KB kumvetsa kuwawa : Now parading with Super league trophy

Kamuzu Barracks

Newly crowned Tnm super league champions Kamuzu Barracks are currently parading with the super league trophy in the streets of Lilongwe and some townships in the capital.

The Lilongwe based soldiers were crowned champions after beating Dwangwa United 4-1 in Nkhotakota to finish with 61 points and a point above runners up and last year’s champions Nyasa Big Bullets.

Kamuzu Barracks started parading with the Tnm trophy from Malawi Defense Force (MDF) headquarters to city centre passing to area 18, 49 then to old town via M1 road to Biwi where the parade will end.

Here are the pictures of Kamuzu Barracks parading with the Tnm super league trophy in the city of Lilongwe.

Kamuzu Barracks

Kamuzu Barracks

Kamuzu Barracks

 

Advertisement

72 Comments

 1. *KUULULA NJIRA ZINA ZIMENE MUNTHU AMALOWERA SATANIC ASAKUZIWA* Si wina aliyenseyo amene amalowesedwa satanic kuti amakhala akupanga zimene titatchule m’musimu. Asatanic amangosankhapo munthu amene angawapindulire _*KODI SATANIC IMAFUNA ANTHU OTANI*_ SATANIC IMAFUNA ANTHU; Akhama/Olimbikira Olimba mtima kwambiri/kapena oipa mtima. Imafuna munthu amene ali ndi luso e.g. kuimba, kujambula, kulemba, kudziwa za ma computer etc. Munthu ophumzila kwambiri/kapena mphwawi kwambili koma okhala ndi kuthekera. Munthu okongola/maka maka wachizimayi. _*ZINTHU IZI NDI ZINA MWA NYAMBO ZOMWE SATANA AMAGWIRITSA NTCHITO POKOLERA ANTHU*_ ❌Chiwerewere – ukangogonana ndi munthu wa Satanic nangati amakufuna ku satanic ko, umakhala kuti watheka basi chifukwa ukagonana ndi munthu wa satanic amakusiira ziwanda zoopsya ndi network yawo ya satanism. ❌Kugwilitsa ntchito ma perfume a satana e.g. Play boy (play boy amapatsa mphamvu kapena kuti ziwanda za ukambelembele/ ukathyali. Kusakhulupilika kwa okondedwa wako. Blute (blute amatanthauza “chitsilu”……bible limati “chitsilu chimati muntima mwake kulibe Mulungu). Perfume ameneyu wa blute ali nd ziwanda zokupangisa kumati “kulibe Mulungu. Perfume wa Pyramid ndiwoyipanso. Pa Perfume ojambula dragon/njoka Ma Perfume otchedwa Sexy, ojambula atsikana a maliseche Perfume wa “Adidas” Perfume wa Blue lady ndi ena ambiri. ❌Kupemphera ma church a satana makamaka kwa ma prophet. Kumbukirani bible linati m’masiku otsiliza kudzabwera aneneli/ma prophet onyenga/a satanic amene adzapange zozizwa zoopsya adzasocheletsanso ngakhale osankhidwa ake a Yehova. Ziwani kuti nthawi yake ndimeneyi yafika. ❌Kuvala zovala za ma lebel a satana CK……means “christian kill”. FFF (mchimodzimodzi kuti 666…) Gucci, Adidas, Dickies, Natas (means “satan”) Billabong Nike ndi zina zotero ndi mbedza zomwe amakolera nazo anthu mkuwalowesa satanic. ❌Kujambulitsa mukupanga ma symbol asatana ndi manja anu ❌Kumanga ma dred otchedwa “hot water”. Pali chinsisi chachikulu mukamaliza kumanga ma drediwa, m’manyika mutu wanu m’madzi, pamenepa mmakhala mukupanga pangano (covenant) kapena kulambira queen of the coast. ❌Kumeta m’mbali mwa mutu mkusiya mzere wa tsitsi lalitali pakati zimasonyeza njoka ya m’bobo, paja satana ndi njoka. ❌kujambula ma tatoo. Imeneyi ndi body art ya kunsi kwanyanja zomwe wajambulazo zimakhala ndi tanthauzo ndipo zimagwira ntchito mwaiwe. ❌Kukhala mfiti suchedwa komanso suvutika kulowa satanic. ❌Pewani maina awa kuwapatsa ana anu; Linda – limatanthauza njoka yokongola Rose – rebirth of satanic empire Diana ❌Arbotion (kutaya mimba) umakhala kuti ukupeleka nsembe kwa queen of the coast. ❌Mnyamata kuika ndolo zimatanthauza kuti ndiwamathanyula. Mathanyula ndi satanism. _*PEWANI IZI N’ZASATANIC*_ ❌Kutukwana. Munthu wa mzeru zake obadwa mwa umunthu satchula ziwalo za mzake zamaliseche. Uwu ndi mzimu wa satana. ❌Kuledzera ❌Kusuta fodya ❌Umbava ❌Uhule. ❌Kuonera ma filimu oyipa (horror) ma vampire series. AMBUYE AKUDALITSENI POWERENGA UTHENGAWU. Mutha kwaziwitsanso abale ena za uthengawu. Zikomo Kwambiri.

 2. Ndimene zimakhalira Team ina ili yonse ikumva kuwawa coz KB simamenya ndi Nbb yokha ai koma ma Team oooonse mmalawi muno kukhala no 6 sikufuna Man koma kuvuta kwa league

 3. Apa nbb singamve kuwawa ngati chitsiru…. atamve kuwawa ndamene anajijirika poonesa mpamvu zake pachabe kutola joka..kkkkkkk…kulandila phokonyore galimoto zakwamanje …kkkkkkk koma luso tv ayi ndiya lusodi apa ndakumvetsani kuti mmatanthauza chani dzina lanuli..kkkkkkkk usakwiye ndizammabomazi amawerenga ndi HASAN GOBA

 4. Akuvetsa kuwawa who?….NBB was just defending the league for the third time, and KB is just celebrating the victory in a military way as soldiers not kuti akumvesa kuwawa, they should celebrate and they deserve that celebration as the first military team to take tnm super league, you will also see the similar celebration if one of these team Moyare, Red Lions, Mafco or Blue Eagles will also take the league of tnm next time!

 5. BB yatenga ligi kawiri motsogozana, moti ikanati itengeso apapa bwezi kali kachitatu. Kodi enanu ndi mitu yanu youmayo ligi simmaifuna? Zoona ligi izingotenga bb basi? Ndiye ukhala mpikisanoso ngati! Bolako momwe yatenga kb coz zinthuzi zimakoma mkulandirana.

 6. kodi Super League imamenyedwa against NBB ukati KB ikumvetsa kuwawa???I thought its now a trend and tendency for teams to parade trophies they have won in the streets!!Ukanalemba kuti Kamuzu Barracks is Parading TNM Trophy in Lilongwe siizikanamveka???No wonder you are mistaking a COASTER for a BUS!!!!!!sukulu zakwacha….eeeeish!!

 7. Neba koma sulira?wapatako cian season ino?nsanje,kaduka,khwidz,avekele league ateteza,zikho zonse atenga hahaha.eni ake azikho til phe ku lali luban kkk.KB kunyada nd league kuno bwela uzaone

  1. Kodi KB imapikisana with bullets bax? Umbuli bwanj @ Ruth? Kumazisata, , NBB are the champ of presidential cup and are the most successful club in the history of Malawi football

 8. Asiyeni asangalale ndizosowa izi pomwe NEBA wakhala zaka zochuluka asanatenge ligi imeneyi ngakhale top 5 osapezeka. Tikati ligi Silver ndi Bullets basi. Congrat KB 2016 champions mwina 2017 azakhala Nebaa

 9. Umbuli siwabwino. Mtima ofunilana zoyipa basi. Kulikonse team ikawina trophy imayenera kuonetsa kwa ma supporter awo. Madrid, Barcelona. Samati Madrid ikumvetsa kuwawa Barca ayi. Umbuzi ndi umbuli basi.

  1. AYI SI BULLETS YOKHA KOMA INKATAMIKA KUTI ITENGA..KOMANASO PAJA ALUZA BUS TU….LOL! NEBA CHAKA SUNACHIMALIZE BWINOTU ICHI

Comments are closed.