Saliokha a Peter.
Patangidutsa tsiku mtsogoleri wa dziko lino ataopseza kuti boma lake linjata anthu onse osamalika pa Facebook, naye sipikala wa nyumba ya malamulo walangiza a Malawi kuti pa Facebook sipotukwanila.
Malingana ndi a Richard Msowoya amene ndi sipikala wa nyumba ya malamulo komanso wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani chotsutsa cha Kongeresi, pa Facebook simalo onyozelapo atsogoleri.
“Ndikulangizeni achinyamata, muleke kunyoza atsogoleri anu pa Facebook,” anatelo a Msowoya polankhula kwa ana amene asonkhana mu mzinda wa Lilongwe ku mkumano wa aphungu a ana.
“Achinyamata ambiri mukutha nthawi kukhala pa Facebook ndi kumatukwana atsogoleri anu, kodi zimenezo zipindula chani?” anafunsa a Msowoya.
Iwo anamema achinyamata kuti akuyenela kutengapo gawo potukula dziko lino.
“Palibe zomati ine ndachepa, aliyense akuyenela kutengapo gawo popititsa dziko lino patsogolo,” anatelo a Msowoya.
ukamalimbana ndi ana amatha kukuvula buluku kapenanso kukugwira za mkabudula. chachikulu apa abwana musamatikwapule ndi ulova komanso umphawi mukapanda kusiya makani ndiye eeeh maphuzo ake akhala a gold

Panyapake pitala ndi dpp
Panyapake pitala ndi dpp
Fuck the border
Fuck the border
Sibwinodi , kumakhala kuyaluka komanso kudziyalunsa thats true

Poti sitimathaaaa kutukwanako
Tinskayeseraaaa tione kuti mupanga bwanji

BREAKING NEWS
Muwawuze asiye Katangale kaye
BREAKING NEWS
Muwawuze asiye Katangale kaye
We will not follow idiot president him out country out freedom not for him and internet is for petter

Asiye kusuka mkamwa? Poti apeka ndiwowo
Asiye kusuka mkamwa? Poti apeka ndiwowo
Kusuta et
Kusuta et
Mwayambano kutipheranso ka ufulu kochepa komwe kaja?

Aaaa musamatiopseze mukufuna tizikusekeleran ngati mwakanika mungovomeleza bwa? Ngati mukukanika kumanga ndende ndiye mukatisunga kuti bwana?

Kutukwanizana sibwino tiyeni tikonze polakwikapo pokambi rana tilikonde dziko lathu inde atsogoleri ena sail choncho koma be zimatha pokambirana

Zoona!! You can’t be popular bcoz of disgrace your country on internet that’s very shame.

Zopusa eti? ?
Zopusa eti? ?
Zachamba kukamwa konunkhako
Zachamba kukamwa konunkhako
Asaiwale kuti kuli ufulu wakulankhula.
Asaiwale kuti kuli ufulu wakulankhula.
m.fu,,,usless
m.fu,,,usless
Zazii,,,inee nde singasie,,muconstitution mulibe zmenezo,,
timatukwanadi chifukwa chakuti atsogolelinu munatenga mphavu zonse za democracy chifukwa chakuwawidwa timatelo.

Zake
Zake
Koma muzifunse inu mukuti atsogolerinu kuti nchifukwa chani akutukwana achinyamatawa,mukapeza chifukwa solve de problem munthu satukwana pa zabwino

Pamnyero pake iyeyo
Pamnyero pake iyeyo
Flames mmawa kuponda chikopa khalan busy ku ndi maprogram opanda phinduo president in: Mukuyetsa anthu angaope nyasizo!? Mmalo moyendetsa dziko basi kungocha kusambasamba wakuparliament kukakambirana useless story,

Sikutitu ndikutukwana akudananako akuluwo ai koma chilungamo chomwe anthu akulankhula pa fb pano ndipo sitileka ataaa atatani

mwaloleza kulima chamba,mukuona ngat tikasuta chibwele ndi chani??? tazionelen!!!

Otukwana mu English so?
Otukwana mu English so?
ndimulumisa galu akuteroyotu anayambisa fb ndagogo ake amalogera ya free akukana angasiyye kkkkkkkkk

Guys ndikunena poyera kuti president amene akunena chocho ndi obwera awo ku Malawi kuno sikwayo that’s why akutipanga chocho poti kukuuzani kuti muzipita kwanu mumakani muzingofa bass akufuna kuziwa zambiri za komwe anachokera agaluwa inbox me

Angopanga log out basi Athana nazo
Angopanga log out basi Athana nazo
Guyz thats a Gud advice to malawians who claim to be God fearing Nation…..”tileke kutukwana every where”..koma poti wanena Langizoli ndi president…kapena kyt munthu amene Mulinaye Bad mind mdikale…chikuoneka choyipa pa zifukwa zandale……Thats very Bad..zina kumanvako Guyz…
Langizoli ngakhale ku church amanena ndinthu…even our parents..amatilangiza..
anywae apakamwa powola can Argue and continue kutukwana !!!!

Ali kuti pamene timava agulu inu munyumba yamalamulo anthu Ali pa Fb simakape sauzidwa satukwana sanena zoboza ayi kodi thoako lako ndiye watukwana ayi wachita zopusa ndiye alikukuwuza ya very good Malawi

MUSATI KANDE PONYELA PLIZ
MUSATI KANDE PONYELA PLIZ
Ngat president yemeyo akunyoza amalawi ine ndiye ndilekelanji kutukwana amatiyamba dala atisiye ndi umphawi wathu zimatikwanila.
Zoona man
Xured abwana.

Atero ndani ?
Atero ndani ?
kodi iyeyo dzikumuwawa? amaona nati iyeyo akamatitukwana pa radio kumatinena kuti ntchentche amaona ngati amalawi zikuwakomera? ifetu sitilingati akumipando akewo omaombela m’manja zinthu zoipa m’malo momuza munthuyo pamene akulakwisa kuti akhomze.olo polalikila ukazaona anthu ayamba kung’ung’uza timangoleka.

Mukalimbana ndi ndale muzafa ndi mtima .komanso olimbana ndi ndale ndi munthu okutha ma plan komanso………….loading

Ine ndingoti asogoleri notse panyopanuuuuu

Tizasiya mukazasiya Cash gate FUCK U O
Tizasiya mukazasiya Cash gate FUCK U O
Kodi mwayesa kuti ku Police kukhale koopsezera anthu kuti asamalankhule za kukhosi? This is a democratic country everyone has the right kulankhula mmene afunire! The only problem is that munangotipezerera basi a Malawife, but what you have to know is that oweruza adikira oweruza nanunso nthawi yanu ikubwera muzanjatidwa there is nothing last forever muziwe zimenezo ndiponso Oli zanuzo
haaa za kukhosi zizikhala zotukwana??……khan ndiyot tisiye kuyakhula zotukwana…..i think its a gud advice for Malawian sometyms who claim to be God fearing country…….koma poti wayakhula ndi president ka pena munthu oti mumadana naye ndikale..nde mwachitenga ngat ..okhomerera pakut pakamwa panu ndipowora ndikale….anywae…
Kaniso amawelenga zotukwana za pa facebook sitisiya ndipo tipitiliza agalu amenewa akutionjeza

The wrapped message belongs to the one who post this nonsense information. (You are more than stupid)
true bro idiot just same the late #Idi #Amin.
It seems you have miss my point

Musiye kaye kunyozana nokhanokha akuluakulunu (andale) ndinu mukubwelesa chisokonezo ndi kugawikana. andale nonse ndinu zitsiru unless mtasiya ndale zachikalezo

Anem anga Mickey Magalass kkkk tulukaniko uku muchimwako. kkkkkk……

Izi ndiye zausiru foni yogula ndalama zanga wina angandilese kutukwana zopusa eti

Kodi kumunena munthu nzako kt ndi ntchentche sikutukwana?

Ngati akufuna kusiya kuva kutukana angofa mene afera asogoleri ena aja Fuck agalu sitinatibe titukana kumene muonatso pankholopano ,

AKUTUMANI KUTI MUTUKWANE MUNTHU OSALAKWA KODI OTOLANKHANI WAMKABULAWO MUZAFA IMFA YOWAWA KWAMBIRI!!!

Kwa Munthu wa zelu zakhala pa zisilu iye ngati ali ndi page ape Block anthu azichezapo yekaha watikwana

Tsogoleri akakhala galu omutsataso amakhala agalu ndaonera Msowoya

ma yuthi akamashambula muzaziwe kt zinthu siziri boo.kukhomelela kwambiri nkhalambazi.zikufuna zizifewa zokha pomwe ife tikungochoma kukachasu.KODI ZIKUSIYANA PAT KUNDENDE NDI KUNJA KUNO

ndie zachamba zimenezo tizingomuyang anila chaponda akumenya maizegate osamutukwana? ndie asiya kubako

if u cant beat them join them.let th majority rule.

Ukumasowa nkhan ett ndieno osamangokhla bwanj ukasowa cholemba…palow ndkutukwana tym ina yache…

He’s right!!
He’s right!!
nkhaniyi ili mchichewa enanu ndiye mukuthila mang’ombe mchizungu, komaso olembanu ndiye kuti liu loti speaker lilibe chichewa chake

Panyopano asogoleri nose zausiru
Panyopano asogoleri nose zausiru
MAFUMU ASAMANYOZESO OTSUTSA,PAC NDIPO ASAGWIRITSIDWESO PA MBC TV KUNYOZA

Utiyo ameneyo?
Utiyo ameneyo?
Kkkkkkkkkk adayamba ndi iwowo kutukwanitsana mmisonkhano ya kampeni ife tikuchita kutsata

Kunena zoona zake za nkhanizi ndizakuti achina msowoyawo akapita madera ena kukapangitsa misonkhano kumeneko mmalo mokamba mfundo zomanga dziko amayamba kunyoza chipani cholamula zimene achimatafe timazitengera ndikuyambanso kunyoza mopitiriza chimene chili chithu cholakwika kwambiri

Iweyo ndi osogoleli akowo Mache……………. anu panya panu bava

Nde iwo akufuna azititukwana pa wailes poti ndiyomwe akugwilisa ntchito potukwanisana? Akunama. Ife zinthu tikuzimvera mafb chfkwa pawailes amakondera iwowo.

kachikena wanyera son nyammau ndawatukananso abwere azandimange agalu amenewa akongoonga chuma chaboma ndie zikutipweteka tisatukane

Manyi nde ndiomwewo mukupangawo tizasiya akatilanda fon

kkkkkkkkkkkkkkkk ayambe mcp kuiletsa ugogodi kenaka anyamata awo pano pa fb asiye mwano.

Ine ndimamuona ngati ndiwanzelu munthu ameneyu, zinazi kumangomvetsela koma mukayamba kutengapo mbali nanunso mungotukwanidwapo

ndani opanda khalidwe akuteloyo
ndani opanda khalidwe akuteloyo
WHEN A BABY IS CRYING: Thats a good advice ngakhale sindikudziwa ngati pali mnyamata kapena anyama amene amatukwana azitsogoleri pamenepapa.Anyamata amangopanga react/coment pa ma posts malingana ndiuthenga wumene wabwela.Komanso ngati alipodi ena ake amene akumawatukwana, iwowo azitsogoleriwo asathamangire kuwaopseza kapena kuwanjata anyamatawo koma adzikhala ndichidwi choti amve dzifukwa zimene akutukwanidwira chifukwa some criticisims carries positive messages.Parents are there to guid children but there are other times when parents can also learn something from children.No body knows everything in this world unless if he/she was born in Heaven.So on this earth, everybody can learn a thing or two from onother person regardless of age or academic differences.So those parents should not rush into shutting up the mouths of the youth but rather, they should try to hear what message is in their noise/cries because when a baby is crying,there’s always something that it wants to be adressed by his/her mother.

Ayamba liti kugwira ntchito ku facebook akutelowo? Misala eti?

pamsana pako ibu wava
pamsana pako ibu wava
akamalamulila ngat mwana atukwanidwa
akamalamulila ngat mwana atukwanidwa
Sitizasiya chifukwa mulibe phindu atsogoleli,timangotaya nthawi yokuvoterani

Mulibe zochita et…mwasowa nkhani zoyika et..moti muzipanga zotukula dziko apa

tikanena kuti ndende ndi za a mphawi chifukwa choti Chaponda sakumangidwa ndiye tatuķwana?

Zaziiii. Ayendese bwino dziko satukwanidwa koma ngati akupanga zopusa aziona

Zamanyi bs
Zamanyi bs
Koma Pitala Amineyu Wacitikamwai Poti Ndimapephera Ndiyendingoti PACAKUTIPAKE!!!

mukutiyamba tikatukwana muzit zalowa ndale.

Kkkkkkkkk
Kkkkkkkkk
kodi ali ndi poem yoti “DZIKO LILI M’MANJA MWA AGALU ” by Robert Chiwamba ndindani ??? share ku inbox

Ndani
Ndani
pakakhala palibe zolemba osamayamba dala anthu, musamale amwene mudzafera kutulo, mwanva?

Kutukwana?
Kutukwana?
ineyo ndikukaikira ngati ndingakwanise tsiku ndikutha osatukwanako Boma nde kaya tiziona

Kod ndani akuteloyo
Admin Atiuze bwino bwino amene akuteloyo
Kkkk atiuze basi
Akut pitala muthalika kkkkkk!!
Ndulephela kulithula dzinalo lundilela kamwa

Iweso ukuti sipikalawe chimutu kukula ngat nyumba yopanda plan

apa nde wandiyamba dala Galu iwe olakwa ndiamene anakuika pa pando kachikenanso pa amako

sikutukwana kma kuselewulana pachimalawi, anthu asatsuke mkamwa? akunyadila chinyanja alekeni

Panyopache ameneyoo
Panyopache ameneyoo
uyanya
uyanya
Kkkkkkkk apa tingoyamba kumene
Kkkkkkkk apa tingoyamba kumene
Zivutirapo kutero.
Zivutirapo kutero.
akutukwana ndan apa mesa ndizomwe akuchta amalaw atopa

tisiya koma kulalata ndikunyoza sitisiya coz sizinalesedwepo apa.

MWAWUZESO PANYELO PAWO AKULANKHULA ZOPUSAZO AKULEPHELA KUPANGA NJILA ZOBWELESELA CHUMA KUMALAWIKO AZILIMBANA NDI FB PALI MZELU ?ANDIPEZE KU greytown south Africa pa min cash tyres 91 Durban strt

Sizikugwilizana musakhangati alipo munthu amene anasegula face book Malawi muno…..nd pamakhala anthu amayiko osiysnasiyana and apa its jct a social net yochezela nd hu r u to stop it …..ngati zikumaku bhowani musamawelenge……..And go to hell……hu the hell r u….

Kodi anthuwo asachape mkamwa,Hiyaa
Kodi anthuwo asachape mkamwa,Hiyaa
Asiye kutuma mafumu muma tv athu
Asiye kutuma mafumu muma tv athu
Aktelo ndan??
Aktelo ndan??
Apenga.. If people were talking good things about Dem. Sakanayankhula zimenezi. Komabe tisiya.

akutuma?
akutuma?
Iyenso asiye kutukwana pa radio including pa Tv!

Wanena ndi ndani?
Wanena ndi ndani?
Watukwanidwa akakambe ku Police wayandikana nayo, Pomwe amaloleza Facebook ku Malawi sanaziwe kuti kuli Anthu wosiyana zochita