo anapangidwa ati kidnap…
Chonchi national football team yingachite bwino? It does exactly what is happening here.
Kamulepo kalua he is a good actor kkkkk mr james bond!!
last time when chaponda burn his office people was sayn thats not true chaponda cant burn his office alipo waotcha akufuna kuti tiziganiza kuti waotcha yekha after 1 week ndalama zinapezeka and everyone started believn kuti Dr burnt his office!!! same in this scenario wht if those guys abducted him want us to think mmene mukuganizira kuti he’s jyst kidding!! the trueth will be reviewed
choka iwe kamlepo ndiye ukumuphunzilatu
man ndnu akape heavy are yu saying muthu opangidwa kidnap amaoneka choncho hahaha akufna kunamiza mwana chan ,, ndye bwezi mwana wake ali busy ma dance ku comesa last friday bambo ake atasowa think malume ndi tricky offcourse zthu dziko muno szikuenda bhoo kmano tasamange zthu zoti tizipuzana wats dat ,,childship mission zachikalekale
Aubrey Mazinga you are very right
U r ryt my bro the problem is :,most of DPP guys r on social media trying to defend their masters but we as malawians know the truth so if u see these cadetes all over social media just leave them ,thus y they r beating police now by blaming them kut akusapota mcp ,ungoziwilatu kut ambiri ndi mbuli
Dpp cadets go to hell
no wonder u r writing ” de truth will be reviewed instead of revealed “
Mafia Vs Ninja………kkkkkkkkkkk
hahahaha koma kamlepo tazikulani madram amenewa penapake aaaaaa olo bola akanazipaka matope ndi kuvala kabudula kukhala opanda malaya mwina koma dram imeneyi ndiye aaaa
Uyowoyenge vyamahala ntchewe iwe
Ukulemba waka vyamavi apa pusi iwe
Munthu ali ndi pakamwa adzazilankhulila yekha osati mumulankhulile ai. chilungamo mpaka chidziwika.
bwanji sakuyankhula?
kamulepo pezan njila ina yoyipitsila DPP osat ximenez mukupangaz Amalawi cfe ana wot muzisewera nafe phada wanuo shame on you
Apeze njila inaso bwanji oti ife timadziwa kale kuti DPP ndiyakupha Chasowa, komaso pa 2o July ina ndikhani ikukanikayi yamunthu waACB adaphedwa uja, ndiye mufuna Kamulepo ndiye akudziwitseni zimenezi?
Mukuyankhula ngati pali ulamuliro umene simunafe anthutu anthu a Blessings
kod kamulepoyo ampeza alind mabala kapena akuwonetsa sign yot wamenyedwa?
Mayaz eti kkkkk zinazi koma aaa
wamisala ameneo akufunka ku mental hospital
Kamulepo kaluwa mutu wake sugwira paja mankhwala aanthu openga ngat awa adatha et…. Mu2 mkulukulu kumanama ngat chimwana aone zina osati njira yake imeneyi aaaa kumakula
Vindele vakufikapo imwe mwa vakumwera nkhanga imwe tikumulerani mumautenanti kuno kumpoto mwahuno mukuyooya vinu pakwiza ku mpoto passport kuoko
Big! simukunama chingakhale panopakati alomwewa adzadza kumautenant koma chomwe chimandidabwitsa ndiichi amati tivotela wakwathu koma mavuto sawachokaso kumadzapemphetsaso pakati pano ndikumpoto aleke kuganiza mwauchitsilu chifukwa tidzaleka kuzilandila zitsilu zimenezi.
@Gondwe & Mphamba # Kambani zandale basi osati mtundu kapena chigawo muziganiza mwakuya ngati wanthu osati zinyama!Abale anu nonsenu timakhala nawo bwino kuno kumwera ndipo ena ndima best friend.Samalani polankhula!!!!!
ndiyeno mungatani?palibe zosamala pamenepo
Limaninge waka mahona uko vichewa imwe nozelu
Nkhumba zawanthu imwe machenya gazuzu
waphalire wachewa wakuzala chomene vindele nadi ivimwe
Yai Akulu apa Kamlepo wateta nane DPP nkhuyitinkha kweni unenesko ngwakuti munthu wakusowa wakuoneka nthena?
mukhumba waoneke ngati ula wakasowera ku USA wakuphyoka?
Atumbuka mukutu vyichi azibweni panyoki
Akhaula galu ameneyu pedza ina njira osati dzopunsa dzakodzo
Iweyo mbuzi ..
Inu atumbuka okhaokha dzitsiru dza wanthu ndale simudzidziwa koma kupha ma albino
Wachamba ameneyu
Wachamba niwe mbuyawo
Lkkkkkk
Rubbish, wasting our time
U 2 ur rbbsh
I dn’t cr hu u’r but Ur an idiot fck
I like that, happy?
Chipani chidaipa kale ichi
inuso a 24 ndinu zisilu kwambili kubakila DPP
Mukamutaile uko ameneyo
Akamlepi sewelo ili simunajambule bwino
Akupanga sewero ameneyo! omangidwa amaoneka opanda po2pa palipoxe chidzete chimenecho
U mst be vry stpd boi
Goat
Iwexo chindele chisubweni pamtumbo pako panyini pamako chitsiru iwe eti? kukula mopusa kapena kusayenda? u must stop proveco me i can do anything 2 u foolish!!
cilungamo umacidziwa wekha
watopamo mtchire waona kuti palibe uyo akumutsata mtchiremo komanso after kunva kuti anzake ayamba kulandila ma alawamce ku parliament ndiy wangoti ndinjateni ndikachotse manyanzi kunjako
Stupid dpp kuvutisa munthu chonch zopusa kwambiri sheet,
Am with you
Muzati akufuna kuipitsa mbiri munthu akufa uku. ……..ndani angaipitse mbiri ya DPP popeza mbiri yawo inaipa kale kale ndi chipani chokupha aliyense amadziwa. …….mwawamanga ndi zingwe za blue basi ife taona kkkkkk
Somehow chinachake chachitika kwamkuluyu kuti anthu ife tione ngati azipanga yekha soon after apolisi atanena kuti sangamusake basi iye kupezeka mmmmm
Yah these people r killers and if w Malawians will keep silent and watch will finish all by this idiot mtchona. ……. koma amumva chwe mwana chwe!!
Fulture Wise Ndikugwilizana Nanu Coz DPP Yomwe Ilipoyi Si Yomwe Idalipo Kale Lija Mbiri Yao Idaipa Awa Ndipo Akupanga Mwakufuna Kwao Posawelengela Za Ufulu, Kod Munthu Wamkulu Ngat Ameneo Angapange Zinthu Zot Aipitse Chipan? Kod Jessy Kabwila Sadasakidwe Atabisala Kufuna Kuchitidwa Chipongwe Ndi Akanganya Omweo A DPP Kuno Ku 36? Kuotcha Galimoto Yake Ku Golf Club? Ndie Tidziti Naenso Amafuna Kuipitsa Chipan? Akadafanso Bwez Akut Wapanganso Dala ? Malawi Wafika Pa Chilombo Safuna Oposition
Ndamva zoti ma cadets amenya apolice…..nde amalawi umboni wake ukhale waukulu bwanji kut amvetsese kut DPP ndi yokupha? ??? Still in remembering Chasowa and Njaunju DPP the killers
Otherwise they just inject him so that he can die slowly. Mark my word guys,
Let us hope tht will hear more from him kut oipayo ayaluke……AGALATIYA !!
Pali Mfundo Apa Bwanji Thats True Guys Ur Write Kukamenya Wapolice Iwowo Aposa Apolice? Shame On DPP
Devils in DPP
Munthu sangakabe kwa a neba mkusiyako Malaya ake odziwika bwino ikanakhala DPP akanawamanga ndi mawaya kapena mtundu wins wake osati blue amalawi mmaso mudzayela liti?
Bodza inu nzeru zanuzi izi nde za akafula iwe u dnt knw kut akupangila dala cholinga ife tisakhulupilire zimenezi? DPP cadets yamenya apolice two days ago this is another witness kut chipan chimenechi mchakhaza kmanso chokupha…….mukawauze aputa nkhondo yomwe saimaliza Kamlepo iiiiiiiih ndi chwee mwana chwee
UDF was doing the same things so stop fingering DPP
Apolice kadye makani ndi matama awachita bwino
UDF was doin the same sitikukana bt w r moving forward life ikusintha mwene
Chweee mwana chweeee
Following. ..
wonders shall never end
Kamlepo ndi wa drama kwambiri.. kkk
Wa drama. .munthu aliko ajikaka yekha ha ntchewe iwe …
Mwatondeka waka mwakumana nasimbi zamoto
Mwati??
kkkkkkk kamulepo.com
Ndale za pa flames zimenezo
Uchindele yayi………munthu wangapanga ivo Stupid…
Uneneska vindere va dpp
Nanga iwe admin as a journalist ukuti bwanji?