Mbava zithyola Polisi

Mbava zathyola ndi kuba pa polisi yaying’ono ya Chimbiya m’boma la Dedza.

Nkhaniyi ikuti mbavazi zinakaba pa polisiyi nthawi yomwe wapolisi amagwila ntchito yoyang’anila anapita kukakhala nawo pamalo ochitila chipikisheni.

Mbavazi zomwe sizikuziwika zinakwanisa kuba mifuti iwiri ndi zipolopolo zake mu chipinda chosungila katundu.
Katundu yemwe anabedwa ndi monga zidindo, galasi la sola, mpando wa mu ofesi, ndi makina opanila mapepala.

Pakali pano apolisi sanamange munthu aliyese kutsatila kuchitika kwa nkhaniyi.

Iwo ati akufufuza kuti apeze uyo yemwe waba kupolisiyi.

Advertisement

262 Comments

 1. chiyambi ndichomwe chikuvuta cox pano marecruit omwe akutengedwa kupita kutraining ndi anthu osow zochita kungopangiridwa zochita not ntchitoyo kuifuna,kumangolemba pamtundu pawo basi kumasiya anthu ophunzira ndiosaukira ntchito, maresuits ake ndamenewo kuseweretsa nchito

 2. Mbala masiku ano zinalusa,just last month robers break in the simons town balacks in cape town south africa and got away with fire arms and they are still @ large.

 3. Shame devils, it’s a mission among the thieves and police officers, send a thieve to catch the thieves so why you didn’t to catch them, am feeling sorry my nation

 4. ifeyo tikungothokoza boma chifukwa cha chitetezo chokwanila chomwe chili mu dziko muno tithokoze DPP chifukwa cha upangili umenewu zomwe mwachitila anzathu pa police ya chimbiya mukachitileso ena…zikomo

 5. apolice anapita kokanyera kukonda manyi kusiya nchito pamatako pao ndithu tsono police ndani pamenepo si bola alembedwe okubao

 6. Kkkk …police yaingono ? Police ndi. Pa police bc, nanga ine anditeteze ndani ngati athyola malo oti Kuli Mfuti … Shame ku Malawi

 7. Police Siizatheka,last Month Anagwra Munthu Atalezera Ndkumusegulira Mlandu At
  #Drink&#Capable lamulo lomwe lalowa mmalo mwa vakabu,mukumagwira munthu oti alipa ulendo wake pomwe awa akuba mukuwaonawa mukukanika kuwamanga,mmm?that is injustice,ndye mungayanganire moyo wawina mukukanika kutetezera wanu?kkk malawi acountry of drama

 8. Congratulations Guyz! Ndakusiliran Kwambiri,,, Nxt Week Mukabe Mifuti Kamuzu Baracks Then Mifutiwo Mokagwiritsire Ntchito Pokabela Kunyumba Ya Pitala Zikatelo Timati Chitetezo Nchamphamvu Mmalawi Muno!

 9. Zikuonekelatu kuti Anthu aku Chimbiyao anazolowela kukhala opanda police.Amadyelela nde kuti ndi kagulu kena komwe kamaweluza milandu ndikukhazikitsa bata pa Chimbiya.Nanga Kubwera kwa Police anthu amenewa angakondwe?

 10. If public security institution is failing to proctect itself what more with an ordinary citizen.Should we question the integrity of some police officers?This is not so strange as it is common in other parts of the world especially in South Africa.Govt needs to arm police officers with firearms instead of only handicuffs and battle sticks for beating citizens during vagabond at night.

 11. Pathetic,kumati muli chitetezo muziko muno lust time galimoto inaathera fuel lero ndi izi.Where are we going Malawians?

 12. Akutitu wapolisi amene amayang’anira pa siteshoniyo anachoka kukacheza ndi anzizake pa rodi buloko yomwe ili pafupi ndi siteshoniyo. Pajatu mukudziwa kuti pa rodi buloko ndi godi wazathuwa. Nanga iye akanaweruka m’mamawa alibe kalikonse.

 13. izi ndiye ndi mbili .kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk THE CRIMINALS WENT TO STOLE TO POLICE. NO FEAR THAT THIS BUILDING THE BUILD TO KEEP PEOPLE LIKE US KKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKK ZAFIKA POSAUZANA.

 14. Koma zoterezi zimakhala zoopsa chifukwa kumeneko abako zida. Zida zimenezo zikagwirisidwa ntchito kwina choncho mbamva zoterezi zikagwidwa sizilandilaso chilango choenera

 15. Mbiri yomyetsachisoni apolice kubakumenemumatibelakujammitsewu mwalowelelanso kuntchito kwanu fisi atasowanyama anamudyamkaziwake kkkkkkkk

 16. Ife tikabeledwa timakachita report ku police tsono apapa abeledwa ndi apolice omweo ndyeno funso mkumati akachita report kuti?

 17. I wonder the habit of these Police men amathamangira pa msewu mounting Roadblocks kumatilanda ndalama up to the extent of forgetting their eligible office.Enanunso tengelamponi lesson osamangothamangira pa msewu ndi ma Roadblock with ur mwatenga chani chorus.

 18. Kkkkk apolice tsopano mwadziwa kut khobwe si nyemba zimangofanana msuzi,ndiye mukamang’ala kwandan?.ndpofunika zikabeso ku area 30 kut mudziwe zot chitetezo chilipa 0

 19. Kkkkkkkkkkk a police mukumagwira munthu a kuchokera ku ntchito wangoweluka mochedwelapo basi muli naye Vakabu hahahaha
  .
  Amuna anzanu awotu akuyeresani mmaso kkkkkkkkkkkkkk

 20. Kutheka kuti mu ofesi mo munabwera katundu ofunika wandalama or ndalama zimene nde akulu akulu agawana iyi ndi ndi deal ndithu!!
  Inu munthu angalibe mtima kuthyola police ndikuba sure?

  1. kkkkk kunotu Fikile Mbalula akuti The majorities of these criminals are “Self exile soldiers from Zimbabwe”, Sono pa mpanjepa ndima zim zim ana a panchenga omwewa kapena tinene kuti Umbava wa ngovuta? kkkkkkkkk

  1. Komaso a#mainje mukudziwapo kanthu. Mwakwiya bwanji? Ngati mkuruyi akunama tonse timadalira apolice. Apa zaonetsa palibe chitetezo.

  2. Akulu akulu sibwino kuti munthu akangoyika comment mumutukwane. Ngati ndichizolowezi chimenechi musiyiletu chifukwa ngati munthu waponya nkhani, tiyenera kupereka maganizo athu pa nkhani yaponyedwayo osati kutukwana. Ambuye ndiwabwino chifukwa anatikomera mtima kuti tidzisonkhana pano, pamene wina wavutika timuthandize osati kumunyoza.

 21. a police alikuti nthawi imeneyo?achita bwino to show them that they are nothing!!eating our money but still we leave in danger!!

Comments are closed.