Pataphulika mphekesera zoti mtsogoleri wa dziko lino anachedwa mu dziko la Amereka kamba koti anagonekedwa ku chipatala, mkuluyu ali ndi mwai otsitsa nkhani zimenezo lero mwa yekha.
Malingana ndi a kunyumba ya boma ku Lilongwe, mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika lero akhala akuyankhula ndi atolankhani.
A kunyumba ya boma ati a Mutharika alankhulana ndi a tolankhani lero zokhudza ulendo wake wa ku Amereka koamnso nkhani zina.
A kunyumba yaboma ati atolankhani oposera makumi anayi aonetsa kale chidwi chofuna kumva mtsogoleri wa dziko lino.
“A President akumana ndi atolankhani lachisanu, pa 21 Okotoba,” anatero mneneri wa a President a Mgeme Kalirani.
Anthu ambiri akhla tcheru kumva a Mutharika kamba koti atafika mdziko muno sanalankhulepo ngakhale liwu limodzi ndipo anli okanika kugwiritsa ntchito mkono wawo wa dzanja lamanja.
Atafika anthu amene anali ndi chikayiko kuti mdziko la Amereka mkuluyu amadwala, anavomeleza ataona mmene anakanikila kugwilitsa ntchito mkono wa kumanja.
CHILUNGAMO SICHIZAWONEKS
Inu chilungamo munthu amachidziwe yekha basii kaya anena za bhodza kaya zoona izo ndi zake
chilungamo chake athu akumipandowo akuchidziwa, sangawulule. koma pot ndimatenda bisan akanakhala maliro akadanena’
Atola khaniwa ndifukwa mafico imatibula kukonda boza
KOMASO IFE AMALAWI NDIFE OMVETSA CHISONI KWAMBILI. PRESIDENT ALIYESE AKAMAYENDA KUPITA KUDZIKO LINA AMAKHALA NDI LIMIT. IWOWA CHIMENE WATHELA MWENZI KUMSONKHANO WA UN OMWE UNALI WA MASIKU ATATU OKHA CHIYANI?? KOMASO MPHEKESELA ZA KUDWALA NDIKUFA KUKUNENEDWAKO SIKUNAYAMBILE KUMVEKA KU MA REDIO STATION AKUMALAWI KOMA KUNJA KWA DZIKO BWANJI OSALIMBANA NDI ANTHU AKUNJAWO BWANJI??
Ndilbe Chkhulupiriro Chot Ndiymwe Walankhula Kwa Atola Nkhan
Stupid media!
ndiye ayankhura kuti chani?
Amalawi ndife otemberele dwa zowona azidziwa m mwiniwakeyo.
Anthu akumalawi ndi oipa
lembani ma comment anuwo ife tiwelenge nawo
kodi anafika liti? Why sanafike ku comference room the same day?
It’s too let kutsutsa lero
Nkhan imeneyo yundinyasa kwambili kaya akudwala kaya sakudwala azidziwa yekha mukubisa matenda chinachake chikachitika tidzava.
Kkkkkkkkkkkk ptar akumana nazo relo matenda mbali akathana akutikomweko ndi soja.lusiyasi banda ndiposo wadelela akutiso sakuopa anaziyambila kalekale thaw ya kamuzu ngati anamulephela akuakulu thaw imeneyo Nde unyundendani. ..bajatu musamuiwale lusias amafusa pakana muthu yemwe akumufusayo pakana kumwalilandi Bp ndinafuso
Tamalemban zomveka akulu!
madala. Mwavelanokho ana anuwa akukhalangati akukunyozani km ayisichocho kukudandawulila ndimene dzikolathu likuyendala. Chonde tayesesani kubwelapoyela ndikuwuza thundu waamalawi chowonachenicheni titsana madala zikowathuyu akupiti kuphophotsono likukhalangati lilibetsogoleli OK km ndilindichikhulupililo kut kulilakwathumwakuve ndithu ndikuziwakuti muchitapokathu
Uchisiluomweo matenda pakanaosalakhula kod imeneyindi mbuz yamuthu at akufunika akaumbale
Magetsi zazima
Tiwuzen zoona
Bola asakagwe ndi bp kkkkkk
Timveko zina abale iyaaaaa
koma pitala akangoti wachila bho bho. akutchapani makofi muona… musaone ngat sakuwelenga mwano mukurembao
Kodi sanali pa wailesi? Chifukwa atola nkhani amanama kwabasi.
Anatiuza kuti Peter wafa, lero akukanira anthu kuti inali mphekesera ua m’chipatala. Anthu ake ati oposa atola nkhani?
umbuli ndiumene ukutipha kodi mene munayambila kunyoza munja mwapindula chani agaru inu eeeee tamusieni muthu azipuna zake zinayeratu inu mukhalila yomweo yomanyozayo eeee alesi
Akamasusa azisusa ndi mikono yonse m’mwamba
Now, many will know, Mutharika is a great man.
Amalawi dziwani kut boma lakangalika kupanga ma reformz so,,,kusowa kwa mankhwala + ndalama,,,kuvuta kwa magetsi + madzi & kukwela kwa mitengo ya katundu + kuchedwa kwa malipiro ndizipatso za”public reformz”
From where I’m seating. ..it is 1:15pm. The count down continues. In 45 minutes I want to see my president speaking to journalists in robust health. I guess I will see him gesturing using his right hand and not his left only.
Atsutsaso Chan Poti Zinthu Zimaonekelatu Zokha Nthawi Zina Kuvomereza Chimakhalako Chinthu Chabwino
Abwana awuzeni anthu kuti mukudwala,chifukwatu ndizochita kuwonekelatu nanga muzichita kubisa ngati mutodwala kanyela isiii!!!!
Otsutsa? No Nyazi?
Timvera kwa atorankhaninu zenize pobola osaikidwako bunzi pakamwa
Koma muli ndi mbiri vuto lanu chenicheni ndichani yoh yoh pangani zanu zimene zingakuthandizeni.mukulimbana ndi munthu woti ali ndi ndalama kale zake zinayera kale inu koma kukanda akalungu nsense.kunali muluzi analipo enaso ena amalimbana naye chifukwa chakuchita bwino kwake pano muluzi ali kuti????? Samalani abale polimbana ndi anthu andalama muzafa imfa yowawa
Alı ndı mwaı otsusa kapena ofotokonza? Inu chomwe mukudzıwa ndı kususa bansı?
komaso kuti mufuna a malawi tiziyendela yiti pakuti kamuzu amatichuma chilinthaka muluzi amati changu anyamata pa twon Bingu amati amalawifesiwosauka tiyendepamodzi ndimtimawumodzi amayi amati amayitakatani nangayinuyo muwuzathunduwa malawikutichani azingoyenda popandatsogoleli tatiwuzani
Am waiting
Ayankhule kaya asayankhule ndi ufulu wake mukulimbana ndi munthu oti atamwalira inu simungapasidwe mkhale spoon yake tiyeni amalawi tipeze zochita not kunena munthu oti zake zinayera kale mphindu palibe ngati adwala adwale iyenso ndi munthu
Koma mwaimvesesa nkhaniyi? sakunenakuti ndichibale komamonga tate wazikolino yemwe akudyelela ndalama za misonkhoyathu akuyenera kutiuza kuti adalikuti?ndipo amataniko akalongosol mpamene ifetiziwe chilungamo so usaakhomelele atolankhani pamozi ndi amalawi onse amene alichelu ndikhani yokhuzana ndi tatewathuyu thanx
ooo misonkho yathu ndiye alemelatu misonkho yathu kkkk
Achilomo mbuzi yamunthu,presidentitu amakhala wadziko osati kukhomo
every one has the right of privance
Muha inetu si mphawi ngati iweyo omayang’ana zamwamba kukacha,mbuzi ukunenayo utha kukhala iweyo ndipo yeniyeni ndithu mwina sukumuziwa yemwe ukukamba nayeyo,usamale
Kkkkk kma lol
Atiuzedi akakana timukakamila mpaka alola
looking forward to hea 4rm de bigman himsef.tiuzeni zoona*2
Enafe tatopa ndi za pitalazo.
Atolankhani please Kandifunsireni kwa a president wo kuti “Malinga ndi kasololedwe ka anthu m’bomamu kapangisa kuti anthu akhale pa umphawi wa zaoneni, Monga kukwera kwa zinthu, Kusowa kwa mankhwala ndi zipangizo zina muzipatala, Njala, kuzima kwa magesi , Kuchedwa kwa malipiro, Kuchepa kwa chitetezo, ndi zina zotelo, Inuyo simukuchitapo kanthu mungoti phe.Kodi kuti inuyo mutulepansi udindo wu ndikupatsa munthuoyenera ndikuti muzilamulabe koma anthu azikoli azizunzikabe Çhabwino ndi chiani?”
Out Of Sense!
For what?
Senseless
Mbuzi
Hanif tatchulan munthu woyenerera wot amusiile
Atuledi ameneyo
No sense!!!!!!
yalumpha moto
maro moti alongosole malawiyu akuchedwa ndi zazii??koma peter Aaa kayai
Boma la DPP linachokera kuti? Take it back Tikufuna ndalama zikhale matumba mwa wanthu osati ku capital hill yi.
Inu amene mukuti nonsense nu you’re the one who squandering our money in the capital hill
Ndakhulupiriradi Kt Peter Zinthu Sizikumuyendera Komabe Osadanda Mavuto Onsewo Ndithetsa Vuto Lalikulu Ndi Misa… Komabe Zonse Zitheka
Koma akangoti wavomera kuti Eya ndinalidi mu chipatala ena nde angayalukepotu heavy
Kodi kudwala ndi vuto etii,?
Amalawi24 zining.a siza bho best way mphekesela zoti ntsogoleli wa dziko lino wa mwalila ifeso kuno kuti tidziwe zoti wa mwalila tina ona inu muta panga post yoti watisiya osati wa chedwa kwa merika
Usalankhura komanso upereka moni ndi dzanja la kumanzere ndi umboni wakuti amadwara ndiye apereka umboni woti chiani?
kodi chifukwa chiyani anthu mumamfunila nzanu zoipa??? u like or not but president Peter Mutharika ndi mtsogoleri wa wanu.apresident akululukileni anawa sadziwa chomwe akuchita
Welcome Braz! Anthuwa Umunthu Ndiwomwe Ukuwasowa, Walakwa Chiyani President?
Ngankhale ali ana komandiamene anakavota kut iyeyompaka akhale wamkulu. ndelero akamayankhula musamawakanizeni ayi coz voteyao ndi imeneikulakhula palibechimene angayankhure iwepamenepa adha inu
koma olo muphuphephupe iye ndi mtsogoleri wa dziko la malawi. olo upite ku maiko a kunja kukufunsa kuti mtsogoleri wa dziko la malawi ndindani umutchula ufune usafune…and palibe munthu amene amanfunila nzake zoipa pamatenda iye ndi munthu olengedwa ndi mulungu ngati inu. kukhala president dsnt means kuti sangadwale or kumwalira
A malawi 24 ndinu mbuzi kwambiri lero mkuti ali ndi mwai wosusa zomwe zinkayankhulidwa nthawi yomwe anali ku amereka . Mesa mnkati anamwalira ndiye lero asusa bwanji coz anamwalira ?
zonse za bwino
Mukuikiraso Mwina Chifukwa Chan?
Nthawi yanji?
Tatsekula Ma station ose lelo.24 isatinamize lelo.yoyamba kuvela. ikhala zodiak.Tikuti lelo sitisutha pa Air.
Kaya Ine ndkuyika 4n yanga pa Solar coz magasi anaonongeka kalekale kenako ndkukatunga madz ku mjigo ammatap anafa kalekale,, Nyasaland wanga iwe kod ukulowera kutko?
apuletenti matenda sitibisa timanena ena akupatseni mankhwala.
apuletenti matenda sitibisa timanena ena akupatseni mankhwala.
peter ndimamukonda koma ndikufuna ndidziwe zomwe anachedwela kuja basi
Ndizake zimenezo inu chikukupwetekani ndichani
What ashame to malawis selfish, heartless, insensitive politicians who reguard malawians as fools. Denying an issue which can even be noticed by cats & chickens. Shame!!
Inu apeter ah bwanji munkaleka kuyankhula tsiku lomwelija,pano ndemudziti chani, popeza mwachila ndemuziti msonkhano ahaaaa
Tikudikila
Mmmm kkkk mukati ali ndimwai wotsutsa nkani zimenezo ndekuti zamatendazoso zinali zabodza? Mmmm kkkk
mapilisi agwira tchito we will welcome back on stage
Mwangosutsa abwana Ibu nanga dzanja lamanzere lija munkapelekera moni kwa anthu mnatani? chilungamo chili ndinu bwana
Malawi 24 tomorow dont change subject. Mwatiuza kuti President amadwala. Kodi simukuopa kunjatidwa popeza enafe ufulu wolankhula anatilanda akamuna. But why this hide and seek game. Kodi matendawo ndiopangitsa manyazi?
But have understood clearly what malawi 24 has written? Read again. Unless you have your own agenda
iweyo uku ganiza ngati linali bodza, kukonda chipani kapena peter
U got it wrong. They said rumours and they have posted it. Which means they have evidence. And if u read the post 4rm yesterday. They posted that anyone who post sickness of the president wil be arrested. I dont understand yo corncen here. To be sick or not doesnt matter to me. All we need to know is the truth. And as a matter of fact i have freedom of expression unlike u. And my rights have to be respected, like it or not i wil remain the same. Do u want me to comment what u want and what makes u happy? Ahah this is a free democratic country, yo views are not my views. U have a right to urgue with yo opinion not to imidate my opinion. I think at some stage i must fund a civic education so that u wil understand yo rights and how to pratice them correctly without violating other pples rights.
nde mwati ili nthawi yanji???
LOADING ……….!.
Ine phee patheba kudya Rand next month Botswana
Zikusonyeza kuti ululu wachepa lero than previouse days
Komanso tazionera tokha akugwiritsa ntchito dzanja la kumanzere zomwe sanapangepo mmbuyo monsemu, kukanika kukwera Galimoto, kukanika kuyankhula nafe nthawi yomuchingamira ndiye azisutsapo chani? Kodi matenda/kudwala ndichinthu chochititsa manyazi?
Nawe ndi kangat wakhala akuyankhula kwa anthu pa airport?
kudwala sichi2 chochitisa manyazi koma anthu amatengerapo mwayi kuchita zomwe amadziwapo akakhala kuti muthuyo amadana naye (sikuti ndikumuikila kumbuyo presidentyu ayi)
Baasi nkhani ikhala yomweyi masiku amenewa eti?
Iri ndiro bodza kodi.munthu tingamusenkhe yemweyo ndikumamuda nde chani? m’gwede gwede oseu wabwela bcoz boma likubisa ndi boma lamutenga peter ngat m’tsogoleri wachipani basi. koma zoti peter ndi tate ot adasankhidwa ndi anthu sakudziwa.ine ngati zika voti yanga ndiimodzi yomwe idachititsa kt peter akhale presdent nde ndilephele kudziwa momwe munthu yemwe ndidamuvotera alili?
kulibe amene adzakhale wabwino kwa onse
Chabwino nkhani yatha president wathu mwati sakudwala ndipo samadwala
amwene a Bannet munthu wavomera momveka bwino pa press briefing yake kuti amadwala ndipo vuto la nkono wakumanja mukunenawo wafotokoza
Nanga anthu ena akuti samadwala/sakudwala bwanji man Ashley Bakali.
Press briefn yake itii mesa anakana kma wat nyamakaz ndyomwe umamuvita nde anamupanga inject Jackson wanyamakaz ndemkonowo unapanga namu kkkkk
Kkkkkkkk nyamakazi.com mw
Peter ndchixiru kwambri ..y angovomeleza zot iyeyo amadwala??? Iyaa…it’s better angomwalira bax coz tatopa naye guluyu.. Akagwere
Chimene ndimadziwa ndichoti President amapangisa msonkhano wa atolankhani nthawi yomwe akangosika ndege ku airport ndiye izi ndiza chilendo hahahaha lol
sindimayesa ndi fb yomweyi imalengeza kumwalira kwa nkulu yu koma atolla makani enanu ndi odabwitsa zedi kumene mupita mukafunse bwino za kumwalirako chifukwa munaphatu wachikulire nthawi isanakwane
Ine sindinamuonepo peter akupangitsa msonkhano wa atolankhani pa airport. Mwna ukunena jb
anthuwa mbili akumaziipisira okha then nkumawa blamer ena
Mwina timve mau a peter lelo komatu ayakhule cicewa
Man panjatu ndi robt likumaiwala kuti ndiku Malawi kuno kkk
We are ready to lessening to you Mr President !
chilungamo chili m’ mutima mwawo apulezident, kaya amadwala kaya iyayi akudziwa wokha. kkkkkkkk?
Inu tkamat chlungamo amachdziwa yekha ndye kut, tdakali mtulo. zoona zake ndzot, amadwala KHUNYUU.
Woyamba kudwala khunyu ndiye ndi iweyo.
komano wachedwesa bwanji?mesa maulendo ena amayankhula akangofika kumene?
Ngati ayankhule fundo zoveka konse iyaaaa!! kape wamunthu ngat ameneyo
Following
Kaya poti ine sindili kumeneko nde aaaaah musovenge
Following…………
Alankhula lero tikukumva kuti ati chiyani amati akudwala mwakayakaya.Ena kumakamba zakundata tione lero Mtsogoleri waMalawi akuti chiyani
counting down….2hrs to go….
Zikachitika timvera kwa inuuu
Iwe admin kodi kuli Nyerere kuvayanji?”ndizoona kuti mawa chipwilikiti?
SIZAMWINAzo zopenekeraso….zopanda umboni….!
Welcome
Aaaaa,tiona?
Tiona.
chonde a ESCOM muyatse magetsi ife tionere nawo press briefing
Kkkkkkkkkkk inu ndye mwanena zoona ndthu,,,
hahaha mbc tv isajame bola.
aaa ngakhale atapanda kuyasama iyaaaaaaaa
Mwina alankhula?
sizamwina
Akutinji?