Mayi Hellen Singh amwalira

423

Mmodzi mwa yemwe adapikisana nawo pa mpando wa utsogoleri m’dziko la Malawi pa zisankho za m’chaka cha 2014 mayi busa Hellen Singh amwalira usiku wa loweluka.

Hellen Singh

Hellen Singh atisiya.

Mayi Singh omwe anali mtsogoleri wa chipani cha United Independence Party (UIP) amwalira ku chipatala cha Adventist ku Blantyre atadwala kwa nthawi yayitali malingana ndi maripoti omwe Malawi24 yapeza.

Iwo adali m’modzi mwa azimayi awiri mwa atsogoleri onse khumi ndi awiri omwe adapikisana nawo mu chisankho cha patatu choyamba patadutsa nthawi yayitali mchaka cha 2014.

Mayi wa adalinso mwini wa kampani yobwerekesa magalimoto ya SS.

Zambiri tikupatsirani mu maripoti athu osatila.

Share.

423 Comments

 1. Yeah it is Asian culture manily the hindus amaotcha then they use to get 7 kgs ya phulusa amakalisunga mafupa osalira amataya mu nsinje wa gojezi ndi chikhulupilo chao komanso kuteteza malo oikana

 2. Yeah it is Asian culture manily the hindus amaotcha then they use to get 7 kgs ya phulusa amakalisunga mafupa osalira amataya mu nsinje wa gojezi ndi chikhulupilo chao komanso kuteteza malo oikana

 3. Hei Abubakar shekau,don’t mind people’s language,we speak to communicate,if someone respond in Chichewa it doesn’t matter, neither in English it doesn’t, you can even write in your own native language as well,

 4. Hei Abubakar shekau,don’t mind people’s language,we speak to communicate,if someone respond in Chichewa it doesn’t matter, neither in English it doesn’t, you can even write in your own native language as well,

 5. imfa zimenezi bwanji zikutenga anthu anzeru woti kuwapatsa mpata wo lamulira akhoza kubweetsa dev mudziko muno nkumasiya zitsiru koma imfa iwe ndiwe odabwitsa umalanda pamene anthu akudalira aaaaa RIP

 6. imfa zimenezi bwanji zikutenga anthu anzeru woti kuwapatsa mpata wo lamulira akhoza kubweetsa dev mudziko muno nkumasiya zitsiru koma imfa iwe ndiwe odabwitsa umalanda pamene anthu akudalira aaaaa RIP

 7. iyayi tingoti pepani chifukwa pamenepa panalibeso kuthawa kwina kulikonse ayi apa ndiye ndipamayambi okauona moyo watsopano ngat muntima mwawo munali mzimu oyera. apa sikuti palakwika ayi ndikaona m’bale winaso pomwepa walankhula mwa umulungu walankhula kuti apa ndipamene zolengedwa zamulungu zimutsate polumikiza lamulo lam’baibulo ndiye chisakhale chizolowezi ayi koma tiyeni tiganizile kut tsiku ngati limenelo litakhala kuti ndilanu kapena ndilanga ngat ndisanakonze kodi pamenepa zizakhala bwanji patsikulo eeee apatu ndipaja akulu akulu anati kut ali ndimwana agwilitse.

 8. iyayi tingoti pepani chifukwa pamenepa panalibeso kuthawa kwina kulikonse ayi apa ndiye ndipamayambi okauona moyo watsopano ngat muntima mwawo munali mzimu oyera. apa sikuti palakwika ayi ndikaona m’bale winaso pomwepa walankhula mwa umulungu walankhula kuti apa ndipamene zolengedwa zamulungu zimutsate polumikiza lamulo lam’baibulo ndiye chisakhale chizolowezi ayi koma tiyeni tiganizile kut tsiku ngati limenelo litakhala kuti ndilanu kapena ndilanga ngat ndisanakonze kodi pamenepa zizakhala bwanji patsikulo eeee apatu ndipaja akulu akulu anati kut ali ndimwana agwilitse.

 9. Boat tragey,Rabson chirwa,tony chitsulo,Dj mkhombezi 2day our mother hellen 4 a week!! Malawi we need special day for pray!! Tikanena chitukuko tili pasi , njala ndiyosayamba!! Ndalama zikusowa.

 10. Boat tragey,Rabson chirwa,tony chitsulo,Dj mkhombezi 2day our mother hellen 4 a week!! Malawi we need special day for pray!! Tikanena chitukuko tili pasi , njala ndiyosayamba!! Ndalama zikusowa.

 11. What a sorrowful month is this ? indeed let His words be fulfilled in the book of Genesis “you shall die” indeed today death is claiming our lives today But let no one mourn as those left without expectations that they will die koma David akuti Mulungu munapatsa ‘Mulungu mwalanda lidalitsike dzina lanu R.I.P :T.CHITSURO ;DJ K .NKOMBEZI & PASTOR SIGNH

 12. What a sorrowful month is this ? indeed let His words be fulfilled in the book of Genesis “you shall die” indeed today death is claiming our lives today But let no one mourn as those left without expectations that they will die koma David akuti Mulungu munapatsa ‘Mulungu mwalanda lidalitsike dzina lanu R.I.P :T.CHITSURO ;DJ K .NKOMBEZI & PASTOR SIGNH

 13. Mama u had a vision of changing our country from how it is today to a better level but because the whole system is under the devil,deceiver the cheater it couldn’t work as u planed! Any way,but now u have gone! We just say Rest in pease! We will continue the struggle from where u stoped!

 14. Mama u had a vision of changing our country from how it is today to a better level but because the whole system is under the devil,deceiver the cheater it couldn’t work as u planed! Any way,but now u have gone! We just say Rest in pease! We will continue the struggle from where u stoped!

  • Death isn’t new, Bro. It would have been fine if you cameup with something different which would be new.

  • Death isn’t new, Bro. It would have been fine if you cameup with something different which would be new.

 15. Hellen singh, was a sound brain, Why God is taking good people,leaving Thieves who steal Tax money.Lets hear one big political Thief is gone to Hell tomorrow.

  • Mulungu sindikukhulupilira kuti angamve pemphero lotere chifukwa kunakakhala kotero sibwenzi atapeleka chikondi chake chonse(Jesus Christ) bwenzinso aja anampachikawa atawamwaliritsa nthawi yomweyija, bwenzinso inu ndine titamwalira kalekale coz tiri gulu la afalisi koma chifukwa chotsagwidwa lero tiri busy playing more Catholic than the Pope himself. Nyengo ngati izi tiyeni tiphunzire kupemphelerana wina ndi mzake..

 16. Hellen singh, was a sound brain, Why God is taking good people,leaving Thieves who steal Tax money.Lets hear one big political Thief is gone to Hell tomorrow.

  • Mulungu sindikukhulupilira kuti angamve pemphero lotere chifukwa kunakakhala kotero sibwenzi atapeleka chikondi chake chonse(Jesus Christ) bwenzinso aja anampachikawa atawamwaliritsa nthawi yomweyija, bwenzinso inu ndine titamwalira kalekale coz tiri gulu la afalisi koma chifukwa chotsagwidwa lero tiri busy playing more Catholic than the Pope himself. Nyengo ngati izi tiyeni tiphunzire kupemphelerana wina ndi mzake..

 17. palibe wamzeru ndi imfa, komanso ndinjira yokhayo yomwe Mulungu adayikonza kuti zolengedwa Zake zibwerere kwa Iye mwini,kotero kuti tonse tidzamfa ndithu,ngati silero mwina mawa,#mzimuwawouwusemumtendere.

 18. palibe wamzeru ndi imfa, komanso ndinjira yokhayo yomwe Mulungu adayikonza kuti zolengedwa Zake zibwerere kwa Iye mwini,kotero kuti tonse tidzamfa ndithu,ngati silero mwina mawa,#mzimuwawouwusemumtendere.

 19. What is happening in Malawi , Two days ago was Tonny Chitsulo, yestrday was DJ Nkombe, Today Mayi Hellen Signh I don’t know what tomorrow brings… Lord have Mercey

 20. What is happening in Malawi , Two days ago was Tonny Chitsulo, yestrday was DJ Nkombe, Today Mayi Hellen Signh I don’t know what tomorrow brings… Lord have Mercey

  • KKKKKK ABRAZ MUKADAFUNSA KUTI MAU WA AMATANTHAUZA CHANI KOMANSO AMANENEDWA NTHAWI YANJI KUTI MUNVE NAWO 1.mau Wa timatanthauxa KUTI ndithudi kwamulungu nkomwe tidachokera kwaiyenso nkomwe tidzabwelere tsono ngati adali mbusa adachokera kuti? Mau Wa timanena mu nthawi yomwe tamva uthenga wachisoni ngati uwu ndipo timaunena kwayense yemwe wamwalira regardless of his/her denomination plus apa mmene ndimalemba izi nkuti ndimadziwa kuti iyeyu adali mbusa Wa fellowship

  • KKKKKK ABRAZ MUKADAFUNSA KUTI MAU WA AMATANTHAUZA CHANI KOMANSO AMANENEDWA NTHAWI YANJI KUTI MUNVE NAWO 1.mau Wa timatanthauxa KUTI ndithudi kwamulungu nkomwe tidachokera kwaiyenso nkomwe tidzabwelere tsono ngati adali mbusa adachokera kuti? Mau Wa timanena mu nthawi yomwe tamva uthenga wachisoni ngati uwu ndipo timaunena kwayense yemwe wamwalira regardless of his/her denomination plus apa mmene ndimalemba izi nkuti ndimadziwa kuti iyeyu adali mbusa Wa fellowship

%d bloggers like this: