Modzi mwa ochemelera a timu ya Nyasa Big Bullets, Beleti Severe yemwe amadziwika bwino ndi dzina loti Billy One wapepesa ku mtundu wa a Malawi pomenya mlembi wamkulu mu unduna wa zantchito, zamasewero komaso zomangamanga a Sam Madula.
Billy One anamangidwa lolemba atakuntha mbama mlembi wa mkulu mu unduna wa zantchito, zamasewero ndi zomangamanga, patangosala phindi zochepa kuti Nyasa Big Bullets ithambitsane ndi Be forward Wanderers mumasewera omwe amalimbirana bus pa Bingu National stadium mu mzinda wa Lilongwe.
Mawu ake Billy One wati iye ndi okhudzika komaso wapempha mtundu wa a Malawi komaso a Madula kuti amkhululukire pa zomwe anachita lolemba lapitali.
“Ndikupepesa kwa a Malawi onse omwe anamva zomwe zinachitikazi, komaso ndikupepesa kwa a Madula omwe ndinawalakwira komaso banja lawo lonse ndikupempha kuti andikhululukire pa zomwe ndinachita,”Billy one adauza wailesi ina yodziwika bwino.
mmawu ake Billy akuti sakudziwa chomwe chimamuchitikira kuti afike pomenya mlembi wa mkulu mu unduna wa zantchito, zamasewero ndi zomangamangayu kamba koti mutu wake unali utasokonekera ndi utsi okhesa misozi omwe unaponyedwa pa gate pomwe anthu ena amasokoneza.
“Sindikuziwa kuti zinakhala bwanji kuti ndimenye munthu wa mkulu ku unduna wa zamasewero chifukwa pa nthawi yomwe zimachitika izi mutu wanga unali utasokonekera ndi utsi okhesa misozi (tear gas) yemwe anaponyedwa pa gate pomwe anthu ena amasokoneza.
“Ndipo sindimaziwa chilichonse chomwe ndimachita komanso ndinali odabwa nditazindikira kuti ndinamenya mlembi wa mkulu mu unduna wa zamasewero chifukwa pa nthawi yomwe zimachitika izi sindimayakhulana ndi mlembiyu ndikupepesa kamba ka zomwe ndinachita,” adaonjezera Billy One.
Billy one yemwe ali pa bail pakadali pano azakaonekeraso ku bwalo la milandu pa 21 January 2017 pomwe akakhale akupitiliza kuyakha mlandu ovulaza munthu.
Mnjateni!
Indeed kupepesa uku nkwaboza wabullets sazatheka they dont av manners they are 100% ignorant thats y they called themselves palestines they aren^t malawians mmalawi amakhala wa ntendere dont trust bullets fans
Chimangidwe chimemecho ndiyenso amayambitsa kuba ma glass Ku bingu stadium kkkkkkk
Bola watchukz
Billy one knows why he had to hit him. That’s not the correct reason. He’s just saying that coz the so called victim has some powers next time don’t slap him use a gun if possible
hahaha zi ntchito zako zimenezo ur 40th day has come
Kampopi FC kwawo ndi kupha ndi ndikuononga
Ur apology z welcome man
Masapota abullets onse ndi mbuli munyongeni ameneyo aone polekera
Tiyeni tiwakhululukile masapota onse abulesi komanso tiziwaikiza m ‘mapemphelo kuti auziwe mpila, chifukwa mpila sinkhondo, mmmmmm ndikumva kukoma 5 -1 mbava inu ambuye akukhululukileni
:
Makolo ako sanakulere bwino ntchifukwa chake khalidwe laki ndilonyasa.Ask everywhere civilized people never fight kima izi dzikuonetsa kuti kunthundu kwanu ndinu achoncho.Sinthani abale chaka cha tsopano ichi
Wy fighting
Ndikanadziwa kuti Billy one wapanga zimenezi ndikanamuswa mwachisisi mpira ndimacheza awa?
Akapepese ali ku Maula kuti chikhale chitsanzo kwa mbava zinzake za bullets
Chabwino ife aBullets mbuli,zigawenga inu ophuzila Arobert muli ndi phd mumamwa mowa wa bwino eni cash gate dziko ndilanu ili osamakankhula mokhadzula
Timu imeneyi izisewera kumatimu ang’ono ang’ono basi chifukwa nthawi zambiri amayambisa ziwawa anthu ake ndi amene .Abbilly akhale zaka ziwiri osawonera mpira uliwonse mdziko muno
Ukayambe wabwezera ma mirror glasses and ma Toilet omwe waphwanya ku Bingu International Stadium, then Uzipepesa bwino, Otherwise go to hello with your sorry ,thief criminal
Tamva Gauys Munthuyu Akadya Nyemba Bas Akuthawa Mjala Nanga C Mango Antha Nzeru Alibe Adawa,
Wichita bwino kupepesa
Hahaha mukudya zamba eti!!!
Zoona zake ndizoti a Bullets ndiomwe amasokoneza masewera ampira kumalawi.Chitsanzo anali kuLilongwe posachedwapa stadium ya Bingu kumeneko kwabedwa zinthu kuti tifufuze ndiomwewa a Bulletswa.
Ndkumuzwa bwino uyu akat abande samagwilika
Bb kulibe munthu wa bwino ndi sodomu n gomola
TSiku lina muzauki dziko mzaona chakunda mwajaira nbb.
Team ya mavenda kuzolowera kupisa anthu mthumba xool nje
Vuto ndi Team yake
Mr khanje ndi mr rob mwanena bwino mkuluyu amasokoneza heavy
Ngat Muthu Wapanga Zaugalu Mubwezeleni Zake Zomwezo Koma Ngati Sanalakwe Musamupange Chilichose. Ndie Enanu Musapezelepo Mwayi Onena Mzanu Kms Ngat Adamumenya Zilibwono Chifukwa Amudziwitsa Line Tiyenazoni Anyasa
Ali odala yemwe azindikira kulakwitsa kwake, nanga ife
Ambiri mumatenga mpira kukhala mulungu wanu ndie chomwe chalamula ntima wanu mumachita chomwecho. Sory kwanonse amene mumalephera kugona kupemphera chifukwa cha mpira. Mulungu azaona nanu chochita tsikulina
Very absurd, disgusting, pathetic, uncalled for, embarrassing, unruly, barbaric, talibanic, boccohallamic sort of behaviour. shame on you Dude and all your fellow nyasibibi diehards. I rest my case.
Upepese kwa amene unamenya osati ife ngati kuti tinamva nawo ululu
Nditchito zawo awa or katundu ku studium ndi ma sporter a ndudu fc.
Stupid man sorry for nothing he must pay half million cash
Akuopa ku ndende ameneyo
Tava ase
Bullets supporters mmmmmm
ameneyu anapenga ndi zitatu zija asanamizire tearguts komaso akailowe osati za bail,n
Ukutanthauza chani ukati zitatu zija?
ameneyu anapenga ndi zitatu zija asanamizire tearguts komaso akailowe osati za bail,
Imeneyo Ndiye Bullets Kwawo Ndi Kuba Kupha ndi Kuononga Anthu Osavomereza Ndi Otani? Amenewa Kodi Mukafufuza Si Ana Agulu La Boko Halamu?Ana Anjoka!
Anthu aphuma ngati achina Billy azipasidwa ka chikoti kenakake kti ena azitengelapo phunziro,,sizopepesanzo ai,azipepesa akulira
Hahaha zigogodo ndiza mma 1970s ayi pano babah
Ife Zikutikhuza Bwanji? Iyeyo Anamenya Ifeyo Ngati? Apepese Mzake Amamenyana Nayeyo, Musatisokosepo Apa Ndi Anthu Osaziwika! Pano Tilindizochita Tikudikira Admarc N Cash Gate Cases!
It’s sports NeWS BRO mulikuti?
?
Ali bo
Munthu wamtundu umenewu amafunika kubanidwa ku mipira yonse kwa zaka 10
Ndi mbava za town izi musadabwe nadzo, Munthu wanzeru sangapange zinthu zaumbuli ngati zimenedzi
Chomwe Amakanizila Ku Vip Ndichani Munthu Atalipila Ndalama? Anakunthidwabe
One word is enough “uncivilized”
This guy needs to be a boxing fun maybe zingayendepo….but he is a disgrace to Malawi football
fans ya nyasa bullets khalidwe lawo ndende a young pioneer ya malawi congress party
Kkkkkk wapanga mbili basi.
Billy one don’t say u didn’t know what u were doing bcz this is ur habit. U were arrested b4 bcz of the same conduct, but now u know kuti munthu unampanga chipongweyu ndi olemekezeka. Ur excuse about tear gas is not valid bcz it’s not only u who got affected bcz of that tear gas. Iwe ndi munthu m’modzi mu gulu la anthu osokoneza masewero a mpira wa miendo Ku Malawi. And I Wonder why u r called flames chief supporter bcz according to my opinion u don’t deserve that name. Such an abuser like you
Team yopanga khalidwe, iluze iwine
mamenyamenya mudzamenya nazo mwana wa mulungu
Ndiye masapota a Chingambwe tchito zawo ndi zimenezi ndiku……. mukudziwa:-* :O
Isokheeeee!!!
Mwana wa chingambwe fc ameneyo
mwayamba ndeu eti tikuuzirani amafico tione richard mbulu wamva ?
Anthu ngati awa mukanangowamanga ndipo munaiwala powawonjezela za kusowa kwa katundu wapabwalopo ndipo pamafunika kukhaulitsa zedi
Ok
Anadwalapo khunyu mukhululukireni kkkk
Kkkkkkkkkk ma scandal ku bullets sazatha musova
Welcom Billy One.. winaso akazapanga zopusa mpatse MBAMA ina
balabayo chonde asatuluke mwina akanganyawa angachepese ziwawa
Mbava , zigawenga & asing’anga F.C
Ameneyo ndi galu mbuzi yopanda makutu.
Anachita bwino kunkwapula mkuluyo
WACHITA BWINO KUGONJELA MTUNDU WAMALAWI
I hope it is coming for your deep down heart…?????…if yes that’s ok…
Panopa ali kuti ameneyo
OCHEMELERA BULLETS AMAONJEZA ATENGELEPO PHUNZIRO NDI OMWEWOSO ANAONONGA KATUNDU KOMA ADZIWE KUTI AMAONONGA CHITHUNZI-THUNZI CHA TEAM YAWO YA BWINO IJA
He Must Rot In Jail Typical Of Bullets Supporters,they Are The Ones Who Erupt Fracas In Football Matches
u want my comment ?check #Robert P.Ching’ondo’s comment,,,
Lamuro ligwire ntchito ena atengerepo phunziro,mpaka kumenya Ps,what about munthu wamba.
Chingambwe sichabwino ananu inu gwaaaaaa pandudu
Mungapange manyazi inu bullets? Wachake ndi wachake koma bullets ilipire chindapusa basi!
chindapusacha.agogoako
Kkkkkkk chindapepera amenewa asamusiye
Musanene kuti waonga mbili ya Bullets kulibe komwe wa Bullets adakhalapo ndi mtendere awine aluze chimodzi modzi siyekhayo Vuto ndi team yomwe inadzadza ndi zigawenga mbuli osowa zochita .inu musayankhule ngati anzeru Bullets imadziwika ndi uchifwamba zoona zake
U dont know wat ur saying…your brain needs an operation
He need surgery
Mbalame zawanthu
Yes surgery indeed
ku NBB usavage kwambiri. … sionse koma ambiri. ….and you easily show it publicly. …inenso ndi wa NBB .
U mean ur the one of the savages??@Davish
I can agree with you I regret to be a bullets fan…plenty of zobas
Kkkk maule manyaka a team
5:1 anapenga nayo…
1min past 5(bullets) kkkk
Matthew Phisso ur not a Bullets fan ur one of the KAPADOS
Kkkkk a bullets tangokhalani pansi musatibowepo apa…..amuna anzanu ali Ku pelete uko ndi mi mfuti pita ukapange mfwe mfwe ngati siukadyako jombo kkk
Kkkkk a bullets tangokhalani pansi musatibowepo apa…..amuna anzanu ali Ku pelete uko ndi mi mfuti pita ukapange mfwe mfwe ngati siukadyako jombo kkk
Palibenso zotiwina atiwopsyezeapa chomwe timaziwa malawiyonse bullets sichimatha chaka osanva amaba ndalama pa Gate, agenda magalimoto anuwake, amathila mikozo maplayer a team ina, iiii amamenya azimayi amalonda, zikatele iiii player wakuti wamenyedwa kkkkk team ya mpila imeneyo? Chomwe ndimaziwaine oyitanila ma Tex ndi ogulisa katundu osapachika palumali amakhala opanda nkhalidwe
Mawu opanda chigamba awa man Rob
Koma kulankhula kumaganiza nbb/noma amene ali ndi mbili yakupha ndi ndani? Mwaila nthawi yomwei
Mwayiwala anakupatsani chilango chosamenyaso mpira pa Kamuzu stadium chifukwa chopanda khalidwe a KAPADO INU..mapeto ake anakupatsani pa Balaka kupha konso munthuso okhala sapota wanu agalu inu
Munthu munapha kuBalaka uja inali Nbb?
Someone is smelling MAFUTA
Man ndinu opusa mwanva inu school yake iti yoti ndikunyozera azanu kuti mbuli iwe bwera tionetsane ma paper tione dolo kape or ndalama ulibe WHAT THE FUCK. Usamayese uzayesapamamwa umaphatikize galu iwe, ukunena ife mbulu pomwe makolo ako or a sadziwa komwe komwe anayang’ana
Amangidwe kaye akapepese komko wachibwana
Mogo fc ndia a CHIVALA MIMBA
chamako
Nsena kufika popesa ndiye kuti zilbwino, akhululukidwe bac
Kkkkkkkk vuto ndi CHANDE, Trouble maker.
kma chtsiru chmenech aaaaaaaaa chaonong biri ya bulles. nach osachiones mbona ona bwnji?
ngati wapepesa mkhululukileni poti samkadziwa chomwe amachita koma chisakhale chizolowezi.
Wachita bwino kuvomeleza tchimo lake.
Ndudu ukupanga chani zonsezitu chandeeeeeeee nomaaaaaaa
malawi24 yonama munthu amupeza osalakwa inu wonani mu nation news paper
Tamusungani kaye
mogo fc ndí MABULUTU
bulutu.wa.mako
Mukhululukileni nkhani ndiyoti anthuwa adapenga ndi zigoli ndipo sakhulupilila kuti amwesedwa 5 -1 .
Tamusungani kaye
Kdi Enanu Mumangoti Umbuli Ku Bullets Ndye Kti Ku Club Yanuyo Kulibe Mbuli ? Kuli Anthu Ozindikira Okha Okha ? Kupusa Basi Iweyo Ndiweso Modzi Wa Mbulizo Ku Club Yako
Zakudinya unyaMasapota NBB ndi ambuli ose
Hahahahaha Waziiwala Iweyo Kti Ndwenso Mbuli Yaikulu , Umbuli Wako Waupanila Wayamba Kuseka Wanzako ? Hahahahahahahaha
Kdi Enanu Mumangoti Umbuli Ku Bullets Ndye Kti Ku Club Yanuyo Kulibe Mbuli ? Kuli Anthu Ozindikira Okha Okha ? Kupusa Basi Iweyo Ndiweso Modzi Wa Mbulizo Ku Club Yako
Wa nyelere wapeza nkhani kodi et?
can tear gas cause insanity?
Koma watipangitsa manyazi. Ife bullets timaikonda don’t ever again spoil image of our team…..
kunalibe unyolo kumeneko
kunalibe unyolo kumeneko
Alibeso kalikose gwape uyu musiyeni
Nde muthuso kuti akhale opanda kathu mugayileni zomwe muli nazozo
Mr felix muthandizeni munthu zimene muli nazo sure
Muzibulidwa kumene
Umbuli a buletx
Inu Ndi A Bodza Zedi. Mesa Wakana Nkhaniyi.
Akapuxa azixinjidwa kumene kkk
Mapalestina sasekerera zopusa mbamayonso anachepetsa amafunika ka panel beating ka mphanvu asamaphweketse
Ndi mbuzi imeneyi ilibe ulemu kukanakhala kunja bwezi atalamulidwa kuti asazapangenso zampira kwa zaka Ten
shame
umbuli sizinthu
za manyazi a Bullets
anakamuswa kwambiri naweso…nanga sunamuswe koma ukupepesa.