Ngakhale bungwe loyeza zakudya m’dziko muno la Malawi Bureau of Standards (MBS) lidaletsa mowa wa mmabotolo a plastic, mowawu ukupezekabe pa msika mma boma ambiri mdziko muno.
Diso lakuthwa la Malawi24 lapeza kuti mowawu omwe ukukhalabe mu mabotolo a plastic ukugulitsidwa m’misika ngakhale MBS idaletsa zomwe zasonyeza kuti ogulitsa sakufuna kumvera zomwe MBS ikufuna.
Ngakhale kupakila mowa mu ma pakete komanso m’mabotolo a plastic kuli koletsedwa M’malawi muno Malawi24 yapeza kut ku Lilongwe madera ena monga area 36, 23, Mtandile ndi Mitundu mowawu ukupezekabe pa Nsika.
Mu mzinda wa zamalonda mdziko muno wa Blantyre, Midoli, win, Shooter ndi mowa wina ukupezekabe mu ma dera ena monga Mbayani, Manje, Bangwe ndi ma dera ochuluka ena mu Mzindawu.
Malingana ndi Chigamulo kuchokera ku bwalo la milandu Mdziko muno pa 4 January lidaikira kumbuyo MBS kuti kupanga ndi kulongedza ndi kugulitsa mowa mma sacheti ndi m’mabotolo a plastic mkoletsedwaa.
Mchaka cha 2010 kuletsa mowa wa mtunduwu kudaomba m’golo pamene ma kampane opanga ndi kupakila mowawu adakatenga chiletso ku bwalo la milandu kutsutsana ndi kukanizidwa kupanga mowawu.
M’malingana ndi MBS, iwo anenetsa kuti ulendo uno palibe kampani yomwe ichite matukutuku kupangabe mowawu ndi kulongedza m’mabotolo a plastic.
“MBS ikudziwitsa anthu ndi ma kampani onse opanga mowa wa ma spirits kuti ulendo uno akwanilitsa kuletsa mowawu (MBS therefore wushes to inform the general public and manufacturees of the spiritious liquor that it will implement the ban following the rulling the general public and all manufacturers are heteby advised to comply with the MBS Act Cap 51:02 as stipulated in MS 210 (1990)”. idatero MBS mchikalat chawo.
kodi mukudana ndi mabotolo a plastic kapena mowa??? kapena inu a MBS mwangotumidwa ndima company ena amene akupanga moyo koma pano mwina sizikuyenda kamba kakubwera ka mowayu kkkkk
Koma kumeneko kkkkkkkk SUPER MIDOLI
Midoli ndi 1
Supper midoli ndi deal timwe zimenezi.
Sakuletsa, akugolakhula KT tiwave
Makani akuti akuchita kunenesa kuti sangasiye kugukisa iwo zausilu amakana
Kodi akasiya Muwapatsa tchito ndikunena ndiiwe wa police galu wa munthu wa kutumayo ndani kapena iweyo pita mbuzi yamunthu anthuwo akadyaa Kunyumba kwanu zitsiru inu galu nonse mukulephera ku Manga akuba ndalama za boma
malawi news
Lekan utiphee, supa midoli ndi nyatwa palibexo drink ngat iyi ndie mukut chan????
Midoli Imwedwe Basi! MBS Kwanu Konko!!
Midoli Imwedwe Basi! MBS Kwanu Konko!!
MIDOLi yomweyo kuti wawawa
Ndipo nde ndausosola mu Limbe, midori aaah my favourite K600.00 ndayakilatu
#timamwela Xiwalo Xathu,money Yathu Nd Tikafa Tifa Tokha.Inu Mugopanga Xanu#team_midoli_
Super midoli its a best beer in malawi,what is M. B.S.?asiyeni anthu azimwa wotchipawu mukufuna muwabele alimi asoya,ndi fodya powagulitsa mowa wodulawo? mapazi anu.
mbs siimakhala serious. mowawu ukupangidwa panjewa pompaapa, chodabwitsa mowawu umaphikidwa usku okhaokha.
Someone send me that midoli iwanna feel it am here ghana idon’t it
Kkkk i see u
Kkkkkk
Kkkk im vomiting because this #fucken beer kkkkk
Kkkkkk ithink ma hangover angokupweteka
kkkkk koma anem musandionjezetu ine ndiwa black label Mickey Magalass
Eyetu kkkk anem
Kkkkkk inu koma castlelite size yapajonz
kkkkk Ayi #castlelite kulakasa pakhosi koma #black-label kkkkkk
KkKkkkk ndiye bola whiskyy
Muhule ndiye kumachita kuwatamandila kuwapasa makondomu 30000 aliyense pamwezi chifukwa ndi akazi tisiye ni mowawu ndi wamabiggie ngati ife tinalakwa chani kukhala olezera mowa supereka edzi mwamva tumwe tumwe basi
Mpaka tiledzele kkķkjk
chiwengero chikupita patali kwa anthu omwe amwalira chifukwa cha kumwa zachikasuzo
kuyambila muchaka cha 2010 Malawi lakhala dziko limodzi muno mu Africa limene anthu akumwa mowa mwawuchidakwa chifukwa chopezeka mowa wamasachets kapena mutimabotolo tatingonotingono.koma zomvetsa chisoni ndichakuti anthu akumwalira nawo kwambili mowawu ngakhale boma likungopenya pano ndinthawi yoti boma lichitepo kanthu monga anzathu aku zambia ndi Tanzania anachitila.
Ndiotchipa komaso ukupangisa achinyamata ambili kumwalila kulibwino kumwa mowa odula koma kukhala ndi good life ife tikudandaula kwambili ndipo tikulipepha boma chonde chende pelekani lamulo lolimba zisapezekeso muno malawi
Alese uhule kaya then midoli kkkkkkkkkk pepatu
Dan waganizako ngati muthu winaso anene zomwe akuona
Mmm! Adona Midoli Ndi Deal Pano Ndi 47 Percent Alcohol Zinazi Aaa! 3percent Sungapate Shuwa Ka!!
Umwedwe basi mesa ofayo ndi ifeyo! midori the super
Aliyense adzafa ndithu,siyani nansongole ndi tiligu zikulire limodzi.
Nyatwaaa Ndi super Midolii basiiIi kKkkkkkkkkkkkkk fanta fanta
Kodi Akaletsa Midoli Ndie Tidzimwa Chani Calsberg Ndi Odula?
Uzimwa matokoso
frozy anakukanikani nw u av ventured into midori kkkkk kma malawi
Midoli Dry Gin, 3 Time Distilled.
Lamulo lopanda mphamvu. Komaso corruption dziko lino yanyanya, lamulo silingagwire ntchito.
Mbs toothless amwenye abetcha zina ndalama pa msika ubweranso mutsimikiza inu phe!e
After frozzy mwati muletse zakumwa zamafumu chifukwa sanakukhuthuriren chithumba cha ma K2000… Super Midoli for life
Inu mowa ukupha anthu uwu
Wapha angat??
Wapha ndani midoli munthu wabodza iwe. Tisiyeni ife timwe zimenezi.
Kwathu Ku Ntcheu
Anamwa poison amenewo not Super Wolemekezeka midoli
Kkkkkkkkkk komaso anthu akalamba nawo Ali achichepere
Kkkk samadya amenewo,malnutrition
Kkkkk mwaukakamilatu
nonsese remains nonsese even when spocken by famous scientist (john lennox)
Tumwe~tumwe ,,atumamge~atumange.
kaya zao izo
Wh@ is tha so called M B S doing to end this drama ?
Malawi is not serious
aaah! midoli 4lyf!
just find altenative way not kungofikira kulesa. panopa ndikuthirira basi chibag chikuyamwa mthumba
Midoli e ngakhale azibusa akuukonda kamba ka maonekedwe achikoka
Ndipo ukumwedwa heavy
kkkkk #Msambizi za Kachasu yekhayo tikhoza ku matcher ndipo iwoso akudziwaso bwino lomwe eeeeeh.
Proper pupa# zimenezija zokha nde asayelekeze….size imakana!
Kodi komwe amapangako samadziwako a MBSwo?Mesa akanakachita zitsuzo zaozo kumakampaniko?Mulimbana ndi ogulitsa
chibuku chitiphulitsa mimba kkkk
Oky Nawoso Amamwanawo Ndpomvuta Kt Athese Kugulisako
Oky Nawoso Amamwanawo Ndpomvuta Kt Athese Kugulisako
kamidoli kali boo kamaveka katsabola wez kali nyatwa
Bola Win
kikkkk! end of days, mumwa nazo petro izi.
Midoliyo ndiye ndi deal.
not only Midoli but we say Super Midoli
kma boma ilii aaa akulesa mowa wotchipa komanso wamkaka right choice?ine ndaipidwa nazo sopano,ndingozikhweza basi nanga chibuku ndikwanisa mene mukundioneramu
Ngati akufuna asiye awapase ndalama zopangira business ina koma ife tizimwabe zimenezi kkkkkkkk
Mulese Zinazi, Koma Kachasu Yekha Chonde Tisiyileni, Chonde Pa Kachasu Pokhapo Tagwira Mwendowanu
angosiya asaulese basi nanga titani pamenepa?