Apolisi mu boma la Machinga ananjata mayi wina wa zaka makumi awiri ndi mphambu zisanu ndi imodzi (26) ati kamba kogwlira bambo wina wa zaka makumi awiri ndi mphambu zitatu (22).
Malinga ndi mneneri wa a Polisi mu boma la Machinga, mu mwezi wa Okotobala chaka chomwe chino, Mayi Inness Salamba ati anagwililira bamboyu.
Iwo anati Mayi Salamba anaitanila bamboyu kunyumba kwawo, ndipo atafika kumeneko iwo anavula ndi kumukakamiza kuti agone naye.
Ati bamboyu atapita kwawo anaoneka otopa ndi osokonezeka ndipo atafunsidwa, iye anaulula kuti wachitidwa chipongwe ndi mayiyu.
Apa akuti achibale a bamboyu anakaitula nkhani kwa amfumu amene ananena kuti nkhaniyi apite nayo ku Polisi.
Atamva zoti nkhani yakatulidwa ku Polisi, ati Mayi Salamba anathawa osaonekanso.
Iwo anaonekanso mwezi uno poganiza kuti nkhani ija yaola, koma anangofikila mmanja mwa a Polisi.
Iwo atengeledwa ku bwalo la milandu posachedwapa kukayankha mlandu ogwililira ndipo akapezeka olakwa atha kukakhala kundende kwa zaka zisanu ndi ziwiri (7).
Ayawo ndi ambere chire ma man polo ndi first priority yawo angagwiririredi kkkkkkkkkllkkl
Mwalakhula Mr J.b or Mrs J.b keept up.
don’t talk nonsense.just remember rape ndikugonana ndimu2 mokakamiza asakufuna nomater anampangisa kuti axuke
Tioneseni.mayi.wogwilirayo
Ayi mutsiyeni guyz tsadakozeke dalalayo.
M’bambo iwe acourt akuthandize becoz rape is apartof abuse.
Chancy Shakie, No Comment,
Atatha kugwiriridwa ada awo anadziwa bwanji kuti nkaziyo wamaliza kuwagwirira? Just asking,
Nde palivuto, mwamanga azibambo angati otero?
Juses plz come? For visiting us plz?
Kkkkkkkkkkkkkkkkk ine nde zangondsekesa kod zmayiyo alibe amuna ake kapena alinawo azmayi ena kuchitisa manyaz ok bola dolo waufila bas ndili ine sizngatheke guys kkkkkk kma kumalawi hey kwafikapo
ine chiti ndikambe ndichi ano ndi masiku otsiliza amuna omwe sanamudziwe yesu maso auzimu adzawasowa kuti azindikile oipayo ali pafupi uyutu nde oipayo satana wafika pamenepa zovuta
26_22 Ndinzimayi ndi bambo?
Ur stupid bcz kazi sangagwilire munthu wabambo.onse anafunana
za nziiiii ucal that rape???? Chinzibambo cha zaka 22 zoona kugwiriridwa ndi nzimayi
palibe ngati wagwililidwa akasume basi kkkkkkkk mwina wagayila matenda komasotu guyz pali akazi ena azimphamvu osamangotokota apa kkkkkk komaso ndani amene angalimbe atagwilidwa shaft ndi mkazi kugwililidwa it does not mean all u are saying it is doing it unwillingly ngakhale analowesa yekha after kumugwilagwila iye asakufuna anagwilila basi don’t take it too funny this is bad
hhhhhhhhh kkkkkkk mpaka kutelo kkkkk
zaka makumi awiri ndi mphambu zitatu ndi 22?
Ntayeni mayiyo nyamatayoso ananva kukoma
Kodi abale ndi chichewa chathu chathu cheni chenichi chizitivuta kulemba zoona? Makumi awiri ndi mphambu zitatu(22)????! Muziyamba mwawelenga kaye nokha pilizi.
Fuso lina mkumati kodi ali adimited ku hospital…kkkkkk aaaaaa zina ukaona kamba anga mwala…mmasule mzimaiyo wamulakwila ndiithu. Mmene zimakomela muja? km galu ameneyu..hehehehehe!!!.:…
Kkkkkllkkkkkk Fokofo
munthu wogwiriridwayo ndi wa khunyutu guys
kkkkkkk amangidwe mayi ameneyo zo
Mmmmmmmmm anakambirana vuto mkazi samafunsira
Hahahahaha
Kkkkkkkkkkkkk nkhani zake iii sichina amuna mwanyanya kuchona ku south africa ndemwati mkazi akatopa angapange bwanji? Mkaziyo siwolakwa asamumange
Zinyenganani
Kakakakakaka
Zili kuti zosowazo kkkkkk
Mayio sanalakwe osamangomva amna okha kumagwirila ana ayi zizithekabe konsekonse choncho kkkkkk
Nkhani zina…..mtheradi umaona ngat ukulota ukazibva.Moti ndi nkhani yonena ku police imeneyi.Iye amabva akupanga zosapanganazo?
Kkkkkkkk koma yah
malamulo agwire ntcito yake
mot sanathire madz amoyo? onse anamva kukoma palibe xogwirilana apa!
I don’t think a woman of 26 can rape a 22 yr man unless u said 12 yrs boy….
Rape case has got no age. if its under age like 12years then its defilement.
but real man can’t get raped buy a woman
Really
Vuto lamauka limenero
Aaaaaa xacamba et angomunanizr mzimaio pakat pa mamuna nd mkazi angamugwirire mzake ndndan ngat anatota sanamugwirire koma ngat sanatote anamungwirra. Guyz zingatheke kugonana nd mkaz usana tote? Kufoira et kkkkk.
Zankutu
Za ziiiiiiiiiiiiiiii
Zaka makumi awiri ndi mphambu zitatu is how many years in English paja?
Anali asanachindepo chikhalire kapena bwanji ndiye wamuphunzitsa koma amamva illovo illovo Ali boo
Akanandipeza Ine Ameneyo Sakanazukapo Chifukwa Ndikanamenya 6 Rounds Non Stop
Koma nkhani iyi yandiseketsa kkkkkkk nde mwati nkaziyu ali ndi mphavu zotani zompanga force mamuna kkkk nde mpaka nkuluyu anawutaya kkkkk ine zandisangalatsa ndagwa ndiphwete
abale tatitumizeni ife akatigwilire nawo ….ha ha ha ha ….
mwayi wa nzama wofukula ndi manja khasu lilipo .ha ha ha ha ……
Ndi bambo otani ameneyu? Akuti anakafika kunyumba ali otopa kwambiri? Kutopako ndiye kuti wapatsidwa mimba ameneyu. Ndiye ngatidi bamboyu watenga mimba amusamale ndani poti mayi ogwirirayo mwammanga?
Anthu ena alibe mwayi
Nayenso amafuna nanga amanyekulira bwanji
Mamunayo ndi garu kwambiri pali nkhani apa yoti mkukanena kupolice koma zoti zimakoma zimene zija iyeyo sakudziwa
Rich people do not get HiV, aids.
You are misinformed dude
Hey, wena Kabelo
Malawi sazatheka basi.
Malawi sazatheka basi.
koma man munachita bwino kupanga report ku police ayenela amangidwe ameneyo osangoyendera poti nkazi apezeka ndinyenge ayi guys kunja kuno kuli matenda amulakwira nyamatayo mwina ali ndi nkazi amene anagwirizana zochita si bwino akamupatse matenda nkazi wake wosalakwa she derceve 8 years in prison for rape case
Yawo.com
Bambo chitsilu chakanthu, mayi tsagwirira anayifuna kungoti bambo kubed tsakudziwa . Anthuni mudzitumidza nkhani dzachikoka otsati zolephela kubed ngati izi , bambowe mpaka kukanena Ku police bwera ndizakulipire mlandu mayi anavutika ndiye otsaziwa kuti unagwa mupapa .
Kkkkkk…zimasowa zimenezo,,wapanga mwai mzathuyo…
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
ugalu basi anthu akulu okha okha angagwilirane. nanunso zomangana muziziwona zauchitsiru
Kkkkkkkkkkkkkkkk wakoleleyo ang’oma
No comment
Mwamuna otani mpaka kuvulidwa trausor kkkkkkk nayenso amafuna
Kunena zona pakufunika kuti maiyu alandile chilango chokwana chifukwa ndikulakwa kukupangira chinthu chimene iwe mwini sunafune ndichimozimozi amuna ngati angwirira mkazi yemwe sali wasaizi yako amati wamuphwanyira ufulu wachibadwidwe nanga mwamunayu sanaphwanyidwe ufulu wachibadwidwe ?? MWINA Ali ndimatenda ndiye kuti amupatsira amuonongera tsogolo lake
Akadzatuluka adzabwele kwa ine ndimdzathira sabola adzasiya zimenezo
Ximalowa ixamatote zachamba zimenezo aturutxdwe
Szacilendo nowdez
Anavana kukoma awa
Apa chakula ndichibwana…. mukadzakumana nazo mpamene mudzadziwe kuti kodi mzothekadi mkazi kugwirira mwamuna? Koma choti mudziwe ndichoti azibambo ndi achinyamata ambiri awumirizidwapo (kugwiriridwa) ndi azimayi. Kungoti timawona chinthu chamanyazi kuti tibwere poyera .
Kkkkkkkkkk asaaaaa chani mwamuna wazaka 22 kugwililidwa??
Zonadi akazi akuona zochedwetsa kudikira afusilidwe.
Kkkkk Zikanachitikabe Zimenezi Mmmmmm Amalawi Sazatheka
Makumi awiri ndi mphambu zitatu {23} not 22
kkkkkk dzinthu zikusinthadi eti!
Zamanyi basi kumalawidi eti
Anagwilizana amenewo
Malawi 24 tsopano next>>>
Mayi ameneyo anali ndi nyere yovuta
Kugwililila mpaka ma round atatu,,,,amachindana awa asatipusise.
Zaka makumi awiri ndi mphambu zitatu (22), kkkkk
Proudly powered by Food Association of Malawi (CONGOMA)
nayeso bamboyo ndi opepera osangolora bwanji kufuna kutchuka koma amadzukadi ameneyu chimalora opanda mano chimanga ndizimenezi
Kkkkkkk Oseanafuna
Mkazi wavula zovala zake then wazamvulanso mamunayo zovala! Am sure there was a gun
Kkkkkk machine azigwira ntchito
Pali zina zot ukanva ansala kumaiona wekha.fuso anali pambwamba panzake nndani nanga abamboo anamangililaa kodi pokanika kuchoka waboza kkkkk
Za zi¡!!!
Iyaaaaa inali mission osat zogwrilazo
Paja kuti adagwililira iye mamuna sanakhojele koma sanatote paja adotowo adamuyesa kuti zose sanachite mayi amagidwe paja mamuna adachinda kadziyo amutayi
Kkkkkkk I guess she needed that mans d**k so bad……
Nthawi yake ino yotifunsira akazi. Kkkkkkkkkkkkk
Ndiye kuti naye mwamunayo amafuna,kunena mosapsatira anadzuka bwanji,?or kuti misempha yagwira ntchito yake nde basi kungoti njoo! agwilirana amenewo asaname
Nkanakonda ntaumvera mlandu wake a to z
kodi katunduyo atazuka analowetsa ndani.nanga anazula ndani pamenepo ????
Eish
Mmm coment reserved
Ndikanakhala ine sindikanamumangitsa ndikanangomufunsa kuti ngati angakonde some more kuti tionjezele yachiwili.
MAI you are under arrest
Adolo awanso nd o4ira bwnji? Amayi amafnika nawo aztero. Akazatuluka ku ndende mayiyo mumuuze andgwrire ine
Makumi awiri ndi mphambu zitatu (22)?
Inenso kudabwatu , nkhani ya bodza simasowA
Akazi Mukazifuna Muzingopempha Akuluwa Apepelatu Apa
Inuso mukamapanga post inu nkazi angagwililile mamuna? Mamunayo amabongabwanji ngat samafuna? Zachamba et
Koma nyamatayo ndi kape ,that is not Rape ,nyamata (22) years wa mphavu zake angagwiriridwe nd mayi wa zaka 26 ,that is a lie ,investigate wisely
Azimay ena amatero kaamba kofuna kumupatsa zizobodola mamunayo atsagane naye kumanda shit…osayifunafuna galu ikutombe bwaa..mumve kuwawa
ine ndimaona ngati mamunayo anali mtulo kani amaona kkkkkkkkkkii
Ok
Koma achipatala,anamuyeza ndani pamenepo, bamboyo zinakhala bwanji poyezapo kapena ogwirirao kkjkkkkkk
Mulandu umenewo kulibe…mutaya nthawi bambo
Kkk game un usual
Kkkk gane un usual
Imayimilira ikaona katunduyo mmayesa ndimamuna agwilirira bansi
She did a good job zinanyanya kumangomva azimayi akugwiriridwa basi nawo azibambo agwiriridwe asaaa kkkkkk
mamuna sangagwililidwe ndimkazi coz mbolo sitota ngat sukufuna choncho siingaloweso ku nyini. amazifunaso adawo
Kkkkk koma guys
kodi mkazi atakuuzani kuti akubayani ndi mpeni mukapanda kugonanaye mutani mpeni ulimmanja mwake ndipo sakukusekererani
Umulanda nkubaya nawo
Manje nkhani iyi izavuta,manje gadafi anadzuka bwanji iye mwini wake asakufuna?
Komaditu
Mwaudze bambo amenewo kuti mapwala awo
Sexual intercourse 100%
K
Kaya
achimwene ogwililidwa,nali funso: zinatheka kutelo bwanji musakufuna?munachitapo chani mayiyu atangoyamba kuchita zodabwitsa? musatinamize mumkafunana ndikale ndiye mwangosintha maganizo,ndikovuta mlanduwu inu kuwina oweluza ngati ndi achilungamo.Mukungozumzitsatu apa mkazi wanuyi malo moti mutiuze kuti mwapeza.Mukanangomangitsa chinkhoswe nkuyambapo banja mmalo moipitsa mbili ya wachikondi wanuyi,sanakugwilileni koma kuti mmakondana bwanji simunathawe kapena kukuwa? bodza silabwino musapweteketse munthu wosalakwa,awa ndi akazi anu chonde akondeni ndipo maso awo anayamba mwano,amuna ena sayesa kanthu koma inu nokha basi ndiye inu mpaka kuamangitsa adona amatelo? pitani mukasekese mlandu ndipo apolisi mukauze kuti nkhani yatha chifukwa ndi mkazi wanu.
M bamboyu amamugwilira bwanji?Akunama onsewa zinali zogwirizana
Amene alimumagulu abwino pa watsap please add me 0731821830
Nyele yake ya mtundu chani??? Tandiuzeni bwino bwino sindikumvesa tsopano anaika yekha nanga zinakhala bwanji??
Kodi bamboya kapena anamwetsedwa mowa ngati atsikana atatu a ku mzuzu aja
Kkkkkkk okay
kkkk osangosangalala bwanji man kt akugwililani ena2 akuzisowa. pot (chimalola opanda mano)
Mayi amangidwa kamba kogwilira bambo By Mwayi Mkandawire November 17, 2016 New Military Flashlight Every Patriot Needs to Know About ? Apolisi mu boma la Machinga ananjata mayi wina wa zaka makumi awiri ndi mphambu zisanu ndi imodzi (26) ati kamba kogwlira bambo wina wa zaka makumi awiri ndi mphambu zitatu (22).Malinga ndi mneneri wa a Polisi mu boma la Machinga, mu mwezi wa Okotobala chaka chomwe chino, Mayi Inness Salamba ati anagwililira bamboyu.Iwo anati Mayi Salamba anaitanila bamboyu kunyumba kwawo, ndipo atafika kumeneko iwo anavula ndi kumukakamiza kuti agone naye. Ati bamboyu atapita kwawo anaoneka otopa ndi osokonezeka ndipo atafunsidwa, iye anaulula kuti wachitidwa chipongwe ndi mayiyu.Apa akuti achibale a bamboyu anakaitula nkhani kwa amfumu amene ananena kuti nkhaniyi apite nayo ku Polisi.Atamva zoti nkhani yakatulidwa ku Polisi, ati Mayi Salamba anathawa osaonekanso.Iwo anaonekanso mwezi uno poganiza kuti nkhani ija yaola, koma anangofikila mmanja mwa a Polisi.Iwo atengeledwa ku bwalo la milandu posachedwapa kukayankha mlandu ogwililira ndipo akapezeka olakwa atha kukakhala kundende kwa zaka zisanu ndi ziwiri (7).
Zovuta izi mpaka kuchimwa wapadera kaya
ndipemphe amalawi24 andipase adres ya kwa mkaziyu nane akandigwililile
kkkkkkkk
Udziwa bwanj wagwililira ma hope ake nde upite iwe akangokudulako ndi okwiyatu
Ziribwino
Ine zikungondisekesa kwinaku nkumasilila kuti kaya ineso ndizamupeza wotiandigwirila kaya. Kkkkkkkkkkkkk
Zamkutu, Anangokanika Upereka Ndalama Ndye Wat Alire Kut Akumugwiririra
Makumi awiri ndi mphambu zitatu (22) boza lalikulu
Mzimayiyo ndiosalakwa, aman-wo ndi achisuru and amfuna, why did his penis erect yet he didnt want to ? He’s not worth to be aman
Ndiye yake.
Pafika zinthupa ngati ukuchedwa kumufunsila uyembekezere kuti akufunsila iyeyo akadzi atopa mbwiyache ndiye iwe kumangonyada nayo ndodo yakoyo azikuchindani choncho sanalakwise mkaziyo anatotopa naye ndi munthu mauka amamuyabwa ,koma tamufunseni mzathu ogwililidwayo kuti sanamve nawo kukoma?
keeeeeeeee
kma big mwandiwaza
Mwayankhulatu
Adakumana Nd Mwana Wa Njomba, Kkkkk
Kkkkkk koma guys ndye mmene zimakomela muja, mpaka ukasuma kuti wandigwililila kkkkkk zamanyazi….its tru kuti sanaike yekha mwamunayo panbowopo…kkkkkk bola apa guyz
Nayens amathandizir nawo,, bt mwina amaopa kt amadula mu mpingo,, kkkkk kma amuna enawans ndye ngosekesa bwanj,!
kkkkkkkkk mdaryo anawufr mayi akungowalakwir mwina alind milandu ina!!
KOMA MBOLO IMALOWA ISANADZUKE MASULENI MAYI
Mamuna amagwiriridwa kani?
Sozoona onsewa anali ndi nyere, si kwapafupi mayi kugwiririra,mwamuna wankulu ngati wa dzaka 22. Bwanji kodi?
Kodi iwe unagwa mumtengo wapapaya, mpaka kulira kuti akugwirira. Panti wang’ambikayo ndi uti, tandionetse ndithu kulimba mtima kukalowa ku court ndi mulandu umenewu kuteroku mnzimai wamangidwa kuti amakugwiririra? Iwe munthu sukulu unathawa kale, si iwenso mwana pamenepo ulindi udindo kale wapakhomo pako. Ameneyo ndiye, anakati azikupatsa yeni-yeni yapansi panyanja.
Palibepo mlandu apa komanso iwe admn makumi awiri ndi mphambu zitatu zingakhale 22 ??? Mwinatu chifukwa kwabwera two thousand imodzi ndiye masamu akuvuta eti?
Sanamgwirile anarchist kumangililidwa 22years amatani kuthawa or kumukankha ,,,, Anafuna nayenso muziti amapanga chiwerewere osat amagwirirana no!!!!!!!!!!!!
….Waaaah.! zobeba wati.?
Anagwirizana mbolo ilowa bwanji yosatota?mmasuleni mzimayiyo mesa kufookako ndye kuti anathyapula ma round awiri ndye kuti amava kukoma.
kkkkkkkkkkkk apa ndie timat pusi wagwa popanda agalu
Yes its tru guys…ameneyu kape bwanji…..kkkkkkkk
M’dala Ameneyi Ndionama Wam’va Kukoma Azinena Kuti Wagwililidwa Ha!Ha!Ha!!!
kundichinda ine ndingoti alemekezeke wakumwambayo,
Kkkkkkkkkk koma
eeetu nde chilungamo chaketu adona,nanga mpaka wina amangidwe kuti chani.
MNTHU WA NKAZI SAGWILIRA KOMA MWAMUNAYE NDAMENE GAME INAMKULIRA! Esh ndikanakhala ine
RAPE (Sec 132 of Penal Code). Capacity To Commit Rate. Any person is capable of committing RAPE…Except: 1. A woman 2. A boy under the age of twelve years. 3. Husband and wife, unless it is proven that they have been separated by the court and that they are living apart. Dzivele mtolo mkazi samagwilirira…!
aaaaa mamuna ndyemwe amalox nde osatipakapo yapa iyaaaa and ndma agement kusowa chomanga eti zachamba basi,,,,,,
Kkkk amangidwe
Aaaaa awanso ndiye nd maukatu
Makumi awiri ndi mphambu zitatu si (22)
Zosatheka izi adolowo anafunaso mmm mphamvu zinabwera bwanji if samafuna please musiyeni mzimayiyo.
Mwatero? Kkk
Kkkkk eya bro aaaa asatipusise
Sured
sizinngatheke zabodza amunamizira nkaziyo
Bodza iwe utsiye
Kodi mbolo imatota ngati mwini wake sufuna? Ngati mayi wagwililira imalowa bwanji ili yofota? Musatinamize apa! Anthuwa amachindana mwa program.
U nt lyn man!
understand the meaning of rape by laws of the land
Kkkkkk
Kkkkkk kma adha
Kkkkkk galu bambo ameneyu ndiithu. Km zoona awe….some
It cant happen they are almost same agement
point of correction,, “makumi awiri ndi mphambu zitatu” (23) not 22* as you’ve stated! it’s sad news though!!
chim’bambo chamwaichi chinali kuti mmene amachigwililila??!
Adolowo nd onama ndpo al nd tchimo
Magwiragwira azimayi lero ndizi mankhala anyere mmachekera aja akulowetsani kundende mawa timva kuti mwagwilirira galu iiii kaya gokonko..
Iiiii mwai wogwa ngat zombe ife zmenez timazsowa abwerenso agwilire ine kkkkkk
kkkkkk hey!!! atifike kuno
kkk wanyambitilatu iwee!!
kuli matendatu akupatsani akakugwirirani
Kkkkk zamatenda uko….coz nkhani ndiyonyengana apa. Zatheka bwanji ma round atatu iliyofota shaaa sindikunvetsa ataa… Good news ngati iyii…mkumati wandigwililila koma bongwe bs..
foolish girl,amangidwe basi ngati nyele yinamvuta bwanji sanapite kwa pitala kut akathane naye
Zugwirizana?
Zasemphanatu apa bambo
Iwe wosanena kuti akakwatane ndi bambo ako bwaaa
Zithere komweko kwa achawa please
Bambo wazaka makumi awiri ndi mphambu zitatu(22)
Inenso kudabwatu , nkhani ya bodza simasowA
Zosatheka anagwilizana amenewa
osnandigwililira ine …. ine nde sindingakasume2
Mmmm hahaha koma
kkkk nyere ya achawa kaya anatenga ya nkhumba kaya kugwirira ndi akazi omwe?achawa sadzatheka basi
Ndani adakunamiza kuti ku machinga ndi Ayao okha okha kuliso alomwe achewa umbuli sudzakuthelani
Koma uyu ndi mchawa man
Zonyozana ayii apa. Aliyese amagwidwa nyere. Nkhani ndiyoti mwamuna salowetsa asatote. Mmai wabwino ngati, en zaonetselatu kuti panalibeso zolipilana…kkkkkk km amuna enawa kumbwambwana man…yhoo!…
paja azimay ena ndiziphona osakaika guys
nyamata wamwayi mpaka kugwiliridwa ndi mkazi
Kkkkkkk Realy??
Kkkkkkk
Iii zoopsatu izi
amugwilira bwanji munthu wa mphongo??? Zosatheka zimenezi
Kkkkkkkkkkkkkk
Sanamugwililire anapangana amenewo
Za ziiii, ndiye tiziti chiani pamenepa, mkazi wa zaka 26 sangagone ndi mwamuna wa zaka 23? Ndi woofoka ameeyo bamboyo akanamwa khuzumule uja timati viagra kapena Sildenafil citrate mkazi ameneyo akanachonganso koma mpaka kufika kwao wotopa ndi wofooka zomwezi?
Mkazi ikamgwira nyere kodi mungamuthe. Nthawi yonseyi wosakuwa nkumakanena kwao apo mwinanso anakauza ami ake za ziiii.
Zongoopsera matenda omwewa koma ngati kuli kwathganzi wadya zake m’bambo ameneyu kkkkkk
Za ziiii, ndiye tiziti chiani pamenepa, mkazi wa zaka 26 sangagone ndi mwamuna wa zaka zitatu? Ndi woofoka ameeyo bamboyo akanamwa khuzumule uja timati viagra kapena Sildenafil citrate mkazi ameneyo akanachonganso koma mpaka kufika kwao wotopa ndi wofooka zomwezi?
Mkazi ikamgwira nyere kodi mungamuthe. Nthawi yonseyi wosakuwa nkumakanena kwao apo mwinanso anakauza ami ake za ziiii.
Zongoopsera matenda omwewa koma ngati kuli kwathganzi wadya zake m’bambo ameneyu kkkkkk