Dan Lu kills Facebook with images of his wife’s pregnancy

Advertisement
Dan Lufani

Afro singer Dan Lu has surprised his thousands followers on facebook with a picture that exposes his family’s pregnancy.

The sweet banana hitmaker who is on the verge of being a father after successfully tying a note with Emmie Kamkweche last year, could not wait to share the excitement of an impending fatherhood.

Dan Lufani
Dan Lu posts epic image on Facebook.

On Friday he posted an image that displays their pregnancy to the public.

In the image which shows Lufani laying hands on Emmie’s tummy, the wife just can’t help it but respond with a pride-coated smile.

They are going to have a baby, its all that matters for now.

Dressed in matching Jean outfit, one can tell that the couple dances to the same tunes when it comes to matters of love.

Their uniformity is just unbearable. Commenting on the post, thousands of his followers congratulates Lufani as he awaits his child.

Others admire him for the courage of in posting an image of that nature on a public platform. He is the first Malawian entertainer, very confident to proudly post an image exposing pregnancy.

However it is not bizzaire for celebrities to do such a thing.

The Blantyre based singer is now a man with a name in Africa.

His collaborations with Nigerian artists in 2015 made him known to other parts of the continent.

Advertisement

391 Comments

 1. A big respect to those you are defending such shameful act, paja kumalawi muthu otchuka akapanga kanthu kalikonse evn zonyasa ngati izi, zimakhala zolondola,,,

 2. WHY NOT SHOWING US THE WHOLE THROUGH WHICH THAT PREGNANCY WAS TRANSMITTED? THIS IS WHAT WE CALL SOFT PORN.

 3. Palibe cholakwika apa iye wakhala akunenedwa kut sabelekesa ngat wapereka akuyenera kuima pachulu kut anthu aziwe kut zachitika ma haters ake asowe chokamba

 4. He just want to show people the meaning of his song “Sweet Banana”

 5. Amene mukuti palibe vutonu muzinenanso kuti nane ndinachitapo ndipo chithunzi changa ndi ichi. Munthu umanena kuti palibe vuto kudya njoka chonsecho kukuotchela uyitaya sungadye? Kapena mutipase zitsanzo za Malawian celeb omwe amachita izi poti mukuti ndi iye celeb. Aswiswiri samamvana kununkhadi zoona. Zitsiru zimayimbila mmanja zoputsa.

 6. Malawians, we always act holly but we are not holly at all, we fight abortion but we are the ones aborting,the same gay’s but we are the ones doing it,one of my friends from Europe said one time he thought Malawian we don’t do sex the way we present ourself…shit these are not the days you tell kids ana amagula, most of you commenting that Dan lu walakwitsa kuti tikutsateni moyo wanu ehhhh…I see nothing wrong here..

 7. Anthuwa osat muzit ndi achimidzi km ndibodza kuno kumudzi sitimaphuzila zanyasi km izi ndizachitown coz ngakha dresing yao siyachimidzi zamakono alibe umunthu ose awiri

 8. To those who don’t see anything wrong, let me tell you this :this is Africa, we have our own culture, and whites have got their own too, so take care, mubeleka nazo miyala.

 9. Amwene taganiza bwinobwino ngati ndinu munthu olengedwa ndi Mulungu, zinthuzi ndizoyenera kuchitira kuchipinda osati apa!!!!, ayi kuyalusana kumeneku, naweso #mkazi udzikana osangolora zilizose wava

 10. Crackheads are saying that this is cool wat a hell lot of rubbish. Its actually a disgrace. Ur not Malawians and insane. Mukagwere. Showing a woman’s belly like that is shameful. Mwataya chipangano. Dont buy his music in protest.

 11. Inuso mukunena mo mombakira iye mukuona ngati achita zabwino. Paja iyeyo alibe mphatso imeneyo ndimimba yoyamba chifukwa akuvuta kkkkkkk kaya zako izo

 12. Penapake a Malawi pali chodabwitsa APA??I believe that’s their choice so what’s your business?? Malawi 2minutes INA yake imadzabowa bwanji….kenako mudzapanga post munthu akubiba sure…asaaaaaa kweeeeee

 13. So what, uwu ndiye uselebuwo. U do what ppo critises and think its bad (in their own mind and judgement. A celeb always makes a headline whether in good or bad things. Chose your lifestyle, mind your business. Mukanakhala inu mwapanga izi sumukanatchukapo anta, coz u r not celebrities. Dan and Emmie, keep living your lifestyle and let others keep watching and discussing your videos. Give them some 15 minutes ormore to watch u as they cannot make their own for ppo to watch.

 14. Ndiye anthu ena opusa mukuti palibe vuto akutsutsawa ndi chimidzi zimachitika mayiko akunja. Inu ndi ndani? Munapelekapo mimba inu? Ngati munapeleka munamvula mkaziyo mkumuyanikila pagulu? Mukati zikuchitika kunja anthu oti mulibe ndi ma passport omwe munapitako liti kunjako? Munauluka? Mukangowonela firm mwati ndi real life. Opusa amayimbila mmanja wopusa mzawo. Akuluwa zikuchita kuoneka kuti panavuta kuti mimbayi ipezeke, ngati ndi Choncho mwinanso si yawo. Timati linda madzi adutse uziti ndadala. Mimba si mwana, umakondwa atatulukamo wamoyo. Chibwana ichi satana akuwaona azachita manyanzi zinthu zisanathe mmene amayembekezela.

 15. Oyoooooooo zaulendo uno kaya kuli kusova masiku osiriza awa osadabwa tikungodikira chilango apa wina ariyese aziwe zaulendo wake kt wakozeka bwanji

 16. So stupid and madness.He has been attacked by serious demons hence needs strong deriverance from prophet Tb Joshua.What image is he planting on youth?That is total stupitity.Satan messengers.

 17. Inu munamuona mzungu atavula ali oyembekezela?? Kapena akuyamwitsa pansewu???? Izi zizachitauni koma satanic ufiti uwu ndithu sindikukaika God is watching ….choose Jesus as your lord an saviour!!!!!

 18. Amalawi tiyeni titsegule m’maso kuposta pic…. Yamimba sikuti ndiuhule kapena kusasowa chikhalidwe …..ndimene wazimverera mwini ache so dont judge him

 19. If it was kanye west panalibe vuto koma pakuti ndi Dan Lu ndiye zoyankhula bwee pangani zanu gyz life iyi singatithandize and mind u were not in 18th century let them do wat they want

 20. Nkhaniyi mu chichewa ili chonchi……..

  Dan Lu ayanika mimba ya mkazi wake pa m’mbalambanda
  By Mphatso Khutcha Richard January 16, 2017

  Guaranteed to Make You Laugh – 12 Funny Photos

  ?
  Oyimba otchuka mdziko muno ndi nyimbo za chamba cha Afro, wazizwitsa mtundu wa a Malawi pamene wakhala mMalawi mmodzi yemwe waika zithunzi za mimba ya mkazi wake pa Intaneti.Anthu ambiri ati zomwe wachita oyimbayu ndi kunyazitsa chikhalidwe cha amalawi komanso kulaura. Oyimbayu yemwe watchukanso kwambiri ndi nyimbo yake ya “Sweet Banana”, adalimba mtima kuyiwala chikhalidwe cha ulemu cha chimalawi pamene lachisanu adaika dzithunzi dza mkazi wake Emmie Kamkweche koma dzovula mimba yonse ili padagu pa tsamba la macheza lija la facebook.

  Dan Lu wautsa mkangano pa Intaneti.Malingana ndi mwiniwake Dan Lu, yemwe dzina lake lonse ndi Dan Lufani, poti iye adachilimika kuyimitsa Emmie iye wati ali tcheru kudikira kuti akhale bambo a mwana yemwe akumuyembekezerayo, pamene awiriwa akuoneka okondwa zedi ndi kuyimaku. Koma malingana ndi anthu ena amene akhala akuikapo maganizo awo pa tsambali, akuonetsa osakondwa ndi mchitidwe umene oyimbayu wachita poti wayalutsa mkazi wake komanso wanyazitsa chikhalidwe cha ulemu cha chi Malawi. Malingana ndi macheza a pa gulupu ya whatsap yomwe Malawi24 yawona, yomwenso Emmie ndi mmodzi mwa ma membala, zaonetsa kukwiya kwa anthu pamene anafunsa mafunso mzimayiyu chifukwa chimene achitira izi poti pali anthu ambiri otchuka ndi a ndalama zochuluka mdziko muno koma safika mlingo uwu, koma mkazi wa Dan amangoona ma uthenga ndi mafunso koma samayankhapo kanthu. Gulupuyi yomwe ndi ya azimayi okhaokha, afunsa Emmie ngati mimbayi ili yoyamba ndipo kuti ndi ndani uyo adapereka malango kwa awiriwa pa tsiku la ukwati wawo womwe udachitika mchaka cha 2016.“Koma kudziwika kuli apo koma abale ulemu ndi ofunika, ndi ndani adakulangizani koma?”

 21. Nde popeza watsatsa mimba relo kodi atapita padela ena mau amwano amati UPOLOZA.kodi adzatiuza? komaso iyeyo wangolakwa kutsatsa mimba pagulu ngati pano bcoz mimba anthu amavuula amaba kudzela m’matsenga aaaaaa anthu amavuula mimba ndikuikamo chimwala

 22. live the life you deserve. in this modern life tit for tat its just wastage of time. i saw these pictures also by diamond. comments were just bigup, all the best, thats fine…… now its Dan lu, then alibe mwambo, anakwatira hule, sososo….. just for nothing upto media. hahahaha!!!! malawi 2017

 23. Koma abusa anadalitsa ukwatiwu aona izi????? Nkazi wanzeru sangalore izi .kodi mimbayo ndiyoyamba? Kalionera atitengera kudzenje ndithu.akamazachiranso uzajambule vedio tizaonere nao.kufera u celleb ngati celleb oyamba kumalawi ndiweyo bwanji? Guys thandizeni kutola miyala ndigende kkkkkkkk

 24. Ameneyu ndie kuti zimamuvutatu,bola ikhale take.otherwise adzangodabwa mphuno ngati chidzukulu cha mzungu,tsitsi ngati mmwenye wa sitolo iyo…..!!!!!

 25. His family,his pregnancy,his business.Inu mulowa pati kuti muzilowerera za banja mwake??? Sitikudziwa kuti wasala kudya kangati or wamwa zotani kuti apeze mimba imeneyi.let them be.

 26. mimba zake zimenezi mpaka a nkhoswe awona nawo kkkkk chitani manyazi chotsani pic imeneyi.azimanu ali maso psuu kuwona zimenezo ife ndi awulemu guys longosokani.Nonse ndinu zitsiru za ana zochita mwapamba nkhuku imene imabisa mazira ake kuti anthu asawone kufikira kuzaswa ana ake.

 27. Awa ndi ana oti kwambiri za chikhalidwe sazidziwa akufunika aphunzitsidwe ana amenewa ubwino wosunga chikhalidwe ngati a MALAWI makolo awo akamawona choncho aziti chiani? Amenewa ndi Malaulo.

 28. Malawian bwoy on it! Hehehe tikatengela pa culture yathu adhawa alakwitsa heavy…. koma coz of maufulu tilinawowa its okay aliyense atha kupanga zomwe akufuna. Big up mr Lufani u r real man!

 29. Woyimba wozipasa ulemu anali akale osati alero achamba thoo. Pamenepa wapangisa manyazi makolo, abusa ampingo omwe amapembeza ndi azibale ake , ndikukulupilira kuti munthu wabwino bwino wa nzeru zake sangapange zimenezi mwa uyu mwachuka ziwanda kwabasi.

 30. He posted this on his timeline, it was his choice, its your choice as well to visit his timeline,. If you hate whats on his timeline you can block him or stop following him. Mimba tikumaziona ife mtaunimu zikuyenda pamtunda, or even a very revealing dress, is it a problem because its on fb? He has a life to live and enjoy, enjoy yours to the fullest as well.Nanu musiye kuponya tiana tamchikuta apa, ti ma day old if its all about culture. Even azimayi amene mumaflasha , mabere, ntchafu pa fb musiye if its all about malawian culture, lets not be hypocrites..

 31. Sakukhulupilira kut kwasing’anga anapitako zingathekedi. Paja mnzathuyu anali ndivuto loti samamera Fupa mkabudula

 32. Palibe nkhani apa mukakamba zachikhalidwe ndiye chinatayika kalekale popeza kale kunalibe zovala timayenda bwamuswe chimenecho ndiye chikhalidwe chathu chenicheni chamakolo

 33. mwaiwala zanu za usiku zinja mukamba za dan apa naye ndimene wavela mesa nda mkazi wake,mimba ndiyake mwanayoso azakhaka wake ndiye mukungoyakhula zambiri apa,mukamba mutopa zake zukuyenda muchedwa nazo izi poika izi sikuti sananganize ayi kaya tamayakhulani malo molimbika ntchito kkkkkkk hahahahah

 34. Zinazi zimavuta kuyakhula kwake onsewa awa akunena kut palibe cholakwikawa apa kut muwafufuze ambiri mwaiwo ndiokwatira enaso pano azikazi awo ndioyembekezera kma avala mozilemekeza ndithu kunyumbako…anyway tisaweruze akudziwa ekha chochita nafe Otilengayo….

  1. Yes coz we have got our own culture ,we are malawians and we are supposed to behave as malawians not this one .As acitizen of Malawi am not happy

  2. Wachita bwino Dan Lu coz amalandila chitozo kwa anthu ambiri kti samabeleka & pano akufuna mtundu wa a Malawi udziwe kti iyeyo ndi Mamuna…which culture??? Monga iweo zomwe umapangazo u follow ur culture??? NONSES

 35. What’s wrong with you Malawians?Why do you always poke your nose into people’s affairs? Mimbayo ndiyanu? kapena ili pamutu panu? Let them live their lives to the maximum, samadya Kwanu. Zomwe mumapanga zija ife timanena kanthu?

  1. I support you bro, i just don know, girls do post semi nude pics here and we comment cute, nice and whatever comments, they walking hal naked mtaunimu timawaona but we always sayiys their own business. In addition if its about culture bwanji tikumaona ma day old pa fb, mwana oti if its culture amayenera kukhala mchikuta, we comment congrants, kodi culture yavuta poti ndi dan Lu? Les go tp work guys ameneyo zake zinayera

 36. Come on we are in 20th century l dnt see any problem wth that,jst get a life!!!!!!!!Unless if he offended Mw 24 wth us de fans we want to see more of this.

  1. To you all who side with this post, do it the same with your wives once they are pregnant! You keep your privacy, but your encouraging this man to post this! Hypocrisy!

 37. or azungu amabisa izi amavara big t.shirt, or long dress labwino lokongora kodi mzungu ndi wakuda akuyenera kubisa ndani kapena kuvura mimba yo chakura apa ndi umburi a dan lu ndlama zabwera mochedwa kwambiri onse wa zikuonetseratu kuti ndi ma empty tins angopeza ndlamazo kuti zatero koma ndi ma cerebrity achimidzi mburi timaona ma celebrity ari ndi mimba ma black americans atavara bwino mobisa mimba koma awa achimidzi mmm ai! azungu amabisa izi for ulemu koma awo ndi umbiri wawo kusadziwa ucerebrity weni weni pano ndi ndizo ukuvarana nazo mimbazo ku shower kwanu amakulamgani ndi mahule anzanu sizachilendo

 38. Kkkkkkkkkkkkkkk…The next thing you will hear is Dan Lu is now a Gospel Singer…and is invited to perform on Bushiri’s platform..kkkkkkkkkkk..

 39. Maybe this comment won’t be important for the majority of people here. Some of you will ignore it, most of you won’t bother to read it, and it will go unnoticed along with other comments, maybe I will be criticized for this, but I just want to let you know that iam selling potatoes at a reasonable price.

 40. Oh!This world’s going where now many questions but no answers. I think Dan luu and his wife next time they will pause in nudist just the way they started.pregnt is something that must be respected and hidden to all parents and relatives according to our culture. So should we say mr Dan lu and his are normally in the sense this act?please respect your privacy and your culture as well as your country.

  1. Mwamuyankha bwino munthuyu akundifunsa kuti which culture but akuti ali mphunzitsi eti. koma akuluwa tingoti zochitika zawo zikufanana ndi akulu awo owonetsa mimba ya akazi awo pamtunda.shame at you.

  2. Just mind ur business tichedwatu iye akupita kkkkkkk culture yanuyo mupite mntown BT muzaone mimba zili mma legens kumalawi kuchitisa manyaz kwake agalu inu

  3. Kuvala mosazilemekeza ndikuvuliratu osavala kathu ndizithu ziwiri zosiyanna mwina chichewa chimakuvutani…Chosangalatsaso ndichakut pamene agalufe tinali busy kukambirana zathu galu wamkuluwe wabwera ndichiwewe chako afta that ife tathawapo watsala wekha ndiugalu wakowo..

  4. Galu ndamene amaganiza moperewera monga ukuganiziramo # .Sam ndipo iwenso ndimmodzi wa mbuzi zinzakozo how can u call ur fell humanbeings agalu I think nanunso achimwene munalowa nawo evil mongokudziwitsani ine so galu watch ur comments mxiew

 41. bt 2say de fact Dan Lu has joined abandon Wagon hw cn pure Malawian post dat pic?……satanic mwafika nayo poyaluka nayo2 apa

  1. Osaombera mmanja zilizonse nanu inu poti ndi celebrity basi,,,, thupi ndikachisi wamlengitu osaiwala nzeru ndi mzimu zizigwira ntchito nthawi zonse!!

  2. Osaombera mmanja zilizonse nanu inu poti ndi celebrity basi,,,, thupi ndikachisi wamlengitu osaiwala nzeru ndi mzimu zizigwira ntchito nthawi zonse!!

  3. Aaaaa..mwinatu mzisatila life yama celeb b4 kuwaloza dzala.Ma celeb salingati munthu wamba ndi anthu apa red carpet, follow Jayz,Beyonce, nick minaj ndi ena ambiri you wil get some life people.

 42. Based on our country culture, pregnancy is something we keep hiden and respected.we only cerebrate when when we have a newborn baby.as for dan lu,he did what he think is the best way to cerebrate bcz we dnt know what he been going through concerning babies.as for you my friend who congraturate and see no wrong with the picture,have you ever done this b4 or you just do this bcz she is someone else’s wife? Watch yr comment

  1. Smepeople jst comment, they dont know wat pregnancy is alabout, they are nt married either. They wil face the reality of it, chachuluka nchibwana pa fb pano. Mind u this is Malawi not USA we are proud ov our culture. Thats why mkazi oyembekezera amaziwika ndi maina ambilimbili. search u wil find, sizinthu zomabweretsa kugulu poyera pambalanganda. Mwina simunamveko zamkazi obereka mwana in MJ, Dowa. Muzaziona

  2. Even myself i was about to put my comment ku page yake but nditaona momwe anthu akumuyamikilira pazomwe wapangazi ndinaona kut kut ambiri akungofuna kuonekapo ngat anzeru pomuyamikira..some thy said..Malawians chimidzi tiyeni tikaone maiko anzathu momwe akupangira mkazi akakhala ndi mimba ndinawanvera chisoni anthu omwe akutengera chikakhalidwe cha Maiko ena..Aliyense payekha ayenera kukhala ndi umunthu kutengera zomwe ena akupanga zimangoonetseratu kut sungathe kuzipangira chiganizo pawekha koma ena akutsogolere..Ambiriwa akumuyamikira coz ndi Selebo koma akanati wapanga izi ndimunthu opanda dzina osatchuka aaaaa kunalitu kumutukwana mpakana kutchura nzankabudula…Sizoona izi..

  3. kodi ngat timafuna kut mimbayo ikhale yathu man aaaaa njee man inu tenganipo point pankhaniyi nde muone chomwe ife tikukamba..its about Ulemu omwe munthuyi amalandira nde izi zadzidzimitsa anthu ambiri…kodi oyimba okwatira ndiyeyu ekha ku Malawi konsekuno ?? nanga enawa bwanji sanapange zimenezi ?

  4. Waonetsa kupusa kwake mkulu ameneyu ndipo anthu amene mukuti enafe chimidzi kuno siku usa ndikumakawi ndipo enanu zowerenga mmabuku kapna usa yo mmunapitako usiku

  5. Satana amakondwera ndizinthu ngati zimenezi, posachedwapa timva kuti wajambula ponography. Ngakhale mutati mufufuze iyeyo mimba yake anaiwona ndi bambo ake ndi adotolo basi

  6. Za satanic sidzipanga manyazi chifukwa zimakhala zopanda nzimu ngakhale atsogoleri adziko sanapangeko izi ndiye tu ationetse m’mene amapangira baluuniyo kkkkkkkkkk paja ankati samatha kukhutitsa nkazi ndie waona ngati nzakutulo nkana wabweletsa nyasidzi apa shame.

  7. It’s too early to be over the moon coz he don’t know what is inside.Mimba ndi mwana choti unyandire ndi chani?Mwana wa abusa watani?

  8. Mmm this is too much pa chikhalidwe chathu timayenela kubisa only mamuna wako yekha ndi yemwe amaiwona.mmm apa ndiye watiyalutsa bwanji.ife ndi azungu ndi awir osiyana.zikubwela mochedwa izi thats why ,koma chonsecho makolo ake ndi abusa koma waganiza bwanji iyeyu?mmmm za manyaz

  9. Kodi ana abusa zomwe amachita ndizoyalukatu komanso chomwe mungadziwe ubusa wamasiku ano ulingati ntchito zina zachisawawazi

  10. Ndeno inu mulindivuto? Someone’s privacy thing is someone’s public, stop being too archaic , muzisintha a Malawi , let Dan lu cerebrate I support you my best musician

  11. akuluakulu tisadane ndimalawi, malawi ndidziko lomwe mumapezeka anthu ndichimodzimodzi mupite dziko lilinse mukapezanso anthu komanso mukapeza kuti kulienanso amene anatengera za anthu ena.ndiye munthu uyu musamudwabwe mutha kumanena kuti umbuli simudziwa chimene wapangira zimenezo adziwa ndimwiniwake koma zomwe tikupangazi tizidziwanso kuti kuli Mulungu

 43. Nkazi wake,mimba anapereka yekha,picture yake, he posted it on his fb acc.inu mukusiya life yanu kulimbana naye Ali ndi vuto ndi ndani pamenepa??simungatukuke chifukwa chilimbana ndi moyo WA anthu ena. Bachedwani nkukamba iye Ali pheee zake zikuyenda inu busy with ur sharp mouths here.Why can’t you waste ur time on something profitable?? Hiyaaaaaa

  1. Ukatchuka kwambiri munthu umapanga zithu momasuka ngakhale chikhale choipa anthu amakuyamikira kut ndichabwino ngakhale pansi pamtima tikudziwa kut ndizolakwika zachitika apazi…anyway kma osamuphatikizapo Mulungu ndizithu ngat izi pliz…

  2. Dan Lu wachita bwino coz wanyozedwa kwa nthawi yaitali kti samabeleka..keep it up Dan Lu yemwe zikumunyasa anyambite ku ujeni..,

 44. Kkk kazi ndi wake mimbayo ndiyawo…kaya afuna akhale maliseche ndi awoo!..kaya athuzulana ndizawo zimenezo…kaya ayifinya mpaka atabereka nzao zimenezo…ife tiyeni tizingo ona ndani saziwa kuti pa FB apaaa! Kkkk

 45. Zautsiru basi celeb celeb wachani! Kuyalukatu uku koma a Dan Lu wa makolo awo alipo. Angasekelere zopusazi azichimwene, nkozi, sister & the like . mwinatu ndi satanic yatchukayi, God forbid it. wazionongera mbili nsakunamize & chiwelengero cha anthu okukonda chichepa. Next time u wil post naked photos of ur so called wife in the name of celebrity. Zautsiru !!!!!!!!!!!;

 46. mmmm ndi mimba yakuti ndikuonetsa pa gulu choncho guys kumakhala ndi wulemu zinazi chauta anazilenga kukhala malo a ulemu not public like that please tikudziwa ndinu wodziwika ku anthu koma zinazi muzipanga za umunthu .

 47. Ngankhale katakhala kamimba koyamba ngati zimakhala choncho! Kusoweka umunthu ndi manyazi. Mwina adachita kukasulitsa kwa sing’anga. That’s moral dilution at it’s peak. Shame.

 48. Hw did they kill facebook??? Wabodza iwe fb ilipo, if the fb is dead then where do think u posted ths to?? Eeee koma chingendechi.

  1. Martin Junior Tamuuzani amwene mnzathuyi… iyeyo ndamene samatha chizungu… In english, kill can be used in many different ways as u have already said as a metaphor

  2. James Brown, u cn follow me where i chat wth frnds, n uzaona kt i like comenting wth njira yanga cholinga macheza azikoma, i do coment in groups n if u c wat ma coments says, u wl feel the same way as u r ryr nw. Jst follow me n u wl c wat m tlkn abwt………..Kodi iwe umaona ngati azamasewero aja monga Isack n Jacob, zonse zomwe amapanga ndizokhazo zomwe adageirizana. Noooo men pena amaonjezerapo kt zikome, so plz dnt bother ur self abwt me, u cn coment wth anything u wanna say, n that wont bother me, and if i like i cn coment on wat u wrote, thats hw we kp being frnds on fb. But any way u know btr thn all fb users…… Thnx Mr J.B

 49. Abusa anamangitsa ukwatiwo,akulu ampingo,azichimwene awo amayiwa apongozi awo kupatikiza dziko lonse tilipano kuonesedwa mimba inkabisidwa ija mdzila la ufulu ndi u celebrity!!

 50. Aaaaa koma ndi za chamba is nkona ena amafika polankhula zoti ndi wa pansi pa nyanja. This is Malawi not America. That is part of private. Ulibe mkhalidwe and mutu mwakomo mwazaza ziwanda. U need deliverance. Very stupid. Ndasiya sindizakukondanso. Ndimayesa ndiwe wa nzeru

  1. Okondedwa a Daniyele Lufaniko, ndati nanenso ndiyamikile anthu onse amene akudzudzulani maka maka pa mchitidwe womwe inu mwachita povundukula malaya a amayi akwanu ndikuwonetsa pathupi Pawo Ku pfuko la dziko lapansi. Izi ndiyesa mwachita poganiza kuti anthu omwe akhala akukukondani kwa nthawi yaitali achita nanu chimwemwe ndikukuyamikilani kuti moyo wanu kuti ndi wa chizungu.
   Komatu pamenepa ambwiye mwalemba mmadzi malinga nkuti tsopano a Malawi ambiri masiku ano adapenya kupatulapo awo amene akukuyamikilani chifukwa nawonso akuti amakonda moyo wa chizungu chikhalilecho akuiwala kuti mtundu uliwonse pa dziko pano uli ndi chikhalidwe chake choncho mulekeni nzungu akhale nzungu chifukwa wakuda ndi wakuda basi ngakhale atayera khungu ngati mwachitila inumu a Daniyele.

   Tikapita Ku ulaya, maka maka Ku England, timawona azungu akuchita zofanana ndi zomwe mwachitazi komano sachita kufika povundukula chovala mpaka anthu kuona mchombo wa mai wa pakati, woiwona mimbai ndi inu eni ake kudzanso anamwino ku chipatala panthawi ya sikelo basi. Umenewutu a Daniyele ndi mwikho( abomination). Musamaiwale kuti kwanu ndi Ku Nyasaland osati Ku Chicago (U.S) ndipo anthu mudziwaonetsa ma vidio a nyimbo za bwino, osati zithunzi za akazi anu. Kumbukilaninso kuti amene akuona zimenezi si ife tokha anthu wamba, komansotu achibale anu maka maka kuchipongozi, choncho matamawo tachepetsani ndinu wankulu.
   Musapangitse anthu kuganiza kuti muli pa ubwenzi ndi Satana yemwe ndi mwini wa mkhalidwe womwe mwachitawu. Pomaliza, chonde musapse mtima, koma mmalo mwake mundikhululukile pokudzudzulani. Mukatero Chauta adzakudalitsani, ndipo mudzakwatulidwa nawo pa nkwatulo uli nkudzawu, amen.

Comments are closed.